KOMA MWAMVA? ~ DZULO TU ATAKUMANA NAMIWA NDI KUNKUYU KU BICC MPAKA KUOMBELENA MMANJA ~ ZOONA IZI?

  Рет қаралды 30,414

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 69
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu Ай бұрын
100% mr. Namiwa, our future leader, hope he'll be safe.
@Ceciliachitsa
@Ceciliachitsa Ай бұрын
God Bless Malawi 🇲🇼 Amen 🙏 Chisankho Ichichi Chizayenda Mwachisomo Ndikuona Choncho Sure Ndithu Olo Wina Atafuna Asokoneze Koma Mulungu Amukantha Ife Tipemphere Kwambiri Kut Satana Achite Manyazi
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO Ай бұрын
Namiwa ziwa kuti a Malawi timakukhulupilila ndiye usaime kumbuyo kwa wandale wina ai koma kwa ife a Malawi ❤❤❤ 🔥🔥🔥♥️
@LeonardShuger
@LeonardShuger Ай бұрын
Sanayankhe mogwila ntima
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Ай бұрын
Namiwa is a real freedom fighter
@kennymwanyongo8165
@kennymwanyongo8165 Ай бұрын
Unfortunately, it's always easier said than done. There's always sweet Rhetoric than action by our so called public officials.
@LufingoMulungu-z7u
@LufingoMulungu-z7u Ай бұрын
Kuwombera mmnja ndi chikondi
@phillimonmaila4269
@phillimonmaila4269 Ай бұрын
This Guy is Lying..he want when they announce the winner others will be going to court while Chakwera is on the Seat
@Ybm-o5y
@Ybm-o5y Ай бұрын
Namiwa ndi iwe ndi machine
@bigmount563
@bigmount563 Ай бұрын
The question says, nchifukwa chani inuyo a mec mukukakamila smartmtic?pamene anthu onse akuti ichoke
@Enock-gu5ff
@Enock-gu5ff Ай бұрын
Ine ngati Malawian ndaphunzira kuti munthu wa cauta angoti wapurumuka m'manja mwaie amene ana murenga ziwani kuti AMAKHALA mfiti kuposa kare ndie akunkuyu sangamanene kuti io sanagwidwe ufiti zoti uyu ndiopempherazo rero acirima kuribe ifeso osarafe sizikuenda madvuto ndiocuruka anthu sangapite kunseu kumeneko nde kuopya kwambusa wakugwa ifeso ngati amarawi tikueneranso kudziwa vuto rathu tiri ngati mzimai amene amango pasidwa ana opanda banja . I hope panopa taphunzira tadziwano ngati amarawi kuti kudziwa kurankhura pakokha sikungatithandize .yankho roonekeratu ndi DPP ZIPASO ZOONEKERATU ZIRIPO
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Ай бұрын
Mmmmm kunkuyu is a clever man eish
@SouthCluster8
@SouthCluster8 Ай бұрын
Mukulimbikira kuyankha mu English choliga wakumudzi asakuveni.
@ESAUPhiri-k7n
@ESAUPhiri-k7n Ай бұрын
Watching from nkhatabay
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t Ай бұрын
Ife amalawi smart matck ichoke basi kma mukanga makani ifeyo kuwina mcp sitizalola chifuwa tikuziwa kuti mcp kwake kwatha basi amalawi sakuifunaso mcp
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 Ай бұрын
We need to review mpesi qualification for such position.... Amalawi kupusa tikupusisidwa bdi makape mbava zopusa ngati achina mpesi...panya pawo
@JamesMaduka-wk8xi
@JamesMaduka-wk8xi Ай бұрын
Ifeyo olembesafe mutigwila koma mulindimavote omwemwavotelakale kutumidwandiboma musanamizewanthu mulindi ma I'D extra oti mcp muyiwinise
@TonyMhone
@TonyMhone Ай бұрын
Mr. Nkukuyu well articulated indeed but not followed. Very sweet lip talk but to follow is very difficult. Not easy to swallow your own shit.
@PetroHerman-z5g
@PetroHerman-z5g Ай бұрын
Ku Malawi kulibe a police ngati apolice alipo akugwila nchito yanji?
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 Ай бұрын
S A very stupid answer. A. Malawi sakudand aula za procurement ya Smartmatic machine. Tikumana kuti machine amenewo asagwilitsidwe ntchito. Point blank. Another stupid explanation. Akuti chisankho sichikubeledwa chifukwa sichinachitike. How foolish is this guy? If he doesn't know chisankho chimabeledwa a long way before voting. I.e kalembera,system ya technology,handouts,etc.
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 Ай бұрын
MEC ndi NRB yelephera kukonzekera chisankho. A lot of loopholes have been identified like multiple registrations. NR B registering minors. NRB rejecting to register potential voters in some regions in the country citing machines breakdowns,lack of internet,shortage of stationery,demanding money from people who want to register etc
@KalongaWhy
@KalongaWhy Ай бұрын
Iwe onama sumagwira mfiti asanatambe ku Mozambique sanagwidwe ufufana agwile motan
@McshonWilliam
@McshonWilliam Ай бұрын
Nde zogoneka khosi polankhula zikutathauza Chan and funso limodz kulkyankha motenga MA minis ambir cholinga mupusise a Malawi ok let's wait and see
@InnocentHassan-m3r
@InnocentHassan-m3r Ай бұрын
Namiwa ndamene tikumuwona kuti antha kutithandiza
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Ай бұрын
apatu machine wa stiwakuwafuna si a mtendele oyambisa khondo tivote basi mene iwo anawinila kuti alowe boma basi palibe za machine
@EvasonThupilifana
@EvasonThupilifana Ай бұрын
Musikhala siliyasi ndi nkhani mukakhala mipanda muzamazitenge ngati ndinu madolo
@BrightZionga
@BrightZionga Ай бұрын
Mwangogwila wa ku Blantyre basi agalu inu
@TonneckMessa
@TonneckMessa Ай бұрын
Inutu mwatamba kale ndipo takugwilani ndipo ndinu mfiti zothelatu. Koma samalani.
