What was Kamuzu Banda nationality, tribe and parents?
Пікірлер: 297
@manfredjamesbrown40512 жыл бұрын
I have been following this channel for a long time now...To be honest with, i like your channel ....Anthufe takhala mu mdima kwa nthawi yayitali..... Nkhani zambiri zimene mumafotokoza ndizoona zokhazokha.. Ambiri wa akumatsutsa ndi ana ama 80s ndi 90s..Nkhani zambiri zi enafe tinkazimva pa nthawi yo mwama mememene without real facts.... Mwachitsanzo Pa History yomwe tinkaphunzila mu STD 8 yakale B4 MANEB , tinkaphunzila kuti chipani cha MCP adayambitsa ndi Kamuzu Banda...But i do remember my class History teacher (adatiuza poyela kuti MCP adayambitsa ndi Orton Chiwa ndipo ananenanso kuti in case pamayeso funso litabwera tizingoti adayambitsa ndi Kamuzu Banda....Honestly i salute you.. Nkhani yama Card ndi msonkho..Ndizoona ndipo ine ndinawona ndithu azimai amimba akudulitsidwa ma Card awiri yake ndi ya mimba yake .. Makolo athu ankachita kuthawa akangomva kuti kwabwera amsonkho...Ndipo atonga ankauzani mwachiningá mu Chitonga kuti KWAZA CHIMKWAWU CHAMBULA MAZILA ADA " monga mmene timanenela mwambi omuchenjeza mnzako kuti anthu ena asamve KUTI 'PANSI NTEDZA...Ndimmene zinalili ndithu pa nthawiyo ndipo anthu angathamanga kuthawa osati zocheza....
@fatimachidima42602 жыл бұрын
Iam with you on dis one...
@FOSTERLUPIYA-zc1xvАй бұрын
Ndinu ana ndipo simdziwa kanthu uyu ngwa bodza.Angofuna kudzitchukitsa
@richardwelliala29252 жыл бұрын
I like when you say eeeee! 😀😀😀 Keep it up. I.like your channel..watching from California USA 🇺🇸
@anniekhonje78533 жыл бұрын
Ine I left Malawi and live in Zambia koma ndima yankhula chiwewa bwino bwino,even this article am very much able kumva
@mwai723 жыл бұрын
Not the same thing...Zambia ndi Malawi they all speak a similar language.
@thomluciouss73603 ай бұрын
This is what I was heard about the real story of our kamuzu Banda thanx for updating us always
Ngati Kenneth Kaunda anali mtonga ndiekuti sanali mtonga waku Zambia ayi course Ku Zambia kulibe mto nga yemwe mfundawake ndi Kaunda ayi kumalawi konko nkomwe kuli atonga otchedwa Kaunda osati kuzambiya ayi
@g_forcemusician424211 күн бұрын
Kaunda bambo ake anali busa from nkhatabay full stop
@duncanchizizi6543 Жыл бұрын
Very informative
@user-pl1tw2gn4u5 ай бұрын
Well done Mr Bakili Muluzi tv
@enockchipinga76683 жыл бұрын
Interesting
@user-iv3do9vk3u9 ай бұрын
The truth serves us right that he was the first president of Malawi and he comes from kasungu ! Dr Banda, the son of the soil may he rest well... Anyone against that, that's your problem fotsek
@GiftBanda-jb1js10 күн бұрын
I agree with you
@hamdanmasuku4800 Жыл бұрын
Thanks for this story
@abdulrafiquekalembo4693 жыл бұрын
This is what we call investigative journalism.and if understood very well it can cover the truth.my advice to some of u is that don't ignore everything
@mwai723 жыл бұрын
Actually this is the TOTAL opposite of JOURNALISM, investigative or otherwise. This is total rubbish.
@abdulrafiquekalembo4693 жыл бұрын
@@mwai72 you just can't digest the truth.wa Youth iwe.
@mwai723 жыл бұрын
@@abdulrafiquekalembo469 hahahaha!! No..."boni fili" weni weni ine. I think when you do JOURNALISM, if this is journalism, you need more air tight solid facts to back up what you are saying....may be that just me.
