Kucheza ndi Mkulu amene anawona zowopsa pomwe amkapita ku South Africa mu njila zamadulila Part 1

  Рет қаралды 120,186

MALAWI 265

MALAWI 265

Күн бұрын

Пікірлер: 111
@TiyesiFidesi
@TiyesiFidesi Ай бұрын
Khaniyi ndi zoonadi mmmmmm ineso ndinayendako mchire ndipo khaniyi ndi 100 percent
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana Ай бұрын
Zothangazo ndizoona ine ndinaziona zimenezo sizabodza pamavuto muthu mumapanga zoti sunapangeko kwaomwe an aziona akudziwa
@JohnnyFlyKanula
@JohnnyFlyKanula 5 күн бұрын
Nkhani izizi zimaoneka zophweka ukamazimvela choncho kma ukazakumana nazo ndipamene umazat history is the best teacher, kwa amene anaendapo ma ulendo atali atali iziz avomeleza
@Lydia-t4b
@Lydia-t4b Ай бұрын
Koma zinazi kuthawa mavuto kwanu kukazilowesa ku mavuto oposa omwe mwasiya kwanu
@EvahMw-bz6yo
@EvahMw-bz6yo Ай бұрын
Eeeeiiiiish 💔😢 izizi zikukambidwazi mzoona musazitenge easy tiyen tisamale Guys
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@EvahMw-bz6yo osamanama kuti anaenda ntunda woposa tsiku lonse pa ntchangala kukadutsa kumusi kwa mudzi mpoenda mwina 30 miniti olo onenepa mwina 40 to 45 basi komaso kulibeko phili makosana koma mwina anaenda kumasenga vuto opanda passport kudalila zitsamba eya mavuto sathawika mwina anawatsitsila ntete pa waa kapena komaso samalani izi ulibe passport ndiposo chizungu sumanva tswana sumanva isizulu sumatha chona sumanva mayooo koma zitsamba bolo lili lodzaza kudi mukuiwala mulungu kutsata milungu mudakaziona kwainu opusanu izooo
@MaulanaBanda-r5o
@MaulanaBanda-r5o Ай бұрын
Exactly zomwe anandiuza brz wanga and mzao mmodzi mgulumo anatopadi transporte nkuzati musiyeni koma nzake wa bro wanga anakana anamunyamula nkumuika pa phewa mpaka kutuluka naye mu nkhalango
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@MaulanaBanda-r5o kkkkkk komatu
@nyondoandrews1621
@nyondoandrews1621 Ай бұрын
Ayi izi sizaboza zotheka ine ndinayenda muntchire
@Spenceea6KMG
@Spenceea6KMG Ай бұрын
I am wiating for part 2
@giftevans2957
@giftevans2957 Ай бұрын
Nice 👍
@KettieNathaya
@KettieNathaya Ай бұрын
Ma passport ndi chida chachikulu koma umphawi umapenegetsa munthu
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@KettieNathaya zooonadi akumapusisidwa pouzidwa kuti zitsa izi zazi
@KELVINGezakanjan
@KELVINGezakanjan Ай бұрын
Khan 😢😢 yovetsa chisoni ulendo uwuwu simajock ayi ndizoona ndipo musayese bodza ine naziwona 😢😢😢😢
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@KELVINGezakanjan kodotu amanewo amapita kuitale kumasenga mkuvutika pati
@chifunirosaka9077
@chifunirosaka9077 Ай бұрын
Zosakhala bwino akazi mpakana kumango gonedwa mwachipongwe chomcho koma umphawi sinthu
@InnocentKasiya
@InnocentKasiya Ай бұрын
Zoona ndithu 😢😢😢munthu wamkazi ndiye ali pachiopsezo chachikulu ndithu.. Moti ambiri amakafika ndi matenda komanso zimimba za matraspota.. Nkhaniyi ikufunikira kufikira a Malawi ambiri 😢😢😢
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@InnocentKasiya vuto ndoti akaziwa akumapita kokango boletsa ndiye mpovuta iwo kuti azinama pamauthenga ena izi zoti sizizatha aziyamba apanga ma passport basi osati mulole nkumangona ndinjala zokudya zilipo atalola si amachita kuti ndikanjoye mayooo
@alexbenard1104
@alexbenard1104 Ай бұрын
😢😢amw tikuzunzika moopsa kwambiri
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
Koma bodza ilo palipo poti mkuyenda 2hous bodza laufiti ilo openga iwe
@VickyChide
@VickyChide Ай бұрын
Eeeee kupita ku Jon ndikulimba mtima
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 Ай бұрын
Border yowolotsa anthu munkhalango ndi ya Zimbabwe kulowa South Africa osati Mozambique kulowa Zimbabwe.
