tikusowa ma fees sukulu ikukanika nkumene, may the Lord help kwa ena onse amene mumatenga dzanja lanu kuthandiza ana ovutika munjila zosiyana siyana, .. sorry ndangopezelapo mwai kuti l can speak on this thank you
@GuejendraMk10 күн бұрын
Sulemani Kwa ine ali ndende ngatMalema wa SA. Kulan khula mosaopa. Sinamvepo zot akufuna kumuchita impeach. Amantulusa koma amalowanso. Kuno vuto ndi chani
@MathewKalinkhu10 күн бұрын
Brother, sangawamange, palibe chifukwa chowasakila a police, akinena Chilungamo chokha chokha. APM basi, dziko lawonongeka economy ndi boma lake la MCP.
@noahkalima529410 күн бұрын
Titani poti tatani kale,, piter wapita kale pampando
@MacxwellStuarts-h9r10 күн бұрын
Ndizoona kuti boma la mcp mosogozedwa ndi achakwera laononga ziko la Malawi mu zinthu zonse koma ndimafuna ndipemphe nawo ngati mkotheka andale onse zipani zonse titati tisiye ntchitidwe olalatirana sizingatithandize sizingatisungire ulemuu
@ABDULEasha8 күн бұрын
❤dpp.akafuna kumanga munthu akamange chakwera .
@TopClass-p9r10 күн бұрын
APM,vote yanga.
@MosesTangwe-q8o10 күн бұрын
Aaah kumangidwa kwachani waba chandani kuti ammange.tsogoleri wadzikoyo simunthu? ndipo ngati sakuchichita bwino anthu azingosekelera cz of ndi president?
@SherifaG.Mlelemba10 күн бұрын
Koma Suleman🙆🙆🙆😀😀😀😀
@AlexiousAjibu10 күн бұрын
Chilima uja asanamuphe 😅😅😅😅
@HamzahTwaib10 күн бұрын
Selemani ndiwe katundu serious ❤
@JamesSank-h9u10 күн бұрын
Tikufuna Tikufuna Tikufun adadi
@LucksonKumwenda-p2f7 күн бұрын
😂😂❤❤ Kma Yaaaaaaaaa
@JamesMateyu10 күн бұрын
Apm my only vote
@hanifahmponda87119 күн бұрын
Aaaa iyi mcp kuyitsekekela tibwelela ku CHIPANI CHIMODZI
@REXCHARLESKAJAWO10 күн бұрын
Ana amunatu awa, 😂😂😂 oowooo!!!
@WanangwaMfune10 күн бұрын
Tiona zonse end of September 2025, ngati ena sazazimangila ndi mwai kkkkk
Mukuthatu mau apa nde magesi tizizangounikila pokudya pokha paja ndi zomwe mmapanga, dpp inasinthapo kukhala (diesel petrol palibe) nde muzapangeso ma albino analibe chitetezo muzabwelezeso tizathamangisanapo
@LinlyMathewe10 күн бұрын
MCP chitetezo chonwe anapreka kwa ma albino ndi chotani?musatinamize imene ija inali propaganda amaoha ndi a Mcp