ZOMWE WAKAMBA BON KALINDO 🤔🤔 PA 19 June 2024

  Рет қаралды 155,818

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 281
@MisheckAselo
@MisheckAselo 3 ай бұрын
Timakudyadirani DC osamanyengerela amenewa, anthu oipa a kumkuyu musaiwale witika mulungu akukuonani
@VictorPhiri-vo4qj
@VictorPhiri-vo4qj 3 ай бұрын
Oh the blood of Abel cried to God and God heard the voice of Abel's blood,surely the blood of nine innocent lives,can not speak to the same God who does not change,surely the same God will hear them.
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 3 ай бұрын
Amen
@RashidSaid-lk6bb
@RashidSaid-lk6bb 3 ай бұрын
Ur a real man DC .B. kalindo and GOD must give long life and protection and don't stop am from south Africa port Elizabeth
@NastonVickta
@NastonVickta 3 ай бұрын
Komano pempho langa kwa Inu a president a anthu osauka a BON KALINDO, musazamalize ngati agalatia opusa, tiimilireni nyengo zonse,
@RobertChikawonda
@RobertChikawonda 3 ай бұрын
Kunkuyu akuyankhula ngati akuyankhulila kumachende
@MikeDael
@MikeDael 3 ай бұрын
Palibe amene angasekelele chipani chokupha ngati McPherson.
@mariezorgen7735
@mariezorgen7735 3 ай бұрын
God protect Malawi
@ChisomoSpacer
@ChisomoSpacer 3 ай бұрын
❤❤❤😂😂 kalindoyo athawitsa sthu chakachino
@JamesStanford-my1zj
@JamesStanford-my1zj 3 ай бұрын
Boma ili likuenera kutura pansi udindo
@YaphetGwaza
@YaphetGwaza 3 ай бұрын
​@@ChisomoSpacer11111111111111811111111
@MollysFanny
@MollysFanny 3 ай бұрын
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 ай бұрын
A Bon Kalindo mwalankhula za mphanvu kwambiri, George Kasakula akupanga campaign ya chakwera, zomwe akupanga akulakwa.
@MuhammadSauzand
@MuhammadSauzand 3 ай бұрын
Nyengo ino ndiyoyikano m'manda mcp. This is the fall of mcp.
@GeorgeMuserima
@GeorgeMuserima 3 ай бұрын
Bon pankhani ya ku MBC yo I support you 100 percent ndipo anandinyasa kwambiri moti ndinakalipira GOtv ndisakufuna chifukwa cha program achibwana ngati imene ija
@judithmichael-h9u
@judithmichael-h9u 3 ай бұрын
God protect you Mr president Bon kalindo
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 3 ай бұрын
Eti ayamba kuopa Ndege kkkkkk asaope naonso awachotsele zipangizo zina mu Ndegemo ikagwe iwo akaphyere momo akuopa Im'fa??? Anzao anaifuna?? Ameneyu ndi galu kwabasi ..azipita kolumbilitsako mbuzi yamunthu
@SimeonSanex-vw4py
@SimeonSanex-vw4py 3 ай бұрын
Bon kalindo umayankhulira bwino kwambiri mopanda mantha,coz polakwika sumasekelerapo,always we proud of you BON
@HamilBilly
@HamilBilly 3 ай бұрын
Keep standing for malawian mr kalindo,big up
@TatendaBanda-ef4mp
@TatendaBanda-ef4mp 3 ай бұрын
The DC, inuyo simusekelera zopusa.
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 3 ай бұрын
Iwe ndi kuktunda iyaaaaaa mumatiimira ndinu zonse mu zonse ❤❤❤❤
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 3 ай бұрын
Achewa Muzilimbikila Sukulu Osati Muzipha anzanu kamba kofuna udindo kapena chuma, zitsilu inu
@noelkachali7581
@noelkachali7581 3 ай бұрын
Take back your words
@HarmonyChisuse-i2p
@HarmonyChisuse-i2p 3 ай бұрын
Tili mu nyengo yong'alura bas ,ing'alulidwe🔥🔥🔥🔥🔥😛😛🔥😛
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 3 ай бұрын
Mr DC agogo anga ati akufuna akupaseni n ,gombe chifukwa ndinu Muthu olimba mtima
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 3 ай бұрын
Apaseni basi
@ChrissySalimu
@ChrissySalimu 3 ай бұрын
Makwana bwana DC matiimilila anthu osaukafe
@EstherChirwa-s2e
@EstherChirwa-s2e 3 ай бұрын
MCP chipani cha kupha chamagazi ...... Kodi a chakwela analidi Abusa????
