ABWANA PAULENDO - BLESSINGS CHIMANGENI

  Рет қаралды 16,383

Mpungwe-Pungwe mw

Mpungwe-Pungwe mw

Күн бұрын

Пікірлер: 173
@brianjames211
@brianjames211 2 сағат бұрын
Those who live their life by the sword they'll die by the sword, God has said it all
@kennethnasteve4721
@kennethnasteve4721 2 сағат бұрын
This song reminds me BINGU once this song come out that means something big happens 😢
@MtendereChimbuto
@MtendereChimbuto Сағат бұрын
It came out in 2007 0r 2008
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu 32 минут бұрын
Exactly
@dalitson3558
@dalitson3558 3 сағат бұрын
God help us we’re going through a lot tikuvutika chifukwa anthu ochepa
@victorauwana7258
@victorauwana7258 2 сағат бұрын
Komatu ndiye lelo ndilezela ,,, nananangati wafa mmmm ayi munthuyu wawononga ziko
@AmissKumakanga
@AmissKumakanga 2 сағат бұрын
Ineyo panopa misoz yachimwemwe irimasaya mwanga murungu atimenyera khondo❤❤❤❤
@ronaldordinga6537
@ronaldordinga6537 Сағат бұрын
@@victorauwana7258 anthu mkuyankhura ngati MLI ndi umboni oti munthu wamwalira bwanji
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 Сағат бұрын
you can say that again umamwa chani ase kkkkkkkk
@RuthTimothyChirwa
@RuthTimothyChirwa 3 сағат бұрын
I like this song keep it up my brother ❤❤
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 2 сағат бұрын
Ambuye please tengeni satana ameneyuu 🙏🙏🙏
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Сағат бұрын
Ambuye please chakwera mtengeni akuchinda akazi ayeni
@vanessachimbayo1247
@vanessachimbayo1247 Сағат бұрын
Zoonadi mpaka pamenepo
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 53 минут бұрын
Kkkkkk koma ndaseka,ameneyu atsogole basi
@HawaMamo-q2v
@HawaMamo-q2v 40 минут бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂koma abale
@IdressaMussa
@IdressaMussa 3 сағат бұрын
Chakwera 💔💔💔💔💔 ayende bwino 🎉🎉🎉🎉🎉anali oyipa ngat 🎉🎉🎉kambuku 🎉🎉🎉🎉🎉🎉 nyimbo 🎉🎉🎉🎉🎉ya chakwera 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@EphraimNyirenda-e3s
@EphraimNyirenda-e3s 2 сағат бұрын
Nyimbo iyiiiiii ikangolila ndkt China Chake chachitika😭😭😭
@BlessingsCperumal
@BlessingsCperumal 2 сағат бұрын
Are u seriuos
@GraceMakawa-b8e
@GraceMakawa-b8e 2 сағат бұрын
Ndipo zoona
@PeterNamphwanya
@PeterNamphwanya 3 сағат бұрын
Tivine kaye koma otsaiwala mother's day ikubwela🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb 2 сағат бұрын
Commission of enquiry ija anakoza
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Сағат бұрын
Nde Mene dzatelemu Dani Lu mukuti bwanji apatu nde ndalama dzija simudya kujijilika umakagwa matope mubwelelaso kwa Dade kapena Mwangi Taya thawi pachabe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 Сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@adsonphiri6497
@adsonphiri6497 Сағат бұрын
Guys kodi zikuti bwanji tiuzeni bwino
@rashidadan2533
@rashidadan2533 2 сағат бұрын
What goes around comes around
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 28 минут бұрын
Honest this ikayikidwa something happens
@ellensambo6323
@ellensambo6323 3 сағат бұрын
😢😢 nyimbo iyi mmmmm Ambuye ankhuze Malawi
@ThomasChiwaya-qx9mf
@ThomasChiwaya-qx9mf 2 сағат бұрын
Ndikufuna Charly patache choipa chisata mwini
@Mpungwe123
@Mpungwe123 2 сағат бұрын
Iponyedwa imeneyo bwana khalanibe pompa zitheka ndithu
@kingstonekalonga8435
@kingstonekalonga8435 3 сағат бұрын
Achimwendo Mulipo koma kumeneko kkkkkkkkkk azanu oipa mtima ndamenewo ikwaswndera ifa 😂😂😂😂😂
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 сағат бұрын
Apule mungamuphe mzanu atagwira colona zoona? Colona ndi woopsa lero ndi zimenezi dzakutsatilani, ngati zikumbvekazi zili zowona
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 3 сағат бұрын
Oyenda ndilupanga azafatso ndilupanga,palibe wamuyaya pa dziko ask kamuzu Banda
@festongreston
@festongreston 3 сағат бұрын
Let the will of God fulfill
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw Сағат бұрын
Nyimboy simatuluka wamba ikatuluka choncho kumakhala kuti wina Akuonana maso ndi maso ndi anthu omwe anasogoza.
