ANTHU A KU NTCHEU AMULANDILIRA MICHAEL USI CHONCHI POMWE WAFIKA KU NSEMBE YOKUMBUKIRA A CHILIMA

  Рет қаралды 70,585

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 153
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 2 ай бұрын
Anthuwatu mmitima mudakali moto olo muntima mwangamu ndangoona mpando wakhala usiwo zandikumbutsa achilima moyo kuwawa😢😢
@JoelMwambira
@JoelMwambira 2 ай бұрын
Saksa
@RobertChikawonda
@RobertChikawonda 2 ай бұрын
Ndipo mmene wawawila wangau esh
@NearBanda
@NearBanda 2 ай бұрын
Mary chilima akumvetsa chisoni koma this word 😢😢😢 continue Resting well skc
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 2 ай бұрын
Ndiponso,ine kulira kundimvetsa chisoni
@gracemaluwa4674
@gracemaluwa4674 2 ай бұрын
Mai Kaliati pitilizani mtima wanu wabwino ,musasiye Mai Chilima okha munyengo yowawitsayi Amen
@MarthaBanda-ye4pt
@MarthaBanda-ye4pt 2 ай бұрын
Ambuye mulimbikitseni mwana wanu Mary Chilima akuvetsa chisoni 😭😭😭
@AminahMussah
@AminahMussah 2 ай бұрын
ndipo amphwa kwambili 😭😭😭😭
@henrychawinga4639
@henrychawinga4639 2 ай бұрын
AMEN
@mphatsomonjeza4371
@mphatsomonjeza4371 2 ай бұрын
God is with her 🙏🏻
@LywellChilupsa
@LywellChilupsa 2 ай бұрын
Ndipo ine ngati ndilire
@AntinHawile-rw9fj
@AntinHawile-rw9fj 2 ай бұрын
kulira kosalekeza tikulira nanu mayi mary chilima km ambuye yekha ndiyemwe akuziwa kwezan maso kwa yehova ndpo zonse zizakhala bwino mama😢😢
@nysonchapasuka7270
@nysonchapasuka7270 2 ай бұрын
May the hand of Almighty God keep on strengthening you Mary Chilima in this critical situation you are going through. We are still mourning together. We understand that SKC has created a huge gap in your life Mama and other lives too but we must look up to Jesus Christ who has a final say.
@CharlesChilinde
@CharlesChilinde 2 ай бұрын
Mzimu AChilima uwuse mumtedere ndi ntchito zonse anati gwirira ngati dziko. Koma pamwambo umenewu pali ine azikakhala ndi ine mukuwadziwa nokha Mulungu awa Kathe chifukwa Ali ndi mtima osiyana kwambiri ndi momwe AChilima amakondera anthu awo owa tsatira mu U.T.M.ngati chipani. Mulungu odziwa kusunga ndi tothoza ayang'anire Mai Mary Chilima ndi banja lonse Sa ❤❤❤❤❤,, 🎉🎉🎉
@GladysMwantenga
@GladysMwantenga 2 ай бұрын
Apa mpomwe nda ziwa mau aja kuti atatanthauza izi😭😭😭pochoka mzako pali malo💔 continue rest in peace DR.chilima
@Martha-m6e
@Martha-m6e 2 ай бұрын
Mai Kaliyati pitilizani kufungatira Mary chilima.
