Рет қаралды 7,330
Samson Phiri
Mpingo wa Zion umamveka ndi mkhani zosiyana siyana. Kupatulapo kuti amalesa anthu awo kumwa mankhwala Ena akuti amalumpha moto. Kodi iwowa ndi ndani? Taonani