Akufuna kubera chisankho pogwiritsa ntchito ana

  Рет қаралды 17,566

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

23 күн бұрын

Пікірлер: 167
@user-pf5hu2pd2b
@user-pf5hu2pd2b 21 күн бұрын
The best speech since, this is a Man who stand for his country
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 22 күн бұрын
Akuluwa ndi Mchewa wen wen wa chigawo chapakati ndipo wayima pa chilungamo osaopa Ng'ona za MCP, Viva Malawi. ❤❤❤❤
@mafukenimasangwi5487
@mafukenimasangwi5487 21 күн бұрын
Chilungamo nchewa wen wen nayenso watopa
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 21 күн бұрын
Ndipo live ndi wanyau uyu wen wen kma wasankha kuima pachilungamo
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 22 күн бұрын
Apapa zingowonekelatu kuti chakwera kuzawina 2025 anthu sazalola ayi 😂😂😂. DPP ipondeni kumeneko 🇲🇼🇲🇼🇲🇼✅
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 22 күн бұрын
Apm alowa mophweka kwambiri and let's support him.
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 22 күн бұрын
@@patrickmacheso5062 yeah kwambili bro
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 21 күн бұрын
Mchewa opita ku sukulu uyu big up osamangosekerera zopusa ndalama a kudya okha😍
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 16 күн бұрын
Kkkkk simuvota kapena muvota nanga mukutanthauzanji​@@patrickmacheso5062
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i 22 күн бұрын
Oooooh.....my beloved Country 😢😢😢.....nkuluyu tigwirane naye manja...
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b 22 күн бұрын
Chakwera azipita kwa ku Rwanda 🇷🇼 pajatu anali mkulu wa zigawenga kumeneko ķwa Paul kagame
@EdwardRichman-zs5pl
@EdwardRichman-zs5pl 21 күн бұрын
Nde usamale tili pompano
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 16 күн бұрын
Mbuli iwe palibe chomwe ukudziwa
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 21 күн бұрын
Bolani tidzangovota popanda chaunzika coz ziku pita ku sizikhala bwino. Ndiposo awa ndamene atuluka poyera nanga omwe sanabwere poyera big up man ambuye akutetezeni🔥🔥🔥
@user-dq9oe8sp8k
@user-dq9oe8sp8k 15 күн бұрын
I support that mortion
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 21 күн бұрын
Mchewa odana ndizoputsa uyu❤❤❤❤❤❤❤❤
@LoveHere-ki8ck
@LoveHere-ki8ck 21 күн бұрын
Good speech my brother, Malawi need leadership like you ❤❤
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 21 күн бұрын
Kalembera wa pa central please chifundo kachale cancel it,,
@user-wg7bw7py3z
@user-wg7bw7py3z 22 күн бұрын
Zikomo kwambiri, Ndikuthokoza amabungwe wa kulowererapo
@AbuMussah-wi7gb
@AbuMussah-wi7gb 22 күн бұрын
The best speech number one
@Moses51
@Moses51 21 күн бұрын
Andu okonda Malawi ndamenewa
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 21 күн бұрын
Good seeds are still available in the garden of the Lord, congratulations 👏
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 20 күн бұрын
Sure
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 21 күн бұрын
May God bless you sir well spoken here
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 22 күн бұрын
Mulungu akalemba walemba bas ,zanjat Lalemba Khoma Kuti achakwera umfumu wawo walephera , zanjat Lalemba iri zonse zobisika mulungu wazisiya pa mbeeeee
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga 21 күн бұрын
Ndipo zowona
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 21 күн бұрын
Mbambande Mchewa wen wen Salute u bradah
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki 17 күн бұрын
You are the best dude! Keep exposing chakwera and his company.
