ZILIPATI PA MIJ FM NKHANI YA A EVANS MUMBE OMWE ANAPANGA MISALA ATALAKWITSA ZIZIMBA PART 1

  Рет қаралды 62,402

MALAWI 265

MALAWI 265

Күн бұрын

Пікірлер: 111
@WilsonMohammed-i6v
@WilsonMohammed-i6v Ай бұрын
Wow i saw za nkhuku mu film, inayake and also za nsapatozo iiih nollywood osadzaitola
@ChristianMaganga-y5d
@ChristianMaganga-y5d 6 күн бұрын
Tiyeni tiope mulungu akwezendi nthawi zose ❤❤❤😊
@ArnoldChimtengo-c9z
@ArnoldChimtengo-c9z 2 ай бұрын
Ndye munthu wasankha Kupeleka msembe km kukanika kuphaso msembeyo kkkk
@godfreymanyungwa7019
@godfreymanyungwa7019 Ай бұрын
Uyu ndi evans lumbe osati mumbe ndiwa mmudzi mwanga uyu 😅😅😅
@GetrudeMazingaDon
@GetrudeMazingaDon 2 ай бұрын
Eshh neba wakumudzu kwathu iwe mmmmm
@SérgioFernandoKangombe
@SérgioFernandoKangombe Ай бұрын
Nde zopusatu anthu mukumufusa dzina NDE bwanji kungokhala osamufusai
@YusufMoyo
@YusufMoyo 2 ай бұрын
Tiyeni tizinkhutisidwa ndizomwe mulungu amatipasa
@EsetaGerate
@EsetaGerate 2 ай бұрын
😂😂😂😂 munthu unari ndalama kare chofunira kunkhwima nchani
@SirpromiseMatabwa-q2e
@SirpromiseMatabwa-q2e 2 ай бұрын
Bola yogona ndimkazi wako eyayoyotu than others
@TywongyMunthali-y4s
@TywongyMunthali-y4s Ай бұрын
Eti inu,,,koma ayi osafuna kusiya uhule
@phillippk983
@phillippk983 2 ай бұрын
Evance Lumbe like am dreaming eishiiiii
@DoricaGoweka
@DoricaGoweka 3 ай бұрын
Zilikotuuu pa MW pano 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 3 ай бұрын
Tizivomeleza zomwe Mulungu watipatsa basi,,,,,ndithudi Mulungu salakwitsayi zotipatsa Mulungu ndiye zabwino za original satana ndiwonyenga
@LindaKapito
@LindaKapito Ай бұрын
Koma gys Tiyeni Pena tizikwanitsidwa nd kochepa komwe kakupezeka
@MaxwellChaminju
@MaxwellChaminju Ай бұрын
Kunjakuno kuchitika zinthu eti😂😂😂
@Felix-i7b1j
@Felix-i7b1j 24 күн бұрын
Chomwe ndimadananacho ine chomabitsa maina omwe akukhudzidwa ndinkhani zanuzi
@ulemuchisale
@ulemuchisale 2 ай бұрын
Following
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 2 ай бұрын
Eish koma zoopyatu
@MariamJaffali
@MariamJaffali 3 ай бұрын
Following mwachidwi
@WilsonMohammed-i6v
@WilsonMohammed-i6v Ай бұрын
Nollywood ilipodi😂
@alicegama8138
@alicegama8138 2 ай бұрын
Bola inu mumafuna kukhwimila mwana wanu ife anakhwimila mwana wathu anthu ndioyipa
@zephinatkavala9920
@zephinatkavala9920 2 ай бұрын
Bilitsi ndiye njoka yanji nanga??😅😅😅
@EnertNkhwazi-tf9iu
@EnertNkhwazi-tf9iu 2 ай бұрын
Kumalawi kokoma bola kungokhala ndi data basi
@MatatizhoAlan
@MatatizhoAlan Ай бұрын
Bola yosavala sapatoyotu kkkkk😂😂😂
@Itz_telloztreker
@Itz_telloztreker 3 ай бұрын
