BASITU... MR MWANAMVEKA ATATUMIDWA NDI MUTHARIKA KUKALANKHULA,.. APEZEKA ANYOZASO ANZAWO MOTERE

  Рет қаралды 32,050

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 144
@InnocentNitamanMilanzi
@InnocentNitamanMilanzi Ай бұрын
Opanda mfundowotu ndiye alipo ambiri nanga chikangawa mfundo zake zili kuti ife kumuyang'ana adad
@mollymasangano473
@mollymasangano473 Ай бұрын
My vote APM Boma ilooooooooooooooooooo❤🎉❤
@franciskapakasa36
@franciskapakasa36 Ай бұрын
illiteracy at its best, God will surely give the poor Malawians wants , not again to the DPP in Government,Chakwera Woyyeeeeee
@RABSONSIKELO
@RABSONSIKELO Ай бұрын
Cha dad chala mmwamba et!!!
@LovelyDumplings-yf7pd
@LovelyDumplings-yf7pd Ай бұрын
Zinayamba kale kale zinthu ukwera tinazolowera olo zikwere timagulabe chipan sichipatsa ndalama olo boma silipatsa ndalama timasaka tokha patchito timagwila
@prudomaninc7643
@prudomaninc7643 Ай бұрын
mmutu mwangozaza mamina okha okha...... tazinenani chilungamo
@bs-malawi
@bs-malawi Ай бұрын
Kkkkk
@LimbaniLumanga
@LimbaniLumanga Ай бұрын
mwasowa zokaba et ine ndizavotela chikomeni
@GidionMateche
@GidionMateche Ай бұрын
Koma ine kati ndaonongeranji bundle wanga ndikumavela mbwelela ngati izi
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w Ай бұрын
Dpp my best party ❤
@hastingskayange
@hastingskayange Ай бұрын
Nima soap adali pa k80.00 osati k300.00 ayi ...auzeni anthuwo za kukwela zithu kosaganizila amphawi..malata adayambiri k4,500 ndipo cement adali k4,500 koma pano malata ndi K12,500 cement pano ndi K22700;Kodi dziko litukuka bwanji ngati zithu izizi zili Chocho..😭😭yanga vote ndi APM
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 Ай бұрын
Zithu zikusitha dairy man u should to read baibulo man, siolamurira amakweza zithu koma nthawi man...
@BenardMando-v5p
@BenardMando-v5p Ай бұрын
Kulesa kuti wa chipani china asabwere kudera lina sizabwino,kumeneko ndi kugawa dziko ,Malwi ndi mmodzi uyu
@RiteRoderick
@RiteRoderick Ай бұрын
Garu wanu Chakwera akupangazo bwanji? 😂😂😂😂 Mukhaula tikuzapha muzaona wina azayerekeze kufikako
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Ай бұрын
Ndipo asabwere kuno iyeyo chakwera wakoyo
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu Ай бұрын
Kmtu muziziwa kt nayeso chakwela amalesa a DPP kupita kulilongwe
@RiteRoderick
@RiteRoderick Ай бұрын
@@MussaZakeyu Ndipo brother anthu Enawa ndiogona bro
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Ай бұрын
Anayamba kukaniza kulilongwe ndi chikangawa wanu uja kuzolowera kupha anthu
@Daniel-cf4tu
@Daniel-cf4tu Ай бұрын
Kkkkkk koma azigogo awa atisunga?
@GiftNyamulani
@GiftNyamulani Ай бұрын
Muthalika anakalamba ndpo sakwanitsa ukuenda mmisokhan yakampen.
@halordbwato
@halordbwato Ай бұрын
I see side effect of zidovudine
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Ай бұрын
2025 boma ❤❤❤❤❤
@prudomaninc7643
@prudomaninc7643 Ай бұрын
inetu ndikuti chakwera sachoka 2030 wooooo tazilubwani
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Ай бұрын
Chakwera akalamura nyumba mwako iweyo
@LovelyDumplings-yf7pd
@LovelyDumplings-yf7pd Ай бұрын
Tsankho amwana veka siyani tonse ndife a malawi
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Ай бұрын
Wina alira chaka chake ndi chino ndpo chakwera achoked tikufuna adad
@leonardzchavula3139
@leonardzchavula3139 Ай бұрын
Mr Mwananveka are you sure people have been dismissed??? No media has carried that information of mass dismissal.
