ANACHEZA NDI MOSES KUNKUYU WA MCP PA KULINJI KU TIMES RADIO PA NKHANI YA ZISANKHO ZA 2025 ~ KOMA MMH

  Рет қаралды 16,768

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 101
@petertaulo8014
@petertaulo8014 14 сағат бұрын
This country need serious demonstrations. We don't need to beg or ask anyone to demonstration because it's our rights.
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 13 сағат бұрын
Ndigwirizane ndi Bayana Chunga, dziko la Malawi ndilomvetsa chisoni, makamaka boma ili la MCP. Kaya ndichifukwa choti anakhalitsa kunja kwa boma kaya. Zamanyazi.
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 15 сағат бұрын
Tiyeni kuma demo guys tikayipase 🔥🔥💪💪
@bettieulaya5702
@bettieulaya5702 Сағат бұрын
Kuli madhemo achani
@StewartKalipinde-g2j
@StewartKalipinde-g2j 15 сағат бұрын
True
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
More fire guys
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 11 сағат бұрын
Wayana chunga God bless you ❤❤❤❤
@MisheckMwale-v8q
@MisheckMwale-v8q 13 сағат бұрын
Thank you wayana
@issahmaloto9141
@issahmaloto9141 11 сағат бұрын
MCP yationongera dziko😢
@RodgerChaula-r5z
@RodgerChaula-r5z 2 сағат бұрын
More 🔥🔥🔥🔥
@RodgerChaula-r5z
@RodgerChaula-r5z Сағат бұрын
Bayana you are the best
@MzadziWanga
@MzadziWanga 14 сағат бұрын
Ma demo awa mwapangira malo olakwika coz ku Lilongwe anthu ambiri analembetsa ma id nde anthu sangazatuluke ambiri , mukanapanga ma district atatu awa, zomba Blantyre n mzuzu kma Lilongwe nde aaa
@YohaneChinthomba
@YohaneChinthomba 13 сағат бұрын
😂😂😂 Is Mzuzu district?? Kapena ndikhalepo mbuli?
@MzadziWanga
@MzadziWanga 12 сағат бұрын
@@YohaneChinthomba whatsoever as far as I know, mzuzu is also involved in government activities , whether is city or district I don't care bola ndapereka maganizo anga kt ma demo akanachitira Madera ameneo, nde bweran mudzachonge aphuzitsi
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 14 сағат бұрын
Mukusokoneza dzikoli ndi inu olemba za unzika amene mukufuna kuti kusogoloku Amalawi azavutike awine amene mukufuna
@robertmkandawire9898
@robertmkandawire9898 13 сағат бұрын
We need audit of NRB, cause they are not serious!!😢😢😢😢
@JamiesonKaunda
@JamiesonKaunda 12 сағат бұрын
Nsambo ndiwe mbuzi ya munthu ukulephela kuyankha momveka
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 12 сағат бұрын
A Parliamentnso Sakutithandizanso.A Speaker Sadaipange Table mpaka parliament kutsekedwa Abale tithandizeni Amalawi pakupanga Zinthu Zanu Parliament.Okusankhanitu ndife mukutipondelezafe.
@nellietchuwa9913
@nellietchuwa9913 12 сағат бұрын
Bwanji ma concern s anu mkatenge injunction yoyamba kalembrera than kuupita nndi mademo
@Tophillpvtsecondary-x7l
@Tophillpvtsecondary-x7l 13 сағат бұрын
Malawi need God intervention , truth shall be seen when God will say its enough
@MosesDicostar
@MosesDicostar 3 сағат бұрын
Ife tikuyenda wapasi kuchoka ku zambia kubwera kumalawi kuzapanga ma demo
@RobertCosmas-bo1uo
@RobertCosmas-bo1uo Сағат бұрын
Kd mwadziwa relo kt bill kt idutse imayenera kuvota ndiye mukukakamiza zichan
@isaaczuze
@isaaczuze 4 сағат бұрын
Agalu awa achoke basi....zisilu za anthu ....chakwera waononga ziko
@nellietchuwa9913
@nellietchuwa9913 12 сағат бұрын
Even nthawi amapanga lamulo poyamba amavomera to suit their narrative by then now is haunting them (dpp)
@StevenFombe
@StevenFombe 6 сағат бұрын
Kodi Gregory gondwe angayankhure PA radio exclusive interview with Briana banda
@isaaczuze
@isaaczuze 3 сағат бұрын
Moses kunkuyu anapha Allan Witika .....munthu woyipa iwe
@FrankKasiya
@FrankKasiya 10 сағат бұрын
Koma jakama mukumuziwa berani muone ndimupanga hare
@Kamwachale
@Kamwachale 15 сағат бұрын
Please whose is near chimwendo Banda that magetsi kunsanje NDI Madera ena a Ku BT magetsi akuthimathima paene akumawanamiza wanthu Kuti magetsi ansiya kutima.
