Iwenso kalindo ulibe nzelu azimayi okubelekela malo osayenela muzipatsla za boma mwina mulibe zimbuzi ma bafa ngakhalenso ma school momwe mukanayamba kukonza ma department a bomawo kaye kusesa timayambila munyumba kumakamalizila panja.
@WilsonMbendela21 сағат бұрын
Kkkkkk ngati anibe longwe
@Dellingsmunthali21 сағат бұрын
Ayende mwa amwenye timalipiro sitilibwino
@AlexNsambo9 сағат бұрын
Zowona amumba mupitirize makamaka macampani za amwenye komanso magalaja amwenye muli mavuto akuluzedi oyendesa akabwera amakumana ndi mabwana Malo mokumana ndi ogwira nchito
@Ayanali-cr4vy21 сағат бұрын
Mesa ndi Born Kalindo ndi amene ankasapota zithu zoipa mu 2019,2020 pano mawu thoooooooooooooooooo Malawi Muno ambiriwa ndi Nazikambe. Atupele Muluzi my Vote
@Eric-gb9ms20 сағат бұрын
Ndi chifukwa chake anatulukamo anawona Kuti sizingamuthandize nanu think before you talk
@GraceShaibu-i9d19 сағат бұрын
Zaziiiiiii vivaaaa the Dc❤❤❤🎉🎉🎉🎉
@Eric-gb9ms19 сағат бұрын
@@GraceShaibu-i9d yes we love him DCCC
@NelsonMhango-j1d21 сағат бұрын
Sounds good
@EsetaGerate13 сағат бұрын
Ma bus aaziikhare ng'oma 😂😂😂 koma DC ayi taa
@MtambulaNyirongo9 сағат бұрын
Nenatu
@SuzgoChauma21 сағат бұрын
Abweleso kuno ku mzimba Raiply campani
@surpkaymw221 сағат бұрын
Katundu madzi
@GeorgeMateyu-q3f20 сағат бұрын
DC... (Respect big)
@LufingoMulungu-z7u13 сағат бұрын
Big mn iwe ndiwedi mwana wowopsa kwambiri
@DouglasBizaliyeli-kb3qm21 сағат бұрын
Uremu upite kwainu the DC kuswa kuswa
@ChimwemweKuvala-y7y11 сағат бұрын
Hot 265 pliz check the date on ur cover letters. today is friday 17/01/2025 not 18/01/2025