@user-dx4zu1wv4q
@user-dx4zu1wv4q 22 күн бұрын
Best tv bakili muluzi
@HanishaissahKagansa
@HanishaissahKagansa 21 күн бұрын
Zambili mwalankhula kale ine ndingopereka madalitso kuti mulungu akudalitseni komanso musasiyile panjila chonde
@VictoriaWilly
@VictoriaWilly 15 күн бұрын
Kulankhula kwabwino zedi 🤝 Ana asaphwanyilidwe ufulu powagwilisa ntchito za ndale
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 22 күн бұрын
Chonde amabungwe tithandizeni amabungwe, not speaking only but let's unite and show them actions b4 it's too late plz😮
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 21 күн бұрын
Fact
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 22 күн бұрын
Kuyankhula kwabwino awudzeni amenenewo
@user-hd7wq2yc6m
@user-hd7wq2yc6m 21 күн бұрын
Nkhani ndiyoti justice Chifundo Kachali atule pansi udindo woyendetsa zisankho mdziko muno zaonekerathu sizizakhala za chilungamo
@MasiyeDayton
@MasiyeDayton 21 күн бұрын
Walankhu bwino kwambili a bro wa ❤❤❤❤❤❤❤
@QADA-D-MW
@QADA-D-MW 21 күн бұрын
Watching from Cape town graders
@user-iz1qi3db2g
@user-iz1qi3db2g 15 күн бұрын
Good job awudzen mr
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 22 күн бұрын
Nanenso ndine Mchewa koma chakwera ni manyi kapena osomera pa njira
@chrisboyce2
@chrisboyce2 21 күн бұрын
Ife kuno ku Ntcheu Central Chakwera tamukana ndipo tikufuna APM 💙 Zachibwana 2025 palibe
@user-mq2or1lz8h
@user-mq2or1lz8h 15 күн бұрын
Kuswa kuswa ngati akukana abwere poyera ife tapita zikomo 😂😂
@tamanimakawa7252
@tamanimakawa7252 17 күн бұрын
Good speech boss... Keep it up
@user-hi8qd8bz5f
@user-hi8qd8bz5f 22 күн бұрын
From a distance God is watching.... The politicians should know this is earthly things. The owner of this earth will soon come.
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 22 күн бұрын
Amen,,, soon Jesus the King is coming.
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 21 күн бұрын
God is in control
@islamaameen2177
@islamaameen2177 22 күн бұрын
I respect you bakili muludzi tv
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 21 күн бұрын
Bwana izi mukunenazi sizingatheke popeza bungwe la NRB linagulidwa ndi mcp party
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 21 күн бұрын
Amabungwe bwerani poyera tithese mchitidwewu, chifukwa kupanda kutero anthu ena azinyenga anawa mwadala ndipo musokoneza zina mwa ntchito kumabwalo a milandu maka pa nkhani zokhuza kugwililidwa Kwa ana, mukanyonzera uthengawu muzandikumbuka!
@mosesnyangato4900
@mosesnyangato4900 18 күн бұрын
Amabungwe , amene mukulikonda dziko lanu chonde lowereranipo pankhaniyi, dziko lionongeka ili
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 21 күн бұрын
Amabungwe keep it up mukuitha zedi
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 20 күн бұрын
Boma loyaluka paliponse..kukhala ngat mwana osamva ......heeeey km abusa mukulaula mipingo
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 21 күн бұрын
Very Good Bakili Tv ❤
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 21 күн бұрын
MEC, police,judges belong to mcp don't be cheated palibe chimene angachite
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 20 күн бұрын
Exactly
@MussaMalon
@MussaMalon 22 күн бұрын
Ayambire bas chakwera ndigalu
@user-if3vo1cl8j
@user-if3vo1cl8j 22 күн бұрын
Kalembera wa chiawo cha pakati akhasule ayambirenso
@yusufbanda4980
@yusufbanda4980 22 күн бұрын
Osokonezaso nd mafumu mmaderam chfukwa iwowo nd amene akuchta kuziona live koma chfukwa chot alandla kangachepe kamene kakuwapanga kugulitsa ma ufulu a anawa. Komaso a leader of opposition amafunika ayake kwambr pa nkhan ngat zmenez osat azngolandra nde akaonaso kt mmisonkhano mwawo mukudzadza akungoona ngat awna kale 😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@lilmajormajawa8855
@lilmajormajawa8855 21 күн бұрын
Exactly like here in kasiya
@christophermkhize1991
@christophermkhize1991 22 күн бұрын
Ulemu wanu big man timakunyadilani
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 22 күн бұрын
Powerful speech guys ❤❤❤
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 21 күн бұрын
Yes mean point they must cancel ayambileso kulemba chifukwa chakwela alemba mafana kwambili kulilongwe
@user-po6ir6eh4z
@user-po6ir6eh4z 21 күн бұрын
Kalembera ameneyo apange khasulidwe mcp yachuluka chinyengo amabungwe tithandizen kumenyera nkhondo zikoli lili mmanja mwa asatana
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 21 күн бұрын
Kumatu chakwela komaso naye khumbo ndi muthu opanda chilungamo mmm ambuye atione ife ku Malawi kuno
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 22 күн бұрын
Eishhhhhhhhhhhhh,,izooooo!!!!! Reality,,, koma these politician eee!!! Panopa satana wapanga umfumu,,,guys mukuyesesa kunena gamo koma sindikuvesa kuti malamulo aja a constitution athu amalawi ma page tasetela kapena?