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Ай бұрын
Ngakhale munyoze dpp Mulungu nde adziwa zonse
@HeneryPhiri-nv9pu
@HeneryPhiri-nv9pu Ай бұрын
Fundo.muribe adpp congerecy.singaturuke.m,boma
@SintaMbendera
@SintaMbendera Ай бұрын
Boma sitikusintha chakwera basi timisonkhano tozizila
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 Ай бұрын
AMWANAVEKHA KUKANIKA KULANKHULA. KKKKKKKKKKKKKK BOMA MUDZATENGA CHONCHI
@HanneckManili
@HanneckManili Ай бұрын
Kodi awa amayankhula mbwelera chonchi? Ndkangomvatu kuti Mwanamveka.Musanamize anthu apa, DPP failed uz, MCP has failed us too
@BlessingsNamilonje
@BlessingsNamilonje Ай бұрын
Ineyoo ndizavotela DPP koma anthu ake alibe chikoka choyankhula bolankoni suleema😢
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh Ай бұрын
Dpp my vote si choncho kod u nid to work hard brah mukuperewera pang'ono ofunika muzibangula ngt mkango
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 Ай бұрын
Kkkkkkkk 😅 MCP My vote koma amwene mwnadikumbutsa malemu izeki ndi jakobo 😅😅😅😅 mwasera bwanji
@HeneryPhiri-nv9pu
@HeneryPhiri-nv9pu Ай бұрын
Nsonkhano ukuchitika koma apeter,paribepo koma,Ari moyo. Kapena,, akudwara muzintenga,petermuthalika azirankhura yekha pasonkhano nkharamba kuno ai
@MaupoMhango
@MaupoMhango Ай бұрын
Aaaaaaaa izi nde zausiru. Inu boma linakulanikani kare osapusisa opusa kare apa.
@DanielMtawa-q4b
@DanielMtawa-q4b Ай бұрын
Sizikumveka akuti chani amenewa
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 Ай бұрын
😂😂😂😂
@DerlinNyirenda
@DerlinNyirenda Ай бұрын
MCP my vote
@Kamwachale
@Kamwachale Ай бұрын
MCP knows that DPP is the only party in Malawi with good strategies that is why MCP is now busy scouting DPP members with millions of Kwachas to buy strategies and be taught how to run the government.
@LovelyDumplings-yf7pd
@LovelyDumplings-yf7pd Ай бұрын
Kkkk koma zovetsa chison ku dpp kuli zithu kkkkk
@DykeMasho-u8g
@DykeMasho-u8g Ай бұрын
To be honest dpp singadzawine 2025.
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g Ай бұрын
Dpp moto❤️
@RiteRoderick
@RiteRoderick Ай бұрын
DPP yanyamuka ❤❤❤❤❤❤
@PatrickMwale-t1y
@PatrickMwale-t1y Ай бұрын
Mcp.vot
@BandachisangaDoreen
@BandachisangaDoreen Ай бұрын
Mesa munali momwemo tidakuchotseraninji ngati mumapanga bwino agalu nonse musamatipusitse
@StanleyDama
@StanleyDama Ай бұрын
Ippwoye
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa Ай бұрын
Zokayikitsa ngat mudzawine fundo zake zimenezi kulankhula kwake kumeneku ngat muli pa malilo
@PeterChipwaila
@PeterChipwaila Ай бұрын
Chipani chinatha ichi kamba kodzikonda anthu awa yangotsara midalala pa front how can they win
@ChristinaMitepa
@ChristinaMitepa Ай бұрын
Albino party
@RiteRoderick
@RiteRoderick Ай бұрын
Boma iloooooooooooooooo ❤❤❤❤ DPP my vote mpakana kale💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿
@IphanBintonChilonga
@IphanBintonChilonga Ай бұрын
Amwaveka fundo alibe nkhalamba party muuzane dziko lino simudzalamulanso Chakwera 2030 woooooo chanu palibe
@mphatsomonjeza4371
@mphatsomonjeza4371 Ай бұрын
Udzailira voti tako iwe
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 Ай бұрын
😂😂😂😂😂 agogo team....mulimba inu ndi MCP mbwelela zake zimenezi 😢😂
@AkimumusaMusaakimu
@AkimumusaMusaakimu Ай бұрын
that's true must go chikangawa
@isaacchirwa9518
@isaacchirwa9518 Ай бұрын
kkkkkkkkkkkkkkkk nde kukhala vice president wa dziko ndekuti tabetsa eishhhhhhhhhhhhh, basi dpp woyeeeee dpp woyeeeeee kkkkkkkkkkkk funduless
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh Ай бұрын
Akulu awa ndiyenso ai,zinatheka bwanji kuwina u vice president?
