Chikuchitika ndichani Amalawi 🤔

  Рет қаралды 19,134

Malawian Cameras

Malawian Cameras

Күн бұрын

Пікірлер: 140
@MercyChipeta-h4d
@MercyChipeta-h4d 2 сағат бұрын
Iwo a president osayankhulapo bwanji pa zonsezi, nanga nduna even imodzi osasusa zomwe anthu akuyankhulazi, something is wrong somewhere 😮😮😮
@fannyzimba149
@fannyzimba149 2 сағат бұрын
Chilungamo chilipo penapake akuchidziwa
@EdwinMbewe-wu9jd
@EdwinMbewe-wu9jd 2 сағат бұрын
Hi got no time for this nonsense
@MikeEvason-rx4qf
@MikeEvason-rx4qf 2 сағат бұрын
Am with you🎉
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 2 сағат бұрын
No smoke without fire... something is not right here
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu 2 сағат бұрын
Exactly sister
@whatsonbanda4277
@whatsonbanda4277 Сағат бұрын
Pena umapenya dimu.
@GiftNgwira-e8l
@GiftNgwira-e8l 3 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Sikusonyenzeratu kuti anthu chakwera sakumufuna waononga dziko lamalawi
@AmzeruOsakala
@AmzeruOsakala 33 минут бұрын
Alomwe osat dziko
@OwenchangnyaMkandawire
@OwenchangnyaMkandawire 39 минут бұрын
Kusauza Malawi choona kumasonyeza poyela Kuti adindo alibenawo ntchito amalawiwo.kudzimva, kudzikonda.matenda wutha kubisa koma imfa sungabise.useless government with useless people.
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 3 сағат бұрын
Afe watikwana tilibe naye ntchito munthu wankhanza
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 39 минут бұрын
Bola zikhale zoona please my God uyu chakwerayu mutengeni basi
@SaidyKamala-jj7lo
@SaidyKamala-jj7lo 2 сағат бұрын
Guys tikapuma kumwamba amalawi seriously 🎉🎉🎉🎉🎉
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 3 сағат бұрын
Akachita zabwino umalandira zabwino Ukachita zoyipa umalandira zoyipa
@HajjAmadu-e1u
@HajjAmadu-e1u 3 сағат бұрын
Koma abale chonde Mulungu wa kumwamba mutengeni satanayu atitha ndthu
@mailos.laisoni7001
@mailos.laisoni7001 2 сағат бұрын
mutenga aise ukhare phee mesa abwera kuno ku garden. City 🏙️ afa Phee
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 40 минут бұрын
Azinka asaaa! satana otheratu
@somzyg-wb1ez
@somzyg-wb1ez 3 сағат бұрын
Zikachitika tionela kwa inuyo
@JoelKacheche-x6i
@JoelKacheche-x6i 35 минут бұрын
Anthu ena mimba zawo ndizo Zaza ndi mpweya wamabodza,President chakwera alipo sangafe mwawuchisiru monga anthu mukuganizira ndipo akuyendesabe boma mpaka 2030.Moti ena omwe mukusangala pakalipano musogola kumwalira president chakwera alipobe.
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy Сағат бұрын
Kaya wafa kaya sanafe we don't care about him 2025,,is coming soon
@JemesMalawa
@JemesMalawa 2 сағат бұрын
Abwele ku ntundu wamalawi atiyakhule tiwanve ngattidi ali moyo pajatu amatu kususa galu mkukumba 😊😊
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa Сағат бұрын
Abwele azatanunso ngt wafa wafa basi,wachita bwino kufako watikwana wakumoto bas.
@trickermussa472
@trickermussa472 Сағат бұрын
Akudandaula ndani bcz amene akusangalala taona?
@MalawianCamera
@MalawianCamera Сағат бұрын
Muft mwatani kodi 🤣🤣 alibe azibale ao apulewo? 😂😂
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain Сағат бұрын
Koma muthu wadwala, akanapanga address the nationa ,kutiuza za well being ya muthuyo, a spokesperson awo, kuli akubanja, kuli ma minster, cabinet, we need to be up dated on our pastor
@HarryKandani
@HarryKandani 2 сағат бұрын
Lets wait till mawalo tiwaona ku limbe komenya golf
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k 38 минут бұрын
Zinachitikanso kuLilongwe Bingu atamwalila achewa anasangalala Apopo ndiye wina aziloza chala kumwela?
