Minyama yathu ngati amalawi ikuchokera pati?

  Рет қаралды 74,829

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Күн бұрын

Пікірлер: 218
@farookousmane715
@farookousmane715 Жыл бұрын
We are all Africans...when I see a burund person I see myself.
@raspeterkasengwa1390
@raspeterkasengwa1390 Жыл бұрын
Though you don't show your identity. You remain iconic
@Wesleywisk-lf5hw
@Wesleywisk-lf5hw Жыл бұрын
Achakwelaso uthengau ukupezeni
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
Malawians people please let's wake up and fight for this country chakwela akutitenga wezi kwambili
@BenissoneErnesto-kn9bd
@BenissoneErnesto-kn9bd Жыл бұрын
Komaditu brother Malawi ndikachani panagaga ngati pamenepa anyamatuso ambir Ali maiko ena kuthawa kupandako kanthu kumalawi zinkhale Ng,OMA watani kd komatu zimenezi siku Lina zizamusata
@rickiez
@rickiez Жыл бұрын
And I quoted "za mawa sizidziwika" ndili wokudzika kwambiri. Thanks for the information may God bless you
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Жыл бұрын
Zoona zake bra
@AishaMweso
@AishaMweso 11 күн бұрын
Zikhale koma mmmmm mtule pas
@stevechikaonda3145
@stevechikaonda3145 2 ай бұрын
I must admit that this unknown guy is intelligent and wise
@SufiaanMsusa
@SufiaanMsusa Жыл бұрын
Am here waiting you boss from Johannesburg
@HusseinMm-z3j
@HusseinMm-z3j Жыл бұрын
Zikomo brother mumatitsangalasa 🙏🙏🙏🙏
@fedson2050
@fedson2050 Жыл бұрын
Chakwera suzamva Munthu opanda Nzeru iwe ndi Mnzako Zikhale N'goma
@raytavares2256
@raytavares2256 Жыл бұрын
Thank you for revealing the TRUTH. You must write a book about this history. It's true Malawi never ever bothered to help South Africans and yet today they still go to South Africa to work. Even now they follow the same patterns. Look at how they prefer keeping criminals and yet on Sadec. Do you recall how Kwacha Ng"ambi committed crimes more than Bushiri in South Africa? And South Africa will always be loyal to Malawi. Look at the Wenela period?
@sammyree8843
@sammyree8843 Жыл бұрын
I have been following for while brother very educative as we grew up in a country that real history was hidden to us. Please can I donate to you?
@henrysoko3283
@henrysoko3283 Жыл бұрын
I wish to donate too, this man has brain washed me
@OmarAskimu-cn4ti
@OmarAskimu-cn4ti Жыл бұрын
Even makolo athu anatiuza zakuipa kwa MCP
@titomethiwa4213
@titomethiwa4213 Жыл бұрын
Zikhale ndichisilu ndimuthu oipa kwambiri
@christophermomba7127
@christophermomba7127 Жыл бұрын
Thanks for information keep it up Bakili
@johnsong7236
@johnsong7236 Жыл бұрын
i always smile and learn something at the same time
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 Жыл бұрын
Ndizoona, tilikonkuno ndipo akutisunga ndiomwewa
@NgendahayoSosthene-qn7qn
@NgendahayoSosthene-qn7qn Жыл бұрын
mukanena dzina ra charichi cyo ndikanafufuza umboni wa nkhani imeneyo rero romwe.
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 11 ай бұрын
This is very powerful massage ❤❤
@Gibbs-yp6um
@Gibbs-yp6um Жыл бұрын
Mumakwana munthu wa'kulu kip on giving us nothing but the best history.
@johnman4619
@johnman4619 Жыл бұрын
Ndizomvetsa chisoni mbiri yadziko lathu mutati muoni the holl Africa ndife thokha amalawi tilindi mbiri yoyipa mu independence koma zonzezi ndi Cecelia and John tembo
@TriciaMalikebu
@TriciaMalikebu Ай бұрын
Kamuzu & his party, MCP will never change
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson Ай бұрын
Uchitsilu basi, zelu ngat mazula ku john sadziwa businesses safuna ntchito koma jerous ndi anthu.
