No video

ZOMWE AKAMBILANA KU HOT CURRENT LERO PA 21 July 2024

  Рет қаралды 15,897

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 28
@Rometcma
@Rometcma Ай бұрын
Mary chilima is not a politician so musamavutitse zinthu munthu nsiyeni agwile ntchito zake 😢😢😢😢
@PociahMack
@PociahMack Ай бұрын
A UTM mitu sikugwila kma kumangotukwa ndi kupanga ndale pa maliro achilima malo momamulemekeza
@jameshuwanzulu
@jameshuwanzulu Ай бұрын
Ukudziwa bwanji kut ndi a utm amayimbawo phone wo,, chifukwa za ku boma kut akumayimbaso ma phone kut mayiwo akatenge mpando wina ku boma ??
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 Ай бұрын
What you’re forgetting is that, when UTM was formed, Manganya was not there. The death of Chilima is already political and you can’t take it out. Manganya has been appointed by Chakwera, not elected. Chilima was elected by the people not appointed. So you must differentiate between Isi and Chilima. Usi is not for UTM Usi is for MCP, he is there to advance Chakwera’s agenda.
@user-nr8oq4tr1i
@user-nr8oq4tr1i Ай бұрын
UTM it's Chilima and Chilima nde UTM. Apapa, zero pa 10
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 Ай бұрын
Unfortunately UTM will not survive I think
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
Inuso musamayankhule kwambili ngati agalu bwanji hule la mr sadick mia likadali ndale and panopa chakwera akudyaso katundu wa mia😂😂 molimba mtima si monica ndi nkhalamba
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr Ай бұрын
Kodi program mwaiyambila pakati bwanji? Komanso a Chunga alikuti? Mwaichepetsanso nthawi chifukwa nkhaniyi ndiyaikulu timakuyembekezerani kaya 🤔 komanso weekyi kwachitika nkhani zikuluzikulu zoti timafuna timve zandalama zathu zinapezeka Zambia ndiizi azipeza achinthyola banda zija. Ndiponso ndinakupemphani kalekale zoti muwaitane a john Kapito or Samuel Lwala mu program zanu musamangokhalapo nokhanokha and we miss Brian banda ajona wo akapume
@LindaMsiska-p3u
@LindaMsiska-p3u Ай бұрын
Inunso muziyankhura bwino kodi muli mbana ndi utm bwanji? Utm ikutsogozedwa ndi mulungu
@ShagaFologonya
@ShagaFologonya Ай бұрын
Sa UTM
@user-bs4ux8qe3p
@user-bs4ux8qe3p Ай бұрын
Chilungamo mr DC chikuyenera kumakambidwa...
@DesmondOzuzu
@DesmondOzuzu Ай бұрын
The problem is Mr usi has been avoiding this members since the death of SKS he should face Them tell them the truth
@AngungaThatcherNgoma
@AngungaThatcherNgoma Ай бұрын
Program yeni yeni ya original sinayambire pakati, pa platform iyi, atenga this part. Nde osadabwa.
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
Aku banja akudziwa kuti chakwera anapha mr chilima 😢😢
@stubish0p-fl2zf
@stubish0p-fl2zf Ай бұрын
Kodi abale ma supporters a manoma a bellets amakwanisa kunena kuti ngati ma team awo sakuchita bwino, amatha kunena kuti ma player simukwera bus kaya ndi coach simukwera bus zikutikanika bwanji ife kuti tiwawuze anthu onse ogwira ntchito ku immigration kuti tisamuwone munthu ali mu uniform ya ku immigration akubwela ku ma office kuti akukagwira ntchito, chifukwa ntchito yake sikuwoneka, kuti akupangire passport akufuna kuti upereke siphuphu, komanso mwezi ukatha akutinso alandire kuchokera ku boma, koma ma passport mkumati ndi a Malawi sikutotola kupusa uku.
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
Koma ngat azinga chilima ,angavute Mary chilima?uhhuh
@phillipchiotcha3197
@phillipchiotcha3197 Ай бұрын
Ndie hot current imakhala ya 25mins
@Betty-fe9ql
@Betty-fe9ql Ай бұрын
UTM yathapo
@JaphetSakala-pq4fl
@JaphetSakala-pq4fl Ай бұрын
Mmmmmmmmmmmmmmm😊😊😊
@meesailikeyougirlmoosa9801
@meesailikeyougirlmoosa9801 Ай бұрын
Bola chithepo chipanicho bas wadya balalikan
@jameshuwanzulu
@jameshuwanzulu Ай бұрын
Zosatheka zimenezo
@faithkamlongera5128
@faithkamlongera5128 Ай бұрын
😂😂😂
@austenbushiri-cx1kh
@austenbushiri-cx1kh Ай бұрын
Eeee zovuta 😊
@user-ti9yk4eg2l
@user-ti9yk4eg2l Ай бұрын
Mai chilima omweo apitilize udindo wa amuna awo UTM ndy itha ku wina , vuto adakali mchisoni
@user-nr8oq4tr1i
@user-nr8oq4tr1i Ай бұрын
Nde akatsogolera nkuzawina UTM ticket, Kodi ndekuti adzakwatiwanso because president sangakhale opanda mamuna kapena opanda mkazi. Kapena mwawapedzera mwamuna Mary kuti adzakhale first gentle man?
@Lee-lee-w1r
@Lee-lee-w1r Ай бұрын
@@user-nr8oq4tr1i😂😂😂
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr Ай бұрын
Kodi program mwaiyambila pakati bwanji? Komanso a Chunga alikuti? Mwaichepetsanso nthawi chifukwa nkhaniyi ndiyaikulu timakuyembekezerani kaya 🤔 komanso weekyi kwachitika nkhani zikuluzikulu zoti timafuna timve zandalama zathu zinapezeka Zambia ndiizi azipeza achinthyola banda zija. Ndiponso ndinakupemphani kalekale zoti muwaitane a john Kapito or Samuel Lwala mu program zanu musamangokhalapo nokhanokha and we miss Brian banda ajona wo akapume
CATHY MAULIDI ZOMWE WAONA KU PP CONVENTION
18:14
HOT 265
Рет қаралды 7 М.
So Cute 🥰
00:17
dednahype
Рет қаралды 43 МЛН
❌Разве такое возможно? #story
01:00
Кэри Найс
Рет қаралды 6 МЛН
Just Give me my Money!
00:18
GL Show Russian
Рет қаралды 990 М.
KUYANKHULA KWA JOYCE BANDA
21:25
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
BON KALINDO KUNG'ALULA MWA NYOO!! 5 September 2024
43:54
HOT 265
Рет қаралды 10 М.
Knowledge And The Glory Of God - Randy Skeete
1:31:00
2CBN TV
Рет қаралды 1,9 М.
Akufuna kupha mafumu a ku Ntcheu; Umboni wa mfuti 400 tili nawo
8:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 104 М.
So Cute 🥰
00:17
dednahype
Рет қаралды 43 МЛН