@isaacmanjele6487
@isaacmanjele6487 36 минут бұрын
Zaboza ndithawi yomwe micheal usi amapanga za neef kenako wina ayikapo mau ake aboza propaganda at its pick
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 Сағат бұрын
Kumwalira kwa ma President onse ndikhala ndikumadandaula kuti bwanji Ambuye nwatenga Kamuzu Banda,bwanji mwamutenga Bingu wamutharika?koma na Chakwera yekha nditha Kusangalala kwambiri ngati zingakhale zowona kuti wamwalira chifukwa ndi wonzuza amalawi,chigawenga chakupha,wa boza ,wakuba misonkho ya amalawi ndinso mfiti yothelathu zimene zikumupanga kukhala mbuzi yama President yoyamba kumalawi kuno
@MusaMajudu
@MusaMajudu 3 сағат бұрын
Ya Allah amalawi anatopa nawo
@MMADICHANDE
@MMADICHANDE Сағат бұрын
Dzikoli amusiire mangayo asampomboneze chonde 😭😭😭😭😭😭😭😭
@ShymanJamaicasingini
@ShymanJamaicasingini 55 минут бұрын
😂😂😂😂😂
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 3 сағат бұрын
Ndipo nde tili ndiphwando weekend yi la mowa 😂😂😂😂😂😂
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 23 минут бұрын
Kalipo Kalipo maybe akudwala
@victorauwana7258
@victorauwana7258 49 минут бұрын
Awile dyechikangawa
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 сағат бұрын
mwasowa zonena kd anthu amen amakodwerawa malawi yotse kd
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 3 сағат бұрын
Ngat apule ali moyo abwele atìlankhule kuntundu wamalawi athetse phekeselazi
@PeterChimbayo
@PeterChimbayo Сағат бұрын
Koma akaona antha kudzinvera chisoni..
@BostonMalack
@BostonMalack 57 минут бұрын
Kodi ngati ndizowana nde chimanga chizingowa pa madenga ammanyumba mwathumu or fertilizer atsika mitengo komaso kuti umphawi tilinawo kumalawi kunowu ukutha akamalowa mmanda
@giftkayome3568
@giftkayome3568 Сағат бұрын
Ndinakakhala ine ndikanangotula pansi udindo apa zikuwoseratu kuti sakufunidwa
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 3 сағат бұрын
Tiva zonse madzulo ano kuti ndizoonadi wapita mulungu adalitse chakwela ngakhale ali ndikhalidwe loipa koma ndikumufunila zabwino komwe aliko
@BrightZionga
@BrightZionga 56 минут бұрын
Afe basi akudikila chani ngati pali achita iye kupatula kuba iyaaa
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 32 минут бұрын
Abale anthu kumasangalala chonchi kungomva kuti wina wamwalira? Which means something is wrong ngati asanamwaliredi a chakwelawo aganizepo bwino something somewhere is wrong
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin Сағат бұрын
HAHA pajatu amatelo president akamwalila amatha kulengeza kuti akachititsa msonkhano kwakuti Koma akudziwa kuti wafa, Inu dzikoli simunalisziwebe??
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 21 минут бұрын
🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔
@Belinda-c6e
@Belinda-c6e 2 сағат бұрын
Kusonyeza kuti manganya akhala president????????
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Сағат бұрын
Chakwela watisiya basi amalawi onse sanganame Okay ngati ndizabodza abwele atiyankhule chakwela apa
@HaroonAlibarara
@HaroonAlibarara 3 сағат бұрын
Dan lu zikuvuta iwe ngat wamwalira sunanjoye kkk
@FelistusEmmanuel-f1o
@FelistusEmmanuel-f1o Сағат бұрын
Waiting official results ndabuka kale nkhuku yachikuda 😅😅😅
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 33 минут бұрын
Zikom timakukonda komano zilipati akudwala kapena ayi?
