ZOTSATIRA ZA MA VOTE A CONVENTION YA PEOPLES PARTY ZATULUKA NDIPO AWA NDIWOMWE APAMBANA PA MA UDINDO

  Рет қаралды 13,824

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 28
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 8 күн бұрын
My Vote UTM woyeeeeeeee UTM Moto 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@GroupFortyfour
@GroupFortyfour 9 күн бұрын
Awawa ayimwena smart 🎉🎉🎉🎉 against all odds 🎉🎉🎉iyiyi amayiti nkhondo ya pansi😅😅😅
@Malawian-q5f
@Malawian-q5f 8 күн бұрын
Zopanda chikoka, ndakanika kumalidzitsa😂
@DanielChiwawula
@DanielChiwawula 8 күн бұрын
Machine machine ndi Mr chivunde munthu wachisoni uyu
@user-wd5tw1mz8h
@user-wd5tw1mz8h 8 күн бұрын
PP VS chikangawa akufuna atigulise, nankhumwa. JB chakwela ndichipan chimozi
@AndrewChirombo
@AndrewChirombo 8 күн бұрын
Olengeza ma vote woo mmmm akuoneka ngati samasambatu 😂😂😂😂
@KinziWindasoni-h4b
@KinziWindasoni-h4b 6 күн бұрын
Chipongwe
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 8 күн бұрын
Za masanje izi😂😂😂😂😂
@user-wd5tw1mz8h
@user-wd5tw1mz8h 8 күн бұрын
Pangani zonsezo koma tikumana 25 dpp my vote Jb ndiwa mcp anagulidwa kale
@JoycieMbaya
@JoycieMbaya 9 күн бұрын
Positions which went unopposed, Pali chifukwa chovinira?
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e 9 күн бұрын
Zazii chovira nchani pamenepo ngat apambana😂😂
@user-wd5tw1mz8h
@user-wd5tw1mz8h 8 күн бұрын
Anagulisa ndegeyathu uyu galu wamunthu jb dpp my vote
@SamuLameck
@SamuLameck 6 күн бұрын
Kutukwana siudolo atakhala amayako akutukwanidwa ungave bwanji kupusa
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 8 күн бұрын
joice sungawine iwe unaba ndlama zambiri mkuthawira kunja nyani iwe wadzabweranso ukufuna chani
@hardworkkayuza6353
@hardworkkayuza6353 9 күн бұрын
Zopanda chkoka pp vomerezan munatha
@Nadeon-y2k
@Nadeon-y2k 8 күн бұрын
Adachotsa chidwi cha a Malawi awa cashgate idapweteketsa dziko imene ija
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 8 күн бұрын
Mayi uyu ndi crook muzazindikira bwino asogolo
@GroupFortyfour
@GroupFortyfour 9 күн бұрын
Tonsefe tilipo chifukwa Amayi Anthu 🎉🎉🎉🎉🎉Ndi Munthu yekhayo Amaganizira Ana ake...Iwowotu anachita kukhomeleledwa 😅😅😅😅😅😅 Chifukwa cha luntha lawo 😂😂😂😂😂
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 9 күн бұрын
Kodi olengezawo ameta stayilo yanji?😂😂😂
@lifredchikumba420
@lifredchikumba420 9 күн бұрын
Democracy's
@SoftChampion
@SoftChampion 9 күн бұрын
Ubwino wa Democrancy umasankha chipani chomwe chimakufikapo nde tiyeni tisawanyoze
@kondwanlackson8319
@kondwanlackson8319 9 күн бұрын
Kkkkkkk palibe nsisi
@JahmarleyMilanzi
@JahmarleyMilanzi 9 күн бұрын
Null and avoid akuchukuka kwambiri cfk chani akuluakulu poti nose ndinu ophunzira nokha nokha
@JoycieMbaya
@JoycieMbaya 9 күн бұрын
Kodi ma position onse were not contested?
@GroupFortyfour
@GroupFortyfour 9 күн бұрын
So unique 😅😅😅
@DeborahHetekere
@DeborahHetekere 9 күн бұрын
Zipanibe zonena kt tsogolo zilibe enewe congratulations
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 9 күн бұрын
All political parties whose founders and political leaders have won or retained their positions are not democratic .
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 7 күн бұрын
Mukamati Jb anaba ndalama zidayamba ndi Kamuzu ndi mcp yake kuba ndalama zimene malawi palipose ikanakhala town koma anaba kumakabisa kunja ku Barclay's Bank Mk 3.Trillion,,,,ndalama zankhani nkhani nkhaza kwa Amalawi ambili anaphedwa ku ng'ona ena kunyongedwa ma khadi kufuna osafuna,,,school primary kunalibe zipatala zaulele kunalibe bwanji lelo anthu anayivotelaso mcp?? Palibe wandale angabwele wabwino never osewa ndimbanva ndiye osamatchula munthu ngati kuti iyeyo ndiye oyamba kukhala president ayi mcp ikulamulilaso pano bwanji,,mbilizake aliyese amkadziwatu koma anayivotelaso
Road from hell | Carte Blanche | M-Net
12:59
Carte Blanche
Рет қаралды 7 М.
Остановили аттракцион из-за дочки!
00:42
Victoria Portfolio
Рет қаралды 2,7 МЛН
Фейковый воришка 😂
00:51
КАРЕНА МАКАРЕНА
Рет қаралды 7 МЛН
FREDO MASINTHA
12:07
Fredokiss
Рет қаралды 21 М.
KUSEMPHANITSA KWA ZIZIMBA, ZOMWE ZINAPHETSA SAULOS CHILIMA 🤯😭
35:46