ZAULULIKA ZA IMFA YA CHILIMA-KOMA ANTHU AMALIMBA MTIMA

  Рет қаралды 17,373

MPUNGWE-PUNGWE MW

MPUNGWE-PUNGWE MW

Күн бұрын

Пікірлер: 51
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u Күн бұрын
Ife tidadziwa kale ndipo pastor mulibe mulandu kumwamba chifukwa dzikoli likukana chilungamo. 💪💪💪🇲🇼💯✅
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 20 сағат бұрын
Mau amphamvu abusa ine ndigoti Amen anayiwala kuti ku Mwambaku kuli mfumu ya ma mfumu amene sagona or kuwozela chilungamo ich ndipo chayenda ngati madzi sure. God bless you
@HawaHussein-d4l
@HawaHussein-d4l Күн бұрын
Ameen zoona zake reality my comrade ambuye azikusamalani ambuye atiyankhe
@DavieMaloya
@DavieMaloya 15 сағат бұрын
Dzoonad pastor mau a phamvu
@HamzahTwaib
@HamzahTwaib Күн бұрын
Paster mwalalika zoonad apapo munthuyud anapha chilima mmmm 😭😭😭😭
@supa4dupa
@supa4dupa Күн бұрын
Mulungu athandize a Malawi,Zikomo🙏🏾
@RACHEALKanyenda-b8f
@RACHEALKanyenda-b8f 17 сағат бұрын
Ambuye zonse tikuzisiya manja ...muweluze ndinu Yahweh
@InnocentMkhoma
@InnocentMkhoma Күн бұрын
Amene anamuika Chakwera ndi mademonstration amuchose okha osalimbana ndi a opposition omwewo amuchose basi Zazii iiii zimenezo abusa.
@RosePhiri-n8q
@RosePhiri-n8q 15 сағат бұрын
Manthadi siabwino mulungu athandize mau amphamvu abusa
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 22 сағат бұрын
chakwera ngati akapumumuka kumwamba ndiye kuti aliyense akapulumuka chakwera ndi tsatana
@ehinsupport3217
@ehinsupport3217 17 сағат бұрын
Pastor wotani fiti yachabe chabe pa ujeni pakopo ,galu iwe wabodza. Ndipo usamanamudze anthu mbuzi iwe
@georgeaiwa8661
@georgeaiwa8661 23 сағат бұрын
Inu zimene mukukamba ndizenizeni ndipo ndi ndendende Wopha anthu kenako iyeyo nkukhadzikisa Commission of Inquiry, zili ndi mutu zimenezo? Amene akupangitsa manyazi kwambiri ndi abusa anga a SEVENTH DAY ADVENTIST a TY Nyirenda. Iwo awonetsa kutsatira NDALE ndi DYERA. Awanso ayenera kutula pansi kapena kuchotsedwa pa Udindo wa SDA Zikomo a Pastor Emmanuel
@PaulineKamwana
@PaulineKamwana 16 сағат бұрын
Kkkk pastor ng'alulaisation period,inutu akutapani ,kkkkk okumva wamva nanga tisowanso umboni wanji? RIP SKC😭
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Күн бұрын
Zoonadi comrade zimenezo ndi zimene timadziwa agalu oyipa awa.
@EnockMvula
@EnockMvula Күн бұрын
Mkunena zowona anamphadi chirima ndi chakwera apusisa ndani tikuziwa kuti anampha ndiyedi ndipo nayoso afa ameneyo awona murungu simunthu ndimunthu wankhaza iyundi munthu woyipa satana murungu akuwonadi sizaboza ndipo chirichose chimene akupanga ndipo kumpha chifukwa chandare mzanu ndipo akurangeni
@WestonGawaza
@WestonGawaza Күн бұрын
Kulankhula street zowona zake amalawi kuzungulira kulakhula malamulo akuti bwanji wa kupha wa kuba waboza ndende zachisoni akumangidwa wakunena chulungamo
@SifatiMoses
@SifatiMoses Күн бұрын
Olo kumuombera modzi mwa anthu omwe anatenga gawo pa infa ya chilima ndi anthu ena aja.
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Күн бұрын
Ndipo live anapha ndi Chakwera bas mcp yakupha nthawi zose
@verinachiponde6922
@verinachiponde6922 Күн бұрын
Zoona izi chifukwa chiani a kamajekete amamanga anthu akangokamba nkhani ya ndege?
@JonhKapatjika
@JonhKapatjika Күн бұрын
Boma latengedwa ndi asatanic
@NewtonTembo-q4t
@NewtonTembo-q4t 15 сағат бұрын
Zoona zake
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya Күн бұрын
Wakumva wamva....kuyankhula nde kwayankhuridwa
@GolosiMalapata
@GolosiMalapata Күн бұрын
Auzeni kuti avetse anthuwatu kuwopa kuti anene ntchilungamo. Boma lopanda nzelu
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u Күн бұрын
More 🔥 fire 🔥🔥 kuti lapu lapu
@StaffordNgalande
@StaffordNgalande 23 сағат бұрын
abwana mukunena zoona
@FransincoChirwa