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 Жыл бұрын
Thanks very much continue doing that
@charlesRajabu-cc4bx
@charlesRajabu-cc4bx Жыл бұрын
Always you mumanena chulungamo mumayipasa fire
@Littlefair7
@Littlefair7 Жыл бұрын
Amalawi ambiri ndi ma illegal immigrants ku America, koma ali ndi ma business, amaloledwa kutenga loan ku bank even kugula nyumba kapena galimoto pa ngongole,, ndipo akuchita bwino kuposa ma americans. Boma la America limatolera misonkho kwa onse koma mabulutu amene akuyendetsa dziko la malawi sakuona patali.
@MussahGeorge-f5n
@MussahGeorge-f5n Жыл бұрын
From Pretoria, love ur stories
@jonathankwangulero4450
@jonathankwangulero4450 Жыл бұрын
Chakwera and his MCP has failed Malawians... But, politicizing the issue of Refugees is wrong. Ma refugee kulikonse amayenera kukhala in designated places. It's no rocket science.... Mpaka Refugee azipanga business aaah sizowonaa
@idrissaKGO
@idrissaKGO Жыл бұрын
Jerous siimapindula gyx amalawi
@BlessingsBanda-qn7xr
@BlessingsBanda-qn7xr Жыл бұрын
Mngopusa zikhale mbale zake mapoto ake komaso paniyo pake 😂😂😂😂😂😂
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂
@wysonnamaona6497
@wysonnamaona6497 Жыл бұрын
With you all times... Thank you for opening up our eyes.
@khumbozimba-r4h
@khumbozimba-r4h Жыл бұрын
Chanel yomwe ndimaikonda palibeso kuposer iyi ulemuwanu big
@alexKaudzu-f6o
@alexKaudzu-f6o Жыл бұрын
Pilizani bro kutsegula maso a Malawi
@EphraimNaveya-fc4iu
@EphraimNaveya-fc4iu Жыл бұрын
Nice 👍 talking sir,mcp it's one party that makes Malawi to be poor/minyama country
@bjmtalimanja5073
@bjmtalimanja5073 Жыл бұрын
Andrew chimwendo kumwamba siwukalowa ndithu
@johndaka6368
@johndaka6368 Жыл бұрын
We are proud with u in Africa
@DanielNgondo-rr9gd
@DanielNgondo-rr9gd Ай бұрын
11 minutes ago.....58 thousand viewers....ayi zikomo
@maxwellchibwe5956
@maxwellchibwe5956 8 ай бұрын
Ngakhale ena atsutse or ayi koma nkhaniyi ndiyoona kamuzu doesn't been regarded as pan africanist or one of greatest African leaders we had in Africa. Muone mu history ya Africa ikuonetsani zimenezi
@BensoPias
@BensoPias Жыл бұрын
Best historian your nomber one
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 Жыл бұрын
Auzeni asiye majelous
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Жыл бұрын
Ife kuno ndiye tilipo samativutisaso achewa ngovuta ndaonela pa chakwela
@JonathanMtambo-w6e
@JonathanMtambo-w6e 5 ай бұрын
This shows exactly that we are acursed nation
@SandraMoses-y4l
@SandraMoses-y4l Ай бұрын
Abale anzanga zikufunika tikavote mwanzelu serious chakwela ayi ndithu
@ElliasChikuluwadza
@ElliasChikuluwadza Ай бұрын
Kkkkkk Kma mbakili muluz ndi mamunadi.
@parker2104
@parker2104 Жыл бұрын
You know man I hate being a friend with this refugees, samanvetsetsa tikafuna tipakambilane zithu, ndamakani especially Ma Rwanda iiiiiii
@angelj3771
@angelj3771 Жыл бұрын
Zithu ngati zitizo?
