Ayiii amakampanga brief za lipoti lake lomwe momwe adaphera Saulos Chilima.
@edgarjere642016 күн бұрын
Munthu izikhala busy ndi family ana anga ndadwesa chani not zandale zilibe phindu.
@patrickzulu513617 күн бұрын
Mai wazobwilabwila yemweyo my foot
@PrinceBlessings-bv5bs17 күн бұрын
😂😂😂😂 Zilikotu 🔥
@EdwinChonde17 күн бұрын
Malawi akanakhala wabwinobwino 1992, sitikanachoka kuchipani chimodzi kubwera ku zipani zambiri. In un so a Kali do munachoka Ku uphunzitsi kubwera Ku ndale.
@stynessphiri16 күн бұрын
Ati uyu atipha 😂😂
@SasterMalanga17 күн бұрын
Ndikukayikira ngati ndi mawu abwana kalindo
@MchachaGoodson17 күн бұрын
Timomulowela mntchire uyu aziona
@GregoryMatambo-m6y17 күн бұрын
Iwenso unathawa uphunzitsi kufuna kulemela
@IsmailRahim-yy3yr17 күн бұрын
🔥🔥🔥
@MosesSoko-y8h17 күн бұрын
Kkkkkkk koma dc kuzidya ngati ngawele?
@AlexChagunda17 күн бұрын
DC the president of poor Malawi
@user-do2cs8nf4b17 күн бұрын
Kkkkkk wadzobwirabwira, ndalama ndi satana
@husseinmponda17 күн бұрын
😂😂😂 lero lokha ndaseka
@OwenNyambose17 күн бұрын
The dc
@MussaAndreQuenessi17 күн бұрын
Auze mau the dc
@raymondmikondo210217 күн бұрын
Ati uyu aťiphatu
@kennedymakhula120316 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@ChaposaChaposa17 күн бұрын
Ulemu wanu big
@JULIUSLAYTON-z8x17 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂atipha uyu
@Christopher-xc2ey17 күн бұрын
Kkkkkkk
@PatriciaChiwerenga17 күн бұрын
😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@user-uq6ph3ox2u17 күн бұрын
Ena tikawaika lero mmanda ndalama zapension 4 years osatuluka😊
@FrancisMazamba17 күн бұрын
Chochi sanadyelele mmm zowopsa koma
@user-zg6mn8qr4m17 күн бұрын
The DCcccc
@DackforeMpanje17 күн бұрын
Citini copanda kanthu paja ndico cimasokosa
@GeshoMwakitwile17 күн бұрын
Chitsiru iwe wagwa nawo alomwe anzako ngat mukufuna kuchokamo muno Malawi pitani kwanu ku mozambique tatopa nanu ife
@peterchikwakwa847617 күн бұрын
Don't say that, they will not welcome us here
@SydneyMwale-u9w17 күн бұрын
Tsiru nidani kodi.zakubowa tu
@KhalideNerve-mu1eq17 күн бұрын
Mboli yako😂
@edsongeorge803217 күн бұрын
mutu wako sugwira aise ndiwe mbuzi kwabasi ......
@GiftKananji17 күн бұрын
Panyo pako galu iwe moti suziwa chikangawa ndi mbuzi ya munthu
@GeshoMwakitwile17 күн бұрын
Bon kalindo ndiwe size yanga sungazuwe zimene president amayendera ,munthu wankulu ndi amene akuziwa zomwe akuyendera iwe ndiwe bulutu sungaziwe
@MussaChilembwe17 күн бұрын
Zikukusangalasan pano ndi chakwera zimene akupanga kumalawi mcp ndiyakhaza kwambili
@FionaKhoma17 күн бұрын
Mbuziiwe galu athu akuphainu
@Themaso-w2v17 күн бұрын
Olandira ma 30 pin aja ndinu eti ,tikuonani muli against kwambiri, ngati simufuna kumva zoona osangotseka makutu bwanji