No video

A MALAWI ALANKHULAPO PA ZA CHISANKHO CHA MCHAKA CHA 2025

  Рет қаралды 57,199

Hanifa Mw

Hanifa Mw

Күн бұрын

Dzika za dziko lino zati momwe zinthu zilili dziko lino zizathandizila pakasankhidwe ka atsogoleri kuyambila mchaka cha 2025 mpaka 2030 pomwe ambiri akuonetsa kukhumudwa kwawo pa momwe zinthu zilili dziko muno maka pa chuma

Пікірлер: 315
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera 5 ай бұрын
Ngati utavotele mcp ingoziwilatu zoti ndiwe otembeleledwa
@petersonmatumbo3757
@petersonmatumbo3757 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂 Ndipo live
@JeraldMasudii-im5qu
@JeraldMasudii-im5qu 5 ай бұрын
Palibenso pano kuzavotela boma la mcp
@raffickchicco2724
@raffickchicco2724 4 ай бұрын
Ndipo kungo elekeza ku muikaso gwape uyuyu akuthani
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 5 ай бұрын
Chikuni chamoto kusunga moto, DPP woyeeeee❤❤❤
@raffickchicco2724
@raffickchicco2724 4 ай бұрын
Ndendende mene ndikuganizira ine
@Fatima-li5rg
@Fatima-li5rg 5 ай бұрын
Achakwela ndi mbudzi ya munthu ndi chilima Kodi anthu awiriwa alibe achibale awo woti anga khale nawo pasi kuwalangiza anyani agulu awanthu
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 5 ай бұрын
Kuwaona amene akuti ndi a chair lady wo mmmm Ali mbuuu kutuwa amvekere zinthu zikuyenda bwino,azimayi omvetsa chisoni kwambiri
@patrickkapinga7091
@patrickkapinga7091 5 ай бұрын
Ndipo mzimayi opanda mzeru ameneyu dzithu dzikuyenda sugar 3pin thumba lachimanga 50 pin amayi inu mumudziwe yesu ngati lili dyera mmmm
@MatthewsJanuary-wr3rf
@MatthewsJanuary-wr3rf 5 ай бұрын
Ndipo ndinziyi opusa ameneyu
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq 5 ай бұрын
Ndipo azimayi inu ndiwofunthatu uhule basi
@daviechinthengaofficialcha7190
@daviechinthengaofficialcha7190 5 ай бұрын
Eti eti koma dzikoli .. Malawi dziko lomvesa chisoni.
@user-ce6hy6tp7e
@user-ce6hy6tp7e 5 ай бұрын
Km animal opusa komaso bambo opusa iwe molars wakut chakwera ndi galu kwambiri azalamura kunyumba kwanu iweyo mamuna opusa zed azikalamura iweyo ndi nkazi wako hiyaaa
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 5 ай бұрын
APM my vote
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 5 ай бұрын
Komatuu Iwe Edward Frackson Gama, anakuphunzitsa kuyankhulayo ameneyo amatha kuphunzitsa.
@ayamimustaff-jo2cy
@ayamimustaff-jo2cy 5 ай бұрын
Dpp kuyakhula koma kumeneko dpp boma leni leni
@user-cy5ko2qw5d
@user-cy5ko2qw5d 5 ай бұрын
Hanifa more fire, APM my vote
@user-ez1kc7zp9m
@user-ez1kc7zp9m 5 ай бұрын
Mr.boniface mavuto inu mumakwana, APM My vote
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq 5 ай бұрын
Umakwana mr gamah zoona Apm basi alowe ❤❤❤
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y 5 ай бұрын
Chakwera obowa, APM my vote
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 5 ай бұрын
Chakwera walepherela basi, tivotele APM basi, ine ndili ku South Africa koma ndikumva nawo luwawa chifukwa banja langa lonse lili ku Malawi. Achoke chakwera basi.