@LouisAndrew-jr1yj
@LouisAndrew-jr1yj Ай бұрын
History is the best teacher ✌️
@AfiyakazembeKazembe
@AfiyakazembeKazembe Жыл бұрын
Zoona big ine Kuno Western Cape Harare
@AleksaWilliams
@AleksaWilliams Жыл бұрын
Kumakhaladi ndi umunthu,ndizoyilanad zithuzi
@MefaKumwenda
@MefaKumwenda Жыл бұрын
Than you for explaining all history
@ALuz980
@ALuz980 Жыл бұрын
Ndizoona Khalidwe la nyau siligatithandize
@BrownChinkhota-o2h
@BrownChinkhota-o2h Жыл бұрын
Ngati a MALAWI sitinathandize pomenyera ufulu chifukwa tilibe zothandiziraa
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 Жыл бұрын
Tamugwileni mum'menye nachimutuyo, ana omwe anabadwila ku Malawi ko, ndi Malawian, chotelo akuzunzisa anawo
@jeanmariehavugineza9382
@jeanmariehavugineza9382 Жыл бұрын
ine ndimafuna gupana support nchito zanu mutipatse number kapena njira yina kuti titandize nshito yi
@pastorbinuelf.lamusse6203
@pastorbinuelf.lamusse6203 Жыл бұрын
Timakunyandirani big kuchokera Kuno ku Moçambique Maputo.
@alickchiumia2616
@alickchiumia2616 Жыл бұрын
KUKANGOCHA KUMANGOGANIZA ZOTI MUNENA CHIYANI CHOKHUZANA NDI MCP .
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 Жыл бұрын
Chakwera ndi opanda mutuu
@matembanevermind-po3me
@matembanevermind-po3me 9 ай бұрын
Tchutchutchu mofatsiliranso ndpo,mumakwana bigy
@JafaliAlli-w7m
@JafaliAlli-w7m Жыл бұрын
zikhale ng'oma mulungu amulanga pompano ndi juma yemweyo mulungu akuwuona akuzunza anthu
@isaaclano6599
@isaaclano6599 Жыл бұрын
A malawi chikondi alibe muli anthu ochita aKU Malawi tikuwaziwa chifukwa cha DNA ya makolo Yolanda chikondi kusakhana zigawo Kuno kunali mnyanata ophunzila amathandinzila ANC Za chumaKoma anamwalira ndi covid Koma Amanda Kuti Malawi Juli sanje Koma Kuno anatengedwa ndi Trevor Emmanuel
@PreciousDouglas-d7v
@PreciousDouglas-d7v 7 ай бұрын
Ur de best tv
@MichaelWilliamsNyirenda
@MichaelWilliamsNyirenda 3 ай бұрын
Malawi amangoziwa kutamba usku
@sipplezulu
@sipplezulu Жыл бұрын
Africa tigwirizane ndife anthu amodzi
@wysonnamaona6497
@wysonnamaona6497 Жыл бұрын
Zikhale ng'oma amadziwa iye ndi kuvala Zima trauza zikuluzikulu basi
@alickchiumia2616
@alickchiumia2616 Жыл бұрын
KODI BASI NKHANI IZINGOKHALA MCP MCP . MUNALUZA INUYO A DPP . TIMAKUZIWANI KUTI NDINU MA CADATE A DPP PANO ZIKUKUWAWANI
@idrissaKGO
@idrissaKGO Жыл бұрын
Timakunyadilani bg
@LloydMkandawile-c9p
@LloydMkandawile-c9p Жыл бұрын
Kulibe zuko lomwe lilibe wobwela ziko lose lapasi kuli athu wobwela so tisamapange zithu ngati wozindikila kwambi pomwe tili wosawuka
@PromiseBarton-em1ll
@PromiseBarton-em1ll Жыл бұрын
Chakwera zikhale ng'oma anthu awa ndimbuzi za anthu😭😭😭
@PaulKwenda
@PaulKwenda Жыл бұрын
Iwe ndiye mbuzi
@YunusuOfesi
@YunusuOfesi Жыл бұрын
Zikhale ng'oma ndigalu alibe chisoni ndi azawo
@DaudBonomali
@DaudBonomali Жыл бұрын
Nkhani ndiyakuti pa 30 pano agalu amenewa adzipita basi kufakufa pa 30
@SharifahWillardChampionn-rn8cm
@SharifahWillardChampionn-rn8cm 5 ай бұрын
Machende kamudzu sanali Malawi galu wachabe chabe anangowononga zinthu
@YAKOBEJUMAH
@YAKOBEJUMAH Жыл бұрын
@gabrielmaluwa1038
@gabrielmaluwa1038 Жыл бұрын
iweyo ndi dolo
@TonyBanda-ch6vo
@TonyBanda-ch6vo Жыл бұрын
Koma inuyo bigy munabwera respect to you .