@ChristinaMitepa
@ChristinaMitepa Ай бұрын
Ziyanthu izi ndizomwe zinayambitsa mavito onse tikuwaona panowa
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er Ай бұрын
Adad motoooooioo
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 Ай бұрын
Kunalibekotu anagona eti😅😅
@LovelyDumplings-yf7pd
@LovelyDumplings-yf7pd Ай бұрын
Kkkkk koma amwana veka muchokera dpp woyeeee kkkkk
@LimbaniLumanga
@LimbaniLumanga Ай бұрын
kkkkkk kd mwatitegati zisilu zanu et
@MsondaBanda
@MsondaBanda Ай бұрын
Kkkkkk walala walala
@JamilaJafali
@JamilaJafali Ай бұрын
❤❤❤❤❤
@StanleyDama
@StanleyDama Ай бұрын
Pathako Panu!! nkhalamba za DPP
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 Ай бұрын
Koma akulu inu
@NolityKondowe
@NolityKondowe Ай бұрын
Anthu akuyoyang'ana.Anthu dpp sakuyifuna.
@PeterChipwaila
@PeterChipwaila Ай бұрын
DPP ndi zero pa zero mungonamizanapo apo
@LovelyDumplings-yf7pd
@LovelyDumplings-yf7pd Ай бұрын
Kkkk koma zovetsa chison ku dpp kuli zithu kkkkkkoma mazila omweo
@Musa2Musa-z5e
@Musa2Musa-z5e Ай бұрын
Kuyankhula kukuvutatu
@jomochirwa
@jomochirwa Ай бұрын
Mavuto sadabwele ndi chakwela ,mavuto adayamba kalekale ngakhaleso pa nthawi yanuso a dpp mavuto adaliso ambirimbiri wosamapanga mabodza apa ayi,inuso ndiye amene mudawonongaso zeedi kudzikonda ndi kudzikundikila.mwinaso chikhala kuti covic ikadapeza inu ndiyeso mukadatizuza kwambiri chifukwa a dpp mwachuluka kudzikonda zeeedi.
@AugustineIshmael
@AugustineIshmael Ай бұрын
Kod akungowatuma anthu bwanji sakubwela yekha peter muthalika
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 Ай бұрын
Ukalamba wafuta
@jamestimothy1537
@jamestimothy1537 Ай бұрын
Kodi ku Dpp ko kulibe odziwa kulankhula? Mukufuna kuononga chipani, eti.
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 Ай бұрын
CHAKWERA MY VOTE
@Musa2Musa-z5e
@Musa2Musa-z5e Ай бұрын
Ndimangomvatu kuri mwananveka mwanamveka aaaa
@LovelyDumplings-yf7pd
@LovelyDumplings-yf7pd Ай бұрын
Alibe fundo akuanamiza malawi amwanaveka
@chikublea8982
@chikublea8982 Ай бұрын
Nanga suleiman osapasa ulemu bwanji
@patricknthakomwa5613
@patricknthakomwa5613 Ай бұрын
Politics of tribalism and regionalism at its risk in Malawi.... Yes we need change in Malawi but we shouldn't boundary ourselves.... Let us build policy's and ideology should be the center of the debate not regionalism. Let the people vote based on the policies of the political parties..... This is why we saying Federal system is the only solution that can suit Malawi at this point.