@EstherMaonga
@EstherMaonga 2 сағат бұрын
Ine ndimafuna asafe nsanga azamangidwe kaye ndikuyankhanso milandu
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Сағат бұрын
Mmmmm chikangawa mudzimu yawanthu 9 ija ikukudikila
@HassanSaid-q8q
@HassanSaid-q8q 2 сағат бұрын
Yaaa pano ukuona bwanji kumene uliko..mulungu siosewela naye
@MoosaSidrick
@MoosaSidrick 4 сағат бұрын
Komabe apete watikwana athu Akufa ndi njala usiku onseu ndimangopephe kuti apite ndithu tikapeza komweko achilima Ali paseu akukudila abwana
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka Сағат бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pomuyika aliyese ukhudzidwa pa ifa ya chilima
@WisdomChimalizeni
@WisdomChimalizeni 3 сағат бұрын
Nyimbo ilibwino iyi🇲🇼 oyimba analosera kale
@ShadidaAwal
@ShadidaAwal 52 минут бұрын
Apite bas chakwera galu kwabas 5q
@TiwalumbeNathan
@TiwalumbeNathan 3 сағат бұрын
Let GOD BE GOD
@RabeccaKagona
@RabeccaKagona 41 минут бұрын
Kodi zikut bwanji kumalawiko abale
@user-nt5yn2im6t
@user-nt5yn2im6t Сағат бұрын
Thanks Lord
@Richardbanda-hg6pt
@Richardbanda-hg6pt Сағат бұрын
Let's pray for Malawi something happen
@ThomsonChipwele
@ThomsonChipwele 3 сағат бұрын
Akafa tisangalala
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 3 сағат бұрын
😂😂😂
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 сағат бұрын
Tizika janza nyimbo yomweyo pa bingu stadium
@MarkManyowa
@MarkManyowa 4 сағат бұрын
Akamwalira nanga ndalama asiila ndani🤦 Zimangoona kuvuta koma kuzikonda kuja nkosapindulitsa
@FlorenceDouglas-x5c
@FlorenceDouglas-x5c Сағат бұрын
Koma ma comments ali apa mmmmm 😂😂, ine lelo ndiumwa mowa size kukana pati !!!! 😂😂
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga 3 сағат бұрын
Mulungu amava ndithu
@AugustineChimaliro-e5i
@AugustineChimaliro-e5i 3 сағат бұрын
Achimwendo mwazukako bwanji nthupi
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 3 сағат бұрын
@@AugustineChimaliro-e5i kkkkk
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 сағат бұрын
Kkkkkkk km guys
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 сағат бұрын
Paja amalondola misonkhano yanzawo tiyenitu ku chinamwali kuzomba kuli msokhano lero 😂😂😂😂
@fannyzimba149
@fannyzimba149 2 сағат бұрын
😂😂😂😂😂kamaliremba kkk ndi mzake Jezebel kkk
@omarajibu860
@omarajibu860 4 сағат бұрын
Very educative song
@LinlyMatheweKufakwina
@LinlyMatheweKufakwina Сағат бұрын
😂😂😂😂aaaaaa komatu Malawi muli ndi chipongqe iiiii
@KhadijaMsosa-d7z
@KhadijaMsosa-d7z Сағат бұрын
Amalawi sititha kucheza😂
@NancyLennoh
@NancyLennoh 53 минут бұрын
Kmanso tili pa changu kwambiri 😹🙌🙌🙌
@KettieNathaya
@KettieNathaya 3 сағат бұрын
Chikangawa hoyeeeeeeeèe ukawapatse mon anthu 9 aja
@BonfaceMpokosa
@BonfaceMpokosa 4 сағат бұрын
Ndikhale mbuli ine chete
@AllenBanda
@AllenBanda 4 сағат бұрын
Only God knows
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika Сағат бұрын
Chikangwa kkkkkk
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 3 сағат бұрын
Ukayamba ndi zomwezo umamaliziranso zomwezo,kuyamba ndege kuikwera eeeee mkutsazikana nayonso.
