I love this T. A. interesting speak wisely only ❤❤❤
@RichardjacobKondwani-zt8gsАй бұрын
n
@RichardjacobKondwani-zt8gsАй бұрын
b nhb b n
@RichardjacobKondwani-zt8gsАй бұрын
bb
@KingsleyJamboАй бұрын
Komati sindikuona kulankhula monyoza apa, very brilliant speach
@mollymasangano47316 күн бұрын
Brave Nyakwawa ❤🎉❤
@HopellaBandaАй бұрын
Inde Aunt mfumau Elena Chakuamba ..love uuu❤
@edsonphangula5817Ай бұрын
Congrats wonderful my president good work I appreciate it
@ISHMAELCHITENJE-ri9rqАй бұрын
Nfumu iziyankhula chizungu koma enawa eeeeeew kulemba ayi,mavuto poti amati zapachipale😊
@ImmanuelndagomaKondowe-n1vАй бұрын
Amalawi savotela munthu chifukwa cha chitukuko koma chakudya,mukamfuse Bingu ku ndata
@ElizabethKazambweАй бұрын
😂😂
@IsaacKutachaАй бұрын
That's very shame full to the president
@blessingssaitiАй бұрын
Idzo ndi zowonad even xool sapita asanadye
@SolomonNjolomoleАй бұрын
Nanuso kungokokomeza zamkutu heading apa kuchemerera gwapeyu anthu akudya chitedze apa mmafuna timvere audio aaa
@KennedyPhiri-h9hАй бұрын
Chakwela sitikumufuna kuno Ku makhanga walowa mboma mu 2020 mpaka Pano sanabweleko kuno ndiye akubwela Pano kuzafuna ma vote because we are going to vote now no no gys be wise
Nde alakhwanji powalanda alankhula kwambiri modutsa nthawi koma musasonkhezere milandu apa ayi
@JimmyMulewaАй бұрын
Zonsezo sangapange ameneyo kod mukumuopa tamuuzen kut achoke walephela 😢
@blessingssaitiАй бұрын
Kholo lomwe limanga nyumba nyumba mulibe ufa ndekuti nkholo limenelo ndilopusa
@CEANMALUNGAАй бұрын
Mfumu yanzeru kwambiri kuposanso ena aja. Chondisangalatsa kwambiri ndi kuyamikira Chakwera pa zitukuko zimene zidachitika m'nthawi ya anzake monga Muluzi, Bingu, APM, JB komanso Mia. Mwachidule, sindinamvepo za chitukuko chooneka chimene Chakwera wachita kupatulapo ndalama ya Golf imene yapezeka kumanga sukulu ya Makhanga. Nanga za Bridge ija zoti idamangidwa ndi Joyce Banda komanso nseu ya Makwasa kufik Fatima m'nthawi ya Peter Mutharika ndikunama?
@FidesChandamaАй бұрын
Mwana WA fiti ameneyo chikangawa sangapange muchedwa ndikuyankhula Mfumu owauza mavuto samenewo ai mapeto ake akuphani ndithu
@FidesChandamaАй бұрын
Mungovutika ndi kuyankhula palibe zikulowa mmutu mwake ameneyo zikuyenda mmutumo ndi zopha anthu omwe amutsutse pamenepo ndiwamagazi ameneyo alibe chisoni
@LuciusByson-z7uАй бұрын
Eyendeleso Ku ntcheu akapepese ofeledwa😂😂😂
@paulpaseli6310Ай бұрын
😂😂😂 apitedi akagule batatesi ndi manganya
@isaihmagani5697Ай бұрын
Nde walankhura mosaopa zitizizo
@MaryBanda-n3hАй бұрын
Etieti zanzziiiii
@NeemaMatewereАй бұрын
Exactly my question
@EVANCEKAGONEGONEАй бұрын
Watu tumiza video iyi ndi mbuzi
@HaliJanaАй бұрын
Mr chikangawa asilikalio achani oseo iwe ufa 2025 ndipomwe uziwe kuti nyimbo ya fuko ilibe video
@MaryBanda-n3hАй бұрын
Mutu wankhani kaya mumalembera molaro kuti timvesere aa
@chiletsobisweck5007Ай бұрын
Mfuma idzitero😅😅
@RuthMpambalikaАй бұрын
What do u mean by saying mosaopa kumakamba zobweretsa ndalama
Chakwera wakoyo fertilizer Kodi iweyo ulibe nzeru Ndi agogo akowo maulendo opita kunja ndiye ukambe za mvula Iweyo patumbo pako Mphwanga kutsabwela kwa mvula kuba,kumphedwa kwa anthu,katangale Mulungu amakwiya nazo
@AbdulsharifulKalipinde-m6uАй бұрын
Ndiye mvula singabwele mpakana bwino Mpaka asiye zinthu zimenezo
@talandilabenedictoАй бұрын
Munthu akuyankhura zinthu zothandiza anthu nde iwe ukufuna kumuranda mic? ana awawa ndi aja opusa amafuna adzikanena zabodza kwa mtsogoleri. Mfumu yayikazi koma yanzeru
anthu akudya chitedze iye Ali busy kuyendera mseu anthu akudya mseu???? President oyamba kumalawi opusa osaganizila anthu wakumpha opanda chisoni wakuba ndi wabodza ndi ndi iweyo chikangawa 2025 uona nyenkhwee Malawi wa lero si dzulo
@PenjaniMwaleАй бұрын
Chomwe ndikudziwa ine onyoza olo utampatsa zakozose sayamika enanu ndinu osayamika basi
@BlessingsMalunga-d8oАй бұрын
T A mulolo kwathu
@KennedyMalikoАй бұрын
Apepha zambili kwambili😅😅😅
@ImanRashidi-so4ooАй бұрын
Auzeni kut chimanga thumba ndi K45000
@GiftJulius-gx2kbАй бұрын
Palibe ndikumvapo apa
@MalizeniOliviaBridanАй бұрын
Koma iweo ndiwedi mfumu kapena ukupempha ndalama
@NdamvaScnpАй бұрын
NOSE AMENE MULI KUMENEKO NDI AFITI
@AkimuKavaliraАй бұрын
Kodi ndimsonkhano wa asilikali?
@YoungMwachoАй бұрын
Wadabwa chani?
@FidesChandamaАй бұрын
Anthu sangapite msonkhano WA munthu wakupha uyu wamagazi
@CatherineDesireАй бұрын
Kuchikamwako chakwera
@SaidiMbawa-st6bjАй бұрын
Palibe chomwe chalakwika apa zandale basi Chitukuko chikuchitika kumeneko
@violetpotaniАй бұрын
Ife zanuzo ayi asatikwane uyu
@ThivadoartistDysonАй бұрын
Ngat wakanika 4 years ndeno akwanitsa bwanj mmiyezi yochepa ,koma amalawi muziyamba mwaganiza angapange Chiyan galu ameneyo? You ar wasting time chifukwa mzanuyo zatulukila kwinako
@MarthaMalopa-kw9xwАй бұрын
Very intelligent chief
@BrianChimaliro-fh9ymАй бұрын
Nde microphone alandidwa patpo I think naweso nd wa mcp
@EmmanuelJumbe-i5wАй бұрын
Hahahahaha
@giftsululu4274Ай бұрын
Mimba siikhuta
@EmanuelPintopinto-g3bАй бұрын
T A yopanda nzeru mukuti Kwa nthawi yoyamba chakwera kufika kumeneko nthawi Yonsei anali Kuti zoti wayamba Kampen akufuna akunamizeni ndi madeya changamukani Mai mulibe nzeru kuwombera satana manja kapena musanalankhul mwalandira ndalama