No video

A Michael Usi Alibe Impact Inaliyonse Ku UTM Olo Ukhansala Sangawine - UTM Member

  Рет қаралды 18,418

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

On Nyasa VoiceBox, A UTM member says that Vice President Michael Usi has no real impact in UTM, he cannot even contest as a councillor and win.
Pa Nyasa VoiceBox, membala wa UTM wati Vice President Michael Usi alibe chikoka mu UTM, sangapikisane nawo ngati khansala ndikupambana.
#malawi

Пікірлер: 62
@MPHATSOKALUWA-lm2uy
@MPHATSOKALUWA-lm2uy Ай бұрын
And munthu otan oti nd mtsogoleri km ma meeting amwambo wamaliro osapanga attend kmnso akapanga attend osayankhulapo chonsecho nd mtsogoleri amathanthauza chan???
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 Ай бұрын
Mukufuna achite kukuwuzani yekha kuti ndi sellout?
@SalaJawali
@SalaJawali Ай бұрын
Ndipo zodabwitsatu
@josephinemisomali6840
@josephinemisomali6840 Ай бұрын
Funso mkumati Kodi nsalu zikugawidwa lerozi Kaya ndingongole zomwe zikufuna kuperekedwa lerozi nthawi yonse zinali kt amadikila Chilima amwalire Kaye UTM gwilanani manja Zambiri zichitika Koma osafooka
@LamieTiger
@LamieTiger Ай бұрын
Mbili ya usi amakhala president straight tithakuona khadza Za John Tembo
@user-ck7eb7tb7v
@user-ck7eb7tb7v Ай бұрын
Rest in peace SKC , we shall always remember you, 2025 ndipafupi apa
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Well spoken
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Osamaphweketsa Bon Kalindo. Bon Kalindo analosera za imfa ya Chilima. Ndipo ananena pa 6th June 2024 kuti Chakwera wakonza plan yakupha Chilima ndi ndege. Ndipo anamuuza Chilima asakwere ndege. Pa 10 June ndege ya Chilima inagwetsedwa. Pa 15 June, MCP inamanga Bon Kalindo kamba ka ma audio.
@henryphiri6100
@henryphiri6100 Ай бұрын
Tidzadandaula akadzatuluka kaliati chifukwa ndi chipilala cha chipani
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo Ай бұрын
Very powerful message.
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Zoona Mau abwino kwambili maso kusongolo
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em Ай бұрын
Viva UTM viva
@thomasphiri-zr3xs
@thomasphiri-zr3xs Ай бұрын
Very true comrade le take on Nyalonje has no political impact indeed in her last constituency b4 her lost her seat pipo in the constituency booted her out bcos of her characters manners...........my plea to UTM G.members mama kaliati do a better research on mps to stand in 2025 elections don't just hand pick the rejects from other parties now are paying back what we sow in 2019.
@alinafesalima5597
@alinafesalima5597 Ай бұрын
A Michael Usi ndi munthudi owumila koopsa ine ndagwirizana nanu ndipo sapasa munthu ndalama yake
@thomasphiri-zr3xs
@thomasphiri-zr3xs Ай бұрын
Lets allow new members why pipo r flocking to UTM now.....there is potential to win elections though reqiures proper partners. However let's give chance to madam Mary Chilima if so she can accept to compete any position now or later but God shows that in the years to come Shaun Chilima will bounce back into politics same UTM with powerful change and will rule the country. What late VP Chilima was doing hasn't been fulfilled so spiritually power is coming back to complete where left.
@Marymahendra
@Marymahendra Ай бұрын
Thanks to god you have come out from the lion side completely different between evil people xx
@khumalonyirenda4437
@khumalonyirenda4437 Ай бұрын
Morefire Dr, micheal usi
@VincentMtambo