@manphiri2778
@manphiri2778 Жыл бұрын
Koma nchewa mwamunyoza kkkkkkkkk amangodziwa kudambwe eti
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 Жыл бұрын
Tamuuzeni kumeneko chitsiluyo, ifenso tilikuno kudziko la eni
@jwsitaubi287
@jwsitaubi287 Жыл бұрын
Ngati kuli nyumba zambili za malata ndi chifukwa cha anthu oti anapita ku Rsa Shame
@horagerva
@horagerva Жыл бұрын
Mulungu akudalitseni. Zoona mukunenazo.
@daviemafunga
@daviemafunga Жыл бұрын
Inuyo is bstter kukhara brother wanga
@lesterkenkandoje5375
@lesterkenkandoje5375 3 ай бұрын
It's never too late 😞
@davenchimadzi6529
@davenchimadzi6529 Жыл бұрын
Power bro.
@francombalasa3241
@francombalasa3241 Жыл бұрын
Ndichifukwa chake nyimbo ya fuko lathu imanena za njala, nthenda ndi nsanje.
@HamdanMasuku-b3n
@HamdanMasuku-b3n Жыл бұрын
Ndwe dolo ase keep up
@PhiriJames-nk1qu
@PhiriJames-nk1qu 11 ай бұрын
Ndizowona zake zimezi man
@ChisomoNthukwa
@ChisomoNthukwa 3 ай бұрын
Ndipo MCP sizachokaso m'boma
@George-zd5le
@George-zd5le Жыл бұрын
Malawi zoona zake ndi zomwezo
@lyiemax
@lyiemax Жыл бұрын
Boma lambava ili, very tired of it
@OFG-th3st
@OFG-th3st Жыл бұрын
We appreciate
@innocentliyawo3943
@innocentliyawo3943 Жыл бұрын
Vuto kamuzu sanali waku Malawi hence anali wopanda chisoni
@YunusuOfesi
@YunusuOfesi Жыл бұрын
Koma chakwera ndi zikhare ng'oma aziganiza kuti kunja kuno kuli ife azasitenge ngati ndiwamuyaya sanje silabwino
@CharlesChisoso2
@CharlesChisoso2 Жыл бұрын
Ndipo chàkwera azazioona😢😢😢😢
@jahiemmusa8796
@jahiemmusa8796 Жыл бұрын
amalawi ntisiye mzanje sungathitandze tizingovutika
@FredSalimu
@FredSalimu Жыл бұрын
MCP ndi chipani cha anthu akale
@BdhfbHdhe-pd7nh
@BdhfbHdhe-pd7nh Жыл бұрын
Mcp ndagalu onse
@chippiephiri4505
@chippiephiri4505 Жыл бұрын
Uthenga uwu ndiwoona
@joicemartin-ji5zu
@joicemartin-ji5zu Жыл бұрын
Andrew cimwendo munthu oipa mtima
@julietmwanza
@julietmwanza Жыл бұрын
Malawi back to mcp great mistake full of brood of Gadama matenje and so on
@lacfunnytv1251
@lacfunnytv1251 6 ай бұрын
The last question
@jamesjealous-p4v
@jamesjealous-p4v Жыл бұрын
Zowona ndikumudziwa chimwendo simukunama
@MaliGomani-g7g
@MaliGomani-g7g Жыл бұрын
Inuyo timakudalirani
@mondaywoods2975
@mondaywoods2975 Жыл бұрын
zoona zokha zokha
Ukakwera pa msana pa njobvu😍; President amene anadyedwa ngati nkhuku.
23:12
How Strong is Tin Foil? 💪
00:26
Preston
Рет қаралды 121 МЛН
The day of the sea 😂 #shorts by Leisi Crazy
00:22
Leisi Crazy
Рет қаралды 1,7 МЛН
Kaizer Chiefs 1-2 Mamelodi Sundowns | Referees Are Killing Our Football!
9:56
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 129 М.
Abale ake a John Chilembwe ali kuti?
15:36
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 42 М.
Adaferanji mkulu wa asilikali a nkhondo, General Manken Chigawa
19:53
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 124 М.
How Strong is Tin Foil? 💪
00:26
Preston
Рет қаралды 121 МЛН