@abdulrafiquekalembo4693 жыл бұрын
@@mwai72 sikukhoti,only by making comparison of things, statements,events and movements etc it can lead investigators to something and u can convict someone in court.!!!
@mwai723 жыл бұрын
@@abdulrafiquekalembo469 but courts just like journalists, deal with FACTS, right?
@nareshjatwa16433 жыл бұрын
Thanks for the good story
@danielmaluwa78963 жыл бұрын
@@thatlchiponda3368 iweyo ndie wabodza.This history is true koma vuto munaphunzira history ya mcp
@ellenrahman99593 жыл бұрын
This history is very interesting informative but, I wish you also had the English Chanel or English subtitles.
@brucewarchild21562 жыл бұрын
Ndi za a Malawi izi, chizungu chachani??
@pililani_blessings2 жыл бұрын
Yes...he shud put subtitles
@oktagonmw33403 жыл бұрын
I like your channel.....it is very informative and educational. Keep it up
@kingmanda9393 Жыл бұрын
And Kamuzu also he had his school mate like my Grandfather Mr John Rafael leza Nkhoma who left Malawi 1914 after completing higher education at Livingstone and black Manda who died in UK my grandfather was part of the family of the loya family of Sathe kasungu but Mr Nkhoma died 2000 when he was 109 year he always told that Kamuzu was light and short man they also schooled to at old Bandawe his name Ackim kamkhwala
@user-nf3ik3ff6y9 ай бұрын
Nice story
@zeckbmalawi80179 ай бұрын
We love you boss🎉
@HellenKanyemba3 күн бұрын
Kamuzu anali mmalawi I was a born free back then used to dance for him tsiku lomwe ankatsekulira kamuzu International Airport ineyo ndinaona ndikumva kamuzu akulankhura chichewa ndipo chomveka bwino kwambiri koma vuto lomwe ndimaona ndimaona ine ndilokuti kale muja athu olo omwe ankakhala ndi radio sanali athu wamba Maputo ake kumangokhala ma reported speech anthu tinkangovomereza zomwe wina wanena koma kwaamene nthawi zina amatha kukhala pafupi naye mmmm kamuzu was a true malawian
Thanks so much. Kamuzu banda analidi Ibarra kuchokera ku Ghana
@_mindview_77072 жыл бұрын
Ineyo mbiri ya kamuzu ndinaimva ndi mkulu wina wa mdziko la South Africa 🇿🇦 ndipo anandiuza chimodzimodzi kuti kamuzu sanali mmalawi,anali black American.Anachoka ku America kupita ku Ghana ngati ku exile,after atagwilira odwala mchipatala coz iyeyo anali doctor by profession.
@robertkhoza3 ай бұрын
This channel is a masterclass
@alickwilsonthom70073 жыл бұрын
Program yabwino kwambiri ndithu, ndithokoze potibwezeretsa ku Sukulu mzaka za 1993, ndiri Standard 5, koma zomvetsa chisoni kwambiri kuti m'maphunziro a tsopanowa palibe History yokhudza kwambiri za dziko lathu ndi maiko ena akunja, Ndipo funso nkumati: kodi ndi chifukkwa chiyani kunabera maphunziro atsopanowa; Oti mwana mpakana Standard 3-4 osadziwabe kulemba ndi kuwerenga?
@chifundozintambira522 жыл бұрын
Kodi bwana nkhani zabwinozi mumazitenga kuti keep it up
@StanlyMakulun19 күн бұрын
2:49
@listonnantapo16703 жыл бұрын
MChifukwachake ankangopha anthu ngati nkhumba. Amadziwa kuti ku Malawi sikunalikwawo.