@VincentMtambo Ай бұрын
Kaliati is Very loyal. Ndinaona nthawi ya Bingu sanathawe
@beakab2378
@beakab2378 Ай бұрын
Good message, 👏👏👏
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz Ай бұрын
Uku ndiye akuyakhula was wondering kuti guys how can u trust Micheal usiiiii???
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn Ай бұрын
UTM siinagawanike koma tsopano tingodziwa kuti ma utm members enieni ndi atiwo Ife till nganganga pa UTM
@daviskamonde4882
@daviskamonde4882 Ай бұрын
Reality!!
@suzenzulu9412
@suzenzulu9412 Ай бұрын
UTM should support Kaliyati for presidency.
@AbrahamTembo-z5k
@AbrahamTembo-z5k Ай бұрын
Zikuwoneka kt alibe impact ku chipani, koma ku Dziko, alinayo. PENYETSETSANI KWAMBIRI OSANGOCHITA ZINTHU ZA PHUMA ndi MKWIYO. S.K.C. pomusankha, adawonamo NZERU ndipo ambiri tinakhutira. Dr Michael Usi, ali ndi popularity across the country. Mwina poti ife tikuziwonera patali mwina.
@isabelmartin7567
@isabelmartin7567 Ай бұрын
Usi si wa UTM ndipo kalikonse tikaonana pa 19 Friday li
@user-yv8hc3fd7f
@user-yv8hc3fd7f Ай бұрын
We want Kabambe
@user-mj2te7vl6p
@user-mj2te7vl6p Ай бұрын
This is good
@JamesIngeni-ku3qj
@JamesIngeni-ku3qj Ай бұрын
Manganya is a betrayer and I can believe kut munthuyu ndi oipa nchochi
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Ай бұрын
Vuto ku Malawi ndi kukoza or kiyanjanisa ayi ndithu koma kupasula ndi kibwelesa chidani pakati pa anthu or chipani UTM be careful mawa sikutali chilima anasankha usi chilipo chomwe anawona mwayiye
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Ай бұрын
Zoona abwana amene mukuyankhula,,pitilizani kulangiza anthu a UTM,,Bon Kalindo akufunila DPP iwine
@MsondaBanda
@MsondaBanda Ай бұрын
Utn kuyaghayika
@eliasmgala8469
@eliasmgala8469 Ай бұрын
Micheal Usi mukumunenayotu Chilima dolo amene timamunenayo, anamusankha iye kt akhale Vice wake enanu kukusiyani uko. And I think amaganizadi bwino munthu uja. Imagine akanasankha wina like this one or ena aja!
@GracePendame
@GracePendame Ай бұрын
Ndiwakabudura uyu usi simunthu wabwino ndi yudasi uyu osamusekerera
@EliasKawuwa
@EliasKawuwa Ай бұрын
Anthu a UTM mwadzadza ndi nkhwidzi pa wina ndi zake, mmalo mongwirizana chifukwa chopititsa patsongolo chipani chanu,mmalo mwatsongoza kuika patsongolo zofuna zanu,choncho mwaononga chipani Cha mwini wake Malemu SKC ,ndipo zimene mukuchitazi,anakakhara kuti SKC Ali moyo,nonse SKC anakakukwapulani kwambiri pazimene mukuchitazi,ngati mmene ambuye Yesu anachitira ataona anthu akungwiritsa tchalitchi kugulitsira malonda, the problem is,nonse mumafuna ma udindou Boma,nde mmalo mwake mwafuna kuuikira azanu ama udindo Boma, that's very bad, just feeling sorry for all UTM members kuti atsongoleri anu onse ndi adyera,ndipo chipani Cha UTM chitha movetsa Chisomo,chifukwa Cha dyera, that's why zipani zambiri Malawi muno ndi family parties,at least zimayendako, koma zinazi nde Kaya ndithu,dyera lakula mu UTM,mwaononga chipani chifukwa Cha Nsanje
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Mwana Wa njoka iwe kagwere
@AMONINICHOLAS-g2m
@AMONINICHOLAS-g2m Ай бұрын
Masophenya andari ndi Chilima Inu aye Mp mikuyakhulani mulibe vision
@FrankSpison-o7o
@FrankSpison-o7o Ай бұрын
Yudas 😢
@amosnyirenda-pl1ss
@amosnyirenda-pl1ss Ай бұрын
wasanje ise nikaliyati wako musiyeni usi alamulile
@BellaMandala
@BellaMandala Ай бұрын
Uncle shortawo bas angokhala ku MCP komko bas
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Ай бұрын
