AKUKHOMA NSOMALI OMALIZA PA MUTU WA MCP JONA PAMKUKU NKHANI YA KAFUKUFUKU IJA PAJA AKUMAKANA

  Рет қаралды 26,613

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 42
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 14 күн бұрын
Ndipo ndiye ku police kuli kuuuuba kwambili , komaso sisonama kuti DPP ndiye # 1 kuno kwathu ku Malawi, opc ndiye akaswiri!!! Pankhani yakatangale ikuba heavy
@marryphili5419
@marryphili5419 19 күн бұрын
Akunama angovomereza Kuti smart Matic yizipita tizagwirise ntchito manual azawone amalawi ambiri tasiyanisa DPP ndi MCP DPP kunalibe njara chifukwa fertilize wumapezeka Pena Pali pose Komaso mutengowabwino wakumuzi amakwanisa kugura Koma MCP anthu akulephera kulima chifukwa alibe ndarama zogulira fertilize
@SymonNkhoma-cs5si
@SymonNkhoma-cs5si 19 күн бұрын
Dzikoli kulibwino litategedwa ndi Dziko la Mozambique kuti mwina tichangamuke tikupusa kwambiri .
@JustinKondowe
@JustinKondowe 19 күн бұрын
Mistake ya MCP kumpha kunja munampha chilima munapanga big Mistake ,chimwendo ,kukuyu, zinkhale ng'oma. Simupenza mtendere mpaka imfa yanu pamodzi na pule.....mwadzi wa munthu siwamaswera muyakuka kwa manyadzi ,mulungu aliko, their is no screat under the earth.
@NafeAlie
@NafeAlie 13 күн бұрын
Chimwendo nyumba zako imozi ndizatengako ndipo ina ndizapasa mai anga ku chiradzulu
@AseChimwene
@AseChimwene 2 күн бұрын
Akunama a m c p sangawine
@Neo-d7s7i
@Neo-d7s7i 8 күн бұрын
Akudalira smartmatic
@BlessingsmChiipira
@BlessingsmChiipira 13 күн бұрын
Ukunamatu iweyo
@raphaelmatias7194
@raphaelmatias7194 15 күн бұрын
Olo utamwa mabotolo 40 antojani, mcp never again. Mapwala Anu a mcp nonse.mukuwadyesa anthu manyi agalu
@BlessingsmChiipira
@BlessingsmChiipira 13 күн бұрын
@@raphaelmatias7194 komanso olo utamwa mabotolo 70 antonjani , DPP never again, ma alubino pano ali pamtendere, pamtumbo panu a DPP nonse, mwalodzedwa etii
@BensonNyirenda-j9f
@BensonNyirenda-j9f 13 күн бұрын
Afrobarometer results ndi chenjezo kwa okhuzidwa kuti sakuchita bwino asinthe mchitidwe wawo wa zinthu.
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 15 күн бұрын
More fire comrade osaopa osatopa osafooka Mcp thawi yanu yatha mbuzi nonse mcp nonse ndi ma carward crocodile team zasatanic chikangawa team imeneyo utuluke
@TameeraInglis
@TameeraInglis 18 күн бұрын
Ngati sanapangidwe shake bwanji akukodzedwa kkkkkkk tsanzikani. Basi MCP
@JonasMaster-ei6jt
@JonasMaster-ei6jt 10 күн бұрын
Bodza iwe wa kuli ji ukunama ndi mzakoyo
@YovitaBanda-k4y
@YovitaBanda-k4y 14 күн бұрын
Amalawi ngati sangavotele dpp nde azavotela ndani utm? Chifukwa amene angatenge voti yake kupatsa mcp ndiyekhayo amene Ali wa mcp osati amalawi amene amalima omwe akugula zinthu odula pakalipano omwe amapita kuchipatala amaswala, momwe zilili panomu ndakaika kuti azavotela mcp
@MolesBrown
@MolesBrown 15 күн бұрын
Uyutu anamupatsa zambili adpp kaya dpp ikaluza adzani ee
@TecnoPop3-k2c
@TecnoPop3-k2c 15 күн бұрын
Anapanga zimenezo ife autm sanatifunseenafe komanso anatiphera msogoreri wathu ndeutm inari kudpp chifukwa chakupyantima kafukufuku ameneyo abwerezenso
@MuhaShaibu-x5x
@MuhaShaibu-x5x 19 күн бұрын
This government s killing us, Roger
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 17 күн бұрын
Ndi pofika Chaka camawa dpp iikwana 70 pereset chimwendo akudalila smantmticis achose imeneo awone
@AbdulMmadimwanyalisi
@AbdulMmadimwanyalisi 15 күн бұрын
Koma ngati azapezeke prezdt othesa katangale ku police ameneyo azakhala number 1.chifukwa kupolice kuli katangale onyasa.