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 2 ай бұрын
Ndipo kwambiri
@TizifaBanda-xn5tm
@TizifaBanda-xn5tm 2 ай бұрын
Mai kaliati...is the true politician and kholo.ku UTM musadzapange mistake kutaya Mai ameneyu
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 ай бұрын
Marry kumvetsa chisoni mwana wa eni ake mayo ine😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@WilliamMasula-cb1mg
@WilliamMasula-cb1mg 2 ай бұрын
I feel sorry for her
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 2 ай бұрын
​@WilliamMasula-cb1mg kwambiri tu, Dziko lapansi hmmmm
@fannyzimba149
@fannyzimba149 2 ай бұрын
Koma ndipo zovetsa chisoni 😭😭😭eish
@MemoryNyirongo-gt4mn
@MemoryNyirongo-gt4mn 2 ай бұрын
Palibe chobisika padziko lapasi zingabisike bwanji zidzaulilika (muuse mumtendere achilima tidzakusowani mpaka kalekale) Amen
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 ай бұрын
All of us we are still shocked and you will see someone saulting on this shameful time,it's better if you don't have something to say just keep quiet coz this is not a time to play with, this is time for the tears respect is needed
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 ай бұрын
Rest well Mr Chilima mayo Marry wanga ine usamale ndi usi chonde ndi mfiti yayikulu iyi😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 ай бұрын
Guys don't forget that no one knows when you will die, this is by only Him The Lord Almighty
@ChristinaNyirenda-zb1if
@ChristinaNyirenda-zb1if 2 ай бұрын
Mulungu ndiwadongosolo azaziona tsiku ndilimoz
@stevenkambuku
@stevenkambuku 2 ай бұрын
Koma imfa ya SKC mmmm I am speechless, Mhsrip
@FanscioDancun
@FanscioDancun 2 ай бұрын
This is like bringing tears again
@SimeonAbraham-u2j
@SimeonAbraham-u2j 2 ай бұрын
Myambo yokumbukila SKC izichitika mochuluka mpaka Wina chikumbumtima chimuphe ndithu
@DolicahGift
@DolicahGift 2 ай бұрын
😭😭 Ambuye pitirizani kuwusamarira mzimu wa mr chirima 😢😢😢
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 2 ай бұрын
We need your mercy our father 😢
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di 2 ай бұрын
Corridors of justice shld prevail O, Lord. Rest in peace SKC
@Melinavituhs-tc8ys
@Melinavituhs-tc8ys 2 ай бұрын
Mary khope yake ikadali nchisoni zuchita kuoneka ngatiso alipamalilo lero mzimu wa Saulos Klaus chilima uuse mumtendere ❤️😭😭
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 2 ай бұрын
Ifa ya skc ma guys ndiyo pweteka paziko la pansi. MCP is a devel goverment.Nkhalani olimba a merry chilima, Kwa ine no vote for mcp mu umoyo wanga wose
@rhodahjere8747
@rhodahjere8747 2 ай бұрын
Ambuye limbikisani Mary chilima dzikoli ndowawa 😭😭😭😭😭😭
@JoyceChawawa-og1cj
@JoyceChawawa-og1cj 2 ай бұрын
Only Almighty God knows
@Adamuson
@Adamuson 2 ай бұрын
Azakhari sadaname kutchura bambo a Sikono kuti ndi nkhwari.
@Raph-kayRaph-kay-g5v
@Raph-kayRaph-kay-g5v 2 ай бұрын
Koma mmene akuyang'anira patrisiayu pavuta apa
@DolothyMussa
@DolothyMussa 2 ай бұрын
Mayi chilima mulungu akutothozeni ndipo akupaseni kulimbika mtima muzakaonana nawo mukachita bwino moyo uno muuse mu mtendele achilima misozi siyikutha kuno eshhhhh
@ChrissieGome
@ChrissieGome 2 ай бұрын
Mzimu wa vice president , continue resting in peace
@CharityMhone-uk9ym
@CharityMhone-uk9ym 2 ай бұрын
Pa ifa ya chilima manganya samaoneka lero watenga udindo akuoneka kamunthu koipa kapha mnzake chifukwa cha mpando chitsiru
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo 2 ай бұрын
Mayi kaliati mulungu adzikudalitsan ndithu
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 ай бұрын
Let's only pray for his soul rest in peace but don't create violence because of his death.love one another something bigger gonna come to our nation
@SolomonBewula
@SolomonBewula 2 ай бұрын
Lero nsiku lomwe alengeze zakuchikangawa kod Komatsu alengeze basi lero ausi mmene zinayendela
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Koma dzikoli abale Mulungu pitilizan kuwatonthoza Mai Chilima pamodzi ndi ana awo R I P SKC😭😭
@UsenLashid
@UsenLashid 2 ай бұрын
Bambo asikonowo musamale nawo ameneyo ndi mbulu akuoneka ngati muli limodzi Koma Ayi makendulo amuontche munthu woyipa
@charleskhomolina2385
@charleskhomolina2385 2 ай бұрын
😢😢😢Imfa yosayiwalika
@abwinoamatani4921
@abwinoamatani4921 2 ай бұрын
A usi ndiopanda manyazi, kuyandikana ndi Mary
@hopembendela
@hopembendela 2 ай бұрын
Nkazi wa chilima akunvesa chisoni koma
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 2 ай бұрын
Manganya 😭😭 pachoka nzako pali Malo, Ambuye mwalolelanj izii?