@DanielNandajester
@DanielNandajester 12 сағат бұрын
Paja afumu anafera PA wire amagets cholinga escom ioneke yolephera
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
A mcp akuchoka basi olo.atani ndimenyela ufulu basi osalola zopusa kuyambila kale timavota opanda id
@jacquelinChitsulo
@jacquelinChitsulo 4 сағат бұрын
Oh oh anthu amalandira ndalama kuti azipondereza ufulu wa a Malawi?, this is very pathetic kutichotsera ufulu wathu, Ndakhumudwa now i can understand why ku Kenya kuja anthu anakalowa ndi ma Demontrations ku Parliament.1
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 12 сағат бұрын
It's. true kunonso ku CK Zimatero ndipo anthu amangibwelera ngakhale kwa a DC anthu akubwelera Ziphasonso OSapatsidwa ndiyeno mzikazi zikalembetsa bwanji anthu alibe Ziphasozo
@DavidJabesi-r1h
@DavidJabesi-r1h 4 сағат бұрын
Akulu akulu a NRB pogwila ntchito yanu lekani ku masewela ndi nzelu za amalawi inuyo chifukwa muli m'mipando musaganize kuti kunja kuno kulibe anthu anzelu mukanakhala enamukanagwila ntchito yanu mokomela amalawi onse osati kugwilisidwa ntchito ndi anthu a ndale,
@GRIGORYLASTON
@GRIGORYLASTON 13 сағат бұрын
I CAN'T HEAR THIS BUT I THIS WEDDING WILL BE THE BEST
@LovemoreCathy
@LovemoreCathy 12 сағат бұрын
Wochunga inu ndi 1..Ulemu wanu 💪🔥
@aubreymagombo5907
@aubreymagombo5907 13 сағат бұрын
Capacity alibe ine ndina lembesa 2022 mpaka pano card sinatuluke ndilibe ID pano
@JulieNdekha
@JulieNdekha 13 сағат бұрын
Peaceful much kulibeko unless ngati ndiza church... Izizi musanamepo apa
@EllenGomani-i4f
@EllenGomani-i4f 11 сағат бұрын
Nsambo ndiwe chitsiru kwambiri
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 2 сағат бұрын
Sambo sounds sketchy 😢😢😢
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 13 сағат бұрын
Nawe Patrick kankwatira sukumva kuti nkhani n ma numbers mu parliament mo iwe chibanzi chinakudya moyo cha mcp mafuso opoira ukumufunsa nthendayo
@JosephLidi
@JosephLidi 12 сағат бұрын
Mukuthandaudza chani mukamati ngati zitachitike mwayambaposo kutenga mbari?
