A Layton mango hi sindikukunxiwani Ndine mwana, kma pakhani iyi mboli zanu, mumve kumene muliko mwayaluka, Mr bornnnnnnnnnnn kalindoooooooooo, kawawa😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@stanleykaludzu-bm4pmАй бұрын
Ulendo wa ku 2025 ukunka nukomerabe....big up the DC
@FauzaTabu4 күн бұрын
Muthu oyipitsitsa kwambili ndi ameneyuyu mukunena kalindo
@MustaphaCassim27 күн бұрын
Kodi chakwera ndi busa kapena wasataniki? Mc cathy chakwela mbuzi chilima mbuzi nduna zonse mbuzi imodzi imidzi..
@alickkachepa3801Ай бұрын
Kkkkkkkkk kalindo eti ndi wowopya 😂😂😂
@harrykadango487124 күн бұрын
We say Azaan not Muazzin. In fact, Muazzin is the one who calls people to prayers while Azzaan is the actual calling of believers to go to Masjid and offer their prayers.
@shealtielmajawa823426 күн бұрын
Mafanaaaaa
@user-lk8kj9zv6xАй бұрын
Lyton tinakutuluka ndi mbava kuchita kukhala ngat simsilamu nayenso ndi mbava yotherati
Mabodza ngati akazi kkkkkkkk, propaganda iyi yopusa galu Kalindo iwe
@Henry-vw2czАй бұрын
Lyton mangochi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂kapolo galu
@FrankKambwani27 күн бұрын
Kuyaluka kuposa kugwidwa ufiti mayi busa😂😂😂😂
@ChimwemwePhiri.124 күн бұрын
Ndikape Laiton Mangochi yu............
@AchinaKellzАй бұрын
Akulu akulu kuli mulungu osi milungu osayiwala
@user-gq1lj6nc8hАй бұрын
Mission failed 😅😅😅😅 mr mangochi
@PetroJackАй бұрын
Kkkkkkk mangochi wayaluka😂😂😂😂
@PhillipAcquaronАй бұрын
Ati munthu woyipisitsa kkkkkkk
@zimmekapachika678414 күн бұрын
Msu ndiye apita kale asasa koma ukufuna kusokoneza gulu,😅😅😅😅😅
@giftmandozamkwatula50329 күн бұрын
Life yabwanji iyi😂😂😂
@user-lz4kc5ob1t25 күн бұрын
umenewo nde umbuli wa mangochi
@JaneMoyo-ws2diАй бұрын
Wina ayipe koma zochitika nzimodz. Azbambo uthira kuwiri sumaakhala nza zimayi izi. Kumaona nkhani zokamba pa foni a Lyton
@kondwaniselemani85584 күн бұрын
Chakwera simungamukwanitse mwachepa muuzane nonse ndipo kongelesi ma vote ale ndi achikhalire
@IssahBannet3 күн бұрын
Mboloyalo wanva napamnyelo iwe
@Wilardmavuto15 күн бұрын
❤
@erickhowoya9894Ай бұрын
😂😂😂😂😂 mangochi alibho, kumachenjera pa town
@user-gm9xj1wc2m13 күн бұрын
Izi ndezachamba
@danielsulani8689Ай бұрын
❤❤❤❤
@George-e6h7 күн бұрын
Mbava zokhazokha kuopa kuberana 😂😂😂😂
@user-iw6cz5ft2lАй бұрын
Layton mangochi wathera pomwepo bas?
@williamsalexmbonga24 күн бұрын
Nde mijedu imeneyo azibambo akuluakulu ngati inu mupindula chani kodi nde maumboni anu alikuti timve kuti a Mangochi ananenadi zimenezo? Or mukupanga sewelo la Nyuwani?
@AmaliYahaya27 күн бұрын
❤❤❤👍👍
@IshmaelLifah5 күн бұрын
Izoooooooooooo
@PatrickMlawe-we3ie22 күн бұрын
mangochi 😆😂
@HAMISI26512 күн бұрын
Munthu oyipisisa kwambiri 😅😅😅😅 koma mangochi
@EdwinBanda-ee1bz27 күн бұрын
Kkkkkk
@teezdadaАй бұрын
Lyton Mangochi 😂😂 anthu amutsika
@FefieTenisha-du7geАй бұрын
Great for debunking him... I wish you had maintained your patience until the big fish behind the scene was exposed by Lyton... Next time take your patience until everything gets exposed
@ChristopherMadulira28 күн бұрын
Apap bas galuu wagwidwa app
@bakolomanyenje836025 күн бұрын
Kalindo ndiwachabe ,,, kalindo wants to be consulted,,,, ka share kake ,,
@user-ek7ny9wi4gАй бұрын
Mangochi ndichitsilu chamuthu moti ndakwiya naye
@GavenElias15 күн бұрын
Andalenu mmmmmmmm mbava zachabechabe
@islamaameen2177Ай бұрын
Koma Malawi yoh
@jamesgama5489Ай бұрын
Lyton mangochi mbala yeniyeni wayaluka.
@simonabraham724126 күн бұрын
How can I get in touch with Mr Bon Kalindo? From Zambia.