@SteliaKolomba
@SteliaKolomba 2 ай бұрын
Ndakumbuka SKC😢😢
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 2 ай бұрын
Manganya zoona ukumva bwanji muntima mwako pomuona nkazi wanzako akumvetsa chisoni ambuye akukhululukire sukudziwa zomwe ukuchita
@NatashaBema
@NatashaBema 2 ай бұрын
Mfiti ilibe chisoni anwene
@manzyhetekele8697
@manzyhetekele8697 2 ай бұрын
RIP SKC😢
@JoyceBAllubi
@JoyceBAllubi 2 ай бұрын
Ambuye mutonthozeni mwana wanu
@amoschataika7440
@amoschataika7440 2 ай бұрын
Yudasi izi ndizomwe umafuna kuti uzikhala pamenepo. Iwe munthu oyipa kwambiri. Nzimu wa Chilima ukukanthe kosalekeza.
@lillianmwanza4218
@lillianmwanza4218 2 ай бұрын
Mzimu wachilima ungokatenga
@amoschataika7440
@amoschataika7440 2 ай бұрын
@@lillianmwanza4218 kkkkk ndipo inu
@Fatima-db8ut
@Fatima-db8ut 2 ай бұрын
Lord have mercy
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn 2 ай бұрын
Woyeeeee mama Mary Chilima
@tulimwalwimba6544
@tulimwalwimba6544 2 ай бұрын
Chilima! Eish
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
Usi ukutaniko uko machende ako anagulisa chilima ulibe manyazi chakwera bwanji wayiopa ntcheu😂😂😂 mapwala ako
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di 2 ай бұрын
Convensiion ngati ingokhala mawa iii.
@SabinaNkhoma-sf7kz
@SabinaNkhoma-sf7kz 2 ай бұрын
Km ndizowswa kwambiri zandikhudza mary akuvetsa chisoni
@chrissiechandilanga4995
@chrissiechandilanga4995 2 ай бұрын
But death 😢
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 2 ай бұрын
Chifukwa chani awayika moyandikana chonchi? Kulakwa.
@WestonGawaza
@WestonGawaza 2 ай бұрын
Kupepela amugulisa mzawo mukumuyitanatso nose ndinu akupha
@DavieKidison
@DavieKidison 2 ай бұрын
Zambili tikaziwa tikazaseka maso zinthu zamundale sizimaveseseka pakufunika mzimu wachiziwitso pamalawi anthu tisekule maso
@LimbikaniChirwa
@LimbikaniChirwa 2 ай бұрын
Zausilu zosezo zitayene , mnavapo wakubanja wa anthu 9 aja akuonesapo action yiliyose yokwiya ,zitayeni zimenezo mngafelezaine
@FloridaMakwinja-eq2ek
@FloridaMakwinja-eq2ek 2 ай бұрын
Chisoni chandigarh Usi Akuma bwanji
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Ausi mukumbva bwanji mpando mwakhalilawo zomwe mumafuna ndi zimenezo, Koma mukumbukire kuti lino ndi dziko si inu amuyaya
@YusufIbrahim-w1g
@YusufIbrahim-w1g 2 ай бұрын
Usi yu ndisimene ankamvuna simenesi mulungu awawone agalu amenewa
@ChifundoSaladechitalo
@ChifundoSaladechitalo 4 күн бұрын
Mulungu apilize kukhala ndi may Mary chilima
@FelixBoss-yn9pe
@FelixBoss-yn9pe 2 ай бұрын
Mmmmm mbola fanzi iyiyi ikuoneka yosasangalala
@maulanaallie6194
@maulanaallie6194 2 ай бұрын
Ndye asangalala bwanji mwambo wachisoni ngati umenewu nanu
@FELIXMAJAWA
@FELIXMAJAWA 2 ай бұрын
anthuwa sakukondwera ndikupezeka Kwa usi mitima yawo ikuwawa ngati ineyo
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu 2 ай бұрын
Manganya yudasi km ukumuwona mery mene akuwonekera agulu lnu nose ndi chikangawa Lazaro aphangaka fiti skcpitilizani kupuma mtendere
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki 2 ай бұрын
Marry maso ndi maso ndi mfiti yomwe idagulitsa mwazi mwamuna wake Ku MCP in exchange for His position,,Marry you are a strong woman trust I wouldn't afford to see USi face to face
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
Me , I would forget ndine namalira, I could freak out.