@user-yt8qn1uv3d
@user-yt8qn1uv3d 5 ай бұрын
Dpp my vote
@funnynyirendafunny7888
@funnynyirendafunny7888 4 ай бұрын
Nyamatawe wayankhula 💯 osati azimai ndazimidala opanda nzelu😊 iwe wayankhula momveka ndithu
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 4 ай бұрын
Big up Mr bonfec mavuto💪💪💪
@georgesmart3791
@georgesmart3791 5 ай бұрын
Mwayankhula zamphamvu mr MaKalani... 🔥 🔥
@user-uf1tz7bp5q
@user-uf1tz7bp5q 5 ай бұрын
Eduwadi ngama wanena bwino kwambili❤❤❤
@AnastasiaChakwiya
@AnastasiaChakwiya 5 ай бұрын
Mbuzi zazimayi Apm my vote
@mphatsomonjeza4371
@mphatsomonjeza4371 5 ай бұрын
Adya chibanzi mbuzi zaanthu
@AnnieKazembe-ic5vp
@AnnieKazembe-ic5vp 5 ай бұрын
Mbuzi zazimayi bwino 😂😂😂
@user-cp8rz3qs8l
@user-cp8rz3qs8l 5 ай бұрын
APM my vote ❤❤❤
@Santo-B
@Santo-B 5 ай бұрын
Mr gamah number one ❤
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 5 ай бұрын
Dpp woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
@frankiejackzy9862
@frankiejackzy9862 4 ай бұрын
Boma lomweri mudabadwa ndi Umphawi Aghalu inu....mwati azimai enawo amaberekadi mxiew kwambiri 🤗
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 5 ай бұрын
Mr gamah mumakwana lazalo azipita
@AlickTchokola
@AlickTchokola 4 ай бұрын
Padziko palibe mtendere dziko lonse lapasi kulibe chabwino yanganani kumwamba kwamulungu ziyenda koma sidzitsintha nthawi siyili kumbali yathu
@user-ef7lq1zj9n
@user-ef7lq1zj9n 5 ай бұрын
Amai awili awo ndigalu kwabasi sakuwona mumene kwacha yagwera akufananisa ndi kunja amadziwako ndipo kunja anthu amagwila ntchito ndalama amayipeza Koma kumalawi or maganyu akusowa sakuganizila Za tsogolo la adzukulu bwanji iwowo akalamba or atamwalila Palibe vuto iyaah kupusa
@AlickTchokola
@AlickTchokola 4 ай бұрын
Kaya tikufuna dziko liyipirayipira mawu amulungu sanama matsiku otsiridza ndiamenewa
@MussaZamesi-rs8nm
@MussaZamesi-rs8nm 5 ай бұрын
Hhhhhhha
@estherkauyange6548
@estherkauyange6548 5 ай бұрын
Komatu malawi ndi anthu olimbikila kwabasi chabe azisogoreri ake sakondabdziko lawo
@YawakaNyirenda-hu1hr
@YawakaNyirenda-hu1hr 5 ай бұрын
Mr good point
@danielmagwaya1074
@danielmagwaya1074 5 ай бұрын
DPP mare fire 🔥
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i 3 ай бұрын
Mmmmm amai inu maiko ake ati
@user-yf3st5yb1n
@user-yf3st5yb1n 5 ай бұрын
Flackison gama wanena zanzeru kwambiri.osat galu winayo ndi azimayi ake opanda nzeru aja.yomweyo gama.ndapereka coment kamba ka (Edward flackison gama)
@user-xl6qs1sy7x
@user-xl6qs1sy7x 5 ай бұрын
Azimayi amene alibe nzelu angoziyakhulila zazii
@user-rf4br1fv2z
@user-rf4br1fv2z 5 ай бұрын
Mandala achambo andisangatsa osawangira ena ai
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 5 ай бұрын
Azimayi akudya akukhuta awa mmakwaomo mkutheka ali ndi azibale awo kubomaku
@chikokaSagonja
@chikokaSagonja 4 ай бұрын
Mcp ndiolephela ma subject onse palibe yopambana even 30 percent onse kumangothera 10percent
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c 4 ай бұрын
Good a Gama zikomo osachita matha
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 5 ай бұрын
Sizikuyenda, tisinthe boma basi, chakwera out.
