Ndipo mayi uyu wakana ndalama uyu ndi wa mzeru kwambili ndipo God bless that mama ❤❤ wothandiza sayenda ndi camera 📷
@josephmsyali8 күн бұрын
Mmmmm inu do you think God can come to you in person
@KennedyPhiri-h9h8 күн бұрын
Zako izo koma zomwe wapanga mayi uyu ndi zofunikila kwambili because helper don't take photos that is not helping but lough on you
@JoyceLiwonde7 күн бұрын
'ndipo 😂😂
@JohnNakoma7 күн бұрын
Ndipo live
@Spycekiddymw7 күн бұрын
Live pat
@dajmussa2331Күн бұрын
Bas zimachitika ena kufuna ndalana ena kuzikana no problem aliyense ali ndi ma principles ake ena safuna chidule ena amafuna kuthandizidwa after kuvutika for so long. Osalodzana dzala ❤❤
Nde akanagula tomato akanatani naye. Tomato ali naye kale mu Ekhaya.
@TadalaTembo8 күн бұрын
Eya ndizona@@msatisi.reangfordphiri
@JoyceLiwonde7 күн бұрын
Chilipo chomwe anaona maiwo pekana ndalama 😮😅
@anastasiamanjolo5 күн бұрын
Keep doing good madam Mpinganjira,,women needs support,and it's very rear for a woman to support a woman
@christinachikadza37605 күн бұрын
Nzimayi wanzeru anakana ndalama zakumidima. May God will bless your business. Osamakonda zaulere amalawi musakudziwa komwe zikuchokera. Bola kumadya thelere uli pa ufulu😂😂😂
@ZahirMatiya4 күн бұрын
Ameen
@TriciaMacloud-zv4kf5 күн бұрын
Wow this woman is a genius, I wish mwayi umenewu unakandipeza mum Mpinganjira that will help me to boost my business
@IreenFaiti10 күн бұрын
Mai akutha diza awa. God bless her works and her charities 🙏🙏
@PhillipKatundu-f7x10 күн бұрын
Don't take chances for poor people..... to me she did a good job n she teach them a good reason and I appreciate
@favourmvula64359 күн бұрын
God bless and protect the poor lady ❤
@FridahShawa-h8z8 күн бұрын
That's true
@josephmsyali8 күн бұрын
God will never come to you in person Mwaiona anabwerera kumagunabe ndalamazo let's change our mindset please za camerazo mulungu ndiye akudziwa
@ShabaniKuswere8 күн бұрын
Uli ndi umboni kuti anabwerera kuti akalandire? Mai mpinganjirawo analankhula chifukwa Cha manyazi chabe@@josephmsyali
@JamesSuman-if2xo9 күн бұрын
Kuthandizako she is doing so good. But next time drop the cameras at home.
Anthu olemerawa akuopsa masiku ano. Palibe ndalama yo dza mwaulere. Big up mama kunsika wa mbulumbuzi
@TriciaMalikebu6 күн бұрын
Why have cameras when carrying out charity work? I applaud the lady who refused the money. The Lord will bless her in a different way🙏🏽
@AbdulrazaqHussain11 күн бұрын
She did good, why camera and whole social media when doing good charity?she is doing it for fame, too bad
@LouisShaffie-sp2xu11 күн бұрын
I don't see no problem coming with cameras and the whole social media team man, that's an initiative that needs records, she need to report to her boss ain't nothing to do with fame, patha kuzafunika ma audits nthawi ina yake remember its an initiative she can't handle it on a personal level, a team is needed man, stop badmind, komanso ma camerawo ndofunika cuz enaso akaona pa social media kuti someone is doing this kinda good job nao atha kupangidwa motivated nkuyilowaso nawo kukathandiza wina wake pena pake, zinthuzi zimachitika kwambiriso ku maiko aanzanthu koma sitimayankhula koma poti wapanga ndi mmalawi eeeeee😅 anyway I ain't got no prob with the woman who rejected the offer, I ain't got no problem with Triephornia, I ain't got no prob with you either, the problem I have right now is that am out of weed😢
Mukafuna kuthandidza km cameraman popo dzoputsa bas akutameni athu Kama dziwani tinadzipedza ndipo tidzadzitsiya bas
@Jimmy-e6r9x11 күн бұрын
@@LouisShaffie-sp2xu The whole of this essay pa social media ngati pano and a mere comment for that matter who has got time to read the whole of this?