@AustinBanda-ee6sb
@AustinBanda-ee6sb 2 ай бұрын
A Malawi anzanga kuweluzana sibwino chili chonse akudziwa ndi Yahwe kuti zinakhala bwanji ndi chilungamo chizadziwikabe pangatalike maka
@ChristopherChimbalanga-ez5he
@ChristopherChimbalanga-ez5he 2 ай бұрын
Rest in peace SKC 😭😭😭
@Nadeon-y2k
@Nadeon-y2k 2 ай бұрын
Kodi zikatero ndiye kuti Manganya adasiya kuchita zitsuzo
@JonathanMsiska
@JonathanMsiska 2 ай бұрын
Koma tiuzane zoona pano Matinitedi tisiye kuvala aliyese nkhope Yake ikhale poyera.Mukazawona munthu wavala tinitedi kumaso ameyo ndi munthu oyipatsitsa.
@cmsanyama200
@cmsanyama200 2 ай бұрын
Kutsutsula chilonda chosapola bwanji?
@ziwani3682
@ziwani3682 2 ай бұрын
Rest in peace skc 😭😭
@EllenNgoon-nc8vg
@EllenNgoon-nc8vg 2 ай бұрын
😢😢 koma dziko iri
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
Akuziona ngati Ali pamwamba yudasi akamayenda akuchita kunja nja
@mphatsosadiki4983
@mphatsosadiki4983 2 ай бұрын
Only God knows😢
@NoelBurton-x1z
@NoelBurton-x1z 2 ай бұрын
SKC forever ❤
@vitumbikomateche
@vitumbikomateche 2 ай бұрын
Skc for life
@Biath-m4b
@Biath-m4b 2 ай бұрын
Zimene sitimkaembekezela poti Ambuye munalola tilibe mau ife
@JaneMasikini
@JaneMasikini 2 ай бұрын
Ma comment ali apa eee mphawi kuchulutsa zochita matukutuku aeni ake akubanja azisiya zonse mmanja mwa mulungu koma wina busy kumuloza chala munthu eishh
@GodsFavourite1
@GodsFavourite1 2 ай бұрын
Usi amabisala mu tinted😮
@MisheckAselo
@MisheckAselo 2 ай бұрын
Eee koma anthu kumuyang'ana kwakeko yudas 😂
@PatrickViyache
@PatrickViyache 2 ай бұрын
Dzimu wanu ukawutse muntendele skc❤❤❤❤
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k 2 ай бұрын
Yudas wankulu usi kulandilidwa
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 ай бұрын
Nkhalani ntcheru ndi usi uyo ndi fiti
@thomasmwitiya1447
@thomasmwitiya1447 2 ай бұрын
Yudas kulandiridwa
@mosespemba8822
@mosespemba8822 2 ай бұрын
Is that KABAMBE I'm seeing?
@clairemyegha4315
@clairemyegha4315 2 ай бұрын
Yes
@HanifaAdam-tm9yv
@HanifaAdam-tm9yv 2 ай бұрын
Yes with his madam
@janemutipe8152
@janemutipe8152 2 ай бұрын
Yes he is
@ellahmvula
@ellahmvula 2 ай бұрын
Yes
@aafrogarrix
@aafrogarrix 2 ай бұрын
KOd uku zimachitikila kutiko
@AnusaNkhoma
@AnusaNkhoma 2 ай бұрын
Mmmmmm😢😢
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi 2 ай бұрын
Tizakhala osauka ovutikitsitsa padziko lapansi chifukwa chakaganizidwe kathu , tinayenela dzinthu zikachitika tizivomeleza maso athu nkupenya kwamulungu koma osati kumalozana zala.