Munthu opengadi kwambiri kusankha Kupha mwana instead of yosagonana nd akaz Ena.... fotseki .... akanangoferatu bac
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 2 ай бұрын
Ndekuti ndahule amagona ndazimai ambilimbili ndinkona sanasankhe njila imeneyo
@chisonimponda363
@chisonimponda363 2 ай бұрын
Ndipodi nane wandinyasa
@EvanceBonjesi-n2z
@EvanceBonjesi-n2z 2 ай бұрын
Tigaikeni namba timvane mutipase map tipiteko
@BatchEvance
@BatchEvance 13 күн бұрын
Mulungu akwezeke ndinthj
@YusufAnafi-f9w
@YusufAnafi-f9w Ай бұрын
Tiyen tiziphuzira kumvomereza ndi chimene mulungu watidalitsa nacho
@MayamikoJeke-d5m
@MayamikoJeke-d5m Ай бұрын
Mwatikumbutsa ku Sayama Factory ndi Mathambi Market
@ThomasChiwaya-qx9mf
@ThomasChiwaya-qx9mf 3 ай бұрын
Ndalama sizimakwana man kuluyu zinangovuta bas
@christopherlowole8665
@christopherlowole8665 2 ай бұрын
Next part
@MALAWI265-x1k
@MALAWI265-x1k 2 ай бұрын
Next sunday
@ZainabKin
@ZainabKin Ай бұрын
Mmmmm ay kumaopako mulungu
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 2 ай бұрын
Oh things are happening 😢😢
@MartinNgoma-tp2jk
@MartinNgoma-tp2jk 2 ай бұрын
Tipaseni nambalayo tikaone
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 3 ай бұрын
Koma ya kulisindu 😂😂😂😂
@Kelvin-hj5qv
@Kelvin-hj5qv 3 ай бұрын
Khani Zina ukamava kamba mwala 😂😂
@Kelvin-hj5qv
@Kelvin-hj5qv 3 ай бұрын
Next please 🙏🥺🥺
@nonontsane2521
@nonontsane2521 2 ай бұрын
Part 2 chonde
@PatrickBeula
@PatrickBeula 2 ай бұрын
Next pls
@FelixBoss-yn9pe
@FelixBoss-yn9pe 2 ай бұрын
Ndeno uwona nyekhwe ase owooo khala pheee
@joycefatch
@joycefatch 2 ай бұрын
Kusakhutisidwa
@robenmatchilinga604
@robenmatchilinga604 3 ай бұрын
Next
@MALAWI265-x1k
@MALAWI265-x1k 2 ай бұрын
Next sunday
@LuciusLungu
@LuciusLungu 2 ай бұрын
Kkkkkkk mwalemela tuu
@CarolineMoyo-l4f
@CarolineMoyo-l4f 14 күн бұрын
Umphawi sumapha magaye tiyeni tiope Mulungu
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 2 ай бұрын
Part two please
@MALAWI265-x1k
@MALAWI265-x1k 2 ай бұрын
Next sunday
@chisonimponda363
@chisonimponda363 2 ай бұрын
Ndiye alibe umunthu,kusankha kupha mwana wake than kugonana ndi akazi eni,uchitsiru..... ndi uhule. Kuvomeleza za uhule unlike loving his family
@charleschij524
@charleschij524 2 ай бұрын
Eti eti zachibwanatu
@DavidMalewa
@DavidMalewa 2 ай бұрын
Kkkkkkkkkkkk abwana chisankho sichikhala chako ndiziwanda zomwe zimakupatsa mayankho ndzasatana basi kufuna kukukhaulitsa
@DavidMalewa
@DavidMalewa 2 ай бұрын
Don't play with devil ngati adaiyamba nkhondo ndi Mulungu kumwambako ndiye ife ndindani be extra careful guyz tidzafa ngati chitsiru .
