Bakili Muluzi tv is not just a man but he is a digging history man. Very intelligent.
@NickyJohn-m7z11 ай бұрын
King history i am so proud of you brother❤
@georgeaiwa86612 ай бұрын
Live long BAKILI MULUZI TV. I wish I could see you personally, but regarding security reasons, I support you being unknown. you are actually the Best on how you display your exposure of what you impart
@christophermkhize199111 ай бұрын
Never sleep waiting for this, timakunyadilani kwambili bro Allah must protect this man
@joekawenga316311 ай бұрын
Khaaaaaa!!! Machine awa. Big up brother.
@chrismakhela713311 ай бұрын
Our man is indeed arrested.. 😢😢😢 I watched this video months ago 😢😢😢 please release Free our man 😢
@ibrahimjackson-cg6tc11 ай бұрын
I was waiting this video from yesterday, thanks Boss
@jacksonmaster228811 ай бұрын
I was waiting for this since yesterday
@BenissoneErnesto-kn9bd10 ай бұрын
Samuel doe anali munthu oyipa kwambir palibe chinalaksika kuphsdwa anazunza anthu osalakwa komanso anapha anthu osalakwa ochuluka watching from mozambique
@chirwaellace1093Ай бұрын
Koma Bakili Muluzi tv history umakhonza 100% mmmm big up
@YusufRahimu-be9hu11 ай бұрын
GOD BLESS YOU FOR BEING TRUTHFUL PERSON
@PatieKates9 ай бұрын
22
@JaphyJ11 ай бұрын
You deserve respect Mr historian
@mussapeyala598111 ай бұрын
We really appreciate your information..ulemu wanu.
@KhimzyMike1311 ай бұрын
Aah uyu wamangidwa basi chifukwa Chan ukubwereza zimenezi tinayivera kale iyi " kutheka Pali zake yemwe akupanga zimenezi pofuna kuti weni weni yo "atulusidwe
@bakilimuluzitv337111 ай бұрын
Ndie ukayimvera wapeza kuti ndi yomweyo?
@KhimzyMike1311 ай бұрын
@@bakilimuluzitv3371 sorry sir ❤️ ndinayamba kukusatilani kale kale ndipo zomwe zikuvekazi Bola zisakhale zowona 🔥
Ifetso tipanga kwa president chakwera chifukwa akujayira kwambili
@philliphofenkuwanje55092 ай бұрын
❤❤
@ishmaelmkuluma201311 ай бұрын
Mbambande brother 😊
@CharityGondwe-bw9gs4 ай бұрын
❤
@JoshuaNgosi-c8u2 ай бұрын
Anali wa khaza samuel doe
@kimbonhlane544411 ай бұрын
Just when they thought they had extinguished the fire, boom 🔥! 😂
@HamzaManda11 ай бұрын
Where is new video muli bise ndi MA history amene munapangs kale kapena zoonadi akumanga yettiiii
@veronicamalisero26713 ай бұрын
so does that mean prince Jonson became the next president? nanga Charles taylor zinamuthela bwanji
@jonathanmbewe424611 ай бұрын
Yes abigy
@CynthiaBlessings-dx8eb3 ай бұрын
Big up bro
@khalifacalvinajass999811 ай бұрын
King of history I'm so proud
@RiteRoderick3 ай бұрын
Koma yaaaaah Chakwera samala kwako nawenso kwatsala pang'ono kuti kuthe
@GenialaChalera7 ай бұрын
Wa dpp iwe umangokamba zandale umabakira dpp
@isaacschamatwa359611 ай бұрын
Big up
@KupeSuwed-db5cr11 ай бұрын
Ai l think abro wa ndiomwewa but mukale osamala mcp ikupanga zainu bro apo ai izi musie okusatilafe ntilimba ntima koma tikudandaula enafe because munasegula mithu yambili ya anthu so ntikulila ife km bro basi musie please bro anthuwa akukusakani so ukupani but God atetezere inuo zkm kulikose komwe muli ulemu wanu bg
@felixphiri-ky3kv11 ай бұрын
Bg up broh
@funnyvideostv408311 ай бұрын
Mesa kd akumangani inu
@ulemuchisale5 ай бұрын
Amabwezera revenge 😂😂😂😂😂
@ChristopherMapondoАй бұрын
Mumakwana big
@JohnChibalo-wf8gr11 ай бұрын
Dzikomo big timamudziwa zambiri chifukwa cha inu ?
@KimJime-d9k2 ай бұрын
Taphunzirapo zambiri
@joegibsonzulu259911 ай бұрын
Doe anali munthu oyipa kwambiri.He deserved everything that happened to him.
