SUCCESSION IN LEADERSHIP Kodi Dr Lazarus Chakwera akamasankha Vice President awone zinthu zake ziti pa munthu amene akumuganizila kumusankha pa udindo umenewu? #caswelmkanda
Пікірлер: 51
@actuarialscience22836 күн бұрын
Musakhe Nicolus Chakwera==>》Liwakwane dzikoli.
@user-oc8nj3or6y7 күн бұрын
You know what exactly you're talking.keep on shining not only this but again stay blessed ❤✍️🤗
@AlexKaunda-ny2eg7 күн бұрын
Akasakhe bambo ake chakwera machende ake 😢😢😢
@AubreyNyakwawa6 күн бұрын
Abusa musayambe ndale zikuchimwitsani
@faithmwanga60786 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂You made my day
@actuarialscience22836 күн бұрын
William Marion Branham said "Service to G-d is the highest calling. Therefore, anyone who abandons it to join politics is the most dangerous wicked person". Ndiye inu mwasiya za Ambuye kuyamba ndale. Mukhala oyipa ngati Chakwera.
@SolokingChimzy-yt7dj6 күн бұрын
Mbambande bro ufumu wa Dziko sukhuza ana a Mulungu..Branham he's the real man of God
@SolokingChimzy-yt7dj6 күн бұрын
Mbambande bro ufumu wa Dziko sukhuza ana a Mulungu..Branham he's the real man of God