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 20 күн бұрын
Mukuona eti
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 21 күн бұрын
Zoonad big chilungamo ..karembera ayambireso
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 22 күн бұрын
Mulungu akudaliseni ma guys❤❤❤❤
@user-ni3xw4fv4c
@user-ni3xw4fv4c 21 күн бұрын
Akudziwa kale kt adzaluza zisankho km nkhawa ndi yokt akuop unyolo😢
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw 21 күн бұрын
Enanu mungofuna ndalama, mudali kuti nthawi yonsei, the DC iiiiiiiiiiiiii Boni kalindo ndiye omenyera ufulu weniweni! mutu ngati kamba kkkkk
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 21 күн бұрын
Zikuvuta
@MuhireDominic-rw4vf
@MuhireDominic-rw4vf 21 күн бұрын
Mwana phuli phuli wa 15 years kushomola mulandu ku court azikangot ali nd zaka 18 😂😂😂. Ife bas tapulumuka
@user-Grant260
@user-Grant260 22 күн бұрын
Respect elder ❤
@alexsumani6823
@alexsumani6823 22 күн бұрын
Muona MBC ikubwela kuzasutsa izi zochita kuokelatuzi🤣🤣
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 21 күн бұрын
Koma chakwela ndi m,busa wa satana komaso ma bugwe apolice amey ndi ake achakwela
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 21 күн бұрын
Nkhani ndiyoti kalembelayu apangidwe cancel basi chifukwa chinyengo chikupitilila ndi aboma lakubali
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 20 күн бұрын
Mmatha daddaaaa
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 21 күн бұрын
Komano chifundo kachale akuona izizi?
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 21 күн бұрын
Izi nde zothandiza a Malawi osati zitsiru Zina zimati ndizomenyera ma ufulu ali zitsiru za kuba ndi Boma ili
@rashidadan2533
@rashidadan2533 21 күн бұрын
Inshort , we don't want tonse alliance to ruling MALAWl again , We say enough is enough ,no matter what tonse alliance get lost .
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b 22 күн бұрын
NRB MA JUDGE MEC POLICE MDF ,OSEWO NDI MCP PALIBE CHIMENE CHINGACHITIKEPO ZIKULOWA NDIKUTULUKILA UKO NDIE NRB NAWOSO ALOWASO CHINYENGO PANOPA AWADYESA CHIBHADZI KUTI AZITELO
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 21 күн бұрын
Eyaaah onsewo akumawapatsa ndalama so nkhani ndiyoti ma results a MCP tisazawalore basi
@user-it5zv2nz7f
@user-it5zv2nz7f 21 күн бұрын
Ulemu wanu mwakamba chichewa chachimvekele ndithu ndikuphwanya ufulu wa ana zonsez ndi Chakwera akuziwa kut zake zada basi
@georgesmart3791
@georgesmart3791 21 күн бұрын
Nchifukwa chakwera adayankhula mwa matama eti?..wayalukatu kkkkk
@user-dj5hd4ys3n
@user-dj5hd4ys3n 21 күн бұрын
Mumakwana mkuluuu
@paultembo5212
@paultembo5212 21 күн бұрын
Ngati Sing'anga Eliya 😂😂
@FestonJaneiro
@FestonJaneiro 22 күн бұрын
Best TV fire🔥🔥
@MisheckChinjala
@MisheckChinjala 22 күн бұрын
From Cape Town Stellenbosch south Africa...Ndine wa DPP.... please pitilizani kudxudxula
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 21 күн бұрын
Ndi chifukwa akuti wina afune asafune 2025 awina akudalila nawa chakwelayu komatu tidzawamanga a mcp ose 2025 tkawina
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 21 күн бұрын
Ma results a MCP sazaloledwayi apaaa kwawo kwatha zedi
@Pangolinimw
@Pangolinimw 22 күн бұрын
My best tv❤
@user-mx7jg1lu7j
@user-mx7jg1lu7j 21 күн бұрын
Eeeeeee Respect to you big mn ❤
@omarajibu860
@omarajibu860 21 күн бұрын
Bwanji pamene! Muzaziwa liti kuti Mulungu sakukufunani? Akhansuledi.
