ACHAKWERA ABWERAKO KU ULENDO INVAN MAFUNSO AYANKHA KUCHOKERA KWA ATOLANKHANI |

  Рет қаралды 10,513

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 75
@robsontyg3928
@robsontyg3928 2 ай бұрын
Welcome back bwana Chakwela mmandivetsa kukoma
@ChimwemweJuwao
@ChimwemweJuwao 2 ай бұрын
Welcome Mr chikangawa
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado 2 ай бұрын
Mmatathauzo achiani garu iwe kumangokhalira kuyenda yenda ngati ukumwa panadol
@KumbukaniChimbalanga
@KumbukaniChimbalanga 2 ай бұрын
Mwini wa channel chimenechi ndi chitsiru
@KassimSteven-j1z
@KassimSteven-j1z 2 ай бұрын
Kkkkkk koma mene akulakhuliramo amulandara sakuwoneka mene amalakhulila akabwera
@MiracleMalichi
@MiracleMalichi 2 ай бұрын
Ulendo wanu mwabwerako ku Germany ndikutali koma achilima wa ku mzuzu sanabwerere hu!!
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 2 ай бұрын
😎
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 ай бұрын
Kodi ulendo uliwonse wa ku Mozambique, nkhani yake muzingoti Magetsi? For how long?
@IjilanMwalija
@IjilanMwalija 2 ай бұрын
Data yanga ine😢😢😢😢😢😢
@FrankHaruni
@FrankHaruni 2 ай бұрын
😢😢😢😢 ndaonongadi bs
@DL2004-x9q
@DL2004-x9q 2 ай бұрын
😂😂😂abwelako a Chadula
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 2 ай бұрын
Wabwerako zimene unasiya wazikwaniriska kupha anthu
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 2 ай бұрын
Pamako As they say it
@michaelchimwala-x8t
@michaelchimwala-x8t 2 ай бұрын
Chitsiru mbuzi garu wakupha wabodza nyani uyu
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 2 ай бұрын
Zokomera wekha zimenezo
@JoseKeyaton
@JoseKeyaton 2 ай бұрын
Kudari chifunga lelo Koma afika opanda VUto Koma uyuyu ndifiti guys
@franciscomalola92
@franciscomalola92 2 ай бұрын
zoona mr chikangawa ulemu wanu
@DalitsoMichongwe
@DalitsoMichongwe 2 ай бұрын
Ayi zikomo🙆
@MaxwellMilanzi
@MaxwellMilanzi 2 ай бұрын
Kkkkkkkk km ine ndingonse bas
@Bernardwisck
@Bernardwisck 2 ай бұрын
Pantumbo pake chakwera inunso atola nkhani bwino nadzo mulangidwa nadzo amalawi ali okhumudwa ndi odandaula
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 2 ай бұрын
Akanangoti ndinapita kokakwera njinga komanso ndinatchera diwa loti ngozi zichitike ine kulbe.Munthu oipa kwambiri.
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 2 ай бұрын
Zaziiiiiiii mulungu salakwitsa kalikose adziwa pomuyika ameneyi
@KassimSteven-j1z
@KassimSteven-j1z 2 ай бұрын
Omwewo akuwaphawoso
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef 2 ай бұрын
Kutenga nyanga kumeneko
@HaliJana
@HaliJana 2 ай бұрын
MUUZENI CHAKWERA KUTI PAMTUMBU PAKE
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 ай бұрын
Amalawi tisalile ife ndi anthu wotengeka si mumati peter sakulamula bwino achoke mulungu anakuyankhani anachoka lero musamve kuwawa tonse ija ndi imeneyo nsanje ndi yoipa kwambili kumulanda peter boma ndi mademo lero musalile 😂😂😂😂😂😂
@DL2004-x9q
@DL2004-x9q 2 ай бұрын
Malemu Chilimanso osaiwala ndi amene anali mmodzi mwa anthu akuluakulu omwe anamuchotsa Peter pampando
@mandelahindu9226
@mandelahindu9226 2 ай бұрын
Koma chakwela guys pakamwa pake za ubusa basi chifukwa sadziwa chomwe akuchita kumangopitiliza kunama basi ayi zikomo😭😭😭
@kubengovender6996
@kubengovender6996 2 ай бұрын
Iwe utule pansi udindo!! I we machende!! u can't see people are in hunger!! What you will solve that problem galu iwe!!