@BerthaMkwinika-e7s
@BerthaMkwinika-e7s 3 ай бұрын
Bon kalindo pachilichonse chomwe umapanga umalakhula sungapindule kanthu kalikonse
@GreciumMsiska-cz2et
@GreciumMsiska-cz2et 3 ай бұрын
You are definition of a real man
@HusseinAbdullah-l4u
@HusseinAbdullah-l4u 3 ай бұрын
From south Africa great words
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 3 ай бұрын
Power a DC
@yalinhlema
@yalinhlema 3 ай бұрын
This mission must not die in VPs Voice😢
@UmaliDickson
@UmaliDickson 3 ай бұрын
awa ndachotsiru ngati kuli kufuna kuti apange mbiri mudziko yankhanani zina ndikuchokela ku south Africa Port Elizabeth p e
@aggiemlotha1208
@aggiemlotha1208 3 ай бұрын
Manganya maguy .... dzina liziyamba ndi title Dr, professor etc ... ine i choose to listen from people whose their name starts with Dr, or Prof 🎉..... enawa mbola
@BeatriceRobert-jq6ci
@BeatriceRobert-jq6ci 3 ай бұрын
Koma anawaputsitsa ndani koma nde asewera yachabe aaaa mpaka zawo moyo kupita ndinthu mmmmm Mr DC mwayakhula chilungamo
@AlliUsuman-mj1mr
@AlliUsuman-mj1mr 3 ай бұрын
Nanga ndichifukwa chani mu ndege muja munalibe aliyense wa MCP
@DjFiquickTech
@DjFiquickTech 3 ай бұрын
If have knowledge Mr . Bon come with the trueth. Zongosokosa mwayamba kale , we had people like Kamulepo, Chekufwa Chihana, .Koma inuyo mungosokosa apa .come to International court of of justice to assist Malawians. You are now coming up with confusion and you are not president of Malawians.
@FortunePhiri-kl7oe
@FortunePhiri-kl7oe 3 ай бұрын
Fuseck wena
@sopaniisrael5240
@sopaniisrael5240 3 ай бұрын
Kalindo wakhuta thelele
@CatherineDesire
@CatherineDesire 3 ай бұрын
Mnalibeso wa MCP mu ndege muja why?
@yalinhlema
@yalinhlema 3 ай бұрын
Akudziwana
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 3 ай бұрын
Choyamba amange aja anaphwanya magalimoto aanthu a DPP aja , bwanji anthu ameneaja sanamangidwe mpakana pano, koma anthu aku Ntcheu anamangidwa same day, zompusa ,dzikoli silawo lokhatu
@OrtoniMware
@OrtoniMware 3 ай бұрын
Mumakwana boss
@DarwinBobot
@DarwinBobot 3 ай бұрын
OSAOPA OSAFOOKA DZIKO NDI LATHU .MCP MA CRIMINALS
@MosesKalenge
@MosesKalenge 2 ай бұрын
Good news Dc🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@BlessingMkonda
@BlessingMkonda 3 ай бұрын
Ambuye azikudaritsani mumatirimirira
@SaukaniMbiliyawanda-ur7zb
@SaukaniMbiliyawanda-ur7zb 3 ай бұрын
Iwe mesa ukumenyera nkhondo DPP ukanalila 2025 ulila kachikena
@QueenMsowoya
@QueenMsowoya 3 ай бұрын
Dangerous child has spoken 😂😂😂😂
@JacobBanda-s1f
@JacobBanda-s1f 3 ай бұрын
Mukufuna maudindo chabe inu,tiyeni uko.