@FransincoChirwa Күн бұрын
kulankhula mwachilungamo komanso mosaopa komanso chenicheni chomwe chinachitika sakufuna kuvomereza
@AndileyaMkandawire-x8r
@AndileyaMkandawire-x8r Күн бұрын
Khani ndiyomweyo kungomuchosa bas kom amalawi eeeee kaya akuopachani pa uyu mutalika anali ize kumuchosa kom uyu akuti bom ndilomweli kaya achina bon kalindo ama pangisa mademo pa mutalika apa akuti mademo ndi pakamwa malawi
@Laurent-h9u
@Laurent-h9u 19 сағат бұрын
😢😢😢😢😢continue resting in peace skc
@WatsonMsukwa-y5i
@WatsonMsukwa-y5i 7 сағат бұрын
Amen
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c Күн бұрын
Nkhaniyi ndi yastraight
@meeksonmkhala
@meeksonmkhala Күн бұрын
Chilungamo chankhani ichi. More fire man of God
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 20 сағат бұрын
Eeeesh
@pilirani3536
@pilirani3536 Күн бұрын
Amen amen
@SuleimanRabsonMkhunga
@SuleimanRabsonMkhunga Күн бұрын
Nfundo imeneyi omunyasa ndi wa MCP yekha osati anthu ena
@abieahabieh2999
@abieahabieh2999 Күн бұрын
Komadi ife amalawi tinaseteledwa zoona timangokhala phee olo tione kut zinthu sizikuyenda bwino.
@ClementMunyolowa
@ClementMunyolowa Күн бұрын
Unachezapo ndi Shumba pano ali pa low
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya Күн бұрын
Chilungamo chimakhazikitsidwa chete mkumene....bodza ndilimene limatenga mphamvu
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug Күн бұрын
Ndipo panali video yoyambilira anthu akumizi kuchikangawa anatumiza kut kwagwa ndege apoo video yinawoneka kaya yinathera kut video yimene yija sikuyiwonaso ayi
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 22 сағат бұрын
Anayi Isa ndipo munthu amene uja anatsekedwa pakamwa mmmm💔💔
@anniegundaphiri423
@anniegundaphiri423 Күн бұрын
Chakwera pamtumbo pako
@captainmdima1102
@captainmdima1102 Күн бұрын
Aaaa iwe c ndiwe pastor wa propaganda iwe watumidwa uli ndi vuto!
@MzadziWanga
@MzadziWanga Күн бұрын
Ngt mmeneso anatumidwira chakwera kt aononge Malawi 😅
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u Күн бұрын
Iweyo ndi amene watumidwa ndi chikangawa And funk you
@RuthTimothyChirwa
@RuthTimothyChirwa 19 сағат бұрын
😂😂😂😂❤
@MosesChazima
@MosesChazima Күн бұрын
Zowon zimenezo
@VeraVermaak
@VeraVermaak Күн бұрын
Iwe mbunzi yeni yen
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx Күн бұрын
Iweso ndi galu ukuikila kumbuyo zimenezozo
@EnockMvula
@EnockMvula Күн бұрын
iweyo naweso ndi Garu opusa iwe ifeyo tikuziwa Kuti chakwera anampha chirima chimwendo wose ndizigawenga Koma Muri ndisoka ndi ziko iri murungu azakukathani ndipo munapha chirima ndinuyo anthu wopusa agaru makape inu kupusa
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo Күн бұрын
Iwe ND galu kwabas
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u Күн бұрын
Mbuzi ndi imenetu ili ku state house, dziko lopanda president, nanga munthu akatchuke ndi dzina la chikangawa nde zili pabwino??? Ulibe manyazi mwana wa hule galu😢
Wait for the last one 🤣🤣 #shorts #minecraft
00:28
Cosmo Guy
Рет қаралды 25 МЛН
I tricked MrBeast into giving me his channel
00:58
Jesser
Рет қаралды 28 МЛН
CAN YOU DO THIS ?
00:23
STORROR
Рет қаралды 48 МЛН
PIZZA or CHICKEN // Left or Right Challenge
00:18
Hungry FAM
Рет қаралды 8 МЛН
NKHANI ZA LERO_ NORMAN CHISALE__6 November 2024
20:47
HOT 265
Рет қаралды 11 М.
Nyimbo yomwe yavuta kwambiri yochemerera APM Chipani Cha DPP  akuti Muzavotere Mutharika.
4:10
Imfa yolilitsa kwambiri ya Dr Saulos Chilima 😭😭😭
8:13
Honourable SC TV
Рет қаралды 11 М.
KUMASUKILANA M'BANJA ON MZATI TV
59:36
Mzati Radio&TV
Рет қаралды 19 М.
Michael Usi - Wayankha zodabwisa atafunsidwa za Saulos Chilima
10:03
Malawi Top Talent
Рет қаралды 4,9 М.
Wait for the last one 🤣🤣 #shorts #minecraft
00:28
Cosmo Guy
Рет қаралды 25 МЛН