@RoyTrading-b4x
@RoyTrading-b4x 3 сағат бұрын
Blessings Chimangeni on repeat 🎉🎉
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 4 сағат бұрын
Rip chakwelq
@MonijaKataika
@MonijaKataika 3 сағат бұрын
🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔 😭😭😭😭😭😭😭😭😭 🤐🤐🤐🤐🤐🤐🤐🤐🤐 Whatever it is God save Malawi..
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 сағат бұрын
Guys maliro Achakwera alephereka ali moyo wapita ku Israel panop nkhondo ija yavuta anaivotera ija wapita koleresa ndthu usiku Lebanon yaphulisa Israel anthu awiri afa ndye Chakwerayo alikumeneko ndthu
@LonjezoChitseko-lx4qb
@LonjezoChitseko-lx4qb 3 сағат бұрын
Akafa ntendere ufika mmalawi
@JosterNgalawa
@JosterNgalawa 2 сағат бұрын
Apaso chimwendo wasala ndi days yokha ulosi wanga watelo the 4th is kamajekete
@LameckLubanimbewe
@LameckLubanimbewe 3 сағат бұрын
Palibe wa muyaya
@issahmaloto9141
@issahmaloto9141 4 сағат бұрын
Ndichita choyenda maliseche lamulungu lino
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 3 сағат бұрын
Mpaka kuyenda maliseche😂😂😂😂😂
@samchibenene4458
@samchibenene4458 3 сағат бұрын
😂,,,
@AnthroGondwe
@AnthroGondwe Сағат бұрын
Nyimboyi ankolo unaiphazamula tatengerapo phuzilo
@EyobeAyala
@EyobeAyala 3 сағат бұрын
Koma guys zoonad izi kapena ndikulota tandizuseni ine
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 3 сағат бұрын
Iyi ndiye tiyivinadi 😂😂😂😂
@LameckNgwangwa
@LameckNgwangwa 4 сағат бұрын
The more u plant the more u harvest
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu 33 минут бұрын
Mau akulu akoma akagonera.