@Musa1828-l5d10 сағат бұрын
Boma pa MCP kwawo ndi kupha basi
@isaacmussa29423 жыл бұрын
Ndizoona mkulu uja sadali m'malawi ndi chifukwa dziko lathuli lili losaukitsitsa foreigner presdent sangakhare ndi chidwi chotukula dziko zidakanika pa chiyambi basi ngakhale ma plan akamangidwe kuti malawi adzioneka bwino kudavuta dziko loyamba kulamulira foreigner silingatukuke
@takondwabanda19223 жыл бұрын
Munthuyi simmalawi inu osadabwa kut amakanika ngakhale kuyankhula chichewa munthuyu anali waku Ghana nde pot kutsutsa galu mkukumba kaya wakufa sayankhula😜😜😜😜😜😜
@JohnLumwira4 сағат бұрын
Aaaaaaa inuyo ndiinu Malawi kapena bulundi chili chonse Malawi muno chinapangidwa ndi kamuzu nyumba za police ma state house even miseu yonse even ship zapamadzi kamuzu pano chifelene kamuzu tanenani chomwe mwagura ngti pa madzi kapena road transport timapanga ma galimoto kuno afford inuyo munali kuti
@kcrecordsw3 жыл бұрын
My name is Stain Phiri. I was original member of Makasu Band with Bright Nkhata who was one of the real family members of Kamusu Banda who was actualy from Nkhotakota as his fathers home. This man must research properly. I was blessed when i met one very old man in Broadhurdt, Botswana who worked with Kamuzu in South Africa. That was in 1996 when I worked at Botswana Police. This man though he could not see properly, would talk of Hastings Banda, who was their leader as the distributed medicine around South Africa. Who would always say I remember this voice. Am sorry this man passed away, but research has be done in good faith that these lies. Am sorry
@Gundasonic3 жыл бұрын
Even his south african storyvis dodgy... What southafrican languages did he speak ss a black man?
@mrmustdeDj2 жыл бұрын
Kamuzu was a scambag dude..he was never a Malawian..13 years u can’t forget Chichewa..my niece 9 years old went straight to England not even a stopover in a Bantu country 22 years old now with perfect Nyasa language
@brucewarchild21562 жыл бұрын
Iwenso talemba chichewa tikumve asaaa, usatibhowe ndi kamuzu wakoyo
@arthursungitsa2708 Жыл бұрын
This is a fake and shallow narrative. If this is a research then what a joke. In the researchers wisdom, he wants to tell us that Richard Armstrong people were all dead and didn't want to do anything with their Richard. When he died none not even one claimed their son. You want to tell us that the Ashanti and Zongo people sacrificed their Richard or they were bribed by their son to keep quiet. Do you want to tell us that at the college where the so called Armstrong and Kamuzu met they were the only ones in the classroom without other students who could easily identify Richard as Richard not as Kamuzu. Kamuzu must have bribed all.the people at University of Chicago, Scotland and Meharry medical college so that none would know him.Its not easy to fake someone's identity especially at such an International platform holding the title of a President, by now we would have been seeing claims and counterclaim from friends, relatives and peers. Kamuzu was out of power for over 5 years that was the time when all the truth would have come out from those who feared him. People can reject you when you are alive not when you are dead. This is a very fake narrative. The attempt to link Glyn Jones and Kamuzu is another failure. He claims that there is a biography do your research make it available but for this one my dear friend is CHILDISH attempt
@MayesoChingoma-zq8fgКүн бұрын
Nice❤
@evertonbanda60913 жыл бұрын
This is nice story and good narration
@jamesmwakisulu89752 жыл бұрын
Keep on plz
@user-ti4yu6ob1e3 ай бұрын
KK anali mtonga from Nkhata Bay makola ace anapita ku Zambia ko cifukwa can nchito cabe😮
@chisomotaika44793 жыл бұрын
Maybe he was a secret agent. Who knows! Mama Kadzamira maybe will tell us this one day maybe yes maybe not. Malawian untold history.
@McNeverNjanji4 ай бұрын
I like your shannel
@geoffreykankhomba3 сағат бұрын
Ngati if he was a Malawian why we don't have sons and Daughters of kamuzu up to this day ana amene amabeleka ndi Aja achina Johnson anakasiyidwa kunja atabwera kuno kudzapanga claim za Bambo ake after some years anamwalira
@aubreywallo19873 жыл бұрын
Ok tamva nawo
@sulemanbhattay96182 жыл бұрын
Zikomo Kwambiri. Ine ndina badwa ku Mulanje and left Malawi chaka cha 1975. I live in England Koma mpaka lero, sindina iwala ku lankhula chinyanja. So how did Kamuzu forget speaking chichewa. Doesn't make sense. Makes me wonder whether he was really a Malawian or a Ghanaian
@shashamilookofficial195110 күн бұрын
you're a great historian 📣
@Byayerayera Жыл бұрын
Kamuzu remains a mystery even in death
@haroldmatemba32989 ай бұрын
Who is that man next to kamuzu face in that picture c
@FOSTERLUPIYA-zc1xvАй бұрын
Kamuzu was a a real Malawian but was a genius that most Malawians could not believe him to be an African . That's why this is confusing to very few Malawians like you.