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi Сағат бұрын
Abwele anene poyela galu amenei
@AgnessMakuluni
@AgnessMakuluni 3 сағат бұрын
Wapita wapita basi tione ngat ndalama zomwe adabazo aziike limodzi m'bokosi😂
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 сағат бұрын
Aaa anthu akatopa ndimunthu dzimakhala chochi tsikuti kuyamba ayi Bingu dzinatelo paka adapangitsa tsonkhono kuwawudza anthu ku mumati ndamwalila ine ndili moyo koma kenako ulendo unali omwewo NDE CHIMENE AKANAPANGA CHAKWELA NGATI ALI BWINO NSAKUDWALA NDI KUNGOYANKHULA KWA A MALAWI NDI ANTHU AMUKONGA CHIFUKWA ANTHU AMBILI NSITIMUKONDA CHAKWELA NDE INU A MCP KUDZANI NYUMBA YANU UMBONI NDIWUMENEWU ANTHU KUTSANGALALA KUTI WAFA PULE KUTI ANTHU ATOPA NANU ANTHU AKUMVUTÌKA KUCHUMA KU NJALA KU SCHOOL KUNTCHITO NGATI ALIBE PRESIDENT MALAWI MUNO KUTSIYANA KUMANGOTI BOMA NDILOMWELI MUCHEDWA NADZO VOTE ILI MUTIMATU
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa Сағат бұрын
Tiuzeni zoona ngt di wafa,kma ngt ndichoncho ai akakumana komweko ,kumene anamusogoza mzakeyo,kkkk ai jahena wabwino
@Halima-i4x
@Halima-i4x 3 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 ine nangodusamo 😅😅😅😅😅
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 2 сағат бұрын
Iiiiii ineso or phwandoli ndikhoza kukagulaso mowa saiz nditangova kuti wapita yes yes naneso ndingajowe mbaji😊
@EdwinMbewe-wu9jd
@EdwinMbewe-wu9jd 2 сағат бұрын
Zachamba izi ndipo ndizaziiiiiiiii
@SifatiMoses
@SifatiMoses 3 сағат бұрын
Zachamba apite ku gofo palibe zobitsa olo atafa tilibe naye ntchito
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 сағат бұрын
Eeeee koma zoona kusangalala kufa kwa munthu kkkk Apure ndekuti simmakhala bwino ndi anthu. Mkachira sinthani umunthu ngofunikira pamodzi ndi nduna zanu
@JoannaNAMA
@JoannaNAMA 2 сағат бұрын
Koma Ngati mpheketsera imasaduka choona mmmm mpheketsera imeneyi ikhale yoona basi. Munthu ameneyi waononga dziko lathu ayende bwino.
@AREFRIEDNELSON
@AREFRIEDNELSON Сағат бұрын
😂😂😂 atiwononga uyuuu osamamu yikilakunboyo bbbbb
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu 2 сағат бұрын
Chakwera watisiya bas, uthenga ndi umwewu bas don't wait for another report. Paja amati boma ndilomweli ifeso lero tikuti uthenga ndi omwewu bas
@EffitaKandiwo
@EffitaKandiwo 2 сағат бұрын
Hahahaha
@BeatriceLameck-x2o
@BeatriceLameck-x2o Сағат бұрын
Hahahah kma
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 сағат бұрын
Chakwera komwe uliko ngt ukufuna kukhal moyo zako zimenezo kaya ukufuna kufa zako zimenezo ihave no business with u REST IN PIECESSSSSS
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu Сағат бұрын
Leave him alone ,chakwera has along life
@ArronBenson-g6d
@ArronBenson-g6d 3 минут бұрын
😂😂
@NoelChalunda-j2g
@NoelChalunda-j2g 2 сағат бұрын
Kuweruza ndikwake Yehova
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin Сағат бұрын
Chiweluzo chilipamsi pompano inu 😂😂😂😂
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 сағат бұрын
Koma tipephe chilima ndi athu ena anawaphela. Kuchikangawa aja amukokele komweko asakhaleso ndi moyo sitikumufuna afe afe muthu oipa kwambili
@RaffickAllie
@RaffickAllie 2 сағат бұрын
Zikapsa mutiudza nafe makombora tilidze
@fannyzimba149
@fannyzimba149 2 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@Stretor
@Stretor 2 сағат бұрын
Ngakhale kufunira nzako kulowa manda ndi tchimo koma na apa pokha bola zikhale zoona munthu yu watizunsa kwambili
@MuhireDominic-rw4vf
@MuhireDominic-rw4vf Сағат бұрын
Totholan ndevu zonsezo baba😂
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 сағат бұрын
Or atakhal kuti alimoyo palib Malawi angachite manyazi apa tamtuma ndfe kuti kumwalirako kulephereke apita dzikol alingati chakwera akampeza mzake Idi Amini
@usherjamson174
@usherjamson174 Сағат бұрын
😂😂 😂😂
@danielmagwaya1074
