ZODABWISA ZIMENE PETER MUTHALIKA WACHITA KOMANSO WAYANKHULA ATANGOFIKA LERO PA BANGULA KU NSANJE

  Рет қаралды 49,567

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 99
@MKANDAWIRE-z6s
@MKANDAWIRE-z6s Ай бұрын
Kunena dzoona m'malawi mtsogoleri odziwa mavuto ndi Peter mtalika, God bless him!
@SammyCMW
@SammyCMW Ай бұрын
woozaa
@EdwinGama-n7w
@EdwinGama-n7w Ай бұрын
My vote ✅
@BintaChirwa
@BintaChirwa Ай бұрын
My vote,from copperbelt
@GeorgeChipanda-n8e
@GeorgeChipanda-n8e Ай бұрын
My vote APM
@Samson-ve5rs
@Samson-ve5rs Ай бұрын
APM my vote💙💙💙💙💙💙
@MiriamSalome-c3z
@MiriamSalome-c3z Ай бұрын
Ife ana Adadi pheeee kudikilira siku lokavota💙💙💙💙💙
@OmarManjawira-up3ns
@OmarManjawira-up3ns Ай бұрын
Fir real bro,,,,😊
@LimbaniSamueli
@LimbaniSamueli Ай бұрын
Ineso zavotera Dpp 💙💙
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga Ай бұрын
Ngambwi ngambwi anthu ngati madzi🎉🎉🎉🎉my vote 💙💙🗨️🗨️💙🗨️💙🗨️💙💙
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p Ай бұрын
Mcp inaziwiratu nzulo kuti lero kusanje kwajuta ❤❤apm muli upangirari boma ndilomweli koma utsongoleri tikusitha
@CharlesBanda-v8k
@CharlesBanda-v8k 14 күн бұрын
Kunena zoona satana anatinyenga amalawi eish long live APM🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h Ай бұрын
Much more fire postar munthalika ameneyu nde busa osati razalo 2025 tizachita kuthamanga kuka votela apm goooookonko
@AdamkalushaAlabi
@AdamkalushaAlabi Ай бұрын
Zoona adad❤️❤️❤️❤️
@Staphelsavimbindhlovu
@Staphelsavimbindhlovu Ай бұрын
Love dad❤❤❤
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Ай бұрын
Akupangila msonkhano ku ntchito kwa kwakale kwa chakwera chipiki😂adad woyeeeeee💙💙💙💙💙❤❤
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr Ай бұрын
Kkkkk😂 chipiku eti
@MercyMusopole-q2r
@MercyMusopole-q2r Ай бұрын
My vote
@isaacmhango-h8z
@isaacmhango-h8z Ай бұрын
Akapume gogo uyu, Chakwela!! Booma!
@JamesKhudze
@JamesKhudze Ай бұрын
Apm ❤❤
@StellaKabango
@StellaKabango Ай бұрын
Pena gt ndibwere kusanje komwekotu AP M my vote
@Robert-wi1hf
@Robert-wi1hf Ай бұрын
Adadi nafenso ku Zambia tilinanu
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa Ай бұрын
My home . APM MY VOTE❤🎉
@AngelaGraysham
@AngelaGraysham Ай бұрын
My APM my Dpp ❤❤
@abgi.doctor.august
@abgi.doctor.august Ай бұрын
Mulungu tetezani musungeni ndi kumudalisa Peter Muthalika kuti 2025 adani Ake muwachitise manyazi pamene Inu muzapangise kuti Malawi yonse imuvotere Ndipo Inuyo Ambuye tikudziwa kuti mukumusunga ndi cholinga mdziko lino la Malawi dzina la Chauta litamandike mupaseni moyo wautali msogoleli wanthu Peter Muthalika president Chaka Cha 2025 ❤❤❤❤❤
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Ай бұрын
Ameen
@MagretPhiri-z3b
@MagretPhiri-z3b Ай бұрын
Amen blessings overflowing ❤
@Staphelsavimbindhlovu
@Staphelsavimbindhlovu Ай бұрын
Amen
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n Ай бұрын
Or atabwerera malawi sazasintha mungotaya nazo nthawi zimenezo limbikirani kwa inu nokha chisale ndiyemwe akukondwera pamenepo
@limbanitambala3939
@limbanitambala3939 Ай бұрын
@@user-ii9ch7oz8n Ife tikudziwa kuti azasintha chifukwa zisanzo tilinazo, Bibgu anasintha yansi zomwe Muluzi anasiya ndipo zinatheka, APM anasinthanso nyansi zomwe anasiya Joyce Banda ndipo zinatheka, ndiye chosasinthira nyansi za Chakwera nchani??