anthu ofuna kugulisa utm aja ena ndakuluwa
@JustusSNkhata
@JustusSNkhata Ай бұрын
Komanso kuchoka mu mgwirizano chisalhale chifukwa kuti anthu a UTM asiye kutumikila a Makawi
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh Ай бұрын
Ndipo sidzawaonaso,apa mwayankhula bwino mwandilumbitsa mtima,anandinyasatu short one ameneyu
@LivaneMsyamboza
@LivaneMsyamboza Ай бұрын
Ndipo mwayakhula bwino
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Onse ankayamba chonchi ndi pang'ono pang'ono uzakhumudwa atakhala nsogoleli wa ziko enanu muli ndi nkhwizi chabe ndi mzanu musiyeni ,gulu la kaliat likufuna kubwerera kwao paja ndi a dpp
@IsaacChapotera
@IsaacChapotera Ай бұрын
Mau a mphamvu
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Akaliayati ndi nkhalidwe lawo atamwalila abingu anachita chi.mozi mozi kunyoza mai j b ndiye amene akuziwa mai kaliyati sakudabwa ayi
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Ай бұрын
Anthu akonda ndrama ndi galimoto za Boma,,anthu Albie chikondi
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Inu ndi adpp msatisokose ife ayi adyela ndinuyo mmene anamzuzila adpp lelo adpp bdiabwino kwachilima poti wamwamwalila ayi kaya msanyoze ausi ayi i u ndiamene mkufuna kugulisa chipani kwa adani
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n Ай бұрын
Muziti poti mcp ysmupha nanga mukubisa chani
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Ana anjoka inu mukhalira yomweyo
@beakab2378
@beakab2378 Ай бұрын
DPP mukuinyozayo inamusiya Chilima apite wamoyo, iye nkumainyoza nkupita ku ng'ona zokupha. Phunziranipo phunziro.
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Mau omveka bwino micheal utsi pomwe anaoneketa kuti si wa utm ndi nthawi ya maliro achilimA osayakhula chili conse kungofziwiratu kuti ndiyemwe anapereka chilima manja mwa chakwera ndiye manganya si wautm koma mcp
@SildaKatundu
@SildaKatundu Ай бұрын
Tisankhe Patricia Kaliati kukhala president .Ndipo ndi munthu olimbikira ,opanda mantha komanso ochuluka mmalawi muno timamudziwa ndi kumukonda
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Zoona Patricia Kaliati mpando omwe Ali akhale omweo
@user-hr6dj4xc8l
@user-hr6dj4xc8l Ай бұрын
😂😂😂😂 uko kunali kulira kwa anamalra
@hissimajohn965
@hissimajohn965 Ай бұрын
Za ziii
@retirementtoafrica
@retirementtoafrica Ай бұрын
Alindi impact mudziko lamalawj kuyambira kelekale. Sagawa masweet.
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di Ай бұрын
Say NO to Kabambe (utm presidency)
@user-er7ub4ug7y
@user-er7ub4ug7y Ай бұрын
Atumidwa ndi MCP awa
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di Ай бұрын
Awalandire alendo ofuna kulowa UTM koma osati zogulisa chipani kumpasa obwera (mlendo) kumpatsa u president kodi nkatimwanu mulibe angaimire u president? Mene mwavutikira basi mukagulisa chipani iyo ndi trick Say NO to Kabambe (UTM presidency) pls
Ndikuopsyezedwa Chifukwa Cha Ma VN (Part 2) - Pastor G Shumba
19:32
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 3,9 М.
Пройди игру и получи 5 чупа-чупсов (2024)
00:49
Екатерина Ковалева
Рет қаралды 4,3 МЛН
Happy birthday to you by Tsuriki Show
00:12
Tsuriki Show
Рет қаралды 12 МЛН
Prank vs Prank #shorts
00:28
Mr DegrEE
Рет қаралды 11 МЛН
Ndikuopsyezedwa Chifukwa Cha Ma VN - Pastor Shumba
16:55
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 7 М.
Hot Current Malawi Ma Supporter A MCP Ndi UTM Amenyana Zatani Ku Tonseku?
50:47