@marcotchauya83423 жыл бұрын
Mutiuzenso za Bingu wa Mnthalika yemwe adadziwana ndi Bakili Muluzi atakumana mubungwe la COMESA
@lucianosamuelsergio17353 жыл бұрын
Kamuzu sanali malawi
@xinalungu96164 күн бұрын
If Kamuzu was Richsrd Armstrong WHY IS IT THAT HE USED TO SPEAK BETTER TUMBUKA than English? What I know is that even Mtambo was alleged to be a Burundi becsuse he cant speak good chewa. Kasungu is part Tumbuka n part chewa. Mphonongo, father of Kamuzu (not mentioned in Kamuzus story) was a mixed race man and son of Arab slave traders who used to manage sugar plantations at MARAVI VILLAGE in Nkhotakota. Mphonongo, before marrying naPhiri of chiwengu, Kasungu used to write from right to left, and was not a Banda. He had Swahiri Arabic blood. The name Banda was chosen as an advice warning from chiwengu to evade slave trade stories. He had his cousin called Msimuko. Msimuko went to live east of Jenda in Mzimba. Kamuzu was a SAROGATE son of a cousin of Mphongolo called MSIMUKO of Mzimba conceived around Hoho in Mzimba. Msimuko was the true father of Kamuzu coz mphonongo could not give child.
@asidialuweni5637 Жыл бұрын
That can happen and it is happening people do forget and that its happening even here in south Africa
@frankcholimbirapo2623 жыл бұрын
Koma ndie tiziwa zambir ndith even panopa ndikatenga history k xul kamba ka inu
@medsonkamala90208 ай бұрын
Nkhani iyi ndi yabodza. Kamuzu anali m'Malawi weni weni. Kodi a Malawi tidakhala bwanji? Pali nthawi ina mafumu a ku Machinga ankamukana Muluzi kuti anali wa ku Mozambique chifukwa dzina lake lokanakhala Mulusi osati Muluzi akanakhala wa ku Malawi kuno. Zikomo kwambiri kumpando. A Malawi ndife anthu osakondana ndipo abodza. Mulungu azitikhululukira.
@kingmanda9393 Жыл бұрын
The real name of Kamuzu was Ackim kamukhwala Banda his teacher Phillimon kamukhwala gogo Chirwa is the one who changed his name to Kamuzu because we're sharing the name and Kamuzu was a Malawian check The photo of Jenala Chatikha Banda ( Chatikha) means mwndida pa chitonga on the picture of the sister you will find similarities and his nephew he was residing in Soweto chawelo they looked like his nephew Nkhata
@wallacenguluwe728 Жыл бұрын
the photo next to HK Banda is that of a zambian man called dingiswayo banda
@ranalucky66283 жыл бұрын
Koma analamulirabe mkuluyu ngankhale mnene kuti sanali mmalawi
@jacomw57972 жыл бұрын
The title of this story was about who was Kamuzu Banda but i didn't get it because You didn't describe it briefly
@adamkaisi69543 жыл бұрын
Thanks a lot keep on doing such reports & research
@patricklichapa761 Жыл бұрын
I knew alot of history because of you please keep going report and research other history
@user-tw9vq6to3b8 ай бұрын
Kmatu anthu a ku kasungu makani pambiri ya kamuzu😊
@user-zp8ph8hv2b3 ай бұрын
There is a grain of truth in this conspiracy.. l stayed in Mlw during his reign... Kamuzu couldn't speak Chichewa in his rallies.. He could only say the slogan .. "Kwacha"..