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Koma adadi anasakhidwa ndi mulungu osati zinazi 💙💙💙💙💙 zangotitayisa nthawi basi
@aarondickson70
@aarondickson70 Ай бұрын
God guide APM to pull Malawi in this tragic panishment of fuel, hunger and devaluation currency
@AustinMhone-r3s
@AustinMhone-r3s Ай бұрын
Malawians will see change only with federal system of government not individuals
@HannahKabango
@HannahKabango Ай бұрын
Mulungu mpatse Peter muthalika Moto wautali
@MbeweGreva
@MbeweGreva Ай бұрын
Only hope
@WachiyaoBwintoamosi
@WachiyaoBwintoamosi Ай бұрын
🎉🎉❤
@DennisMdezq
@DennisMdezq Ай бұрын
Apm my vote no matter what 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙
@rhodrick2000
@rhodrick2000 Ай бұрын
Boma ilo 2025 woye😊😊
@SauloKanjinga-f7x
@SauloKanjinga-f7x Ай бұрын
Akantundu ndi omwewoo
@fahadmilanzi
@fahadmilanzi Ай бұрын
Apm and Chisale my vote
@FrankLenzo
@FrankLenzo Ай бұрын
Ndipo adad ndi more 🔥
@FelixChikola
@FelixChikola Ай бұрын
Owina wina APm
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h Ай бұрын
Kkkkkk mmmmmm bas apm booma laathu opanda minyama
@MagretPhiri-z3b
@MagretPhiri-z3b Ай бұрын
Taonani taonani 😅😅 wina akuva kuyabwidwa chauko uko😅
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i Ай бұрын
Munthu amene cikangawa sagona nae tulo nde ndi APM ndi dpp uyu nde amva nae mmimba sanati 2025 ndiyemwe tivotele cimene tikupempha ncoti mucotse smart matic sitikufuna kuti voti yatthu idzapite ku cikangawa ai.
@MagretPhiri-z3b
@MagretPhiri-z3b Ай бұрын
Anamugwesela dala chilima amaona ngt sipazapezeka opikisana nae wakhaula ndithu
@InnocentManda-d6i
@InnocentManda-d6i Ай бұрын
May vot
@YohaneEric-v2e
@YohaneEric-v2e Ай бұрын
Asamayende yende abare tudalira pompo😂
@MadalitsoAbambo
@MadalitsoAbambo Ай бұрын
Ineyo ndimaona kuti peter muli umtsogoleri otumidwa ndi mulungu ndithuu
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs Ай бұрын
Eeeah koma uyu❤❤😂
@storytambala6088
@storytambala6088 Ай бұрын
Nsonkhano, umachitikira pa office ya Chakwera yi?
@LameckTomasi-v7q
@LameckTomasi-v7q Ай бұрын
❤❤
@ABDULEasha
@ABDULEasha Ай бұрын
❤ boma
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Adadi kulibe oyimba music uku mwawona athu kusaza mwana wanu tupere vp
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s Ай бұрын
Anthu nonse aku Lower Shire mangani chimodzi podzavotera munthu APM chifukwa mvuto athu akuwadziwa.inu mayi Gladys Ganda yesetsani ntchito yanu yothangata anthu amalawi.
@JamaliJoseph-l3r
@JamaliJoseph-l3r Ай бұрын
mawa odii mkalembese mzavote next year
@SymonMwingitsa
@SymonMwingitsa Ай бұрын
Akalamba awa angathane ndi ndani
@RodgersMtonga
@RodgersMtonga Ай бұрын
🐓✔️🔥🔥
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h Ай бұрын
Wina afa ndi BP
@FatimaJackson-j8b
@FatimaJackson-j8b Ай бұрын
Kudikira tsku lokavota bas
@ChimwemweMathyola
@ChimwemweMathyola Ай бұрын
Please munthu amene akuziwa wapolice Zina laleke ndi mulewa wapolice pa nchalo please andiwakhule Ku iboxi now
@BlessingsUndih
@BlessingsUndih Ай бұрын
Mtsogoleri wokonda anthu ake komaso oziwa mavuto awanthu
@VeronicaYohane
@VeronicaYohane Ай бұрын
Adad timakunyadilan mukulowa boma tikunkhazikani tikufa ND niala ana ife
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya Ай бұрын
Machine....katundu womanga ndi ma wire..,APM 2025 woyeeee!!!