@lewisdicksonmlozi130
@lewisdicksonmlozi130 19 күн бұрын
Patrick amandisangaratsa dzimau
@FelixKChisale
@FelixKChisale 14 күн бұрын
Iwe usatipusitse galu iwe usapangitse chiwawa muno
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 18 күн бұрын
Jonah chilungamo chizamuphesa 😅
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 18 күн бұрын
😂😂😂😂 exactly
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 18 күн бұрын
Dpp bomaaa
@CostanceLalli
@CostanceLalli 15 күн бұрын
Anthu azavite popanda na id basi mcp izipita basi
@SymonNkhoma-cs5si
@SymonNkhoma-cs5si 19 күн бұрын
Dzikoli kulibwino litategedwa ndi Dziko la Mozambigue, mwina tingachangamuke, tinapusa kwambiri.
@SalatiKiddie
@SalatiKiddie 19 күн бұрын
Dpp ndiyowina ndikale iyi
@PaulChafikirah
@PaulChafikirah 18 күн бұрын
Kabambe vote
@StevenMasamba-y1p
@StevenMasamba-y1p 19 күн бұрын
Kwa ine kafukufuku akunena zoona kt, kuti musimikize aboma avomere kuchosa mashini komanso mtalimanja, chakwera athawa muno mziko
@StevenMasamba-y1p
@StevenMasamba-y1p 19 күн бұрын
Aboma kungovomereza lero kuti mashini kulibe, mawa mwake akuthawa
@DippedJob
@DippedJob 19 күн бұрын
Kafukufuku nthawi zonse amabwera ndipo zimakhara zoona zilibwino
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula 16 күн бұрын
katangare eeee
@alubisabili5188
@alubisabili5188 18 күн бұрын
Tieni naon ameneo
@obulekhwanya8032
@obulekhwanya8032 19 күн бұрын
Mcp yatha
@LennieblessSimbi-q2r
@LennieblessSimbi-q2r 14 күн бұрын
Koma MCP isandiphweteketse ntima kunjaku anthu ambili akumukana achinyamata aona zowawa zomwe sanaoneko ndiye akamati awina akudalila chiyani aaaa ine asamansisiwetse tulo kunganiza kuti awinenso makolo omwe amkalandila ndalama kumudzi onthu okalamba avutika zaka zonsezi ndipo ukawamfunsa akungolila ndiye akudalilachani ameneyi
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 19 күн бұрын
Achakwela munaphelanji chilima soka ndi thembelelo likhale pamutu panu
@GraceMwase
@GraceMwase 15 күн бұрын
Ndiana awo omwe ndi zidzukulu zomwe
@happyluhanga3387
@happyluhanga3387 19 күн бұрын
Taba pangani za medeazo Chimwendo Ali Ku ground akutibula
@AseChimwene
@AseChimwene 2 күн бұрын
Akunama a m c p sangawine
@AseChimwene
@AseChimwene 2 күн бұрын
Akunama a m c p sangawine
小丑教训坏蛋 #小丑 #天使 #shorts
00:49
好人小丑
Рет қаралды 54 МЛН
ПАЁМИ ҶАНОБИ ОЛӢ  2024 - 1
1:45:37
ТВ Симо TV Simo
Рет қаралды 3,7 М.
Izindaba zesiZulu @19H00 l 27 December 2024
23:08
SABC Izindaba
Рет қаралды 18 М.