Akulu nonse pa Times Tv timakunyadirani pa ntchito yabwino yomwe mmagwira kumeneko mtundu wa a Malawi,Bishop Nsusa anayankhula kwa a khristu a mpingo wawo mopwetekedwa mtima chifukwa SKC anali Nkhosa imodzi ya mpingo wawo.
Ndiye zija zochititsa chidwi ngati someone who can sell ice cubes in the eskimo or Atlantic icy regions. It's like someone coming from the house with a filled pale water to throw it inside the sea or any lake or oceans. Even a mad person can't do that.
@JubaSamb-v8s7 күн бұрын
Chimanga adagawa miyezi iwiri yokha kwinako zalowa political gimic
@liliantamaona16697 күн бұрын
😅😅, azibusa ojiya
@SarahBanda-x7k7 күн бұрын
Anawatuma ndani koma mmmm mukunyozesa mulung
@MarySinjirani7 күн бұрын
Kodi Democracy imene tinalandila ku Malawi ndiye kuti ndiyo siyana ndi yamaiko anzathu nanga ku Malawi bwanji..?