@LuciusMadimba
@LuciusMadimba 3 күн бұрын
tikulila komandizotheka kuzikoza 2025 DPP woye
@SuzgoMaiden-x7m
@SuzgoMaiden-x7m Ай бұрын
Mulungu akusamaleni ,mfumu yathu ndiinuyo .moyo waphweteka koopsa 4yrs yomweyi.mabusiness atha eeeeeee
@LottiAffati
@LottiAffati Ай бұрын
eeee guys mawa ndukalembetsa basi chipani koma ichichi cha dpp eeeee tawonani guys asaaaa koma adad inu
@AnnieTwanje
@AnnieTwanje Ай бұрын
Boma iloooo
@DavieMaganga-x2h
@DavieMaganga-x2h Ай бұрын
Ndikungoona kuchedwa kuti adad ndizangowati chongi
@LameckMlauzi
@LameckMlauzi Ай бұрын
Boma libwelele komwe linachokela
@patriciap.bandah3385
@patriciap.bandah3385 Ай бұрын
Wosanyoza dikirani muone zimene Mulungu amapanga tonse tikupita kokalamba komweko
@shaibuenock8128
@shaibuenock8128 Ай бұрын
Saziwa kuwopsa kwa mulungu
@TonexKapito
@TonexKapito Ай бұрын
Mumtima mwathu tavota kale monga ana adad changotsala ndichiwonetsero basi pa 16 Sept pano mu 2025
@DoreenNazombe-i3p
@DoreenNazombe-i3p 27 күн бұрын
Olemu wanu adad
@FrankNyirenda-j5r
@FrankNyirenda-j5r Сағат бұрын
Ili ndilo boma basi pali enso kuchosela
@IZAHAKAStone-l6u
@IZAHAKAStone-l6u Ай бұрын
Dpp woye
@DuncanMbulo
@DuncanMbulo Ай бұрын
Kulibetu woyimba kumeneko
@PatrickWiseman-m8l
@PatrickWiseman-m8l Ай бұрын
Adad omwewo 2025 boma!!!!!
@RodgersMtonga
@RodgersMtonga Ай бұрын
Kod ma boma awiri nsanje ndi chikwawa MP wa dpp ndi modzi eeee anthu akumeneko amavota motani?
@KestenNakhawonga
@KestenNakhawonga Ай бұрын
Ngati adadi sawina ndikusamuka musale nawo ziko lanuli
@HenlyBamus
@HenlyBamus Ай бұрын
Azikwera yekhatu pansanjapo kkkkkkk
@johnmambo4915
@johnmambo4915 Ай бұрын
Kodi chomwemakwezela sound yanu yawusiluyi ndichani nmalo moti anthu tizivela zomwe mwaponyazo that's nonsense
@Jafari-s3c
@Jafari-s3c Ай бұрын
Ndawonapo office ya chakwera Pamenepa(chipiku)
@isaacsnowden7725
@isaacsnowden7725 Ай бұрын
Kkkkkkk
@PiusChawinga
@PiusChawinga Ай бұрын
Mhu
@chikumbutsomatias1117
@chikumbutsomatias1117 Ай бұрын
Uyu nde wakalambira2 moti kukanika kucheukira anthu km kuchita kuzungilira kkkkkkkk
@MagretPhiri-z3b
@MagretPhiri-z3b Ай бұрын
Kukalamba kwao simukugonaso nao tulo 😂😂😂
@LoyceChipwaila
@LoyceChipwaila Ай бұрын
Nkhani yokalamba yikuchedwatsani amalawi akufuna wokalambayo ka.
@LoyceChipwaila
@LoyceChipwaila Ай бұрын
Kukalamba sitchimo koma ndi chisomo chimenecho .
@spargomw
@spargomw Ай бұрын
Peter mngodala coz enafe taona ukalamba kwake, iwe udzalamba? Umunthu pena uzikutsutsani mukamalankhula ngat mwadula mutu.
@HenlyBamus
@HenlyBamus Ай бұрын
Chakwera wakuzunguzani mutu
@AngellachifundoMwale
@AngellachifundoMwale Ай бұрын
Chomwe muwazunzila granny wa mchani dpp simungatiuze izii chisale alipompo 😂😂😂 aaaa mukonza bwanji dziko lomwe munaliononga kale ukuku nde kutiyesa munakati muli ndi new faces without background yokuba zizitayisani nthawi 😂😂😂😂😂😂
@InnocentManda-d6i
@InnocentManda-d6i Ай бұрын
Galu wachabe iwe
@AngellachifundoMwale
@AngellachifundoMwale Ай бұрын
@InnocentManda-d6i Eya koma ndugalu wangawu ine awaa sangandipusise munthu oti guard analemera kuposa abwana ake aaaa zachamba
@RodgersBanda-l6j
@RodgersBanda-l6j Ай бұрын
No mistake lets vote for adad,MCP chipani chakupha sutikuchifuna chalephera kuyendesa dziko lino
@DenisBlack-u2l
@DenisBlack-u2l Ай бұрын
My vote
@ChiccoJali
@ChiccoJali Ай бұрын
My vote APM
@JeannettePhiri-c6b
@JeannettePhiri-c6b Ай бұрын
Boma iloooo
-5+3은 뭔가요? 📚 #shorts
0:19
5 분 Tricks
Рет қаралды 13 МЛН
Who is More Stupid? #tiktok #sigmagirl #funny
0:27
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 10 МЛН
24 Часа в БОУЛИНГЕ !
27:03
A4
Рет қаралды 7 МЛН
MCP ndi Chakwera akuopa DPP; Report ya Afrobarometer ikuwachititsa mantha
13:30
-5+3은 뭔가요? 📚 #shorts
0:19
5 분 Tricks
Рет қаралды 13 МЛН