@danielmagwaya1074 2 сағат бұрын
Rest in peace Chikangawa Chakwera
@moureenmolesi
@moureenmolesi Сағат бұрын
iwe khala cheteeee boma likubisa izi wafa ameneyo
@Aubreysekeyah
@Aubreysekeyah 2 сағат бұрын
Koma nde atangolengexa kungavute
@JonerdandhamuzMisokwe
@JonerdandhamuzMisokwe 2 сағат бұрын
😂😂😂😂koma ndizonadi izi
@IqrahSikweya-wm5mn
@IqrahSikweya-wm5mn 2 сағат бұрын
Kod nanunso zot Chakwera wafa ndindan angatsimikize... Angabwere mkulemba kuti wafa mwa easy?.... ka wafa or Ali ndi moyo we don't care.................. Ma research anuo sangagwire ntchito so far
@SUNGANANIGONANI-l5d
@SUNGANANIGONANI-l5d Сағат бұрын
Ngati zili zabodza ndekuti atiyankhula
@kambauwasammy4480
@kambauwasammy4480 2 сағат бұрын
Ndiye iweyo ukufuna ife titani zazi qlipo qtolqnkhqni qmzeru qmene timawqtsirq iweyo ndiopusa
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 2 сағат бұрын
Yes tiuzen zoona please 😢
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 3 сағат бұрын
Apitabasi palibeso sbuza😂😂😂 chikangawa wamwawlila
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 2 сағат бұрын
Some one do manager the page
@JogaJoseph
@JogaJoseph 3 сағат бұрын
ifetu ma Chanel omabisa khani timadana nawoo mwava etiii ngati mumaopa kumangidwa bwanji osakayamba ulimi eeee
@FatsanTobiyas
@FatsanTobiyas 2 сағат бұрын
Chitsime chikaphwa ndiye
@MosesChazima
@MosesChazima 3 сағат бұрын
Ngat alipo aziwonesele wapita ameneyo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 сағат бұрын
Iiii apite kwachayo adzikagwesa komko kumandako komas ngongole yokwana 16tillion akabweza komko iiiiiiii
@RashidMachika
@RashidMachika 2 сағат бұрын
Oloso ine ndigula nyama ndidye ngat zili ziona
@ellensambo6323
@ellensambo6323 2 сағат бұрын
Limenelo ndiye dziko lapansi ndi anthu ake
@KhadijaMsosa-d7z
@KhadijaMsosa-d7z 3 сағат бұрын
Komatu amalawi sititha kucheza😂
@IyshaBakali
@IyshaBakali 2 сағат бұрын
Vuto lake ndiloti akhoza kudzuka pajatu ndi wanyau
@Ever-yn1ke
@Ever-yn1ke Сағат бұрын
Wachita bwino ameneyo
@MosesDicostar
@MosesDicostar 3 сағат бұрын
Koma ngat asanafe ndy ndkamumaliza ndekha
@JonerdandhamuzMisokwe
@JonerdandhamuzMisokwe 2 сағат бұрын
Ndipo tikakhara limoz😂😂
@Stretor
@Stretor 2 сағат бұрын
Kkkkkkkkkkkkk
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 сағат бұрын
Mundiuze mukamanyamuka achimwen pliz
@BrandinaMphuka
@BrandinaMphuka Сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂
@MosesDicostar
@MosesDicostar Сағат бұрын
Musandisye ndekha
@IsmaelSaide-bp5ft
@IsmaelSaide-bp5ft Сағат бұрын
Let him go
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 сағат бұрын
Ndipo live pano tinyadile kwambiri
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 54 минут бұрын
Kkkkkkkkk
@VdMzembe
@VdMzembe 2 сағат бұрын
Wichita makora kufwa
@YasiniDickson-r8b
@YasiniDickson-r8b 2 сағат бұрын
Ameneyo afe Chocho
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 3 сағат бұрын
God bless you brother thanks
@MalawianCamera
@MalawianCamera 3 сағат бұрын
Thank you too🎉🎉❤
@PeterBartonMadeya
@PeterBartonMadeya 3 сағат бұрын
Apita ku golf mkono uli okufa akamenya bwanji? anthu chipongwe
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Сағат бұрын
Apite basi
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 3 сағат бұрын
Kuzemba kwabwanji uku chikangawa😅
@ErnestAllex
@ErnestAllex 2 сағат бұрын
Kma ngat wafa mukanangoinyotola wezi nkuku zisanatalikile plz😊
@BrandinaMphuka
@BrandinaMphuka Сағат бұрын
Kkkkkkk koma athu mwatopa eti
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 3 сағат бұрын
Ngati amwalira nde apita bwanji ku gofo.. alipo
@AllieKaisi-je6rm
@AllieKaisi-je6rm 3 сағат бұрын
Kufa munthu kusangalala zoona dziko lapansi
@DivineMercy-df2pu
@DivineMercy-df2pu 3 сағат бұрын
Mene MCP inasangalarira mene Bingu atafa .. this life is what goes around comes around.