@GeoffTchezan
@GeoffTchezan Ай бұрын
Iiiii ndatopa kumangonva DPP woyeee!!!😂😂😂 Agalu inu
@YankhoKavalo
@YankhoKavalo Ай бұрын
Boma ilooo
@BillySaukani
@BillySaukani Ай бұрын
Mfundo alibe a vice president kuma ngoti dpp wo yee! M malo mothila mfundo kkkkk koma
@MACFARLANEMULENGA
@MACFARLANEMULENGA Ай бұрын
Mpakana cha "adad" kikikik 🤣
@Johnybegood260
@Johnybegood260 Ай бұрын
Some people are not public speakers he could have left for the other people to speak public speaking ndi skill padela
@StanleyDama
@StanleyDama Ай бұрын
That's a fact Boss
@StanleyDama
@StanleyDama Ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂😂🤣😂🤣🤣🤣🤣😂😂😂🤣😅😂😂🤣😂🤣😂😂😂😂🤣😂🤣😂😅😂😂😅🤣😂🤣😂🤣😂🤣😅😂😂😂🤣🤣😂😅😂😂😅😂😅😂😂🤣🤣🤣🤣🤣😭🤣🤣🤣😭🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂😂😂🤣😂🤣😂😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣😭😭🤣😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😭🤣😭🤣🤣🤣🤣😭🤣🤣🤣😭🤣🤣😭🤣🤣😭🤣🤣😂😭😭🤣🤣🤣🤣🤣😭🤣😭🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😭😭😭😭🤣😭😭😭😭😭😭😭😭😭🤣😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭🤣😭😭🤣🤣🤣🤣😂🤣😂🤣🤣😂🤣😂😂🤣😂🤣🤣🤣😭🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😭🤣😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣😭🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂🤣🤣🤣😂🤣🤣😂🤣😭🤣🤣😂😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😭🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂🤣😂😭🤣🤣🤣😭😭😭😭😭🤣🤣🤣🤣😂🤣🤣🤣🤣🤣😭🤣😭🤣🤣😂😭😭😭😭🤣🤣
@VitumbikoMussah-t5t
@VitumbikoMussah-t5t Ай бұрын
Manyaka eni eni
@MiracleDamiano
@MiracleDamiano Ай бұрын
Ubale wako nd chikangawa akhare dolo nyani iwe
@AnnastasiaChakwiya
@AnnastasiaChakwiya Ай бұрын
Dpp my vote
@PeterChipwaila
@PeterChipwaila Ай бұрын
Kulankhura ngati mkamwa muli mpunga onyika
@KumbukaniChimbalanga
@KumbukaniChimbalanga Ай бұрын
Umuuze mwanamvenkha yo akamapita kumtsonkhano azikhala atakhomzeka mfundo zabwino
@ChimwemweBrighton
@ChimwemweBrighton Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂zovetsa chisoni akuyankhatu ndi munthu modzi
@BandachisangaDoreen
@BandachisangaDoreen Ай бұрын
Inu mudzatsitsa mulibenso mfundo mukusiyana pati ndale ndi bodza chilungamo ndi church
@MacDonaldkachala-cm5gc
@MacDonaldkachala-cm5gc Ай бұрын
Here comes the Bush doctor😂😂😂
@DeveliousMasinja
@DeveliousMasinja Ай бұрын
Eti okhaokhaso kumadisana 😂😂😂😂
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
DPP my vote 💙💙💙 boma iloo
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 Ай бұрын
Et chakwera wandilaura kansima kangonongono 😂😂😂😂😂
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Ай бұрын
😂😂 nawo a Mwanamveka mmalo molankhura fundo Pali pose DPP woyeeeee!!!!!
@MeltonChilambula
@MeltonChilambula Ай бұрын
Sichoncho kodi😂😂
@YusufMapata
@YusufMapata Ай бұрын
ngati wa police amupanga transfer kupita station yina vuto palibe koma munakati ntchito yatha panakakhala vuto mcp boma ndilomweli
@ChrissyBhima
@ChrissyBhima Ай бұрын
Mcp musaname,kuti mavuto anabwera ndi dpp,boza linakukulirani,ngati mavuto anabwera ndi dpp inuyo a mcp mukulepherw bwanji kuwakonza?musatinyase amcp chilungamo mukuchiziwa,koma mwasankha kunena boza ngati mavuto anabwera ndi adad sugar adad anamusiya pa bwa?nanga chimanga anachisiya pa bwa? Nanga mafuta agalimoto awasiya pa bwa?mcp muziweni mulungu
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 Ай бұрын
Mbuzi izi za DPP
@jomochirwa
@jomochirwa Ай бұрын
Ndi amene adzakhale pule after adad cz adad akula sadzatha kuyenda.