@Nilakay0711 ай бұрын
Rfd7
@Nilakay0711 ай бұрын
Gyyy
@Nilakay0711 ай бұрын
Gy
@havardjizale998811 ай бұрын
Akulu awamangadi eti...chifukwa video ili ndi ya kale...Zomwe amati atulutsa Ina sizinakwaniritsidwe...
@daudimatolano17155 ай бұрын
He was a bad guy mmmh
@rangersonngirazi674111 ай бұрын
Amwene inuyo mumakwana.
@alickchiumia261611 ай бұрын
Eti kufuna kutchuka ,kumangonyoza anhhu a mcp . panopo uliko wekha or dpp soyingakuthandize
Koma mu video yo wanena po kuti ndilipo sindinamangidwe.? Bigy yi ainjata magyz... coz mu video mu akadanena kuti mdilipo.. ndithu
@AbuMussah-wi7gb11 ай бұрын
You are expected for everyone
@joegibsonzulu259911 ай бұрын
Mwati bwanji 🙄🙄🙄?
@WebsterMhone11 ай бұрын
Iyitu mnaikamba kale ndipo ilipo kale bwanji zikukaikitsatu simunagwidwedi wamkulu
@malvinhusted624511 ай бұрын
Wasala chakwera
@SHAMIUNAMUSTAFA11 ай бұрын
machine awa
@medsonwalaza881311 ай бұрын
Following
@molicieeosama887711 ай бұрын
❤💪💪🤔👍
@sheila581211 ай бұрын
Yobwereza iyi
@ShayibuJames11 ай бұрын
Ulemu wanu bwana wanga
@shamsdeenuthmanmsikita171211 ай бұрын
Kod boma lamanga ndan 😅😅😅😅 ife tikusisimukabe ndi mbili zosiyana siyana
@PreciosNdlovu11 ай бұрын
big mumakwana
@greenmatias833211 ай бұрын
Nkhani iyi munayikamba kale
@joekawenga316311 ай бұрын
It's a continuous one. Please listen mpana kuthela.
@husseinmoffatt11 ай бұрын
DimakunyAdilAn
@SolomonNjolomole11 ай бұрын
Ndiyakalekale iyi plz
@PromisesStuart11 ай бұрын
Koma Pali ena sanayimve
@bobchola508311 ай бұрын
But this story u already uploaded it some years back
@joegibsonzulu259911 ай бұрын
I cherish this repeat because I never watched it when it was first uploaded.Now I have bee able to watch it😁
@Bosskind-wx7ev11 ай бұрын
𝔹𝕣𝕠 𝕚𝕟𝕦 𝕞𝕦𝕞𝕒𝕜𝕨𝕒𝕟𝕒 𝕙𝕧𝕪
@sibokawana235811 ай бұрын
Tinayivera Kaye iyi pompa
@patrickkamsale639911 ай бұрын
Ife timadxiwa kuti iwe sangakumange
@hardwaremkango691011 ай бұрын
Alengezatu kut akumanga iwe pa radio
@shideshidex567911 ай бұрын
Doe Was Not a Good Person
@DickMdala-pn4pd11 ай бұрын
Koma big tiyankhuleni pazomwe zikumvekazi
@KenChitete-pg3ws2 ай бұрын
Anachita bwino kwambili,,wakhadza adzikumana ndi khadza
@ChristopherMapondoАй бұрын
Mumakwana big
@mathewspmaliko11 ай бұрын
I once watched this same video some months ago. I've that sense that our man is indeed arrested, and this is but a deliberate and planned repitition.
@joekawenga316311 ай бұрын
No, it's another one. That one has part one, two and three.
@KenMasta-w6c11 ай бұрын
Tell your Masters that this man can not be arrested only for giving the nation history alive....uyu Alipo ndipo zikhale Ng'oma sangakwanitse kumumanga.bviva BM tv
@raffickaffick11 ай бұрын
naneso ndikuona choncho video iyi angoibweleza , kunena chilungamo amayenera kubwela ndi voice recording ndikutiuza chilungamo chakhaniyi
@raytavares225611 ай бұрын
It means that they have hacked his phone and are using his KZbin account to trap his followers 😢😢. Ni hope that he has a good lawyer and he has been released.
@AnafieIntuka11 ай бұрын
Support kwa inu Sir ndpo sitizaleka support
@soxdososola293711 ай бұрын
I don't know what is trending on Facebook is true that you are arrested 😢😢😢😢
Kodi mwati Samuel dowe anathandizidwa ndi ma Americans and Charles teller anathandizidwaso ndi ma Americans cholinga cha ma Americans chinali chani pa zithandizo zonsezi kwa anthuwa?