ZOMWE WAYANKHULA BON KALINDO LERO PA 2021 JULY SINDINGALANDIRE NDALAMA ZANU ZOKUBAZO

  Рет қаралды 30,176

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 78
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 2 ай бұрын
Kkkk mzimu.wa a chilima wayamba kuwaopsyeza a chakwerawo ..ndipo chilima awabwezera ..aphedwa chakwera ndi mzimu wa a chilima..kuyenda yendako.akusowa mtendere.
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu 2 ай бұрын
Ndipo the way I feel pain pano,mmene akuwanamidzila anthu pano,kumawombela manja ndithu hhhiii Malawi amayiwala,vuto ndife okomedwa
@NifuDagas
@NifuDagas 2 ай бұрын
Mumatiyimilila Mulungu azikudalisani❤
@AsiyatuAkila
@AsiyatuAkila 2 ай бұрын
I love you DC tikuyenela kt tisambe abale
@HalimaShafie-o7g
@HalimaShafie-o7g 2 ай бұрын
❤❤❤❤ mr bon kalindo
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 ай бұрын
The Dc bon kalindo good Messnge ❤
@AdiniKhama
@AdiniKhama 2 ай бұрын
We're together born kalindo don't give up
@xinalungu9616
@xinalungu9616 2 ай бұрын
Opengawa sitingachite kuwasate ayi. Munthu okhala ndi nsapato ina yoyela ina yakuda ndi wa madrama basi
@vitumbikokamanga5869
@vitumbikokamanga5869 2 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤Timakudalilani bon kalindo
@GiftrichardRichard-re1co
@GiftrichardRichard-re1co 2 ай бұрын
Chonde abon karindo musatisiye tokha muthawiyi ndinu wathuwathu
@chikumpilisi1416
@chikumpilisi1416 2 ай бұрын
Umakwana❤
@ThandoKunene-j9u
@ThandoKunene-j9u 2 ай бұрын
Ndinu nokha Mr DC mumatiimilira
@dytonmoyo4629
@dytonmoyo4629 2 ай бұрын
❤❤❤❤
@JafaliChiwimbi
@JafaliChiwimbi 2 ай бұрын
Chilungamo chayamba kwapeza ndawi yokuthayita
@YusufChipojola
@YusufChipojola 2 ай бұрын
We love you kalindo
@MphatsoMwanyowa
@MphatsoMwanyowa 2 ай бұрын
Kkkk DC sumaopa eeeee wamung'alura chakwela koopsa
@PhilipMatolino
@PhilipMatolino 2 ай бұрын
Kkkk....yomweyo! chikangawa
@Amgwagwa
@Amgwagwa 2 ай бұрын
Abwere andithandize kuumba njerwa
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 ай бұрын
I support The DCs mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi chilungamo chiyende ngat madzi.
@HanishKenneth
@HanishKenneth 2 ай бұрын
😂😂 mangochi sitipanga nao zachibwana
@BrianSanuwedi
@BrianSanuwedi 2 ай бұрын
Umatha born kalindo
@GladMarawaMsowoya
@GladMarawaMsowoya 2 ай бұрын
😂😂 President wathu wathu Mr DC
@DavieMuziwo
@DavieMuziwo 2 ай бұрын
Best DC
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 2 ай бұрын
Kkkk koma Born kalindo chitseko champana Chala
@lovemorenaluso8965
@lovemorenaluso8965 2 ай бұрын
The DC🔥🔥
@TrinityBonjesi
@TrinityBonjesi 2 ай бұрын
Umayakhura Za nzeru kwambil
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 2 ай бұрын
Ndipo aboni chonde musatisiye ife tokha masiku atha kare awa muzapange chipani chanu tizakuvoterani
@MateusEliasluciano
@MateusEliasluciano 2 ай бұрын
Kodi kupeleka mphatso ndivuto Kodi? Malume vutolanu ndilotani?
@KondwanipascalMalembo
@KondwanipascalMalembo 2 ай бұрын
Bwana mumachulutsa intro kwambiri
@Maxcarcare-g1d
@Maxcarcare-g1d 2 ай бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥
@MatressKanyenga-f1z
@MatressKanyenga-f1z 2 ай бұрын
The dc 😂😂😂mwana wachabe kwambili 😅
@FGSKimberley
@FGSKimberley 2 ай бұрын
Osaopa namachende ameneyi osavotelaso
@GregoryMatambo
@GregoryMatambo 2 ай бұрын
Kodi simunatopebe ankolo
@ManesChaphuka
@ManesChaphuka 2 ай бұрын
Big up winiko
@JamesichochowhiteWhite
@JamesichochowhiteWhite 2 ай бұрын
Koma mwini page iwe kuyika mau it that form bwa j?
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 2 ай бұрын
Osagulisa mwadzi wachilima
@KondwanipascalMalembo
@KondwanipascalMalembo 2 ай бұрын
Be straight to the point nginiyi bwana imafunika data
@KondwaniNguleti-x1q
@KondwaniNguleti-x1q 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 Ine kudabwa ndinali kumsika ku Blantyre ndimagulitsa boiled eggs ndinangomva Manganya ati iwe! Ulembane ndi a Mazira anzako ndikupatseni ndalama ine kudabwatu ndati eee izi zayambanso liti kkkkkk
@OnenessLestas
@OnenessLestas 2 ай бұрын
Sanje yakuvutani
@ChizymanJason
@ChizymanJason 2 ай бұрын
Tiye nazo Kalindo 😂
@Jerry-vm6mo
@Jerry-vm6mo 2 ай бұрын
Malawi nde mwapenga Kodi president amayenda daily watch out
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
Ndipo mulungu atichitile chifundo dziko la Malawi ndipo MCP yatikhazika ngati dzikoli su lathu ngati tachita kubwela. Ambuye atithandize
@yohanenene
@yohanenene 2 ай бұрын
DC ati ndine wa nyape😂😂😂😂
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg 2 ай бұрын
Kkkkkkkkkk Kkkkkkkkkk Kuchikangawa kwavuta
@PatrickLikole
@PatrickLikole 2 ай бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥✈️✈️✈️
@DymondMasala-fo4vm
@DymondMasala-fo4vm 2 ай бұрын
Umakwana
@CarolineSululu
@CarolineSululu 2 ай бұрын
Kkkkk the DC 😂😂😂
@clivemhango6183
@clivemhango6183 2 ай бұрын
Ziyenda ndiweyo kalindo?