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 Ай бұрын
Kkkkkkkk
@AndrewDamson
@AndrewDamson Ай бұрын
Manyaka
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d Ай бұрын
Amako ndi amene Ali manyaka
@DeveliousMasinja
@DeveliousMasinja Ай бұрын
😅😅😅😅😅😅koma guyz awawa mfundo alibetu😅😅
@apostledavismsosa
@apostledavismsosa Ай бұрын
Mwanamveka asayambe za sankho apa apo pali Daud sureman osamutchula bwanji? Komanso kunena kotani kot asuleman angaone ngati a vp aaaa asayambe zachamba apa. Amenewa ndiye anyamata omwe agwira chipani mwana mveka usiiretu za sankho
@iamandypandy
@iamandypandy Ай бұрын
Xhokapa
@AbuZunairaHanafie
@AbuZunairaHanafie Ай бұрын
Chikangawa achoke nthawi yamuthela
@ChristinaMitepa
@ChristinaMitepa Ай бұрын
Ndipo singavote
@AustinMhone-r3s
@AustinMhone-r3s Ай бұрын
Only federal system of government will be better for all Malawians otherwise there is no need of voting it doesn't help.
@jacquelinecunningham363
@jacquelinecunningham363 Ай бұрын
DPP and APM my VOTE 🔥🔥👏👏💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙
@GraceChenda-q2g
@GraceChenda-q2g Ай бұрын
Fundo mulibe a mdala Inu,,mungoti dpp oye,,zazi. Nenani fundo zomwe musinthe
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 Ай бұрын
😂😂😂😂
@EmmanuelKambalame-x2b
@EmmanuelKambalame-x2b Ай бұрын
Chilungamo ku Malawi tilibe wot angazalamulire bwino dzikoli
@TitusJabeschikhudzo
@TitusJabeschikhudzo Ай бұрын
Vinyo anatha 😂
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Mphando uwu ikani wamolalo wafundo
@charleslimbani8590
@charleslimbani8590 Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 imasiree dpp
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev Ай бұрын
Koma yah mfundo zake zimenezi
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o Ай бұрын
Kkkkkk kkk kusowa zochita madala team chakwera 2030 woooo
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma Ай бұрын
Kkkkkk munthu akugwelani pasanja kudpp anthu anatha
GWEDE-GWEE YA LERO__UTM🔥 7 November 2024
25:59
HOT 265
Рет қаралды 20 М.
СОБАКА ВЕРНУЛА ТАБАЛАПКИ😱#shorts
00:25
INNA SERG
Рет қаралды 2,6 МЛН
ROSÉ & Bruno Mars - APT. (Official Music Video)
02:54
ROSÉ
Рет қаралды 290 МЛН
ЛУЧШИЙ ФОКУС + секрет! #shorts
00:12
Роман Magic
Рет қаралды 26 МЛН
Mia Boyka х Карен Акопян | ЧТО БЫЛО ДАЛЬШЕ?
1:21:14
Что было дальше?
Рет қаралды 9 МЛН
Tsoka Liyenda Part 1(Malawian movie)
57:30
director Khristal Chris
Рет қаралды 92 М.
Akabatwa nemukadzi wemunhu wawapadhuze kuita bonde
18:15
Manass-Chibanda
Рет қаралды 3,4 М.
Can These Bones Live?
1:32:42
Pastor Esau Banda
Рет қаралды 3,7 М.
DEG DEG SAYID CALI OO DIL TOOGASHO AH LAGU XUKUMAY & DAREEN KIISA OO IS BADALAY
17:26
KUSEMPHANITSA KWA ZIZIMBA, ZOMWE ZINAPHETSA SAULOS CHILIMA 🤯😭
35:46
СОБАКА ВЕРНУЛА ТАБАЛАПКИ😱#shorts
00:25
INNA SERG
Рет қаралды 2,6 МЛН