ArchBishop💯💯💯💯💯💯💯🌟🌟🌟🌟🌟🌟💓💓💓Kodi agalu inu mukufuna chani Kwa ArchBishop mukukhodzachi ndi chiwembu Bakili muludzi TV Bon Kalindo comrade Tanyiwa simunama Report lowowozedwa ndi ana akhomba Phala Ayaluka Achikangawa
@user-ux3ed3ni1p2 күн бұрын
Ife we understand the Archbishop, it is timely and this is what a faith leader must speak to what is hurting the people right now. Ntendele is truth osati zobisazi. Ndani anamanga Martha, Ndani amapa ma albino please chonde tizingo pimbidwa.
@RaphaelWinford-t7u2 күн бұрын
Za church mwawo chukugutsani ndichiyani inu anthu asatanic chilungamo chukuwawani bwanji ana ajoka inu😊😊😊😊 live him alone bishop 😊
@LomezyWhite-vq9bv2 күн бұрын
Uthenga ukagunda umarapa
@chrisschikozera72712 күн бұрын
Bishop sanalakwitse ngakhale muyikile kumbuyo boma chilungamo ndi chilugamo basi
@Bernardwisck2 күн бұрын
Abishop sanalakwe koma anali pa chilungamo chakwera kunkuyu ndi a general comanda ndi amene anapha anthu eight
@jozyomar53612 күн бұрын
Ine abale anganu mukamati ànthu asiye kuyakhula zangozi ndikumakudbwani kwambili coz chakwela ndi anthu ake anawonjezela mukwiyo ponane bodza kudziko kenako kumamanga anthu chowona cha ngozi çhilipo koma tikuwopa kuphedwa coz mcp has money and power inu dikilani azachoke kaye ndipomwe mudzawone thank you bishop never give up truth must be come out asamatiyese opusa awa andale
I AM ONE OF THE EYE WITNESSES OF THE CRUSHING PLANE, BOMA LIKASINTHA TIDZAYANKHULAPO KOMA PANO WE ARE FAR AWAY FEARING FOR OUR LIVES!!!
@RaphaelWinford-t7u2 күн бұрын
We don't care za mavuto tizilimbikila tokha komaso chilungamo tizichiona khani ya chilima simuyisiye choncho akunkuyu ndi chitsilu chimwendo mkaka mbuzi zawanthu devil's atulutse black box basi 😊😊😊 zoona opanda omangidwa zoonadi zake
@AnyuxyJulias2 күн бұрын
Iyitu singathe mwachibwana bwana
@Vincentrami-m9v2 күн бұрын
Munthu amene ali ndi umboni sizingatheke kukakumana ndi prezidenti akaphedwako
@philipgatawa2 күн бұрын
Ngati Pali chirungamo bwanji boma silikuyankhapo za black box
@peterphillips76082 күн бұрын
Truth prevails regardless of the condition of the circumstances
Chimene anabitsila black box ndichani?, makosana a MCP amenewa adzayaluka
@ShareefKalimaКүн бұрын
Chakwela ndi wa kupha ndipo sanayambe kupha chilima ayi sadick Mia kufunsa ngongole kulakwa anamupha.zakupha anthu Chakwela ndi kunkuyu chimwendo nkhan yifika povuta
@moirngwira47482 күн бұрын
They lied from the beginning adindio. Adindio should not lie.
@EmercianahKasiku-en6hl2 күн бұрын
Nkhani izatha Boma likazachokapo emwe ifeyo tikumupanga suspect ndi president wadziko lino nde commission of inquiry yokhazikitsidwa ndi iyeyo komaso momukakamiza and kuti zithe ndikubweletsa poyera black box yomwe mneneli wa Boma Mr Nkumkuyu adati ilipabwino itulutsidwe kaya
@andiwochishadreck37532 күн бұрын
We ar following this story antill
@TonykalicheloKalichelo2 күн бұрын
Km ngat mukufuna kutiuza zot ndege zakumalaw sizipezeka ndi black box kmso zimazaza ndianthu 10 bs ngatiso amalawi tinaona ndimaso kt ndege ija inagwela kumalo koipa kukhalango kovuta kufika bs tiyen tivomelezed
@trifoniachilunda62632 күн бұрын
Tikufuna black box kunkuyu utuluse black box
@AnorldKamponda2 күн бұрын
Msusa ndi Malawi weni weni si za bambo asikonoziii
@GreyPuzani2 күн бұрын
Ndpo black box ikabwel ngakhal one ndizakhutila
@wisdomchilanga7232 күн бұрын
Palibe amene angakhutire ndi report ya kafukufuku wanuyo chifukwa Black box Palibe, kodi ndege imeneyo inali ndi lunzu nchifukwa chake idayamwa magasi kusanduka mafuta?