@ziwani3682
@ziwani3682 2 ай бұрын
Kuononga ndalama zochuluka zoyendera zausiluzo
@IdahMphaya
@IdahMphaya 2 ай бұрын
Zopanda nchere,pano tikudandawula anthu omwe ukuwapha osalakwawo apa ukulankhula zamanyi chikangawa iwe
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 2 ай бұрын
Ukundithela bundle yanga atalankhani ake nkukhalaso aku mbc aah manyaka enieni
@amoschataika7440
@amoschataika7440 2 ай бұрын
Kwenkweni mudapita kokalapa machimo aja eti?
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 2 ай бұрын
Chitsilu chikangawa
@CephasChibaka
@CephasChibaka 2 ай бұрын
No comment
@ComfortChiombangoma
@ComfortChiombangoma 2 ай бұрын
Atolankhani mumuuze Chakwelayo panyapake
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 ай бұрын
Chitsilu chamithu iweyo galu kwambili chakwela wava eti ukuwalakhulitsa athu zimene samafina akulakhula galu
@MichaelJannah-hn9qv
@MichaelJannah-hn9qv 2 ай бұрын
Chikangawa wakupha iwe
@JohnSoweso
@JohnSoweso 2 ай бұрын
He went there 1: for manipulation of report 2: To convince the Catholic clergy that he is innocent but we know that he is a madder 3:He is not shame of trips, he doesn't follow his words 4:He is useless not futurelistic 5: Corruptionist 6:15% of Malawians are elites 75% are poorest Malawi is the poorest country on Earth while it's Leader is on the move of touring other nations
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d 2 ай бұрын
Manyazi bwanji bwana empty speech chikangawa
@SildaKatundu
@SildaKatundu 2 ай бұрын
Waphindu ku anthu a Chikangawa nu,mcp
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 ай бұрын
Kkkkkkk uyo watopa ndi njinga uyo kkkkkkk😂koma tiona dzithu wina angoyenda yenda ndi tikuferanji, osapita ku Ukraine bwanji?mwina kukumana ndi anyamata a russia
@AustenMapoto
@AustenMapoto 2 ай бұрын
Chikangawa
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 2 ай бұрын
Mesa iweyo ndiamene unapanga mayere ako unagwesa vula ya phavu inangokokolora mbeu muminda nikupha anthu iya ungofuna magazi basi ife kumupoto tikhara ni president wanthu
@FrankChanza-l3g
@FrankChanza-l3g 2 ай бұрын
Kd apa a malawi mwatolopo Mfundo yoveka apa
@HendrickBanda
@HendrickBanda 2 ай бұрын
Mbuzi iwe
@Kelvin-hj5qv
@Kelvin-hj5qv 2 ай бұрын
Wosangonena kt munapita kukasokoneza umboni Report yagozi yandenge bwanji galu iwe ukhawula ase tiwonana nex Eyer
@victormbewe7462
@victormbewe7462 2 ай бұрын
Guys tiyeni tivomeredze kuti oimba sangoimba chabe koma amalosera patsogolo kuti tinasankha olakwika Ndiponso Baibulo silinama sionse amati ambuye ambuye akalowa Ku paladizo
@Drmuhammadchiwona
@Drmuhammadchiwona 2 ай бұрын
Gwape
@lizzymotika3895
@lizzymotika3895 2 ай бұрын
Abambo oyipa moyo awa
@ShadreckAustin
@ShadreckAustin 2 ай бұрын
Mulungu. Akuone
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 ай бұрын
Amalawi ukuwaphetsa galu chitsilu mamina Ali mutumo kuchuluka zedi ukhaula 2025 uona nyekhwe ukuwatengelela zoipa amalawi
@felixsaidi6715
@felixsaidi6715 2 ай бұрын
Satana Ameneyii akungowononga misonkho ya malawi
@souzajoaquim571
@souzajoaquim571 2 ай бұрын
Apule opanda m Fundo nkhumbatu nkhumba