@chumasalanje4705
@chumasalanje4705 2 ай бұрын
Iwe dont say like that its clear USI is the one who plan the death of SKC
@GiftKumbweza
@GiftKumbweza 2 ай бұрын
Ndife anthu omvetsa chisoni kwambiri.Eti in this age and era amwene
@WorriedNdhlovu
@WorriedNdhlovu 2 ай бұрын
Mapwala ambuyako iwe
@temwekamlenje4358
@temwekamlenje4358 2 ай бұрын
Akanadikira kaye 40 days a Manganyawo bola kuti alemekeza Mzimu wa anzao udindowo pambuyo.
@vukanifracksonchinkonde7324
@vukanifracksonchinkonde7324 2 ай бұрын
If usi was not eppointed as VP.....would you people continue to say he is yudasi? Where the name yudasi has come from? Do not hate someone because you head from someone that he is bad. Usi has been with our president the late Dr SKC and we have never heardbof any disloyal. It's primitive life to fuel enemity for your personal gain. Sorry for all of you who want Usi to fall and also you want him to feel like he is hated and leave utm.when he leaves you will also talk so much nosesnse Be civilized guys!!!
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 2 ай бұрын
RIP SKC
@georgeraphael8198
@georgeraphael8198 2 ай бұрын
Mwapeza zonena eeeeee😅😅😅😅😅😅
@AgathaJerard
@AgathaJerard 2 ай бұрын
Ausiwo kuchibwanoko Ngati apaka ufaaaa 😂😂😂😂😂😂😂
@lindaphiri3543
@lindaphiri3543 2 ай бұрын
😂😂😂 ndipo zosawakhala
@AustinBanda-ee6sb
@AustinBanda-ee6sb 2 ай бұрын
@ Jane ❤❤ ndaikonda comment yako
@SalaJawali
@SalaJawali 2 ай бұрын
Kodi awa alibe akazi awo mene a kumayenda okhamo
@nishanchiwaya4561
@nishanchiwaya4561 2 ай бұрын
Macomentiwo oonesa kuti amalawi mwatopa ndi ulemu😅😅😅😅
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di 2 ай бұрын
Yudasi. Satana kumuona akuyenda ndi miyendo. MHSRIP SKC
@RichardKuden
@RichardKuden 2 ай бұрын
Dziko ndilovuta ndithu😂😂😂😂😂
@GeoLikwanya-cb9gn
@GeoLikwanya-cb9gn 2 ай бұрын
Imfa yosaiwalika ku fuko laMalawi 😭🇲🇼
@Nunalinn
@Nunalinn 2 ай бұрын
Kodi iyeyo akazake sanapite nao
@CamlonLogistics-ju6mb
@CamlonLogistics-ju6mb 2 ай бұрын
Mary chilima akufunika mapemphelo
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 2 ай бұрын
Ameneyu anayenera naye kumamupempherela coz Ali munyengo yovuta heavy
@EsetaGerate
@EsetaGerate 2 ай бұрын
😭😭😭
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 2 ай бұрын
Mery chilima usamale ndizopasana moni wamanja zanuzo kuli ma poison kumalawi kaya ayudasiwo musamale nawo
@KassimSteven
@KassimSteven 2 ай бұрын
Mawu tilibe infe chathu ndichison bas
Watermelon magic box! #shorts by Leisi Crazy
00:20
Leisi Crazy
Рет қаралды 110 МЛН
Сюрприз для Златы на день рождения
00:10
Victoria Portfolio
Рет қаралды 1,4 МЛН
MICHAEL USI WAYANKHA ZOMWE ANANENA A FELIX NJAWALA KU MZUZU.
8:04
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 26 М.
Watermelon magic box! #shorts by Leisi Crazy
00:20
Leisi Crazy
Рет қаралды 110 МЛН