@BlessingsKandulu
@BlessingsKandulu 3 ай бұрын
tamudulani mutu chakwera kumeneko amalawi plz
@Patricenkhoma09Tricia
@Patricenkhoma09Tricia 3 ай бұрын
Step down babylon your old by evison matafale
@RACHEALKanyenda-b8f
@RACHEALKanyenda-b8f 3 ай бұрын
Ulemu kwa DC
@Grevulo
@Grevulo 3 ай бұрын
Kumwamba kukhale Nanu a kalindo keep on speake the truth
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 3 ай бұрын
Manyazi akuwagwira mene anachitira anthu aku ntcheu anawakhaulitsa a masewera ndi angoni awaliza tu koma angoni
@JamesStanford-my1zj
@JamesStanford-my1zj 3 ай бұрын
😅
@HuaweiIdentity-kt2kd
@HuaweiIdentity-kt2kd 3 ай бұрын
Auzeni osawabisila
@IssahTchakato
@IssahTchakato 3 ай бұрын
Perfect boss
@MbalasoJustin
@MbalasoJustin 3 ай бұрын
Ndiye kuyankhulatu kumeneko mwauze
@CarolynMtegha
@CarolynMtegha 3 ай бұрын
I concur with you Bon,I was bored with kasakura and Mvula since they are the same people who were doing cheap propaganda on times TV.... Please citizens of Malawi what kalindo has said is very right be neutral coz it will follow u
@paulinekayuni1621
@paulinekayuni1621 3 ай бұрын
Zoona akumalankhula ngati a Malawi ndi mbuli saganiza. Ayenera kuziwa kuti anapangitsa okha a Malawi kukwiya mene anapangira handle
@franciskapakasa36
@franciskapakasa36 3 ай бұрын
KALINDO IS JUST ANOTHER OPPORTUNISTIC
@frankjolijo
@frankjolijo 3 ай бұрын
Kwa inutu😅😃😃😃😃😃
@AlinafeMaunda
@AlinafeMaunda 3 ай бұрын
Tapitan uko inu
@FortunePhiri-kl7oe
@FortunePhiri-kl7oe 3 ай бұрын
Mfundoless
@jamesgama5489
@jamesgama5489 3 ай бұрын
Or mabanjatu akutha chifukwa cha imfa ya chilima
@SimeonNkhata-gc8bf
@SimeonNkhata-gc8bf 3 ай бұрын
Niuzeniko bro
@jamesgama5489
@jamesgama5489 3 ай бұрын
@@SimeonNkhata-gc8bf bro umaziwa kungoyipasa motto basi
@SimeonNkhata-gc8bf
@SimeonNkhata-gc8bf 3 ай бұрын
Kkkkkkk okay ndakumvani bro
@SimeonNkhata-gc8bf
@SimeonNkhata-gc8bf 3 ай бұрын
Komano kalindo nikatundu omanga nimawaya
@MichaelChaima-v7k
@MichaelChaima-v7k 3 ай бұрын
Mwana oooopsaah kwambiri from Njeza vg bx 76
@ElizaJoseph-q9w
@ElizaJoseph-q9w 3 ай бұрын
Ulemu wanu akalindo mumatimilira osaopa ayi mcp yathapo bs
@franklychiundah4812
@franklychiundah4812 3 ай бұрын
Zikuonetsaso kuti even iyeyu alibe umboni
@JosephyNgamwani
@JosephyNgamwani 3 ай бұрын
Ndipo zinthu zake sindikuzimvesa kut boma ra mcp limaganiza bwanji panthawiyo osapanga zinthu mwachangu ndizoonad kut inar taget
@SamsonChavula
@SamsonChavula 3 ай бұрын
Tilibe lawyer ife
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 3 ай бұрын
Koma ndiye takwiya kukwiya,moti Wanthu sakukwanisa kugona Ndipo kunkuyuu Lero akuyankhula,koma zikaza mufikira azalira ngati Nkhumba, Chakwera ndi gulu láke azaona tsiku Lina apha Wanthu, koma nthawi ina Yehova mwini azati pasira ngati m'mene adamu perekera Goliath m'manja mwa David.amenewo akuti agula zida zankhondo koma tsiku Lina tizazi tenga ndifenso Ana obadwira komweko
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 3 ай бұрын
inu ndi amfumu. kunkuyu akulankhula Mo pusa kwambili. anthu amenewa atikwana
@jonas-xh4hz
@jonas-xh4hz 3 ай бұрын
mumakwanira atsogo
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 ай бұрын
Dccccc machine our president wa amphawi
@PatrickMailos
@PatrickMailos 3 ай бұрын
Pheeeee kumastand kumvera bon kalindo 💪 the DC
@josephlukhele-v5c
@josephlukhele-v5c 3 ай бұрын
We are Desperate country indeed , anthu ngati DC can not unit Malawians. Supporting you is wasting time. Surely there is no sense padzimene mukukamba. Back to DPP IYAAAA
@MaureenMollen
@MaureenMollen 3 ай бұрын
The great man Bon kalindo❤❤
@EstherBonga
@EstherBonga 3 ай бұрын
Umatiimiliza DC
@NescotNyamwela
@NescotNyamwela 3 ай бұрын
Boma lose la mcp nkhuku za anthu.