Inenso ndi banja langa sitikukhutila ndi report ya commission of inquiry.
@JoshuaJuwawo2 күн бұрын
Report latuluka munyengo ya kugwa kwacha, no fertilizer, no rains nde chodikira ndi chani sanalakwise ife siana
@ShuzgoLiwaya2 күн бұрын
Tilipambuyo panu asusa ineso sindikukhutila
@MACFARLANEMULENGA2 күн бұрын
Kodi anayika kukhala bishop ndani, munthu ndi slam angalankhule zabwino, kungodza ndi shaila law basi
@McDonaldbeketeNkhata-n4l2 күн бұрын
kutha kwankhani iyi ndikubweresa black box basi
@MaxwellMilanzi-w5k2 күн бұрын
Ndipo kuthonthozanako sikuchedwa malingala ndi infayo m'mwe inalili infa ya ngozi ngati iyi hmmmmmmmm ayi kuthonthozana kumvuta man chifukwa mwina kalelo time ya kamuzu BAnda km panopa hmmmmmm
@Kamwachale2 күн бұрын
Let us be talking sensibly, if someone comes in open to say the Holy Spirit Has told me that Chilima was killed, how many will believe to hat particular person. What type of peace people are talking about if the truth of the matter is buried in the ground. So many spiritual facts that Chilima did not die natural death
@gracekusamale74682 күн бұрын
Ai ndikupingo kwao amalalikila khosa zawo
@WilliamNhlane-fd9hi2 күн бұрын
Nkhani singathe pokha pokha boma libweretse black box.
@user-ux3ed3ni1p2 күн бұрын
Anthu akufuna kuti ti iwale. Koma azapanganso. Zizakala iweyo. Ayi takana, this time we will hold those responsible accountable. Black box #1. Ntendele ndi Chilungamo. Its Accountability.
@GreyPuzani2 күн бұрын
Amphongolo mulibe fundo
@NokiaNokia-e2t2 күн бұрын
Amat chilungamo ndi mwano muwona pen agalu inu
@FisherAction2 күн бұрын
Mbongolo simunthu ayi kodi commander umboni woti ndege inagwera kowirira, kunkuyu amati wasamala black box president amati every 4hrs report izimufikira amatero chifukwa chani
@EmilyKanyika2 күн бұрын
Eya zoona
@CharlesKachipanda-jz9jv2 күн бұрын
BOLA WABAYA BASI
@mabvutomichaelpanagona19492 күн бұрын
Ndi mulungu
@blessingsmasina92542 күн бұрын
The truth is all reports are bogus. Olo ndili ine kupanga report labodza nkanatha kulemba bwino kuposa mbwerera zomwe apanga in the name of report...nanunso ma presenters and journalists please sizomabwera pa air nkumakhala ngati mwamvetsetsa report and that it is clear...izizi zomalemekeza chibwana chaziwembu nzosayenera coz anthu ndiokwiya kamba ka nkhanza zimene zaoneka 2024
@FisherAction2 күн бұрын
Palibe kuvomera unless kunkuyu atuluse blackbox chifukwa anatiuuza kale zoti yasamalidwa komanso mzake wa wayana sakulankhula yabwino ayi asamale
@ZechalionSamuel2 күн бұрын
Basi inaya azaipanga lives mawa
@MACFARLANEMULENGA2 күн бұрын
Ngati akudziwapo kanthu bwanji osabwera poyera bwanji . This is nonsense, bwanji osamutenga yemwe anajambulayo mumubweletse poyera bwanji.
@jonesjumbe2 күн бұрын
Brack box ituluke basi
@user-ux3ed3ni1p2 күн бұрын
Innocent sanamvetse bwino, a whole Archbishop shuwa? Ndiye iweyo unavetsetsa bwino zakukwanila iweo. Kamuzu had people like you who propped him and up kuti tiiwale, antu akudyedwe ndi ngona.
@MACFARLANEMULENGA2 күн бұрын
Bishop wa chimaso maso komanso munthu waudani kwambiri
@user-ux3ed3ni1p2 күн бұрын
Words from the pulpit are meant to be heard and spread whether we have cell phones or not. Vayana Don't censor our faith leaders