@trickermussa472
@trickermussa472 3 сағат бұрын
Or angoika komko plz
@LawrenceBamusi
@LawrenceBamusi Сағат бұрын
Ndee ena akuti Usi akungotola ma 3 points awulere😂😂😂😂
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Сағат бұрын
ODI nkagule data ine kkkkkkkkkkkkkk😂😂😂😂😂😂😂😂 yomweyo
@JosephIsaac-s1c
@JosephIsaac-s1c 3 сағат бұрын
Best song ever, once I hear this song I feel cry
@patricksamson4852
@patricksamson4852 3 сағат бұрын
Tidikire ntanyiwa
@JrAlfeoLungu
@JrAlfeoLungu 3 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 ndipo isaphonye ikulondola ndiku garden city
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 сағат бұрын
Mulungu atimvera chisoni ife anthu ake ndipo satana ameneyu wawononga dziko labwino linja
@MuhammadPyson
@MuhammadPyson 2 сағат бұрын
Ammbuye tengen chikangawa
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 4 сағат бұрын
Ndi wamwayi amene amabwelako ndi moyo ku Galden city koma Mulungu akukhuzeni nonse omwe muli kuchipatalachi imfa siyabwino ngati kuli moyo.Moyo kunyenga nthawi yolapa inalipo koma chuma chimanyenga
@MarkManyowa
@MarkManyowa 4 сағат бұрын
😂😂😂😂😂
@MarkManyowa
@MarkManyowa 4 сағат бұрын
Imfa yanji yokondweretsa 🤣😂🤣🤣 Koma ngati sizitheka panopa His days are numbered for sure 😂
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 3 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂​@@MarkManyowa
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂​@@MarkManyowa
@MarkManyowa
@MarkManyowa 3 сағат бұрын
@@ElizabethMulinde 🤣🤣🤣🤣 Akanangopenga Misala onse omwe anatenga nawo mbali pa plan yozimitsa Chilima ndi ena onse aja
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 3 сағат бұрын
Kamajete next
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 3 сағат бұрын
Dankie
@eunicesaiti
@eunicesaiti 3 сағат бұрын
Merci/ Obrigado
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 сағат бұрын
Ndigawa mpunga waulere zikakhal zoona guyz
@GraceMakawa-b8e
@GraceMakawa-b8e 2 сағат бұрын
Mutigaireko
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 сағат бұрын
😅😅😅😅kwachemeratu nanga team yatenga chikho 😅😅
@GoldenHappy-gt6ld
@GoldenHappy-gt6ld 2 сағат бұрын
Ngati zili zoonadi Malawi wapulumuka
@MosesTangwe
@MosesTangwe 2 сағат бұрын
Kanyimbo aka anakomza
@EnerstManess
@EnerstManess 4 сағат бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉Fire 🔥 🔥 🔥 🔥
@KentWilliam-r2v
@KentWilliam-r2v 3 сағат бұрын
Wamwalile bsj
@patesnkajenda4258
@patesnkajenda4258 Сағат бұрын
Kwagwanji kumalawi guys😂😂😂😂
@SmartDavison-nv6ue
@SmartDavison-nv6ue Сағат бұрын
Thambo lakuda lagwa
@CannyMpehla-d1s
@CannyMpehla-d1s 2 сағат бұрын
kod wafadi
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 3 сағат бұрын
Ineyo sindufuna afe,, koma akhale ndi moyo kuti adzazione ndi maso
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 2 сағат бұрын
Ndikukagura sound music basi
@StoniaMoyo
@StoniaMoyo 2 сағат бұрын
Ngati zilitere go well mr chikangawa
@MlambeLodge
@MlambeLodge Сағат бұрын
Afe ndithu akamumange ndimulungu
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 4 сағат бұрын
NDILI KU MSIKA NDIKUDIKILIRA CHI GALIMOTO CHA NKHUKU😂😂
@Martha-m6e
@Martha-m6e 3 сағат бұрын
❤❤❤❤
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 4 сағат бұрын
NDILI KWA TELALA KUSOKESA BLACK CHEERS❤❤❤❤❤
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u 4 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 4 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 3 сағат бұрын