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 2 ай бұрын
Ndipo 😂😂😂😂
@ajasikalonga3210
@ajasikalonga3210 2 ай бұрын
Komanso munthu ameneyu alibe mzeru,palibe chimene wanenapo apa shit
@Vascomw
@Vascomw 2 ай бұрын
Zaziiii
@MaxwellMilanzi
@MaxwellMilanzi 2 ай бұрын
😂😂😂
@giftkamwiyo9175
@giftkamwiyo9175 2 ай бұрын
Iwe ndi galu kwabasi kupita kukangokwela njinga basi
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 2 ай бұрын
Palibetu mfundo apa apule
@Makasigave-b9v
@Makasigave-b9v 2 ай бұрын
Mukanasainilana mgwilizano oti asamakugweseleni ndalama yathu ya kwacha zama maulendo apanyanja agogo abingu amati bwanji pa nkhaniyi inu nomwe achilima munayesesa kulephelesa nzanu atayamba kale ntchitoyi ili kumapeto mpamene osusa munalowesapo kaduka mpaka izi sizinatheke zanuzo ndiye zithekaaa? Mukanawachita suport agogo pano Malawi ali wina chifukwa zimene amapanga agogo zimapeleka chilimbikiso timaliona likutukuka dzikoli amakaniza ndalama yathu kuti chakuba chofiila chizisewelesa poichepesa mphabvu lelo anthu anu akulephela kugula kathumba kachimanga nima soap onunkha ngati uyu m'mene akudulila aaaa maulendo onsewo ma dollers angati amenewo? Ndiye mkumati forex is very major problem in this country? Fake news Lord knows please please world leaders try to make people unite the looking food to feed your people.selassie i
@alomuddin8801
@alomuddin8801 2 ай бұрын
Wabwerako kamachende unwanted prensident 4years without change anything, only to kill Malawian people, no one can love you mbolo yako wava ikungompha anthu kudzera kungozi za magalimoto tikudziwatu amalawi zose
@AustenMapoto
@AustenMapoto 2 ай бұрын
O pusa mbuzi
@JohnMeleka-s1t
@JohnMeleka-s1t 2 ай бұрын
Fuck
@karimshaik4485
@karimshaik4485 2 ай бұрын
Stupid president mbolo yako
@AustenMapoto
@AustenMapoto 2 ай бұрын
Are you fool
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 2 ай бұрын
😎
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 ай бұрын
Chitsilu chamithu iweyo galu kwambili chakwela wava eti ukuwalakhulitsa athu zimene samafina akulakhula galu
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 ай бұрын
Amalawi ukuwaphetsa galu chitsilu mamina Ali mutumo kuchuluka zedi ukhaula 2025 uona nyekhwe ukuwatengelela zoipa amalawi
@babranzima8120
@babranzima8120 2 ай бұрын
Zaziiiii
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 2 ай бұрын
😎
Mzwanele Manyi appointed MK Party chief whip
2:27
eNCA
Рет қаралды 35 М.
Reactions As Rwanda Shuts Down 5,600 Churches
8:02
Adeola Fayehun
Рет қаралды 282 М.
😜 #aminkavitaminka #aminokka #аминкавитаминка
00:14
Аминка Витаминка
Рет қаралды 2,2 МЛН
小蚂蚁会选到什么呢!#火影忍者 #佐助 #家庭
00:47
火影忍者一家
Рет қаралды 125 МЛН
How I Turned a Lolipop Into A New One 🤯🍭
00:19
Wian
Рет қаралды 13 МЛН
Assista na íntegra o Fala Moçambique 29/10/2024
Portal FM | Fala Moçambique
Рет қаралды 884
The must-watch moments of the CNN Presidential Debate
35:29
VP CHIWENGA LATEST
10:58
Rory Studios News
Рет қаралды 2,3 М.
The Problem With Elon Musk
42:46
Johnny Harris
Рет қаралды 4,9 МЛН
😜 #aminkavitaminka #aminokka #аминкавитаминка
00:14
Аминка Витаминка
Рет қаралды 2,2 МЛН