@DicksonLutere
@DicksonLutere 11 сағат бұрын
Ngati inakanika kunyumba yamalamulo basi kungosiya mukutaya nthawi basi
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi 12 сағат бұрын
Mcp chilichose kugwilisa ntchito ndalama chilichose agalu awa ndalama ngabwingambwi mmalo motukula boma pamtumbo Panu
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi 12 сағат бұрын
Galu Sambo pamtumbo pako akupasa ndalama mkukuyu galu
@isaaczuze
@isaaczuze 3 сағат бұрын
Boma la anthu okuba komanso zigawenga ....chakwera akuyenela kuchoka mbuzi ya munthu
@DanielNandajester
@DanielNandajester 12 сағат бұрын
Mmmmm mafuso akukondera times yagulidwa ndi dpp bac aaaa
@isaaczuze
@isaaczuze 3 сағат бұрын
Tiyeni tipite kuma demo lelo chisilu ichi chichoke basi
@DanielNandajester
@DanielNandajester 12 сағат бұрын
Awayana against government
@elsontmsukwa4356
@elsontmsukwa4356 14 сағат бұрын
Why malawi 😢
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga 2 сағат бұрын
akutalikisa kuti anthu alemphele asalembese anthu amenewa akusewela juga apa wina aliyese avote apanda vote basi
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
Wachunga zikomo mukunena zosangalasa simuikila boma kumbuyo
@emmanuelhassan-v1s
@emmanuelhassan-v1s 12 сағат бұрын
Chitsiru chamunthu Moses kumkuyu, did u went to school? Noooooo
@DanielMjasten
@DanielMjasten 12 сағат бұрын
Anthu awawa mzelu alibe zomwe akuyakhuka apa a mcp zikuchita kuonetselatu kuti palibe chomwe chili😊
@ROBERTMUKHAYA
@ROBERTMUKHAYA 15 сағат бұрын
The funding come all over the world sure
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 12 сағат бұрын
Nsambo ndiwe chimbuzi
@DanielMjasten
@DanielMjasten 12 сағат бұрын
Aneyo lD yanga ndikapita kukafusa ngat yatuluka amandiuza kut ili ku INDIA SINABWELE
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 12 сағат бұрын
Inu A NRB mudzinena Zoona Abale.
@StevenFombe
@StevenFombe 6 сағат бұрын
Akwatira kkkk
@aubreymagombo5907
@aubreymagombo5907 13 сағат бұрын
Mademo achitike awo akupanga zantchito yawo basi
@MartinMartin-d3g
@MartinMartin-d3g 13 сағат бұрын
Olo tidzafute ndi chikalata cha amfumu basi asatipusise
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
Asatipusise anthu sazavota tizaone
@LovemoreCathy
@LovemoreCathy 12 сағат бұрын
Mkulu wa NRB phwala lako aise
@JohnsKapaya
@JohnsKapaya 11 сағат бұрын
Zaukatangare basi apo zikavuta tikamngophwanya zose za NRB Iya musativutitse ndikunamiza ap
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
Amalawi anatitola
@CholohLungu
@CholohLungu 7 сағат бұрын
Ife chete kudikila
@HamuzahBamusi
@HamuzahBamusi 13 сағат бұрын
NRb nonse patumbo panu pamanu inu ndi amene mukusokoneza dziko lamalawi lino mwaiwara zoti anthu akufa ndi njala panyini
@khasimMusa-d3w
@khasimMusa-d3w 13 сағат бұрын
Km zisakho izi zizakhala zamagazi ndpo Nd nkhondo Chfukwa boma chnyengo chkulq
@PazAutomb
@PazAutomb 12 сағат бұрын
Kodi ku mademo kumakhala porket money a kakwatila
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 14 сағат бұрын
Inenso ndikubwela kumademo, from mocambique
@PazAutomb
@PazAutomb 12 сағат бұрын
Wayana usamakhale ngati wadzelu.... Ngati wanya budzi Kanye wekha ndi family yako zako zili bwino
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q 14 сағат бұрын
Iweyo mutuwakosumagwila komanso chidule unagwelapo nchumbuz
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 14 сағат бұрын
Iwe usamapusise Amalawi munthu ngati ak usowa chimanga chokuti adye pakhomo pache ndiye achoke ku mulanje akalembese ku thyolo ukuganiza bwanji
