Uthengawutu ufunikila ufikire anthu mumakayamu anthu sakuziwa choyenera kuchita very true angot ndine mulomwe votera DPP ndine wapakati chipan chamakolo MCP or utapha anthu sangayisiye yyyyyy koma malawi tiziti umbuli or ndife ozikonda
@user-zh9kb2sj2iАй бұрын
Chilima ❤❤❤
@user-bz7iv1rq2fАй бұрын
Kkkkkk koma aise iweyo
@petermsamariamapira8933Ай бұрын
Mukulankula zomveka bwino kwambili, i do like it keep up
@user-tq6pg7bv9xАй бұрын
Zausilu
@BenjaminMtimaАй бұрын
Clip yobowa iyi
@arnoldkamanga1335Ай бұрын
😂😂😂Koma this guy
@user-hm7gl7ez5wАй бұрын
Palibe cha nzeru apa . Pitani kameteni ndevu zanuzo . Chakwera 2025 Boma .
@ShukuSh-vi1hkАй бұрын
Iwe ndi chakwera wakoyo nonse nda garu
@user-rm2xv8ys1iАй бұрын
Chilima my vote
@maganizomaseko4653Ай бұрын
Kape 😂
@AbrahamLLoyd-xb2xcАй бұрын
According to what has transpired during the reign of Lazarus Chakwera, the man of God himself, Malawians could never ever repeat the same mistake again by voting for another man of collar.
Iwe ndye chimene tingakuwuze ndchakut Mutharika alowaso ubwino wake avota alikumalawi osat ku Chain 😂😂😂😂
@franktonny732Ай бұрын
your speaking sence tengapo mbali come back and start educating pipo kumpoto kuno kuli democracy since from referendum
@user-xs3pk1vp8iАй бұрын
Chamba chimpweteka kape ameneyu
@user-fz3tm5wj1xАй бұрын
Kodi aise, ukupita kutiko? Ulendo watalika 😅
@irenemakwecha722Ай бұрын
ukupita kuti kodi? SKC for life
@ivychithyoka1551Ай бұрын
Apm boma lathu
@francistsutsu4811Ай бұрын
vote ndimu mtima, umadziwa wekha, osawapusitsa a Malawi
@IMEDISHAMILAАй бұрын
Ndiwe galu kwabas sizikuvekaso nkhani zakozi apa
@goliathkujngo3262Ай бұрын
Kodi ukupita kuti chifukwatu wayamba kupitchama ndi kuyenda eeeee
@Nathkala997Ай бұрын
Kuyenda wapansi mpaka 20+ mins ukuvutikatu
@JosephRabionАй бұрын
Koma mukutukwana achimwene
@kingsleyhopematchaya5184Ай бұрын
Aaaa koma ndi mmene wayendera fodya chakwera voti yanga
@goliathkujngo3262Ай бұрын
Kodi msganizo aiweyo ukufuna ifeyo tipange womwewo iweyo maganizo ako ndi ako palibe chanzeru chimene ukulakhura
@hanifahmponda8711Ай бұрын
Aaaaa iwe wamitsala chilima alipo ku
@user-jw5rx9ze8kАй бұрын
Ku Gehenna ndi mbava chilima wanuyo.
@user-pu3sb2xw6zАй бұрын
Akolo thimakuphaza ulemu thikusiwa kuthi inu ndi achilima mundu wakuba Ole phela
@andrewBwanaisaАй бұрын
Chilima ndie zero bola adadi aise
@user-uc1pd1tc2xАй бұрын
APM woyeeeeeee ❤❤❤❤
@user-ud9wl8yg1tАй бұрын
Why u didn't talk about UDF chipani chomwe chili number 3
@mutafireАй бұрын
Ndinati ndikamba za serious okha okha
@FrynessMoyo-to2duАй бұрын
Mukafika usiku man 😂😂😂😂
@mutafireАй бұрын
apopo inali 6 koloko ndipo
@user-zh9kb2sj2iАй бұрын
Chilima
@atusayeMtalamaАй бұрын
Aliyense president amakondela kwawo Peter nayonso ndiwansankho kwambili
@BraveChimembeАй бұрын
Zaziiii
@user-xj2xt9qe3iАй бұрын
Ka uku ukuyenda uku ndiku china?