@kelvindickson26 күн бұрын
Amangochi apa ndye mwatikalkasa padazitu chifukwa cha ichi padakopako nkhope yophyanyikayo
@user-zl9vj6hc6y25 күн бұрын
Namachende kukonda ndalama 🤣
@user-vu9rt8gj3oАй бұрын
Iwe mangochi ndiwee galu kwambiri
@bakolomanyenje836025 күн бұрын
And kalindo was recording ndikuyakhura mwachocho ,,kuti aoneka ngt. Ali serious
@JosephKeneph23 күн бұрын
Awa ndie ma 3dom fight eni eni, not enawa angokula mazila nkabusula bas, mbambande The DC-BON KALINDO Mr President!!
Lyton mangochi apa ayaluka kuposa munthu ozikozera akuyenda
@user-gk6bf7xe9g29 күн бұрын
okay chabwino
@user-gt8nn5ic1v23 күн бұрын
Mangochi ndiwopusa zedi
@SaidiMbawa-st6bjАй бұрын
Vp nayeso ndi wadyela uyu anthu wa akufuna ndalama ndiye cholinga chawo
@maggiemahewe27287 күн бұрын
Muphana😂😂😂😂
@DaireMusopa-rh2cy25 күн бұрын
But why coming out this early with this info... Tinakaadziwa agalu akumpeza mangochiwo... Mwatilakwila
@JohnOmar-mf2pu27 күн бұрын
Aaaa!! Malawi wamoto anthu oipa sazatha pamalawi😢
@Wilardmavuto15 күн бұрын
yaphedukadi kkkk
@AllanChabwela26 күн бұрын
Kuyankhula kwabwino
@Manuel-cm1npАй бұрын
😂😂😂😂 malaw to the world😅😊
@wangatawamilolic41409 күн бұрын
Akalindo alibe nzeru anangokula mutu
@harrisbanda5891Ай бұрын
Mr VP amalawi 1st a Masauko Banda zikomo kwambiri poima pachilungamo and inudi mwaima pachilungamo chofuna kuzaombola amalawi pamoto, AMBUYE TITHANDINZENI pantchito yomwe mukuigwira pamodzi ndi Borne Kalindo, AMBUYE amadana ndikukwiya nfi anthira kuwiri monga redson Munlo , ben longwe, lyton mangochi , mozes kumukuyu, chakwela , chilima, zikhale ng'oma , mkaka, chimwendo banda , marther Chizuma , simpulekisi chithyola, yolamu, ndi ena ambiri
@user-xe3xo5mu9k29 күн бұрын
Alytoni ndimunthu onvesa chison gyz😢😢😢😢 😂😂😂😂😂😂
@user-ky4ce9gb6jАй бұрын
Anthu mukudyeleradi eti
@LysonMtalika-tb6fkАй бұрын
Nkhanga zaona
@BakaliPhili-es3xj11 күн бұрын
Zawonadi patali
@JosephKuyeli-rc9on27 күн бұрын
Kodi muku jambula filimuu??
@user-dt8nr1zx6eАй бұрын
Mangochi ndi galu
@DawoodIssah-mp1yi27 күн бұрын
Malawi 1st You are true people to be followed thank you Mr president thank you Mr Masauko Banda and entire Malawi first organisation.❤❤❤
@user-vl5on2lj8bАй бұрын
Koma iwe oola nkamwa layitoni usamatipute dala nkhati timakoboli tomwe unapasidwato tinatha usanakwanilise zomwe umafuna shauli yako iweyo ungamakope munthu oti akumenyera ufulu waamphawi? Ndalama zopedza mudzina lomenyera ufulu anthu osauka pomwe ukumenyera mimba yako siichedwa kutha komanso siimapindula tikukuchenjedza mangochi usiru wayambawo usiiyiretu komanso usiye kulimbana ndi president wathu bon kalindo ukuyiputayo ndi minyama pomwe uli waminyama kale .😂😂😢😢😢😢
@gabrielmaluwa103825 күн бұрын
Mangochi wayaluka
@katalamajames4947Ай бұрын
Layton mangochi ndi mbuzi
@lulukunkeyanih827128 күн бұрын
Mangochi mmmm mbuzi
@GraceLimani-zw7dxАй бұрын
Munakadikila akumana ndi anthu odzaapereka ndalama wo mutaika camera pokumanapo kuti ayaluke zeni zeni mangochi ndi Ben zitsiru za anthu umphawi wapweteka
@alexgweje8610Ай бұрын
Mangochi Eish mavuto a munthu
@user-ww7rx6ke4o27 күн бұрын
Km nde yatonyoka osati masewera 🙄🙄🙄🙄awawa apwetekana🤔🤔🤔🤔
@BakaliPhili-es3xj11 күн бұрын
Kkkkkkk yatonyoka? kkk
@OwenNyangu-nv1yt28 күн бұрын
Bola tadziwa kuti mukumagulidwa pansewu muzipita nokha
@user-ni4nw1ee2fАй бұрын
Makhanga zaona
@emmanuelluhana860812 күн бұрын
All what is happening is Childishness. And taking Malawi as playing ground
@shonmike-su7qkАй бұрын
Layton magochi ndi khuluku all
@user-tn2qg1vs9j22 күн бұрын
The dc
@JohnConar-kq4hiАй бұрын
The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC 😂😂😂😂😂😂😂😂
@IdressaMussaАй бұрын
The DC ndikatundu wakulu simunthu wachibwan big up