@LouisShaffie-sp2xu11 күн бұрын
@Jimmy-e6r9x If you ain't got nuh time don't bother reading lad, go look for money. Happy new year. Am still out of weed tho🤦🏽♂️
@BsBGidalah11 күн бұрын
Ndalama zobwela chonch pena zimaopsa kumene ine ndkuwavesesq😂😂
@JoyceLiwonde7 күн бұрын
Kwambili 😂😂😂
@GiftMatiki-cb1tq4 күн бұрын
Cz sisunga kape
@TrizaGeorge-q8w11 күн бұрын
Musiyeni m, zimai abale wanena yekha kuti zomwe Ali nazo zimamukeanila abale athu enatu amadziwa mayu amulungu kukana suchifukwa
@tinkaphethi139510 күн бұрын
We are witnessing politicians dishing out Malawi Kwacha 2000 notes and their bootlickers are busy enlarging such as works of generosity. The Mpinganjira family are what they are taught by their religious leaders. Ambuye akudalitseni Mayi Mpinganjira...you have walked the talk...and not talked the walk!
@MikeNkhoma-w7u11 күн бұрын
Mai ujatu wakana ndalama zija ndi komwe zachikako,sizinachoke thumba loyenera,kumaganiza
@ProspelinaBanda-z2e2 күн бұрын
Kinena zoon mayiwa anakanila ndalamay osati ndintima onse. End panopo amaziweluza ekha
@JoyceLiwonde7 күн бұрын
Mai wazelu kwambili Wachita bwino kukana🎉😂😂
@VincentManganda-cr3sm11 күн бұрын
Yes is true you cant give someone on front of cameras thats risks people are watching
@VictorMakono-n2h10 күн бұрын
She did well,to the beginning of the year receiving money for free charge mmmm that's questionable.
@JoyceLiwonde7 күн бұрын
😂😈
@JoyceLiwonde7 күн бұрын
Ai sitiwadziwa ndi kanyama kanji mpinganjira😂😂😂
@FarhaazbashaMdoka10 күн бұрын
Life is not easy sikadza kokha kaopa kulaula. Ndalama zimenezo ndisabwino or pang'ono
Koma ku ikwitorio sana kumaneko ndi batasa awa😂😂😂😂😂😂😂
@VeronicaSekobi-is6dk5 күн бұрын
❤🎉
@nonontsane25215 күн бұрын
Next part
@MEMORYWillison5 күн бұрын
Owoo😢😢😢😢
@JafaliPeter-m4s7 күн бұрын
It's part of life kukana koma eeee mwai wina ukat ukufikire kkkkk
@DavieOsman-tv7np11 күн бұрын
Ntima wa zongopasidwa mmaiyu alibe🎉
@berthachithumba85937 күн бұрын
Zachifundo amati dzanja lamanzere lisadziwe. I like the woman rejected to receive unknown money
@JoyceLiwonde7 күн бұрын
Amen
@AnthonyMalingana-ie2ue10 күн бұрын
Komano mayi uja chifukwa chimene adakanira akuchidziwa ekha. Tisamaweruze ena please. Tivomereze kut tili mu Nthawi ya Ma Camera. Tikanakhala mu 90s kunalibe kujambula chifukwa ma camera kunalibe. Technology is advanced.
@MEMORYWillison5 күн бұрын
Koma guys
@ABIGAILMpezeni9 күн бұрын
Pantudzu panu mayi chokanila ndalama chani???
@CosmasChikwindi10 күн бұрын
Kodi mai mpinganjila azibale awo onse anawapasapo ndalama?
@gracekazonga34464 күн бұрын
Point of correction she stays in Blantyre nyambadwe puliz
@KachingweGolden-n3k4 күн бұрын
Othandiza samatenga camera ndikumajambula
@LysterNjeulira-kr9cq5 күн бұрын
Ukafuna kuthandiza sitimaonetsela ku gulu!!!!
@TadalaTadz-e7v11 күн бұрын
Ndimayi wabwino .. aliyense ali ndi ufulu okana kapena kulandila .
@ZahirMatiya4 күн бұрын
Chidodo ayi pls
@tinkaphethi139510 күн бұрын
We have many rich people in Malawi but are stingy and greed...Bravo Madam Mpinganjira for being generous! There is a blessing, if not blessings that await you: Luke 6:38 (KJV) Give, and it shall be given unto you; good measure, pressed down, and shaken together, and running over, shall men give into your bosom. For with the same measure that ye mete withal it shall be measured to you again.