@ChipiGrant
@ChipiGrant 6 күн бұрын
Aaaa nanga nyamapanda nawenso waiwalatu iwe kujampa timayamba nyamapanda mesa
@RajabuGereymaleta
@RajabuGereymaleta Ай бұрын
Khan ndi yowona ineso ndinali pompo
@AbdulMmadimwanyalisi
@AbdulMmadimwanyalisi 27 күн бұрын
Mmmmm sizabwinotu izi
@Rhoda-g1y
@Rhoda-g1y Ай бұрын
Zovesa chisoni 😢😢😢😢 part 2
@RobinFiston-v7f
@RobinFiston-v7f Ай бұрын
eya guys ndizowona ma transpoter ena amakakusiyani mozambique ndikukunthawani,mbava
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Ай бұрын
Zomvesa chisoni kwambiri.......anthu tikumvutika...chosecho....chifukwa cha umphawi
@WitnesMaster
@WitnesMaster 22 күн бұрын
tiyapemphelele aulendowa
@ThomasKamwendo
@ThomasKamwendo Ай бұрын
Umatha kachere
@MerviceChisuwi
@MerviceChisuwi Ай бұрын
Zovutatu 😊
@ThokozaniMachesoNamalira-bk1zi
@ThokozaniMachesoNamalira-bk1zi Ай бұрын
Mzimai akwere bus not ma 🚛
@babranzima8120
@babranzima8120 Ай бұрын
I know that khalango ndipo sindizapangaso kuyendaso kukhalangoko
@preciousneddi2564
@preciousneddi2564 Ай бұрын
Anakugonaso nawe?
@babranzima8120
@babranzima8120 Ай бұрын
@preciousneddi2564 ayi ife timangoyenda mchichire kuchinyumbako sindikukuziwa kondikhalqnho yoopsa ife tinalowa cha 6am timatuluka 6pm ndipamene timaona museum tinali ambiti
@FudWellos-y4g
@FudWellos-y4g Ай бұрын
😮😮 zosakhala bwno
@HarryMakwale
@HarryMakwale Ай бұрын
Part 2 please
@siriaufi1021
@siriaufi1021 Ай бұрын
Sad reality. Survive of the fittest
@AdmiringCartoonCat-hv2sf
@AdmiringCartoonCat-hv2sf Ай бұрын
Part please
@DereckMatiya
@DereckMatiya Ай бұрын
Zonveda chisoni
@PatienceMphuche
@PatienceMphuche Ай бұрын
Ulendo wabwz ndikukonzeka moyenera kukwera bus basi osati ma truck
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri Ай бұрын
Ungathamange tsiku lonse?
@ChancyEMathias
@ChancyEMathias Ай бұрын
Next pliz
@EdnahKachalie
@EdnahKachalie Күн бұрын
Eeeee😢
@JUDOULTEC-LAB
@JUDOULTEC-LAB Ай бұрын
Please gyz pezani ma transporter achilungamo osamayamba urendo mulibe ndarama
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@JUDOULTEC-LAB kodi mku kwela yaotenga katundu kusanganiza
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
NXT
@JoyceKachikho
@JoyceKachikho Ай бұрын
Zoopsa kwambiri
@ChristinaJanuary-f2d
@ChristinaJanuary-f2d Ай бұрын
Mmmmm ayi ndithu
@JumahJhanePhiri-e7p
@JumahJhanePhiri-e7p Ай бұрын
Zilango😢
@babacheroocsy1762
@babacheroocsy1762 Ай бұрын
Munthu amati anafika pa beiltbridge bhobho anafikaso ku Mozambique side bwanji this man can lie
@patrickmwandira3013
@patrickmwandira3013 Ай бұрын
Kkkkk
@TempestStudioArea49
@TempestStudioArea49 Ай бұрын
Part 2
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve Ай бұрын
Yinali nthawi ya Bingu ndikale apo
@BlessingsMlauzi-cl4ru
@BlessingsMlauzi-cl4ru Ай бұрын
Bingu ndiyemwe amatenga anthuwo kubwera nawo kuno?