@user-xz7jg2eu6r
@user-xz7jg2eu6r 5 ай бұрын
Kuteroku amalawi nzeru tilinazo kwambiri ndaonera zomwe zanena Edward Gama, komaso kuli zizete zina ndangomuiwala dzina dala wayankhula koyamba asaa wanditengamo bwanji ndikanayqndikana naye aaa
@LeahBanda-oz1xg
@LeahBanda-oz1xg 4 ай бұрын
Ena akuti Boma likuyenda bwino 😂😂😂😂😂Koma awa
@bestactionmovies-ol5oe
@bestactionmovies-ol5oe 5 ай бұрын
Uyo wati ali ndi chiphatso 🔥🔥
@marryphili5419
@marryphili5419 5 ай бұрын
Azimayi awa ndikanawawona maso ndi maso ndikanawagenda mumadya nayo chakwera eti mumene tikuvutikira basi wina aziti dziko likuyenda bwino chiti
@user-ww7pv1xc6e
@user-ww7pv1xc6e 5 ай бұрын
Sumah simbeye ine ndikugwirizana ndi amend a mat chikhale chi panic chimodzi koma tizisintha map resident in phases mwina tizaone kusintha kumpoto pakati ndi kumwera kuthukuka mofanana
@leonardjika2100
@leonardjika2100 5 ай бұрын
THE ONLY WAY TO RESCUE OURSELVES IS I MYSELF TO GOVERN OUR OUR NATION SO HELP ME GOD
@FalukuMustafa
@FalukuMustafa 5 ай бұрын
angakhale alowe winayo palibe chinga sithe
@EyobeAyala
@EyobeAyala 4 ай бұрын
Ukasankha MCP ndiwe, Galu kwabasi😢😢😢
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 4 ай бұрын
😅😅😅😅😅😅😅😅 Tidya ufawo
@PatrickManjomo-dx7ky
@PatrickManjomo-dx7ky 4 ай бұрын
Mr Gamah mbambande zinazo mbudzi zenizeni
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 4 ай бұрын
Zoonadi ifeyo tili pambuyo pa adad
@user-et5ex6if7r
@user-et5ex6if7r 5 ай бұрын
Anthu woyipa inu mukunama chani nanga kugwa Kwa chakwa ndi zamatsiku otsirizanso
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 tidya ufawoooo
@SilivaPetulo
@SilivaPetulo 4 ай бұрын
Amaiwa ndihule
@JacksonMoyo-tm8dv
@JacksonMoyo-tm8dv 4 ай бұрын
Palibe chakwera chimene wachita chilowereni m'boma
@user-ui4ux5kc8d
@user-ui4ux5kc8d 5 ай бұрын
Chipani ndicha dpp basi apm my vote
@user-qe4uz9sq7f
@user-qe4uz9sq7f 4 ай бұрын
😂😂😂😂😢
@misheckchinjala.g
@misheckchinjala.g 5 ай бұрын
Cape Town South Africa Stellenbosch my vote DPP basi
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 5 ай бұрын
Vuto la hule ndilimeneli kungomchinda bwino amazungulila mutu olo osampasa kathu azimayi opusa ngati alimkathu
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m 5 ай бұрын
Tidya ufawo koma achoke basi Apapa mmene ndamvera 97 percent MCP ichoke kkkkkkk park and go
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 4 ай бұрын
Tipemphere kwambiri ambuye atthandize pozasankha asogoleri
@tiwongehojaney5873
@tiwongehojaney5873 5 ай бұрын
Bambo gama mumatha inuyo ndizikonda funds zanu
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c 4 ай бұрын
Mboleyako yamako galuwe chitsiru iweyo galu mcp yamako nyini yes zoona ndigwizana ni omwe ati DPP WOYEEE mcp ikagwere uko
@LukaThawe
@LukaThawe 5 ай бұрын
Man mwayankhula bho sibwino kumasinthasintha boma daily tizakhala tikulira
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 5 ай бұрын
Aaaa anthu ena alibe dzelu ati akugawa chimanga kumudzi. Kodi njalayo wabwelatso ndani ndimayetsa chakwela omweyu nde kukugayiilani chimanga kumatsangalala kkk malawi walelo
@McfrankJackson
@McfrankJackson 5 ай бұрын
Chair ladyyo kwawo sanadyeso ameneyo
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 4 ай бұрын
