Timanyadila poyenela kunyadila timanva chisoni poyenela kumva chisoni, Chakwera siomvela chisoni ai akafike ndipo mzimu wake sunglasses muntendele
@RatifaGrasiyano7 сағат бұрын
Chikangawa kumenya kugwesa eeeee 😂😂😂😂😂😂😅😅
@MartinKapito6 сағат бұрын
Kumenua kugwetsa
@TressLuka7 сағат бұрын
Wafwaaaaaa basi. Nakafike Pelezebuluu 😎😎🇲🇼
@blackcobra-b2y7 сағат бұрын
Inu zitsilu ndi aja mumatukwa Dan Lu kungodziwila zimawu,akapolo inu nokha mukuti muli kwa America komaso nthawi yomweyoso mukuti muli ku South Africa, Kkkkkkk!!!!
@MercySaidi-h6n3 сағат бұрын
Ngati zilizoona ndukuuzani ine mulungu amene analenga iwe ndi ine ,,dziko lapansi lino ndi zonse zomwe zilimo ,,mvula ,,mwezi ,,nyenyezi ndi dzuwa ,Tizimuopa chifukwa ndioophya kwambiri
Chikangawa yenda bwino paurendo wako umawona ngat moyo amagura ndi ndindarama kkkkkk abusa awo kayenkheni mafuso bas chifukwa akuru inu nde mwachita zinthu kuziko kuno my god is good or the time azati menyera nkhondo ife tiri chete amen yehova tiwoneko zina
@RejoiceMollande7 сағат бұрын
We thank God for the revenge
@CHIKOPABC4 сағат бұрын
May SKC's soul RIP
@Stretor7 сағат бұрын
Ngakhale kufunira nzako kulowa manda ndi tchimo koma na apa pokha bola zikhale zoona munthu yu watizunsa kwambili
@SimonKazizwa5 минут бұрын
Ngangaaaa 😂😂😂😂😂
@RobertLuka-wy9cl8 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂Koma amalawi mwatopa😂😂😂
@RabiaNotes-ql8cf5 сағат бұрын
Iiiiiii koma a Malawi 🇲🇼 eishhhh
@dalitson35587 сағат бұрын
Bola zikhale zoona eee wazunza amalawi munthu ameneyi
@patesnkajenda42586 сағат бұрын
No comment guys kufa kwamunthu osanyadila even atakhala oipa bwanji 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
@PaulPhiri-c5u7 сағат бұрын
Kodi mkususa iye anakuuza ndiosamwalira tonse tifabasi wamyaya ndi mulinguyekha tiyeni tiope mulungu mwini moyo nanga mkususanu akati wamwaliladi mzazutsaso or simzavanawo or kupitsko kumaliro wafawafa basi nthawi yake nayo yakwana aliyese alindinyhawi basi
@NebartMwalwimba-u7m7 сағат бұрын
May the good Lord give guide to Malawians.
@LinlyMatheweKufakwina7 сағат бұрын
😂😂koma anthu pliz zikhalani sending moyo wa mnzanu iiii
@janetmoses72662 сағат бұрын
Kkkkkkkkkk. Kufa, uyo ku America embalm, kenako timva kuti wapita ku Russia kukaikidwa😂😂😂😂😂. Amalawi tileke bodza
😂😂😂amwalile watikwana galu ameneu akawapeze athu amawapha aja galu ameneu
@jameskachulu8141Сағат бұрын
Koma ngati ziri zoonadi zili bwino 😂😂😂😂😂
@WarriorKB-u3k6 сағат бұрын
Ngati chikangawa wafadi ndipangitsa mphwando a malawi tisangalale
@chisomokawotcha17667 сағат бұрын
Anadya nyama yowawa osamaseweretsa moyo aanthu ena ayi enawa ndi mizimu
@ephraimkumwenda32478 сағат бұрын
Don't celebrate one man downfall no matter what. Leave everything to God!
@SUNGANANIGONANI-l5d7 сағат бұрын
God use someone to portray his Manner
@BrightZionga5 сағат бұрын
Adanyoza Mulungu kale galu ameneyu apite basi
@BrianAmos-s2k5 сағат бұрын
Do you remember what was happened in Lilongwe. when Bingu Mutharika was dead? Chewable tribe was celebrating for his death.Now???what are you saying.......😂😂😂😂😂 Let them celebrate