@CharityMhone-uk9ym
@CharityMhone-uk9ym 2 сағат бұрын
Zikisiyan pati atafa bingu, Joyce Banda ndi Lucius ndi anthu Ake Anali pa chimphwando ku hotel nde asiyen anthu asangalala ntchito zake zimutsata 😮😮😮😮😮 ngati anali wabwino bwenz anthu akulira ndepoti chinali chigawenga basi😮😮😮😮 chipite
@KentWilliam-r2v
@KentWilliam-r2v 2 сағат бұрын
Eya Kaya chifukwa ndi munthu oyipa
@SteveNkhambule
@SteveNkhambule 2 сағат бұрын
Nde what's funny
@RACHEALKanyenda-b8f
@RACHEALKanyenda-b8f 3 сағат бұрын
Koma Malawi kokoma
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 3 сағат бұрын
Koma anthu ndiye achita manyazitu akamuona Ali ku golf club sartaday lo
@WisdomChimalizeni
@WisdomChimalizeni Сағат бұрын
😂😂😂 Kaya apita sizikutikhuza tudikira Kumkuyu amalengeza za dongosolo la maliro kuti a Blantyre tikasonkhane ku Sanjika Palace
@ManessMaande
@ManessMaande 3 сағат бұрын
Zosakhara bwino mmmmmm
@GaveniShalifu
@GaveniShalifu 3 сағат бұрын
Tiwuzeni zowona zake tiziwe
@ChikuChatenga
@ChikuChatenga 2 сағат бұрын
😂
@HassanjamesKananjie-q7s
@HassanjamesKananjie-q7s 3 сағат бұрын
Basi zikhale chonco
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 3 сағат бұрын
Timva zonse
SHAPALAQ 6 серия / 3 часть #aminkavitaminka #aminak #aminokka #расулшоу
00:59
Аминка Витаминка
Рет қаралды 2,8 МЛН
Epic Reflex Game vs MrBeast Crew 🙈😱
00:32
Celine Dept
Рет қаралды 18 МЛН
iPhone or Chocolate??
00:16
Hungry FAM
Рет қаралды 58 МЛН
Running With Bigger And Bigger Lunchlys
00:18
MrBeast
Рет қаралды 131 МЛН
How to win a argument
9:28
ajaxkmr (ajaxkmr1986)
Рет қаралды 594 М.
LIVE: Reform UK announce private prosecution of men in Manchester Airport fight
34:06
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 13 М.
'Is The Border Secure?': Pat Fallon Grills Dem Witness On Border Security
5:28
ISRAEL ATTACKS IRAN
20:07
NEWS9 Live
Рет қаралды 70 М.
Mkhwebane R10 million gratuity ruling
51:35
SABC News
Рет қаралды 26 М.
ABWANA PAULENDO - BLESSINGS CHIMANGENI
5:20
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 25 М.
TRACKING MILTON: Uninterrupted Live Cameras in Milton's Path | LiveNOW from FOX
11:55:00
SHAPALAQ 6 серия / 3 часть #aminkavitaminka #aminak #aminokka #расулшоу
00:59
Аминка Витаминка
Рет қаралды 2,8 МЛН