@innocentsathasteven4093
@innocentsathasteven4093 3 ай бұрын
THE DC TELL DEM THE TRUTH MAYBE THEY'RE DON'T KNOW ENETHING AT ALL APHUZITSENI CHILUNGAMO NDI MWANOTU PAJA
@George-e6h
@George-e6h 3 ай бұрын
Inu nzeru mulibemo even kuti iwine DPP akakumanani udindo mutukwanaso. UTM munainyozaso. Bwererani ku uphunzitsi.
@ElizahMadi
@ElizahMadi 3 ай бұрын
Salute Mr DC
@MarthaMartha-rw4zz
@MarthaMartha-rw4zz 3 ай бұрын
Akatero nde kuti mbc wo apasidwa ndalama koma ayaruka nawoso amenewa akuona ngt athu akugona et😢
@JamesStanford-my1zj
@JamesStanford-my1zj 3 ай бұрын
Eti
@SophieKamanga
@SophieKamanga 3 ай бұрын
Welcom back DC
@JamesStanford-my1zj
@JamesStanford-my1zj 3 ай бұрын
Uyu Ndie sanyengelera
@JabessKamatuwa
@JabessKamatuwa 3 ай бұрын
Anthu ake atiwo anthu safa pangozi ,tiyeninazo uko,anthu apandenge,amapangira ngozi pandege,pagalimoto amapanga ngozi pagalimoto,apanyanja amapangira ngozi panyanja.panjinga yamoto amapanga ngozi panjinga yamoto.mulungu akati lero silidutsa oro utakabisala kuphanga iwe umapita ndithu,zokulazo umuwuze peter.nkhondo yake iti bambo asikono nhkondo mumayidziwa kapena mukunena yamumkanema.
@PatrickChiromo-qq7xy
@PatrickChiromo-qq7xy 3 ай бұрын
Mawu mawu bwana DC,,,athu awa abomawa atikwana ife,Chakwera akudzikumbira dzenje lokuya kwambiri koma wagontha makutu
@NellieMcjepher
@NellieMcjepher 3 ай бұрын
Namandege
@RaphaelKatimba
@RaphaelKatimba 3 ай бұрын
Simbi sakuyenela kusankhidwa kuti akhale vice president ai. chifukwa nayenso akukhudzidwa pangozi imeneyi. ndipo ndizoona zokha zokha.
@EdwardChiwaula-g5j
@EdwardChiwaula-g5j 3 ай бұрын
Wakhuta thelere ndiwe wakumudziwe iwe ife sitimalidziwa kkkk kwerani ndege mupite ku south osatuma munthu isaaaa
@CollenChapenda
@CollenChapenda 3 ай бұрын
Nthawi yong'aluradi eeee kkkkk
@japhetbanda-b4i
@japhetbanda-b4i 3 ай бұрын
May the Lord guide during this difficult time
@McDonaldNtchirah-bz6do
@McDonaldNtchirah-bz6do 3 ай бұрын
We follow you King big up
@FrankJumah-jc8mf
@FrankJumah-jc8mf 3 ай бұрын
God blesss u born k
@williamalvis6028
@williamalvis6028 3 ай бұрын
The DC
@AlexMduladulaMafuleka
@AlexMduladulaMafuleka 3 ай бұрын
Tamanenaniso za anzanu a Manganya kaya nanga daily MCP koma simukunenapo bwanji za m'bale wanuyi
@innobashirbernard7853
@innobashirbernard7853 3 ай бұрын
Big up our brother Bon kalindo
@wishesnsunza3823
@wishesnsunza3823 3 ай бұрын
Wise and courageous words
@LeadChanza
@LeadChanza 3 ай бұрын
Amalavi ndiwokhwiya zedi kwambiri ndi inu aBon kalindo chifukwa ndinu wodziwika kuti ndi wodzindikira koma mukungoyankhulira kwanu,mukutipusisa kasumen/panseu basi osatikutipasa zochita ife amafoni basi
@LeonardEnock-e1t
@LeonardEnock-e1t 3 ай бұрын
Akut tiku user bundle yontchipa mmmm ndinazimvera chisoni 2000 bundle yikuntchipa munthu wopusa kwambiri moses kunkuyu shame on
@jameschimbe2059
@jameschimbe2059 3 ай бұрын
DC has spoken 😂
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 ай бұрын