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 21 күн бұрын
NRB Komanso chifundo kachali akudziwapo kanthu, they're not colified to run this project, they're crooks
@OZIELBLESSINGS
@OZIELBLESSINGS 22 күн бұрын
Tili pambuyo panu boss❤
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 22 күн бұрын
Ulemu wanu biggy ❤❤
@user-ox4dh3ey6b
@user-ox4dh3ey6b 21 күн бұрын
Love you sir
@danielsulani8689
@danielsulani8689 22 күн бұрын
❤za phamvu
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 17 күн бұрын
Ndpo chisankhwo chimenechi chithela mapenety
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga 21 күн бұрын
mberera zokhazokha tiyeni uko
@Chiso2019
@Chiso2019 21 күн бұрын
Zipani zotsutsa nazo ndizogona kwambili...mose tayambila kumva za ma I'd kuli ziii palibe chikuchita iwo
@user-ky8eq5ek1p
@user-ky8eq5ek1p 21 күн бұрын
Zoonadi munthu wamkulu Mulungu akuonjezeleninzeru.
@user-ni3xw4fv4c
@user-ni3xw4fv4c 21 күн бұрын
Allayancy kulibe ,aona nyekhwe
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 22 күн бұрын
Big boss BM TV
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 21 күн бұрын
Bakili Muluzi the best tv in malawi
@user-et5nz4vz2v
@user-et5nz4vz2v 22 күн бұрын
Best TV ever
@DicksonBlack
@DicksonBlack 22 күн бұрын
❤ number one
@collengoma6542
@collengoma6542 21 күн бұрын
Chakwera mumene amayankhulira ku Blantyre muja amawonekelathu kuti akudalira kubela mavoti chifukwa iye akuziwa kale kuti sangawine pa chilungamo koma akuyiwala kuti even satanayo akumupembeza chakwera akuziwa kuti kamusalira kanthawi kochepa
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 21 күн бұрын
Chakwera ndi goat yeni yeni akufuna kuzabera mavoti
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 21 күн бұрын
Best t v
@moyo77777
@moyo77777 16 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@LastonBlair-pg5pl
@LastonBlair-pg5pl 21 күн бұрын
Koma chakwera zomwe akupanga iye sizabwino ay kma mulungu Alipo atichotsa mu mavuto awa
@user-xt5pk7we5c
@user-xt5pk7we5c 22 күн бұрын
Number 1
@dontreybanda278
@dontreybanda278 22 күн бұрын
Good job
@ChippieMawango
@ChippieMawango 21 күн бұрын
Nice speech😂😂😂
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 21 күн бұрын
Best Tv
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 21 күн бұрын
Koma kuzakhala nkhondo ndithu akazangowina chakwera
@user-gg6uh2wo4x
@user-gg6uh2wo4x 21 күн бұрын
Your respect broo
@user-kg5lf6bd1g
@user-kg5lf6bd1g 21 күн бұрын
Ulemu wanu ndithu
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 21 күн бұрын
Sakufuna free n fair elections thats why they're doing this nonsense
Abale ake a John Chilembwe ali kuti?
15:36
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 32 М.
Countries Treat the Heart of Palestine #countryballs
00:13
CountryZ
Рет қаралды 12 МЛН
How many pencils can hold me up?
00:40
A4
Рет қаралды 20 МЛН
ELE QUEBROU A TAÇA DE FUTEBOL
00:45
Matheus Kriwat
Рет қаралды 32 МЛН
Psalms 115: 16✓ Masalimo 115 vess 16
10:02
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 46 М.
Fr Elizeo Nthalika: Nzeru za Anthu Wamba.
25:47
Ndine Mkatolika
Рет қаралды 1 М.
Gotani Hara ali pa chikondi ndi Nankhumwa chifukwa chani?
8:31
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 48 М.
MVETSERANI NOKHA MR  BRIAN BANDA  EXCLUSIVE WITH HON MONICA CHANG'ANAMUN.
54:40
ZOMWE AYANKHULA ABUSA KU KASUNGU ACHAKWERA ALI POMPO🤔🤔
21:01
Adaferanji olemekezeka bambo Sidik Mia?
25:14
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 131 М.
Countries Treat the Heart of Palestine #countryballs
00:13
CountryZ
Рет қаралды 12 МЛН