Mmene akuyankhulira ena umu , zikuoneka kuti amalawi ambili ku ganiza kumawavuta adakali mu m'dima Mulungu atithandizile kuti tione pa tali ndithu, mmene amaganizila chakwela ziko si lingapite pasogolo ku mbali ya umoyo wa siku ndi siku inde zina ndi zina akuesesa koma sakugwilira penipeni pofunikila , uyu atakhala bambo wa m'nyumba akhoza kupha ana ake why kuwagulira ana zovala zabwino koma ali mafupa okhaokha kuli kusowa zakudya nthupi . Moti tingokhalira zi somo za kumwamba bsi ndi president olimba ntima pa zofoila osati zopindulira amalawi eni pa moyo wa siku ndi siku
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 4 ай бұрын
Bvuto la amalawi kutenga sitimachedwa kuiwala akangotipasa kandalama pang, ono basi timakopeka
@user-ci8el1df1b
@user-ci8el1df1b 5 ай бұрын
Pantumbo panu azimayi Inu mwava
@chisomochavula
@chisomochavula 5 ай бұрын
Walephela chakwela zaka 4 osapangako olo hard yazomwe ananena kwazaka 4 zapitala pazomwe anapanga zasiyana chakwela akapume
@FelixChisoni841312
@FelixChisoni841312 4 ай бұрын
tikalembetse basi. Chrissy Kayeni wanena
@ayamimustaff-jo2cy
@ayamimustaff-jo2cy 5 ай бұрын
Bambo ophutsa kwabatsi tchisili cha bambo mbunzi yeniyeni
@mafukenimasangwi5487
@mafukenimasangwi5487 5 ай бұрын
Uchitsiru kulandila ufa mmalo molandila fetelaiza zopusa basi
@ayamimustaff-jo2cy
@ayamimustaff-jo2cy 5 ай бұрын
Azimayi ophutsa kwambili kwambilitu mbunzi zanzigogo notse
@John-qm8qx
@John-qm8qx 4 ай бұрын
Peter
@user-uj7df9cy2f
@user-uj7df9cy2f 5 ай бұрын
Athuwo azidalila zolandila khuku ya munthu
@gloriambale2277
@gloriambale2277 5 ай бұрын
Mai jere mutu wanu mwanva ......akulu kulu koma mmmm opanda nzeru😂😂
@user-ko2yv4gi5y
@user-ko2yv4gi5y 5 ай бұрын
Ndati ngati kuli galu wamayi malawi yonse ndiye ndameneyo nyani
@chikokaSagonja
@chikokaSagonja 4 ай бұрын
Ndikusimikidza kut onse omwe angazaelekeze kuvotera mcp sazakapulumuka kumwamba
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 4 ай бұрын
😂😂😂😂😂koma zoonadi mzimbe tikulima kumalawi konkuno koma sugar nkumasowa
@IslamMussah
@IslamMussah 5 ай бұрын
Apm ❤vote 🗳
@user-ux8bc6wy1i
@user-ux8bc6wy1i 5 ай бұрын
Munthu oyamba kumene amafika zaka 4 .. Azimayi opusa kwambr
@funnynyirendafunny7888
@funnynyirendafunny7888 4 ай бұрын
Amai Inu agalu kwabasi ziku lanzanu aku vutika ngati inuyo ??? Ndini agalu zimainu .ntchifukwa mmangopanga uhule zazi
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x 5 ай бұрын
Sure APM my vote❤
@MosesBanda-ef6fj
@MosesBanda-ef6fj 5 ай бұрын
Azimayi aku bagamoyo kuyankhula manyaka okhaokha mbuzi za anthu dziko lake liti limene likuyenda bwino agalu inu mukufuna akutameni koma ukachoka apa ukagona ndi njala nyau yanu chakwela yalephela, komanso nanga bwanji nthawi ya Peter tsimunavomeleze kuti kukwela kwadzi sikuti wapangitsa ndi Peter koma ndi matsiku otsiliza kuyipa mtima fiti zadzikazi
@gavannamaseya4870
@gavannamaseya4870 5 ай бұрын
Akuti akulandila ufa ndiye mcp izawina
@JamesChimera-hw1nv
@JamesChimera-hw1nv 5 ай бұрын
Pàmalawi palibe President anachitilapo anthu zofunazawo chirichonse amapanga chofunaiwo
@AmosKalembo
@AmosKalembo 5 ай бұрын
Bomalakendie limeneli
@samalanimacdonald9373
@samalanimacdonald9373 5 ай бұрын
Aaaaa mesa pa barrot paper timuikapo bushiri ,akudzatengelatu for the first time.