@josephmsyali8 күн бұрын
You are right
@tiongepriscillaSanyila10 күн бұрын
Nkhani izitha aaaaa,mayi uja zomwe ali nazo zimamukwana
@MableMachemba10 күн бұрын
Koma inu ananena mombeka bwino kuti zake zomwe amapeza zimamukwaniraa nde kaya nkhaniyi sikutha bwanji?ngati kuti iyeyo ndiwoyamba kukaniridwa ndalama aaaaaaaaaaa Malawi nkhani simawatheratu awaaaa
@tinkaphethi139511 күн бұрын
Anakati sapereka bwezi akuti ndiwowumira oro ali olemera...amayiwo kukana ndi ufulu wawo ndipo ndi pempho langa kuti Mayi Mpinganjira apitirize kuthandiza ovutika chifukwa alipo ambiri..
@AmosMacnight7 күн бұрын
Ukunama triphonia amakhara nyambadwe
@jeanmlombwa7 күн бұрын
Mmmm ku area 43
@IshmaelKasambara5 күн бұрын
Andigaileko ine ndikuzifuna ndalamazo umphawi ukundipweteka kuno
@manuelnamapita628110 күн бұрын
Samalani ndi zaulele muzagulitsa nazo sogolo lanu,zikoli likuyendesedwa ndi satana samalani abale
@RitaHussein7 күн бұрын
Thandizo sitilenge ayi chomaika pa camera ndi chani ngati mwapereka zeni zeni
@Salverbestjunior9 күн бұрын
❤
@Lydia-t4b3 күн бұрын
Nzimayiyu simunthu wamba ndiolemera kuyambira kale koma anthu manena ngati analemera chifukwa cha Mpinganjira.
@pauljosephmakaula68357 күн бұрын
Mayi wa dxiko, okongola ndi mtima omwe ....a Malawi 🇲🇼 zikhulupiliro zomwe zomatisaukitsa...
@MphatsoRichard-mb8wi7 күн бұрын
Othandidza sayenda ndi camera
@SydneyUkonde-r2g11 күн бұрын
Aaaaaa zikhulupiliro vuto lake azimai inu pali dzuwapa kukana zosezo
@PrincehrnNgombayela-rq3gi10 күн бұрын
Mai mpinganjira mulungu akudalitseni nanenso mundiyendere kuno kulikoma
@ErnestMaseya10 күн бұрын
No easy money around the world given to someone without the benefit from the giver.There is something behind
@joegibsonzulu25999 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@EluphyMasala8 күн бұрын
😂 madalitso sasochera
@milcamathias684511 күн бұрын
Mpaka documentary nkhani yomwe ija? Eh eh
@CassimMeleka3 күн бұрын
Mayiwa adakana moona mtima koma zot adawathamangira mmm zabodza koma chabe ,chuma cha enawa amafuna kudyera ena thukuta lawo pa zikhulupiliro ,ngt akufuna zot ziko lowziwe azipanga zimenezo ,ngt kut azithandiza mmona mtima psaakhale camera
Mrs mphinganjira kuli ana ku queens amene Ali ndi nthenda imene amakula mitu akufnika chithandizo,za operation,mwina mutathandizilako kumeko ZIkomo
@milcamathias684511 күн бұрын
Spina Bifida and Hydrocephalus. I covered this story last year at Blantyre Sports Club when they were celebrating World Day. She can talk to Blessings Chapweteka, Executive Director of Child Help, they are helping children born with Spina Bifida and Hydrocephalus.
@slow-kkamanga49066 күн бұрын
but the T is stunning and beautiful
@FredrickSongwe-xc6bw11 күн бұрын
Kk ari Bwino mzimayi, m'daritso siwake wanenawanena
1) Mpinganjira akukanika kupereka ngongole kwa ma contractors. 2)Koma mkazi wake akugawa ndalama kwa anthu. 👆Izi ndizidabwitsa. Ndalamazo akupangira ma rituals. Osalandira ndalama za anthu ngati Tri-hule
@KondwaniMtuwa11 күн бұрын
Easily come, easily gone
@MackstarAbinala-o4x23 сағат бұрын
Palibe zachifundo pamenepo nde kut alindicholinga ndindalayo zachifundo saonesa kugulu