GOD should keep on strengthening ,protecting and guiding you brother " phillipians 4: 13" keep on saving lives.
@BornfaceMteghko15 сағат бұрын
Zooona, ndinaonadi even driver wa min bus anandithandiza zinthu zitativuta anthuwadi ali ndi umunthu
@BiziweckThumpwa19 сағат бұрын
Pena anthu inu mukamaika mutu wa nkhani yanu mukumawonjezapo kaboza, nanga mukuti zoopsa zimakumana ndi driver wa ambulance, pali choopsa chanji mu video imeneyi?
@euwarttawakali432017 сағат бұрын
Ndipo inu... Ine ndili ndimvere zoopsazo kudabwa anthu akungoseketsana
@LASTIZSAUTI16 сағат бұрын
Ndipo inu xachambatu nane ndati ndinvele zazii
@Momweekly23 сағат бұрын
Thats not speed 120
@Momweekly23 сағат бұрын
Vuto driver wa ambulance ku Malawi sanaphunzire za chipatala.😂 They are just ordinary drivers that must change
@ChpCosmass22 сағат бұрын
Mmmmm ok km???
@SulaimanaRajab22 сағат бұрын
@@MomweeklyKu Malawi ndi speed malingana ndi mitsewu Mene yilili