@AbdulChamanyi-sf7gc7 ай бұрын
Umakwana brother
@NdhlaminieNkosi5 ай бұрын
Nde tiziti pa 14 paja ndi Richard Armstrong day😂
@najereeliya77613 жыл бұрын
Sanali mmalawi uyu
@Gundasonic3 жыл бұрын
Clearly, he wasn't
@EDSONMAKIYI-mu8ye18 күн бұрын
Sanali mmalawi
@richardwelliala29252 жыл бұрын
Tifuse nawo apa.. Mwati Kamuzu anamwalira ali ku school. Komano family inapanga kalondo londo ku school komwe anali kuti apeze zowona zeni zeni?? Story yanu nanu is confusing us.😀😀
@DOMINICSELETA2 ай бұрын
Real Malawian
@user-ve7rx7vj1g10 күн бұрын
What about sir Geofrey colby, who was also the governor of Nyasaland by the same time.
@ObedyMakhenjera8 ай бұрын
There is no sense saying something evil against a fellow Malawian like our first President the late Dr. H.Kamuzu Banda when the truth is very clear before us.
@paurosi1232 жыл бұрын
Zikomo, please can you also imvestigate the history of Richard so that this can be linked and closed
@pencilrussell47112 жыл бұрын
Something about kamuzu was not normal, imagine he had official hostess who it is very much questionable if she was not a wife. Kamuzu is very mysterious. I doubt if he was Malawian blood
@Thewarrior709310 ай бұрын
He was not a Malawian
@dausonmariha2195 Жыл бұрын
Now I know
@mariagoba24943 жыл бұрын
Munthu obwera kapolo wa Ku Ghana kamuzu
@Gundasonic3 жыл бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣@kapolo
@MasaukoPhiri-rp2oe2 ай бұрын
Mkuluyu ngwabodza
@GeraldChisokeza-er5cf3 күн бұрын
Ooh ndimkamva koma ndikasutsa
@FrightonKandodoКүн бұрын
He was not a true Malawian that's why he was brutally morderd the people of malawi
@aubs43213 жыл бұрын
Uyudi sanali m,Malawi. You can even see he was half cast
@ellenrahman99593 жыл бұрын
What is half cast, I find this ironic and derogatory. Even if one of his parents was not a black African he was still black because one of his parents was black. There is no such thing as coloured. This how the colonialists separated children born from African parents to look better than their own parents. The system of apartheid thrived on such divisions. This is my experience. Learn from the Australian Aboriginal how the pride themselves. Any woman, man and, child born from an Australian Aborigine, is an Aborigine regardless of whether his father or mother is an Anglo-Saxon.
@aleluyabanda27593 жыл бұрын
Kamuzu was an imposter
@alickrebirth-sj3ci3 ай бұрын
komaso amene anapanga realese Banda from gwero snali Ian mcloud pa 1 april 1960 osat glyn Johns zabodza zinazo
@patlamb3552 жыл бұрын
Strange
@geee7672 Жыл бұрын
Kamuzu was a true Malawian. His challenge in Chewa should not confuse people. You horn the language by consistently interacting with people. In RSA he did not live with Malawians, he lived in a Tswana household, no one has every questioned if ever he spoke Tswana, and yet we all like to question his Chewa skills. However, I agree that much of his other avatars remain a mystery. But he was a true Malawian. That Richarm Armstrong claim should be investigated with Ghana DNA rather than just rhetoric.
@mbizi4573 Жыл бұрын
That's BS. I grow up in Zimbabwe for 10 years of my life. Went to an all white school. Educated by whites. Family relocated to Canada since my mother is a white Canadian and came back in 2018 after 25 years and yet I still speak fluent Shona. That he could convince Malawians that he couldn't speak the language anymore goes on to show how gullible and stupid some of us can be
@geee7672 Жыл бұрын
@@mbizi4573 what is your point? What is BS?
@miryamkatundulu Жыл бұрын
Osamawanamiza anthu
@MaggieYassin-tv7sf11 ай бұрын
Achilungamo ndi inu Ndekuti?