@BigoppotunitiesfinanceAcadamy
@BigoppotunitiesfinanceAcadamy 13 күн бұрын
Mbambande
@EusébioLucianoGaiondo
@EusébioLucianoGaiondo 2 ай бұрын
Eeish
@veronicamalisero2671
@veronicamalisero2671 2 ай бұрын
part two ibwela liti,,,,,hhhhhhhhmmm munasemphana ndi chumatu amkolo.inu osasankha yogona n akazanuyo bwanji mukafuna muzidya n mahule chomacho shaaaaaaa
@chisonimponda363
@chisonimponda363 2 ай бұрын
Eti eti... poti chiganizo chabwino ndi choti ndizigonana ndi akazi anga okha unlike kupha mwana wako aaa uchitsiru uhule
@LucyMachine
@LucyMachine 2 ай бұрын
Next part 2
@TadaDuncan
@TadaDuncan 2 ай бұрын
Mmmmmm km kwana indu
@RahmanSagawa
@RahmanSagawa 2 ай бұрын
Aise kod unapita kut mwina nafe tilowele komweko
@HamphuryMkwanda
@HamphuryMkwanda 2 ай бұрын
Koma nde anakumana nazotu
@mercyc-z2c
@mercyc-z2c 2 ай бұрын
Timadabwa kulimbika koma osabooleza
@tisunganechilale3653
@tisunganechilale3653 Ай бұрын
😂😂😂😂
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb 2 ай бұрын
Tidikila
@christophermsowoya741
@christophermsowoya741 2 ай бұрын
Mmangoika part 1 nkhani zambili part 2 simuika
@MALAWI265-x1k
@MALAWI265-x1k 2 ай бұрын
Pa Channel chino thawi zambir sitimakusiyani malele timayetsa kuti zomwe taziyamba tizimalize
@PETROLJ-n1t
@PETROLJ-n1t 3 ай бұрын
Njinga zamoto ziwiri koma osamakukwanirani 😢😢
@chisonimponda363
@chisonimponda363 2 ай бұрын
Ndipo eti eti
@giftlisimba6628
@giftlisimba6628 2 ай бұрын
Ikani part 2
@MALAWI265-x1k
@MALAWI265-x1k 2 ай бұрын
Next sunday
@PaulNkhata-c3b
@PaulNkhata-c3b 2 ай бұрын
Kumeneko kukufunika ife anthu okhwima nzeru
@TrevorBanda-g4r
@TrevorBanda-g4r 2 ай бұрын
Yehova sachedwa safulumira
@SharifuDayiman
@SharifuDayiman 3 ай бұрын
شرق
@tisunganechilale3653
@tisunganechilale3653 Ай бұрын
Zovuta
@ajaboytheketvchannel1103
@ajaboytheketvchannel1103 2 ай бұрын
Tchuma😅
@JosephMakaika-u8s
@JosephMakaika-u8s 2 ай бұрын
Iwe mulungu akukukhulikirè ukuti mwachisomo izizi ndi chisomo zikugwirizana bwanji 😢😢😢
@AnnieNseu
@AnnieNseu Ай бұрын
Njinga zamoto ziwiri ndi kukhala pantchito.... zimenezozo nzochepa?😢
@WilsonMohammed-i6v
@WilsonMohammed-i6v Ай бұрын
Et et ichichi 😂 nchoganiza mopusa
@AnnieNseu
@AnnieNseu Ай бұрын
@WilsonMohammed-i6v aaaa asatibalalitse anzake we are surviving without njinga zamoto ka salary nso kochepa aaaa
@EdnahKachalie
@EdnahKachalie Күн бұрын
Eeee bola ndkhale mphawi🙌
@ZoomschiramboChirambo
@ZoomschiramboChirambo 2 ай бұрын
Truth is still missing u better stop
@TadalaKa
@TadalaKa 2 ай бұрын
Kusakhutisidwa ndi chimene mulungu wakupasa
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 2 ай бұрын
Anadziwa bwanji kuti wapenga misala?nfiwabodza uyu
@ApostoloLucas
@ApostoloLucas 2 ай бұрын
Amakuyuza ndi anthu ukachira❤
@ShegSamosa
@ShegSamosa 2 ай бұрын
🥺🥺🙌🙌
@ChifundoEleson-i7d
@ChifundoEleson-i7d Ай бұрын
Chachikululu ndi kuopa mulungu basi
@ChimwemweMuhelliwah
@ChimwemweMuhelliwah 3 ай бұрын
Njema ndi TA ...tanenani dzina la mfumu yaying'ono...