@HalimaUka
@HalimaUka Ай бұрын
Izi ndizonadi
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga Ай бұрын
I wonder munthu oti ali ndi passport, why kuyenda zamadulira? 😢
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Ай бұрын
Tayambilani poyambilira mudziwa why
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga Ай бұрын
@mishecksipolo7153 ndamvera koma those are not valid reasons. Ma shortcut zotsatira zake ndi zimenezo
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@ColetteMalunga zabodza analibe komaso kupusa chikhanda
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga Ай бұрын
@@ZimhungaEsther kkkkkkk mpo zukaikitsa bwanji. Munthu ngati wapeza passport osangochita ganyu mkupeza transport ya bus? Changu pena sichithandiza
@DICKSONJACOB-g4l
@DICKSONJACOB-g4l Ай бұрын
Where is part two please
@MandonKaunda-l2i
@MandonKaunda-l2i Ай бұрын
Pamenepo yatha koma zkachika akupasilan ina
@alicembetewa5151
@alicembetewa5151 Ай бұрын
ndizoopsadi kuenda opanda passport
@TaweniChavulaKamwendo
@TaweniChavulaKamwendo Ай бұрын
Eeee ndaopa
@ReginahChilimba-q2r
@ReginahChilimba-q2r Ай бұрын
Mmmmh zoopsa
@MariahHajison-o9l
@MariahHajison-o9l Ай бұрын
Dzafa osakudziwa
@EnelessKamwendo-f7u
@EnelessKamwendo-f7u 23 күн бұрын
Sizabwino abale
@tisunganechilale3653
@tisunganechilale3653 Ай бұрын
Zovuta
@AlinafeMalunda
@AlinafeMalunda Ай бұрын
Eeeee zosayenda
@RosinaWakuthera
@RosinaWakuthera 28 күн бұрын
So sad
@MacdonaldMasamba-e2x
@MacdonaldMasamba-e2x Ай бұрын
Mmmmhhhhhhh km guys!!
@MaryChimela-n5m
@MaryChimela-n5m Ай бұрын
Sad news
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb Ай бұрын
Yaboza
@victormbvundula2665
@victormbvundula2665 Ай бұрын
Sad
@EsetaGerate
@EsetaGerate Ай бұрын
Eeee zovuta
@lifredchikumba420
@lifredchikumba420 Ай бұрын
Nkhani yabodza munthu ungathamage tsiku lonse
@Lydia-t4b
@Lydia-t4b Ай бұрын
Ndipo zoopsatu
@EstoneKambuku
@EstoneKambuku Ай бұрын
Kusadziwa ndikufa komwe. Vuto ndi lotiii munazolowera kunamizidwa, mufufuze Kpna mudziwafusa omwe anapitako SA akuuzaniiii ine aunt anga anayenda 17days ansanafike SA
@babranzima8120
@babranzima8120 Ай бұрын
@@lifredchikumba420 umboni ine ndilinawo kuyenda siku loose ndinayendapo
@chrisluke3555
@chrisluke3555 Ай бұрын
Ndizoona akunena uyuzi zikuchitika ndithu
@FrankKambwani
@FrankKambwani Ай бұрын
Yoo!!😢
@ChristianKadango
@ChristianKadango 4 күн бұрын
Kuthamanga tsiku lonse mmmmm
@MonalisaChilemba
@MonalisaChilemba Ай бұрын
Anthu akuzunzika😭😭😭
@ChisomoVeston
@ChisomoVeston Ай бұрын
P Pp
@IssahIkra
@IssahIkra Ай бұрын
Iwe wabodza iwe kobasi
@RashidRashka-d3l
@RashidRashka-d3l Ай бұрын
Nkhaniyo ndiyoona sakunama ineso ndilikomkuno ndipo ndinayenda ndi azimayi opandad ma passport amapangidwad zimenezo koma mwina inu mumayenda ulendo wabwino koma ine ndaonad azimayi akupangidwa zimenezo ndi ma transporter