😅😅😅
@WisdomChimalizeni
@WisdomChimalizeni 2 сағат бұрын
A St chikangawa mphakati akaphikira kuti kumene kukuoneka kuti kungakadyeke bhoo😂😂
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 54 минут бұрын
Osayiwala kulongeza tsabola wa kambuzi okadyera nyama ku siwa ku kasiyaa hehehehehehe
@EsetaGerate
@EsetaGerate 4 сағат бұрын
😂😂😂😂😂 komatu mukhalike Kodi chikangawayo wafa kapena chani 😂😂
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 сағат бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥😂😂😂😂😂😂
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂 afelanji munthu wakumpa adzake
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc Сағат бұрын
Ndipasen cret ya kuchekuche
@TimothyNkhutembaChirwa
@TimothyNkhutembaChirwa 2 сағат бұрын
Azipita
@ronaldordinga6537
@ronaldordinga6537 4 сағат бұрын
Guys guys kumakhala chisoni😢😢😢
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg 3 сағат бұрын
Rip
@patricksamson4852
@patricksamson4852 3 сағат бұрын
Chakwera sangafe mukunama my president if fit and strong mpaka 2030 woooooooooo
@umalimaganga
@umalimaganga 3 сағат бұрын
Are they saying he is dying Kodi? Or you are thinking like that
@MariaNyamwera
@MariaNyamwera 4 сағат бұрын
Kkkkk kkk koma kumeneko chete ku ma stand
@HakimMataka-t8z
@HakimMataka-t8z 4 сағат бұрын
Manganya wa chithola chikwama BC he is in charge
@UmaliMmussa
@UmaliMmussa Сағат бұрын
Kumenya kugwetsa 😂
@Lushaka
@Lushaka 2 сағат бұрын
E guys don't trust politics please stop stop u must respect to one another u busy talking shirt about Peter or chakwela guys Malawi still going down
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 2 сағат бұрын
How you treat people they'll treat you the same way don't treat people like cabbage
@MzadziWanga
@MzadziWanga 3 сағат бұрын
😂😂😂😂 maliro amaneo musayesere kuwaleperetsa achakwera chifukwa nde tasoketsa kale uniform ya black 😂😂😂
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 3 сағат бұрын
😅😅😅😅iiiiiiio
@WisdomChimalizeni
@WisdomChimalizeni 2 сағат бұрын
😂😂 kumalawi mkokoma koma vuto atsogoleri anthu amatibera happiness
@VitumbikoKaunga
@VitumbikoKaunga 4 сағат бұрын
Zikuti bwanji kulilongwe uko timasuleni
@NayisoniMthato
@NayisoniMthato 4 сағат бұрын
Rest in peace
@ChanceZambika
@ChanceZambika 2 сағат бұрын
Kkkkkkkkkkk
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 3 сағат бұрын
😅😅😅😅😅😅
@AubreyNdeule
@AubreyNdeule 4 сағат бұрын
Kkkk mwatibwanj ku chikangawa?
Nkhani ya Chakwera mene zili inu mukuti bwanji?  Chakwera
5:58
Jay Kawere TV
Рет қаралды 56 М.
Which One Is The Best - From Small To Giant #katebrush #shorts
00:17
Зу-зу Күлпаш 2. Бригадир.
43:03
ASTANATV Movie
Рет қаралды 464 М.
My Daughter's Dumplings Are Filled With Coins #funny #cute #comedy
00:18
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 23 МЛН
When Royal Guards Fight Back!
8:08
Fighting Spirit
Рет қаралды 6 МЛН
Chikuchitika ndichani Amalawi 🤔
2:21
Malawian Cameras
Рет қаралды 5 М.
SIFE MW - AMAFUKENI FT K BANTON & JOLASTO
4:48
TK ENTERTAINMENT
Рет қаралды 21 М.
Abwana ndi ulendo - blessings chimangeni (Official Music
5:15
Uncle Paul Mw🎵🎵
Рет қаралды 2,8 М.
[WATCH LIVE] Julius Malema Addresses The Media
Cool Buzz TV
Рет қаралды 184
Оё инҳо мухолифанд ё роҳзан?
56:34
Ояндаи Миллат | Будущее Нации
Рет қаралды 20 М.
KANKHA - SKEFFA CHIMOTO
6:03
Skeffa Chimoto Music ♪
Рет қаралды 187 М.
Which One Is The Best - From Small To Giant #katebrush #shorts
00:17