@mutafireАй бұрын
yes, decided to showcase mbali ina...but as you can see, i turned a corner and the city appeared.
@Bushiriderick811Ай бұрын
I have been following you broh i want to have my youtube channel nditan bwana?
@mutafireАй бұрын
if you have Gmail and a username here it means you have a channel.
@Bushiriderick811Ай бұрын
Aokhy zikomo bwana
@johnkambala692Ай бұрын
Odala uyu
@jamesgama5489Ай бұрын
Kodi ukumenya ka road work ase, chilima ndiwa timing. Ndale zaku malawi zimayendera region kapena zigawo example ayawo sungasunthe ku udf achewa nde mcp ndi yamagazi atumbuka aford ndi chipani chakwithu alomwe nawonso anapeza chawo chipani cha dpp. Pamene utm ikusowa strong hold ndikuthokoze umalankhula.za nzelu.
@mutafireАй бұрын
Low impact, long distance
@user-ln5hw7dn9gАй бұрын
Chilimayo simunamuyese nkomwe
@paulmakaula4937Ай бұрын
Milward Tobias an independent president...mwala okanidwa uzakhala ngodya...
@mutafireАй бұрын
Tobias nde uti?
@LysonMtalika-tb6fkАй бұрын
APM 2025 Bomaaaaa 🔥 🔥 🔥
@user-ln3zx6wo4wАй бұрын
Munthuyu alindinzelu kwambiri
@CharlsChiyembekezo-xu4wkАй бұрын
ase iwe ndikape
@mutafireАй бұрын
generally
@stevenjosphatАй бұрын
Or mutavotela ndani palibe chingasinthe kumalawi aliyese ndi mbava ine zovota ayi
@mutafireАй бұрын
True
@binalidjeyshabahzombamalawiАй бұрын
Apm ❤
@lastonmasoatenganji-bs5gfАй бұрын
Munthu wankulu ulemu wanu. Mau pang'ono; Malawi idakhala mmanja mwa atsamunda nthawi yaitali. Mbeu ya atsogoleri ake ndi ya atsamunda. Ndichifukwa chake thambo lakuda silichoka pamtu pathu. Akabwera wina nkuyesera kuti alichotse thambolo, ngakhale atsamundao sakondwa kufikira ataikapo wina kuti alibwezeretse. Kuti Malawi adzachoke mu izi ndipokhapokha titasiyana nao atsamunda ndikuyamba kumachita zinthu patokha komanso kugwiritsa ntchito bwino zomwe tilinazo. Atsogoleri adziika maso pazinthu zomwe zingatukule dziko ndipo obwera pambuyo adzipitiriza masomphenyao wina akachoka. Katangale ndi ziphuphu zikhale mdani wa aliyense. Tisamabwereke ndalama kwa maiko ndi mabungwe omasemphana ndi zolinga zathu komanso omafuna chiongola dzanja chochuluka. Malawi ndi dziko lodala ndithu.
@mutafireАй бұрын
zitenga zaka osati masewera kuti zinthu zisinthe
@estherkambewa7791Ай бұрын
Sanje ikuphani
@ivychithyoka1551Ай бұрын
Apm bwana wathu pampando .Apm vote yanga
@user-nr2dz4ks6jАй бұрын
Mkuona ukuyenda pansi
@ivychithyoka1551Ай бұрын
Apm iwe taima kaye watopa
@MatthewsLunguАй бұрын
I thought you will suggest the right candidate Malawians must vote for this coming 2025.
@mutafireАй бұрын
Malawians already know...and it is not the best candidate they want, they want the one from kwawo.