MBAMBANDE DC ASUKULUZE AGALU AWA SAMAMVA IYAAAA NDIPO 21 DAYS IKATHA TIKUFUNA MA DEMO MCP ICHOKE
@JamesChipande
@JamesChipande 3 ай бұрын
Kod ifeyo tiziopa kulolibe kuopa tose nda Malawi nde atimage tose ndiyeka
@RaphaelVivia
@RaphaelVivia 3 ай бұрын
umatiimirila bon
@hiramsibande9395
@hiramsibande9395 3 ай бұрын
Namandege wayamba kuopa kukwera ndege😂😂.. tamakweranitu
@RashidSaid-lk6bb
@RashidSaid-lk6bb 3 ай бұрын
Audze anthu osaphunzirao ndi president chakwera ndipo anthu akugwira ntchito ku Malawi board casting co-operation 2025 ena ntchito izawathera
@NasonBanda-mr1xk
@NasonBanda-mr1xk 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 km DC kkkkkk nde mwati achakwera sakufunaso kukwera ndege hahahahaha
@PatriciaTembo-sz9tw
@PatriciaTembo-sz9tw 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@SimeonSanex-vw4py
@SimeonSanex-vw4py 3 ай бұрын
Chakwera ndege yayamba kumupasa manthaaaa🤣🤣🤣
@gracekwapata
@gracekwapata 3 ай бұрын
The DC💥💥kuswa kuswa basi. osaopa, osatopa komanso osafooka
@InnocentMmanga
@InnocentMmanga 3 ай бұрын
😂😂😂😂
@LexaShaba-sc3iq
@LexaShaba-sc3iq 3 ай бұрын
Pp PPPleaseĺ
@MosesKalenge
@MosesKalenge 2 ай бұрын
Motoo kut 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤
@irenioeugeniosumila6647
@irenioeugeniosumila6647 3 ай бұрын
Zikatchitika tikuvenla Kwa inu a kalendo, mumatihimilila Ifé ovutika
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 3 ай бұрын
Mr DC Muthu olimba mtima kwambili
@BeatriceRobert-jq6ci
@BeatriceRobert-jq6ci 3 ай бұрын
Ndipo inu eti 10am mpaka 5 vice president ngati munthu wamba mmmm ife timadalira kuti chaka chamawa tiona kusitha
@George-e6h
@George-e6h 3 ай бұрын
Za ziiiiiiiiiii
@JabessKamatuwa
@JabessKamatuwa 3 ай бұрын
Wowopwa sadzichemelera,azkoso amkatero anazima ndiana
@RaheemMogoya
@RaheemMogoya 3 ай бұрын
Ndichifukwa sitimavela mbc yamanyi amayakhula mwausilu za ziiiiiii
KUNG'ALULA MOSAONA NKHOPE_BON KALINDO
16:59
HOT 265
Рет қаралды 41 М.
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Senior Prophet Rodrick Mtupa SC
Рет қаралды 39 М.
Do you choose Inside Out 2 or The Amazing World of Gumball? 🤔
00:19
Running With Bigger And Bigger Lunchlys
00:18
MrBeast
Рет қаралды 98 МЛН
BON KALINDO AMAFUNA KUPHEDWA KU PARLIAMENT
38:53
TIDZIWE TV
Рет қаралды 69 М.
Rev Alexander Kambiri  Odala Akufa Mwambuye
19:05
mabena Studio channel
Рет қаралды 212 М.
CHILIBE MANTHA ICHI!
15:35
Shamsdeen Chikwakwa TV
Рет қаралды 535
KWAPHULIKA AUDIO YACHILIMA MU NDEGE ISANAGWE. TAMVANI
10:45
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 415 М.
Zomwe Wakamba Lero Bon Kalindo | Nzeru Zilimo Umu
16:16
Mukuziwa?
Рет қаралды 10 М.
KOMA KULI KUTHA MAU UKU 🔥🔥🔥21 September 2024
18:46
TAMVANI ZA IMFA YA CHILIMA IJA
10:10
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 255 М.
Timothy Mtambo ndi okonzeka kugwira ntchito ndi DPP 2025.
8:19
Human Rights Consultants TV
Рет қаралды 22 М.
MAYI WINA WAGONANASO NDI DOCTOR WA PRESIDENT KU STATE HOUSE
17:36