@SamsonWawa
@SamsonWawa 5 ай бұрын
Mbuzi Za azimayi
@LukaThawe
@LukaThawe 5 ай бұрын
Chakwera akuyesesa kulingana ndi nyengo yemwe atengera mpando wake
@dorcasmwale6328
@dorcasmwale6328 5 ай бұрын
ovotela tonse alliance/mcp ameneyo amadya matgewela amwana osachapa, amatamba ndithu
@Cee-H-Cee
@Cee-H-Cee 5 ай бұрын
Kunena zoona Chakwera akuyesesa ndithu. No need to change
@user-fn6fu4rs8i
@user-fn6fu4rs8i 5 ай бұрын
Kagwere kutali ku bagamoyo iwe😮
@ayamimustaff-jo2cy
@ayamimustaff-jo2cy 5 ай бұрын
Timuyithana kuno kala ngati lamaphosa akumuyitana akafikamo ndi zipolopolo batsi mbunzi yachabe chabe ponyela pa makhepo chakwela😢
@LeoC-in6um
@LeoC-in6um 5 ай бұрын
APM my vote less back to bpp
@JamesMalango
@JamesMalango 5 ай бұрын
Anthu ena ndiomvesa chisoni watengaka chfkw ayamba kugawa zinthu waiyiwala mavuto onse mmbuyomo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 5 ай бұрын
Ndipo anthu ndiovuta zedi mmmmm
@user-mv4us2yx1o
@user-mv4us2yx1o 5 ай бұрын
Munthu ndionvesa chisoni,APM my vote
@joebrown1158
@joebrown1158 5 ай бұрын
Do you understand the language? That man speaks exactly what he said about about the government?
@JamesMalango
@JamesMalango 5 ай бұрын
@@joebrown1158 that was my opinion you have rights to say your own
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 5 ай бұрын
Kkkkkkk awa akuopa kufinyidwa mumsikamo mkona akukometsera hummm palibe chabwino ku Malawi.. 🔥🔥
@aloysiusdidymus7869
@aloysiusdidymus7869 5 ай бұрын
Ufawo tidya😂😂😂
@ChikondiChauluka
@ChikondiChauluka 5 ай бұрын
Boma sasintha ngati malaya
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 5 ай бұрын
Kkkkkkk koma anthu atopa inu ukunena zooona Osama Isa cholinga they must pack and go anthu tikuvutika 🔥🔥🔥🔥💔💔
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 5 ай бұрын
iwe mdala zichende zako ukuwona ngati mcp ingawine
@giftadam2301
@giftadam2301 4 ай бұрын
Kunganiza ngt nkhuku zomwe ukugulisazo😢
@lastonbamusi1013
@lastonbamusi1013 5 ай бұрын
Azimayi mukunama
@Jamu-kp4ey
@Jamu-kp4ey 5 ай бұрын
Ku south Africa kulibe democracy
@anusahjenala1063
@anusahjenala1063 5 ай бұрын
Mzimai alibe chipani alibe mpingo chilichonse iwo ndi lulululu
New EU visa rules to be introduced | BBC News
4:20
BBC News
Рет қаралды 563 М.
КАКУЮ ДВЕРЬ ВЫБРАТЬ? 😂 #Shorts
00:45
НУБАСТЕР
Рет қаралды 3,2 МЛН
OMG what happened??😳 filaretiki family✨ #social
01:00
Filaretiki
Рет қаралды 13 МЛН
Please Help Barry Choose His Real Son
00:23
Garri Creative
Рет қаралды 22 МЛН
Presidential Jets Seizure: Pat Utomi Accuses Amosun Of Contract Violation
40:43
44th SADC summit for heads of state and government in Zimbabwe
2:30:46
CHIBANGILI CHIKUPANGA ZODABWITSA KU BLANTYRE PART 1
13:53
Hanifa Mw
Рет қаралды 28 М.
ZINA UKAMVA: NZANGA WANDIDYERA MKAZI WANGA
18:58
Hanifa Mw
Рет қаралды 46 М.
Nkhani yovetsa chisoni ya mwana wa Ibrahim swed ndi Angella
10:04
OLO CHAKWERA KUTI AKHALE PULEZIDENTI NDIKACHASO YEMWEYU
10:40
Hanifa Mw
Рет қаралды 61 М.