Zina UKAMVA kamba anga KHWESI🥵

  Рет қаралды 18,017

FRANCIS MTAWAYA TV

FRANCIS MTAWAYA TV

Күн бұрын

Пікірлер: 32
@Shem2
@Shem2 2 күн бұрын
Voice iyi,ndinayimvaponso munthu wabodza uyu amangopeka nkhani
@AlishaYasin-t1x
@AlishaYasin-t1x Күн бұрын
Komadi olo zitakhala zopeka he is telling the truth and izizi zikuchitikadi,ife takawidwapo ndalama osadziwa kuti yasowa bwanji,komanso izi za kwa asingangazi nzoonadi ndunena pano ankoloanga ndamisala nkhani zake zomwezi,anasemphetsa zizimba pofuna kupha mayanga mmatsenga,mwatsoka zidakanika,tiyeni titengerepo phunziro,zikomo
@Jofra-pu7sm
@Jofra-pu7sm Күн бұрын
Kaya ndibodza ife taphunzilamo mubodzamo 😊
@IsmailNdemanga
@IsmailNdemanga 5 күн бұрын
Oudio yaphinthu dzikomo kwambili taphuzilapo zambiri apa🙏👏👏
@AjaluIsah
@AjaluIsah 2 күн бұрын
Good advice
@rashidadan2533
@rashidadan2533 2 күн бұрын
Panopa chakwela wakweza fertilizer kufika pa 125 thousand kwacha
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb 2 күн бұрын
Kodi Inu mumangopeza Muthu omweyi bwanji Palibe wina mwapeza bizines yanu yotinamizatu
@MikeLodzi
@MikeLodzi 3 сағат бұрын
mkulu uyu ndiwabodza ndi uja amakonda kukamba nkhani zaku South african uja uyu
@FlorenceMustafa-f1m
@FlorenceMustafa-f1m 3 күн бұрын
Ndipo ndiye taphunzilapo apa kwambiri eee
@PatrickChiwaya-cc9ef
@PatrickChiwaya-cc9ef 3 күн бұрын
Jafari kod ukufuna uxitipusisa eti mesa unakumanaso zooopsa pomwe unali pa ulendo opita ku Joni iwe
@Shem2
@Shem2 2 күн бұрын
Ndi yemweyu inde. 😂😂
@NganoNjazi-r4h
@NganoNjazi-r4h 2 күн бұрын
😂😂😂😂....ayamba kutinamiza
@RoseFatch
@RoseFatch Күн бұрын
Super 😢😢
@LazarusChirwa-su7yc
@LazarusChirwa-su7yc 5 күн бұрын
Koma kudziko kulizinthu abele mlungu ativele chosoni
@YahyaIsmail-b8o
@YahyaIsmail-b8o 3 күн бұрын
Aise iweyo ndiwonama kwambiri mesa iwe ndiwe unazalongosolanso nkhani ya Ku jons nkhani ya nzako amene anaba ndalama Kwa bwana wanu mkuthawa voice yakenso ndiyomweyinso😂😂😂😂😂
@ChikondiKwengwere
@ChikondiKwengwere 3 күн бұрын
Akusiyana
@AlishaYasin-t1x
@AlishaYasin-t1x Күн бұрын
Kuterokotu izizi posatengera kuti kaaya amakamba yekha koma zikuxhitika ndithu,iye alingati driver,kapena kuti advisor,tiyeni tizimgotengerapo phunziro bas
@HawaMamo-q2v
@HawaMamo-q2v Күн бұрын
Zowonadi Kaya zabodza koma muziphuzira
@innocentlipita3630
@innocentlipita3630 Күн бұрын
Koma use standard language the word khwesi ndiye zochani zimenezi
@ElliasShaba
@ElliasShaba 3 күн бұрын
Inuyo mulindi vuto limidzo coz mumabisa pomwe pagona mfundo mukafika potchura dzina simutchura ndiye tiziti ndichani aaaa zaboza bs aaa
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 5 күн бұрын
Nanga choncho ulimi wrniweniu mpama zitsamba amalawii tidzafadi amphawi nditnu
@FeliBanda
@FeliBanda 2 күн бұрын
Kulibwino ndidzafe mphawi
@GreyChilabade
@GreyChilabade 2 күн бұрын
Kod zimangokuchitikila? iwe wekha wekha basi
@davemasanjala6499
@davemasanjala6499 Күн бұрын
taphunzilapo zambiri apa
@JosephSamuel-f6f
@JosephSamuel-f6f 14 сағат бұрын
😂😂😂😂
@abdulwahabmchikoma
@abdulwahabmchikoma 2 күн бұрын
Voice iyiyi ikupezeka paliponse😅🤣
@IbrahimWilliam-s8i
@IbrahimWilliam-s8i 3 күн бұрын
mulinji
@BeatriceKachokaJuma-v1x
@BeatriceKachokaJuma-v1x 3 күн бұрын
Esh dziko lapansi
@GetrudeBanda-sd1yf
@GetrudeBanda-sd1yf 4 күн бұрын
Zoona sichimachedwa kutha
@NickUpoche
@NickUpoche 6 күн бұрын
Akulu akuli Pena amafuna kusocheletsa ana si bho
@EarlyCelebration
@EarlyCelebration 6 күн бұрын
Okay
@GrayManyeka-h7c
@GrayManyeka-h7c 3 күн бұрын
Kuli zinthu
The Best Band 😅 #toshleh #viralshort
00:11
Toshleh
Рет қаралды 22 МЛН
黑天使只对C罗有感觉#short #angel #clown
00:39
Super Beauty team
Рет қаралды 36 МЛН
Сестра обхитрила!
00:17
Victoria Portfolio
Рет қаралды 958 М.
ZOOPSA ANAONA MMALAWI KU SOUTH AFRICA#FrancisMtawayaTV
21:59
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 127 М.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH RICHARD CHIMWENDO BANDA
1:13:46
Zodiak Malawi
Рет қаралды 51 М.
Njira Zamadulira Zimapondetsa MATOPE #FrancisMtawayaTV
9:26
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 13 М.
Tsatane  Tsatane wa Nkhani ya Anthu Amene Akanilirana kwa Wilisoni
17:42
Balanço semanal CK & Govate
Рет қаралды 174 М.
Paul Kagame ali ndi makani opanda ntchito ngati Idi Amin
7:02
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 47 М.
MALO OWOPSA MU MZINDA WA BLANTYRE
6:12
Dreams Media MW
Рет қаралды 18 М.
zinaukamva , N'sing'anga agwira ntchito ndi Apolisi
57:13
Blessings Cheleuka
Рет қаралды 50 М.
NЮ - Некуда бежать  (ПРЕМЬЕРА клипа)
3:23
Николаенко Юрий
Рет қаралды 4,3 МЛН
Ямахау
3:14
Ұланғасыр Қами - Topic
Рет қаралды 224 М.
Qanay & ALI Otenov - Lolly (Music Video)
2:59
AAA Production
Рет қаралды 87 М.
QARAKESEK - “REAL” | solo
3:22
QARAKESEK 🇰🇿
Рет қаралды 767 М.
Милана Хаметова & Milana Star - ЛП ( Премьера клипа 2022 )
2:19
Милана Хаметова
Рет қаралды 11 МЛН
Sivchik feat. Badabum - Бадаладушки (КЛИП 2022)
2:25
FLAGMANMUSIC ® | MUSIC COMPANY
Рет қаралды 5 МЛН