@happyrandall77833 жыл бұрын
Hastings Banda was an extraordinary man who lived an extraordinary life. He was fluent in Chichewa we saw him in several occasions correcting his interpreters. Fake channel, fake news
@user-wd9yd1bg9n9 ай бұрын
Ehich occasion, the guy wasn't amalawi. The only word in chichewa he new was Kwacha
Ine ndimakaikila kuti Kamuzu anali mmalawi nzathu anali wamwano udyo no wonder minyama simatithela mmalawi muno
@andrewbanda9661 Жыл бұрын
Kenneth Kaunda was not Tonga but bemba from chinsali and parents came from malawi
@benimbewe1811 Жыл бұрын
Yes,we had leakages about this man playing a big coverup in human history when we were in school around 1986....
@peterarvaszulu50692 жыл бұрын
If the MCP committed a lot of atrocities why can't they be brought before the courts of law?it's like Malawi has not yet healed from its past political wounds. Don't you think there's need for a truth and reconciliation commission to take place now in Malawi ?
@actuarialscience22832 жыл бұрын
Izi zinakanika kalekale bwana
@mcandrewsmaunda7921 Жыл бұрын
It was not MCP; it was individuals within MCP who committed a lot of atrocities
ine ndinachoka ku Malawi ndi zaka 8 (1974) ndimakhala ku Mozambique /Maputo koma , mpaka lelo ndimakamba , ndimalemba chichewa. Kamudzu 13 years anawila chichewa?
@wanangwachunga90713 жыл бұрын
Kamuzu amalankhula chichewa ndipo alipo ma videos amene amalankhula chichewa
@wanangwachunga90713 жыл бұрын
Ndipo musiyanitse munthu okhala dziko la azungu okhaokha ndi inu amene mumatha kumakumanatso ndi a Malawi Nthawi zonse
@mwai723 жыл бұрын
Kamuzu was away for 13yrs?? Ndithu??? Try over 30yrs!!
@Gundasonic3 жыл бұрын
And howcome his accent didnt reflect the time he spent in western world? Kamuzu history dont add up
@tisuhmakhwah7085 Жыл бұрын
Ine ndinachoka ku Malawi ndili ndi zaka 9 ndpo ndakhala ku Britain kwa zaka 17 bwanj ndimayankhula ndi kulemba chinyanja?
@user-zp8ph8hv2b3 ай бұрын
This conspiracy can be true... The Life president of Malawi ..
@jesselongwe74243 жыл бұрын
Kenneth kaunda is mtonga from nkhata bay, his father went to Zambia by missionaries , Kenneth anapita ku Zambia ali kanyamata ndi makolo akewo moti even family yachina Kenneth kaunda ilipobe ku nkhata bay .
@jesselongwe74243 жыл бұрын
Manowah chirwa was mtonga from nkhata bay not mtumbuka
@nellietchuwa99133 жыл бұрын
Why dobu mean by saying "keneth Kaunda anali mtonga"? U mean now he is not tonga or he passed away 😂
@simbiphiri14253 жыл бұрын
Kaunda is not a Zambia Tonga but Malawian Tonga, the two Tongas from these countries are not the same , research better.
@isaacbanda29733 жыл бұрын
Which is which?
@isaacbanda29733 жыл бұрын
Mwana wa zaka 13 sanhayende ulendo wa pasi mpaka ku South Africa
@eunicemoyo58083 жыл бұрын
yaa zambia malawi paja kale akut adali dziko limodzi ndye ndizosadabwisa kaunda kupezeka ku zambia or malawi
@yamikanimwenda18003 жыл бұрын
Am a fully Zambian what I know is that Kaunda was a Malawian
The real kamuzu was killied and the one who came to Malawi was fake kamuzu no wonder munthu kungopita ku school ku Amerika osatha chichewa ? Bingu anapita kale kale ku school ku america koma atabwera amalankhula chichewa that's why anthu anthawi imeneyo amafuna kuti abvule nsapatao koma anakana chifukwa kamuzu wathu anali odula Chala Cha mmendo
@virginiashumba25742 күн бұрын
Grandfather was one of the people Who went to Gwelo but never spoke what you are telling the world. The story is a half lie. Consult more and more from the people who can shade more right.