KODI MWAZIMVA NKHANI ZA LERO? KOMA KU MALAWI KULIBE KUPUMA KOMA MWATI ZIKUCHITIKADI IZI?

  Рет қаралды 26,469

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 16
@HaroonSaidi-jv3ek
@HaroonSaidi-jv3ek 12 күн бұрын
🤗🤗🤗🤗🤗🤗 aaaaaaaaaa anthu if analephera kupanga compliment vision 20/20 nde apange za 2063 for what nde izi ndi zija za kamuzu zomati atsogoleri ammawa koma mmawalo silimafika kamuzu ndi kuzakhala wa muyaya inu kulankhula ndi kupanga it's two things zosiyana SIYANI NTCHITO YA MANJA ANGA ZINDICHITIRE UMBONI OSATI PAKAMWA LALALALALALALALALAAAAAAAA ZA ZIII
@MagieJames
@MagieJames 11 күн бұрын
Nkhosi ngt kamba Jessy kabwiri a DPP akachitidwa chipongwe umakhala chete hule iwe
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 11 күн бұрын
Kabwila uyambekaye kuzuzula azikwanje ku Lilongwe
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 12 күн бұрын
Timawononga ndalama zambiri kusankha anthu omwe alibe chidwi kapena sadziwa zomwe akuchita.
@JamesYusufu-l6d
@JamesYusufu-l6d 11 күн бұрын
chimenecho ndiye. chamba kodi amcp akudandaula. malawi muno apha anthu angati. nankha okhapidwa ndizikwanje ndiangati
@Edward-y3v
@Edward-y3v 7 күн бұрын
Malawi asogoleri anangozaza mazi mumutu Kaya ndi dziko lanji ili
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 12 күн бұрын
Kodi Anabel ntarimanja waukakamiratu mpandowo
@JamesYusufu-l6d
@JamesYusufu-l6d 11 күн бұрын
kodi tizingokhalila kuva zopusazo. komaso nanu atolankhani muziona nkhani zotola ndizopanda zelu zomwe amcp. ndiamene akuyambisa zisokinezo kwaphela ufulu amalawi akayankhula angomanga ndizopanda zeru zomwe ndikumati ndikumati amcp akuona mavuto zachamba dpp boma mcp mwadesa mazi. sinuso oela zakuvutani. bass zaka 4 koma anthu ophedwa ambili okhapidwaso ambili okufa ndinjala ambili omangidwa pankhani zopusa ambiliso aaaaamcp kagweleni uko mukasambe mwazi ukuyenda pathupi lanulo. zachamba bass
@tracybennie7783
@tracybennie7783 11 күн бұрын
Eeeeeeee. Inu. Thawi. Yatha
@FrankMzungu-v9w
@FrankMzungu-v9w 11 күн бұрын
Kupusa
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 11 күн бұрын
mcp,singaluze,olo
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 11 күн бұрын
chabwinongati,tikamuvotele,,,wina,chifukwa,chabodza,,,,,,,,posakhala,kuona,chitukuko,,,chomwe,wapanga,tiona,,,,,,,,,,ulendouno,
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 11 күн бұрын
mcp,boma
@PeterKathumba-f7o
@PeterKathumba-f7o 12 күн бұрын
Aaaaaaa Kodi kokumbukira chilembwe munauzidwa kuti kuzavalidwe makaka azipani? Kodi anakati sanavale makaka Ndindani akadawadziwa kuti ndi achipani chimenecho? Ndipo kumenekuja pachulungamo unali nsokhano wandale not kokumbukira Chilembwe,,, potengera ndizonenazake; tamanga misewu, tatsegula ndikumanga zipatala mmmhhuu mopanda mankhwalamo? Koma yaaaaa ziliko Yehova atione basi
@lewisdicksonmlozi130
@lewisdicksonmlozi130 12 күн бұрын
Mukuti andale mumadziwana.. koma ndichifukwa chiyani mumakhara mukumapusitsa amalawi
I'VE MADE A CUTE FLYING LOLLIPOP FOR MY KID #SHORTS
0:48
A Plus School
Рет қаралды 20 МЛН
NKHANI ZALERO __ZOMWE MCP IKUFUNA ICHITE__29 January 2025
21:20
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34
OMUKWE - ATAJUGIRE   EPISODE 20
20:44
Mushana Productions
Рет қаралды 10 М.
Cruise 5 With General Vincent Nundwe   MDF Commander   Part 2
1:06:02
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 67 М.
Fighting for my Kids | New Zimbabwean full movie
42:02
magtom media
Рет қаралды 6 М.