@masterkachingwe7448
@masterkachingwe7448 2 ай бұрын
Kuswa kuswa sankiyu DC
@LysonMkomadzinja
@LysonMkomadzinja 2 ай бұрын
DC mbambande
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Boza ndiye likupwetekani
@SafariBvumbwe
@SafariBvumbwe 2 ай бұрын
Mmmmmm inuso kod tiziti iweyo sukuwona
@NerieMkandawire-y3x
@NerieMkandawire-y3x 2 ай бұрын
Tarira kwanthawi yayitari zooona
@MauriceTayali
@MauriceTayali 2 ай бұрын
The DC number one
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 ай бұрын
Koma Peter Mutharika akakwela pa mpando,,asiye sakho akonde Malawian,, chifukwa akadzapanga ngati za chakwela tidzakutchotsa
@WalesAkazianyenga
@WalesAkazianyenga 2 ай бұрын
Kkkkk asiya bwanji ngati dziko amalamula ndiye Mmesa tinkalamulidwa ndi Chisale the bodyguard
@HalimaShafie-o7g
@HalimaShafie-o7g 2 ай бұрын
Chakwera machende anu
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Kalindo upenga ndiwe ndi chamba chako komaso nsanje
@AgnessMatchado
@AgnessMatchado 2 ай бұрын
Upenga ndiwe ndi chakwera wakoyo
@AngozoMalunga
@AngozoMalunga 2 ай бұрын
Mbambande the dc
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 ай бұрын
Malawi Chikangawa Party=MCP=Ufiti
@MassahSym
@MassahSym 2 ай бұрын
The D C !!!!!!!!!😂
@GiftrichardRichard-re1co
@GiftrichardRichard-re1co 2 ай бұрын
😂😂😂
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 2 ай бұрын
❤❤❤❤😂😂
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 2 ай бұрын
Ufune usafune ndi president wako ndi wangaso or APM president wake ndi chakwera basi nsanje ikupwetekani mufa ndi mtima ndipo sadzawina APM mudzaphulika abwerera ku America 😅😅😅😅
@MphatsoMwanyowa
@MphatsoMwanyowa 2 ай бұрын
Panyero pamako wamva,mkongo wamako
@HannahNtenda
@HannahNtenda 2 ай бұрын
Kufuna kutchuka kucomenta kawiri ukusowa zochita😂😂😂
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 2 ай бұрын
@@HannahNtenda if you don't know how to comment be silent mbuli iwe ndi opposition yanuyo
@FanizoKawindula
@FanizoKawindula 2 ай бұрын
Choka mbuzi ya munthu iwe
@chilingachilinga6059
@chilingachilinga6059 2 ай бұрын
Km awa iyayi zikomo
@preciousNtonya
@preciousNtonya 2 ай бұрын
Mizimu yakwiya mutu sukugwira
@SifatiMoses
@SifatiMoses 2 ай бұрын
Siziru za anthu boma lonse langozaza ndi mbava, palibe olo ndi modzi yemwe angavotere MCP, ndalamazo adyereni koma osakavotera 🐔 🐔🐔
@LinosLangishon
@LinosLangishon 2 ай бұрын
Kkkk the DC
@GiboTakondwa
@GiboTakondwa 2 ай бұрын
iiiiii olo ine ndinali odabwa anthu mpaka kukanganilana ndalama chonchija pa ground ine ndinkaona Ngati payambikanso masewelo ampila Koma eti anthu kunali kukanganilana ndalama
@giftedmshan6779
@giftedmshan6779 2 ай бұрын
Anali kuti nthawi yoseyi
@ClydeNyasulu-tk6fj
@ClydeNyasulu-tk6fj 2 ай бұрын
❤❤
@MercyMfune-dc3rq
@MercyMfune-dc3rq 2 ай бұрын
😂😂😂
World‘s Strongest Man VS Apple
01:00
Browney
Рет қаралды 48 МЛН
🕊️Valera🕊️
00:34
DO$HIK
Рет қаралды 4,2 МЛН
ДЕНЬ УЧИТЕЛЯ В ШКОЛЕ
01:00
SIDELNIKOVVV
Рет қаралды 3,9 МЛН
когда не обедаешь в школе // EVA mash
00:51
EVA mash
Рет қаралды 4,4 МЛН
Zimbabwe Vs Namibia Highlights (3-1) 2025 AFCON QUALIFIERS
8:18
A TANGLE OF TRUTHS DNA DOCUMENTARY: TINASHE MUGABE DNA SHOW #tinashemugabe #dnaman
1:04:25
Știrile PRO TV - 13 Octombrie 2024
26:43
Știrile ProTV
Рет қаралды 63 М.
Democratic Alliance updates on the 100 days in government
1:06:01
Akweza cement ndi mafuta ophikira kuti apeze ndalama za campaign
9:31
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 40 М.
World‘s Strongest Man VS Apple
01:00
Browney
Рет қаралды 48 МЛН