@GetrudeMazingaDon
@GetrudeMazingaDon 2 ай бұрын
Yaing'ono ndi njema ,kwa TA njema ndi kwinanso
@vittazomba
@vittazomba 2 ай бұрын
Kukiso mfumu yotchedwa njema tikalowa nseu opita ku mission
@EdwardGeorgeKasabola
@EdwardGeorgeKasabola 2 ай бұрын
Nkhani zovuta
@GetrudMagwira
@GetrudMagwira 2 ай бұрын
Koma zikilko padziko lapansi
@GilbertAlufeyoh
@GilbertAlufeyoh 2 ай бұрын
Ma soba man kuganiza moopepera
@FelixNthungululu
@FelixNthungululu 2 ай бұрын
Poo poor
@HannaMkhalipi
@HannaMkhalipi 3 ай бұрын
Ndipase number yako iwe
@louisbonongwe8537
@louisbonongwe8537 2 ай бұрын
Kkkkkkkk bwinotu braz
@HannaMkhalipi
@HannaMkhalipi 2 ай бұрын
@@louisbonongwe8537 ndikuona sing,Anga ameneyo angathe zimene ndikufuna osatiso zokhwima kufuma ndalamazi ayi
@ZakeyoPhiri-s6n
@ZakeyoPhiri-s6n 2 ай бұрын
Number pls tikaziwonele tokha
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 2 ай бұрын
Kkkkkkkk
@tisunganechilale3653
@tisunganechilale3653 Ай бұрын
😂
@egreymkumba-tj5ji
@egreymkumba-tj5ji 9 күн бұрын
Kkkkkkkkkk
@sahilujameswadison-r9i
@sahilujameswadison-r9i 2 ай бұрын
Next
@MALAWI265-x1k
@MALAWI265-x1k 2 ай бұрын
Next sunday
@patrickzembani4315
@patrickzembani4315 2 ай бұрын
Next
@chriszamanja1555
@chriszamanja1555 2 ай бұрын
Next
@Trynes-p9q
@Trynes-p9q Ай бұрын
Next
小丑女COCO的审判。#天使 #小丑 #超人不会飞
00:53
超人不会飞
Рет қаралды 16 МЛН
UFC 310 : Рахмонов VS Мачадо Гэрри
05:00
Setanta Sports UFC
Рет қаралды 1,2 МЛН
小丑教训坏蛋 #小丑 #天使 #shorts
00:49
好人小丑
Рет қаралды 54 МЛН
Waarom wilden de Russen de tsaar weg hebben?  | ANDERE TIJDEN
21:32
Andere Tijden
Рет қаралды 293 М.
‘Sisobola kulwanira mulambo gwa Ssegirinya’- Owek. Mpuuga
6:27
BBS TEREFAYINA
Рет қаралды 7 М.
The Last Fishing Boat - a film by Shemu Joyah
1:49:51
C. Shemu Joyah
Рет қаралды 292 М.
Chakwera akufunika ku mental hospital akamuyeze ubongo
14:21
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 80 М.
Ogulitsa Ziwalo Xa Anthu  Agwida Ku Thyolo.
1:27:49
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 247 М.
Bakili Muluzi ndi munthu oopsa, wakuba  komanso wakupha.
9:28
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 82 М.
小丑女COCO的审判。#天使 #小丑 #超人不会飞
00:53
超人不会飞
Рет қаралды 16 МЛН