@TonneckMessa
@TonneckMessa Ай бұрын
Guys iyi si Mec ndikhulupilieni, muyambika nkhondo mdziko muno, mayankhidwe omwe ayankhidwa si a serious.
@EleosJari-s5r
@EleosJari-s5r Ай бұрын
Pomwe mungoziwa anthu akuvutika dziko muno ndye zomwe mukupangazo mutha kumapeza matsoka
@MikeSangano-b6x
@MikeSangano-b6x Ай бұрын
Nonse ndinu a Chikangawa party.munya muona.zisankho zikadzangosokonekera maliro inu
@MarthaChigonero
@MarthaChigonero Ай бұрын
Mxiiiii
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 Ай бұрын
Zolankhula chizyngu ndichiyani tsopano
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o Ай бұрын
Uzayakha mirandu iweyoooo
@RichardBanda-o6q
@RichardBanda-o6q Ай бұрын
Wa mec palibe akuyankhapo chanzeru apa
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr Ай бұрын
Namiwa ndi chiphe cha mcp
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya Ай бұрын
Mec manyi akutherani ngati muli ndizolinga zopusa osati kutimikira amalawi
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d Ай бұрын
😞😞😞😞
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Ай бұрын
Kodi. Mukukaksmila. Bwanji
@SainiKamwendo-ec1zm
@SainiKamwendo-ec1zm Ай бұрын
akuti zoti chisankho chidzaberedwa sanganenepo kanthu chifukwa choti chisankhocho sichidachitike, ndiye fuso ndiloti "kodi inu a MEC, mukudikira chisankho kuti chichitike ndipomwe mudzakambe za makina a smartmatic mmene azagwilire ntchito?
@RosinaPatel
@RosinaPatel Ай бұрын
Adya ma bans
@CardoJustin-l7m
@CardoJustin-l7m Ай бұрын
Kunkuyu kufuna kumayankhula ngati mbuyawo chakwera kkkkkkkk koma money kkkkkkkkkk
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman Ай бұрын
Inu Moses kumkuyu Malawi ndi dziko lanu why kulankhula chizungu.
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu Ай бұрын
Vuto lili ku NRB pa nkhani ya kulemba ana under 18.
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 Ай бұрын
Namiwa pangolin
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Ай бұрын
akuti yes tipitiliza 😠
@CostanceLalli
@CostanceLalli Ай бұрын
Anamiwa satinthandidza olo pang
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Ай бұрын
😢😢😢
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Ай бұрын
sizoona
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o Ай бұрын
Anthu oyipa awa koma mumunama
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev Ай бұрын
A NRB panyapanu
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o Ай бұрын
Nanga ana amalembesa ku denza aja
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Ай бұрын
Zianthu za mcp zilibe zelu man what human rights u toiking about nkukuyu
@ElickBanda
@ElickBanda Ай бұрын
Kunoso ku zimba akugawa soyapises
@VitumbikoKaunga
@VitumbikoKaunga Ай бұрын
Namiwa wadya banse
@SaidSamuden
@SaidSamuden Ай бұрын
Mbava izi
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Ай бұрын
Iwe. Ife. Áyi. Chako hi. Chipite. Kukasiya😅😅😅😅😅
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o Ай бұрын
Za ziiiii
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 Ай бұрын
Anthu akumudzi akuvani bwanji
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Ай бұрын
ok tidikile mutambe kaye eeti chabwino
@DerlinNyirenda
@DerlinNyirenda Ай бұрын
Why kutukwana on these issues kkkkkkest
@SteveMbanda-p9w
@SteveMbanda-p9w Ай бұрын
Aaaaa
@WitnessKamoto-bf4pu
@WitnessKamoto-bf4pu Ай бұрын
Zopusa
@SimionDmtande-z8v
@SimionDmtande-z8v Ай бұрын
Our future namiwa
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Ай бұрын
Iwe. Ife. Áyi. Chako hi. Chipite. Kukasiya😅😅😅😅😅
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Ай бұрын
Kodi. Mukukaksmila. Bwanji
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Ай бұрын
Kodi. Mukukaksmila. Bwanji
Akudzinga mkadzi wemufi pamba nekuti aramba kugarwa nhaka Karanganda TV dare ra chief mutasa
1:00:18
M23 and the Congolese Conflict: PLO Lumumba Perspective
12:40
THEE ALFA HOUSE
Рет қаралды 31 М.
UFC 287 : Перейра VS Адесанья 2
6:02
Setanta Sports UFC
Рет қаралды 486 М.
President Cyril Ramaphosa Q&A session in Parliament
2:36:25
SABC News
Рет қаралды 72 М.
Hon Suleman Vs Mr Sambo: Interview Ndi Chimwemwe Magazi
54:59
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 38 М.
В Швеции ищут, кто разорвал подводный кабель
1:01
Euronews по-русски
Рет қаралды 20 М.
Times Exclusive featuring Moses Kunkuyu - 21 December 2024
1:10:04
Times 360 Malawi
Рет қаралды 7 М.