opposition yakedi yaziiii atupele ndia DPP angokhala ziiii akungoyang'anira basi koma akufuna kuvoteredwa
@KaisiAbdullah3 ай бұрын
We olways behind u mr bon
@SirNanjalaMw3 ай бұрын
Umakwana koma kalindo suyangana nkhope ukafuna kungalura chilungamo
@DavidMtambo-zm8ne3 ай бұрын
UTM alliance aford zintheka
@OliveaMapanga3 ай бұрын
Km kalindo umakwana 😂😂😂😂 ati manyaka ngati awa sitikuwafuna ayi
@augustinechibbalazi88973 ай бұрын
My gracious God have mercy on Malawians to transform their nation from rut to prosperity or vision 2063 will remain a political requiem to satiate the destitutes.Let callous religious and political leaders change their minds.
@IshuBillalli2 ай бұрын
Mwina akufuna muchite kwagwira Malo obisika kuti azuke inu zoona ife achinyamata tikuchita mantha kubwelera kwathu kuti tizikapanga ma business kuopa ulamuliro wa khaza omwe uli dziko lathu lomwe tabadwira zoona koma kumati kuli inu omwe mumazitcha kuti ndinu Andale mumathaso kukalowa nyumba ya malamuro zukani zukani atsogoleri athu kwakwana tsopano Atupele ,, Peter muthalika,, Chihana,, Joyce banda,, Inu bambo asikono,, Ndikunena ndinuyo Timothy mtambo ,, ndi ansanu onse ,, tachangamukani please chotsani nyazi zimenesi
@godfreykanjux50873 ай бұрын
mwana ooooopsya kwambiriiiiii
@chrisneySwanepoel-yu5vd3 ай бұрын
Bwana kalindo ingoyambisan chipani chanu tizakuvoteran coz a opposition sali serious kumene
@ClementChilunje-k2c2 ай бұрын
Achewa yo siwose ena anyasidwa nayoso utsogoleri umeneu.
@HopeChimwaza-m7e3 ай бұрын
Mulungu azikudalisani a president athu anthu osauka ife
@InnocentKavalo3 ай бұрын
Koma chilungamo Malawi anachagamuka mcp ngat simukuziwa munalowa chifukwa kunali ma demo ndiye mukuona nga anatha? Mukufunika kumangolapilatu apa no chance
It is true that opposition leaders are dormant whether they like or not but they are. We Malawians are tired and worried about them. May be they're receiving some money which makes them silent, please work up!!!!!!!
@Maxcarcare-g1d3 ай бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥
@twavysibale47513 ай бұрын
Intro yokhayo...mwalamwalatu 🔥🔥🔥
@EliasDzoole-js8vx3 ай бұрын
Ma bodza sangawine olo atatani ine ndineso mchewa awawa kapume
@EmmanuelHussein-k8n3 ай бұрын
Mkulu uyu tidzamulira one day,he got love for his country
@AchinaKellz3 ай бұрын
Ine ndi nchewa koma mcp ndi agaru nyasi zisatiipitsire mbiri uchitsiru umenewu udayamba ndi kamuzu, kuno pakati mcp yaluza ndale mpaka kupha azawo
@tasmania5273 ай бұрын
Si Mchewa iwe, DPP inkazunza aChewa omwewo.
@augustMag3 ай бұрын
Mmatilimbikisa ndi kutipanga lerise up Amalawi ife ❤🔥🔥
@GRACIOUSKENAN3 ай бұрын
My boss booon kalindo,our freedom savior and fighter.
@Uncle_B2653 ай бұрын
Koma zikoli mmmmm zafikapoo
@Vascomw3 ай бұрын
Powerful 💪💪💪 Ife sitikuwopa tili pa buyo pako
@GiftGift-d6u3 ай бұрын
Am not really happy with the way opposition is handling the public affairs,,
@GreysonLimula3 ай бұрын
Opp0dition yadyetsedwa dekhani ndi mcp
@HanifuYunusu3 ай бұрын
Mumakwana ❤❤
@DaudiHAllie-kk1en3 ай бұрын
MCP is now bringing tribalism but just to remind them that Yao ndintundu waukulu kwambiri Malawi yonse
@SaidiMbawa-st6bj3 ай бұрын
Zikuchita kuonesekatu kuti ngakhaleso a tawina a opposition palibe chomwe chingasithe
@SandisLazalo2 ай бұрын
Mr SSS
@KelvinMangwengwe3 ай бұрын
God bless 🙏 you kalindo😅
@SaidiMbawa-st6bj3 ай бұрын
Ndiposo ndizoona kumene kuti achewa ndi ambili kuposa mitundu yose ku Malawiko
Kodi Mr Kalindo, simungakoze ulendo osawadziwitsa ma president a opposition kuti akadzuke...?. Chifukwa Boma la tonse mmm likuning'inatu heavy as tsabora., Chakwera must resign ndithu 💔💔💔💔
@agnesgwaza91653 ай бұрын
😢😢ndip Eeeee atiphweteka
@PrinceBlessings-bv5bs3 ай бұрын
@@agnesgwaza9165 Ine daily mtima kuwawa ndikamava ma challenge awo kuti mpaka 30 years
@Vascomw3 ай бұрын
Tiyipatsa Moto 🔥🔥🔥🔥🔥
@clintonhodda98303 ай бұрын
Opposition achuluka dyera sangagwilizane
@0wenNkhambule3 ай бұрын
Good Messnge Chakwela you mast go
@WorriedNdhlovu3 ай бұрын
Ichi nde ndichi booooni kalindo🎉
@Musa1828-l5d3 ай бұрын
Chakwera anapha Chilima
@mphatsobonongwe81313 ай бұрын
😊
@GiftSimubali3 ай бұрын
Ipatseni moto🔥🔥🔥
@DavidMtambo-zm8ne3 ай бұрын
Aford UTM alliance tidusa popanda opikisana nawo.
@JunaKananji3 ай бұрын
Karido ❤❤❤🎉🎉
@agnesgwaza91653 ай бұрын
Raster kumbuyoko amakhala ali cheucheu😂
@Aubreysekeyah3 ай бұрын
The DC❤❤❤❤❤❤❤
@ChristopherJames-fm8zc3 ай бұрын
The DC
@andrewmtendere31673 ай бұрын
Chi born kalindo❤
@MosesChinzuze3 ай бұрын
Ulem wan boss man tiri pambuy pano
@Martha-m6e3 ай бұрын
Zowonadi anthudi agona.ifa ya anthu onse aja sangawa vote ataa.
@LatifBeni-e6z3 ай бұрын
Mbambande madala mumakwanila
@SyilesChebomba3 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@oskidooscar74683 ай бұрын
Koma why sakuyamkhulapo za manganya ku mcp
@kaungabondera8923 ай бұрын
When are we protesting
@RosemaryKhungwa3 ай бұрын
You are talking sense bro
@MustafaMachika3 ай бұрын
❤❤❤
@davedavie62113 ай бұрын
Osusawa sakutithandiza
@Extratremendouszeus3 ай бұрын
Welcome the dangerous child
@Extratremendouszeus3 ай бұрын
Peter nayenso akugona kwambiri.....Chikangawa mmene amasokonezera 2020, Nde mukudikira a Malawi kut aonde kaye kenako akuikeni pa mpando inu muzidzanjoya.kodi a Peter ,kufatsa kumeneko kwamtundu wanji ....check out
@mipeacemakermw95013 ай бұрын
Mwatukwana president 🤣🤣🤣🤣kzbin.info/www/bejne/jYOnnIRuqMRmas0si=PkGoYsuJRKSW0v4p