@SteveKaphamtengo-gf2mp
@SteveKaphamtengo-gf2mp 14 сағат бұрын
Dziko silawo dziko ndi la amalawi Ife zachibwana ai ngat NRB sinapeleke chauzika ndiye kt at adzavote ndi NRB Ife ai
@AdamJames-x7x
@AdamJames-x7x 14 сағат бұрын
kumkuyu ndiwe wabodza kwambiri, mutu ngati choswera malambe galu iwe
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 15 сағат бұрын
Me demo will show omwe Ali ku parliament kuti azixitengera serious akapasidwa nkhani ndikunena izi cz ku parliament pakakhala nkhani yoti ndiyokhudzana ndi boma zimangofafanizidwa
@AcksensioChikondi
@AcksensioChikondi 14 сағат бұрын
Eeeeh kunkuyu 🔥
@MartinMartin-d3g
@MartinMartin-d3g 13 сағат бұрын
Apa pakufunika amalawi onse akalembetse ku lilongwe
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 13 сағат бұрын
Opita kumademo ndiomweoso akuvutika inuyo munasakhidwa kudzadwila tchito zamademo
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 15 сағат бұрын
Funso mumayenera kuwafunsaso oimira bomawo bwana nkukuyu kunena kuti iwo maganizo awo ngotani pa zomwe anthu akufuna kuti aliyese azakhala ndi ufulu oti azavote sizimenedzo zakunyumba yabomako cz anapita koma sakuyankhidwako
@McshonWilliam
@McshonWilliam 14 сағат бұрын
Mademo bas iyaaaaaaa
@bs-malawi
@bs-malawi 14 сағат бұрын
Eti amwene akuchita kuzembazemba kkkk
@JudithMaida-ug4oi
@JudithMaida-ug4oi 14 сағат бұрын
I think bwana Kumkuyu mayankho awo akumabwera ngt muja achitira khoswe kuluma nkuuzila akuziwa chobwera mawa kkkk tisamalitse kayankhulidwe kathu
@PatrickRobert-y5x
@PatrickRobert-y5x 13 сағат бұрын
zachamba
@RoseThindwa
@RoseThindwa 14 сағат бұрын
Tiyeni tiyeni
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan 14 сағат бұрын
Panyapake nthwendayo pantumbopake
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 14 сағат бұрын
Kunkuyu ukamuwudze chakwera adzivala condom akupasa mimba akazi ayeni
@petertaulo8014
@petertaulo8014 14 сағат бұрын
Anthenda penapake ndinu opusa kwambili
@khasimMusa-d3w
@khasimMusa-d3w 13 сағат бұрын
Km kukuyu wayakhula ngat si wa MCP
@JumaKachala
@JumaKachala 12 сағат бұрын
Nkhaniyo ndiyowona bro
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 14 сағат бұрын
Iweso kunkuyu unalowa ndi mademo usamale ukamayankhula
@SteveKaphamtengo-gf2mp
@SteveKaphamtengo-gf2mp 14 сағат бұрын
Mademo afike madela ose osat kulilogwe kokha ai kms ikhale dziko lose
@petertaulo8014
@petertaulo8014 14 сағат бұрын
A Sambo pathako panu
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q 15 сағат бұрын
Mafuso ake ndiye amanyitu akutuman
@petertaulo8014
@petertaulo8014 14 сағат бұрын
Moses kumkuyu pathako pako
@PhillspicJere
@PhillspicJere 14 сағат бұрын
Inu kutukwana sikukuthandizani tangonenani mfundo, umakhala uchisirutu umenewo
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 15 сағат бұрын
Tivota opanda I d bola chiyao baa😂😂
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
More fire guys
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
A mcp akuchoka basi olo.atani ndimenyela ufulu basi osalola zopusa kuyambila kale timavota opanda id
@HarryMkango
@HarryMkango 11 сағат бұрын
Asatipusise anthu sazavota tizaone
Angry residents shut down spaza shops
8:59
Newzroom Afrika
Рет қаралды 53 М.
She's very CREATIVE💡💦 #camping #survival #bushcraft #outdoors #lifehack
00:26
How do Cats Eat Watermelon? 🍉
00:21
One More
Рет қаралды 12 МЛН
Chimwendo amafuna kulepheletsa mwambo wa Mulakho wa Alomwe
4:39
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 57 М.
She's very CREATIVE💡💦 #camping #survival #bushcraft #outdoors #lifehack
00:26