Ineee ndinkadziwa zonsezi kale kuti MCP inkafuna kuipitsa Mbiri ya DPP pomapha albino Kuti aziti ndibDPP koma inali MCP yomwe inkapha albino. Izi ndinkadziwa
@augustinechibbalazi889721 күн бұрын
My fellow,Malawians both MCP and DPP have the records of massacre.During MCP regime many died.During DPP twenty northerners were butchered(killed) live in Mzuzu.Which of the two is better party in Malawi ?
@AaronMsewezi19 күн бұрын
Uzayankha bodza lako ili pa tsiku la chiweruzo , ndiye iwe kufuna kwako ndikoti dpp iwine , walephera kale dpp iwe ,
Mutayimika apo Chakwera penapo Peter Muthalika ndikumuuza mwana aliyense kuti pankhope ukuona apazi talozera angamaphe ma Albino ndi ndani? Inu mukuganiza mwanayo angaloze ndani? Your guess is as good as mine
Komadi mcp ndiyoipa ndye bambo wa sikono amafuna usongoleli koma akulemphelaso
@IpianaNdovie16 күн бұрын
Za mabodza izi
@AaronMsewezi19 күн бұрын
Inu DPP si chipani chamyaya, chifukwa chani mukukakamira zinthu zopanda pake , so ndiye kuti Chilimayo munapha ndinu a DPP ,
@MfipaKapwera19 күн бұрын
Wuyahlanya wene.
@InnocentMtafya-c6b18 күн бұрын
Inenso ndadabwa nayetu nde kuti naonso akubwezera kuononga mbiri ya MCP,nde kuti ngozi ya ndege anachititsa ndi iwowo ? ignorance has no defense indeed....