@ZathuzomweBenitoBLP
@ZathuzomweBenitoBLP 29 күн бұрын
That's bad
@Callen-q8o
@Callen-q8o Ай бұрын
Iwe onama kwabasi
@LeonardChisare
@LeonardChisare Ай бұрын
Amwene musatelo ndinaziwona
@lifredchikumba420
@lifredchikumba420 Ай бұрын
Koma khani iyi ndi yabodza
@ImranWyson-e9o
@ImranWyson-e9o Ай бұрын
Nkhaniyo ndiona 💯 ndiona ndimaso anga live😢
@MosesDicostar
@MosesDicostar Ай бұрын
Ase ine ndli ndzanga anayendesedwa wapasa kuchoka kusanje Mpaka ku Mozambique koma anabweleraso wapasi pano alikumalawi komwekuno
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@ImranWyson-e9o zoona ndikhani yabodza
@darlingtonkamanga4858
@darlingtonkamanga4858 Ай бұрын
Eeeeee zoopsatu
@dalitsonambazo
@dalitsonambazo Ай бұрын
😢😢😢😢
@PacianKayira-po6xf
@PacianKayira-po6xf Ай бұрын
Zoopsatu
@davidjoemalungah6338
@davidjoemalungah6338 Ай бұрын
CDM YOUR RELIABLE CAR DEALER
@BlessingsLikhomo-k7x
@BlessingsLikhomo-k7x 19 күн бұрын
Zachison
@PatrickKalunga-vn1nj
@PatrickKalunga-vn1nj Ай бұрын
Eee zachabe
@MassaMokowa-n3q
@MassaMokowa-n3q 20 күн бұрын
@chibest Chimwe Bonongwe?
@ManblesserPeter
@ManblesserPeter Ай бұрын
Inenso zinandichitikila 2013 tinayenda ku Limpopo river komwe kuli ng'ona
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
@@ManblesserPeter komatu azathu mulibe tsongolo bodzatu
@HalimahMdala
@HalimahMdala Ай бұрын
Part 2 pls
@SheriffMpoya
@SheriffMpoya Ай бұрын
Part 2
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther Ай бұрын
Bodza amalawi iwe wabodza
@DCwachinyamata
@DCwachinyamata 22 күн бұрын
Wabodzadi akuluwa bwanji
@pempheromulepa9281
@pempheromulepa9281 16 күн бұрын
Nzoona
@BennettNjedza
@BennettNjedza 29 күн бұрын
Ofunika mapemphero
@EnelessKamwendo-f7u
@EnelessKamwendo-f7u 23 күн бұрын
Sizabwino kwambili
ZOOPSA ZOMWE ANAKUMANA NAZO MMALAWI UYU
22:32
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 35 М.
Cat mode and a glass of water #family #humor #fun
00:22
Kotiki_Z
Рет қаралды 42 МЛН
小丑教训坏蛋 #小丑 #天使 #shorts
00:49
好人小丑
Рет қаралды 54 МЛН
IL'HAN - Qalqam | Official Music Video
03:17
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 700 М.
The Fruit Of Sin 2024 Best Malawian film
1:53:28
Aaron Chambo TV
Рет қаралды 95 М.
Kucheza ndi wa Sataniki Mpakana Waziwulula Yekha
20:20
Morton Baghaya
Рет қаралды 230 М.
TIKUferanji 25 JULY 2015
26:27
Edson Gunsalu
Рет қаралды 135 М.
Tsatane  Tsatane wa Nkhani ya Anthu Amene Akanilirana kwa Wilisoni
17:42
Balanço semanal CK & Govate
Рет қаралды 161 М.
Miracle Chinga - Kubadwa Kwa Yesu (Official Music Video)
4:55
Miracle Chinga
Рет қаралды 507 М.
Mayi Wina Watopa ndikugonana ndi Ndondocha
31:46
Mvangeli Online
Рет қаралды 12 М.
Cat mode and a glass of water #family #humor #fun
00:22
Kotiki_Z
Рет қаралды 42 МЛН