BON KALINDO WAMANGIDWANSO NDI MULAMDU WINA🤔🤔🤔

  Рет қаралды 23,518

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

A BON KALINDO WAMANGIDWANSO CHIFUKWA CHOPEZEKA NDI MFUTI.
Atafunsidwa kuti apolisi anadziwa bwanji kuti Kalindo ali ndi mfuti.
Kasambara anayankha kuti: " Kalindo anabwera nayo okha mfutiyo pomwe amafuna kuti apasidwe chilolezo".
Khwima Mchizi yemwe akuyimilira Kalindo anafunsa Kasambara kuti pa nthawi imeneyo anawamanga a Kalindo atabwelesa mfuti yo?
Kasambara anauza bwaloli kuti sanamange Kalindo chifukwa anamupatsa mwayi kuti akabweletse zikalata za mfuti wo.
Bwalo loweruza milandu lawuza Kalindo kuti akumuganizira kuti anapezeka ndi mfuti mopanda chilolezo, mu chaka cha 2021.
Boma lidabweletsa m'bwaloli Innocent Kasambara, yemwe ndi wapolisi wakafukufuku.
Kasambara wauza bwaloli kuti akufuna Kalindo akhale mu chitokosi cha apolisi kamba koti mpaka pano , iwo sanawauzebe apolisi komwe anagula kapena kutenga mfutiwo.
Iye anaonjezera kuti apolisi akufuna Kalindo awalondolere komwe anagula mfutiwo.
Atafunsidwa kuti nchifukwa chani akubweletsa nkhaniyi pano, Kasambara ati kuyambira chaka cha 2021, a Kalindo akhala asakuonetsa chidwi chobweletsa mfutiwo.

Пікірлер: 73
@MabvutoMwakalinga-yl3ft
@MabvutoMwakalinga-yl3ft Ай бұрын
Apa mpomwe tikudziwa kuti activis weni weni ndi uti ... Onse ankalubwa aja angoti ziii Chibanzi chili kukamwa.... Komatu amkati Kalindo ndi osokoneza
@umalimaganga
@umalimaganga Ай бұрын
Boni Kalindo sangagwiritse ntchito mfuti he is and I quote "an African man"
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s Ай бұрын
Amumanga munthuyu opanda mlandu amulipile Basi a kalindo amalawi akuvutika ife kuno kumudzi kuno tikufuna APM 2025 mufune musafune and he will rule malawi again
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
Nanga ena amapezeka ndi mfutiwa bwanji samamangidwa
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Ай бұрын
Alipo munthu amene wakaika mfutiyo kunyumba kwaoko this can't be True
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Ай бұрын
Thanks potipasa update yazomwe zikuchitika bro
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m Ай бұрын
The DC anyway tilikimbaliyanu bwana
@hot265.
@hot265. Ай бұрын
A police adadziwa bwanji kuti Bon kalindo ali ndi mfuti? Welengani yakho ku Description
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw Ай бұрын
Thanks for updating us only for born kalindo muzitipanga update kut tiziziwa kut pano zili motani kwa apresident athu a Kalindo
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m Ай бұрын
Wina nso uyuyu wadzuka nso mumutani ulemu wanu mr kambanje ❤ boma iri kuba mkhanza
@MathewsMANDUTU-lh6oo
@MathewsMANDUTU-lh6oo Ай бұрын
Chakwera ndi anyamata ako mumasule freedom fighter wa dziko lamalawi,,,,, president Dr Born kalindo mwasanga,, pangani njira zothesa njala yomwe mwa wapalasila amalawi.. Capetown south Africa.
@augustMag
@augustMag Ай бұрын
Ndi Professor Arthur Peter Muthalika yekha amene amanyozedwa anthu kuyakhula komwe amafunira koma palibe amene anamangidwa kapena kuphedwa ndikukumbukira bwino msundwe pipo Saulosi ndi Razor Chakwera zionesero amakagona mnkhonde mwa nyumba ya state house ku 18 kusala pang'ono kukagona pa bed la Peter Muthalika koma lelo mukukanika kuyakhula zakukhosi kapena zionesero lelo Bon Kalindo wayankhula zoona zokhazkha akumangidwa palibe Democrats apa
@user-fs1ox7ou1b
@user-fs1ox7ou1b Ай бұрын
Aaaaah zopanda umboni anthu mukudana ndichilungamo
@austenbushiri-cx1kh
@austenbushiri-cx1kh Ай бұрын
Zosayenda komabe aaa bho bho bola moyo inshallah
@ElliotOrban-th3qn
@ElliotOrban-th3qn Ай бұрын
Osataya mtimaa big DC ndinu nokhaa sianyan enawa
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 Ай бұрын
Best TV
@user-ix7pb6hk2w
@user-ix7pb6hk2w Ай бұрын
Zonse zomwe a MCP akupanga aziwe kut alephela ndipo maloza dziko lawo lomwe
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m Ай бұрын
Bon kalindo alibe mlandu and mfuti yo mwaipeza kut zaziii bodza basi or mumumange Bon kalindo koma adzuka ena apo ndipomwe mudziwe Kut amalawi atopa
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Shame on chakwera mmalo mothana ndi umphawi akuthana ndi the dc iiiiiii
@user-tn2qg1vs9j
@user-tn2qg1vs9j Ай бұрын
The DC ❤❤❤
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Ай бұрын
Aaaa mfuti akusowa zomumangira
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Ngati kuli dziko romvesa chitsoni
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Amalawi tikuvutika ndipamene mbewa zina zikufuna kubweresa age limit. Mr DC akuyakhula chilungamo ndipamene chigulu china chodana ndichilungamo chikumumanga. Kumalawi kukuonesa kuti 80% anthu sakuganiza bwino sakuziwa kuti ziko lathu zinthu sizikuyenda bwino. Pamene 20 % anthu awa ndi amene akuganiza bwino akuziwa kuti Malawi sakuyenda bwino. Pakhala povuta kuti tikhale ndi musogoleri wabwino anthu ndiwochepa akuganiza boo.
@MustafaKadango
@MustafaKadango Ай бұрын
Boma lachakwela silizawinaso
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m Ай бұрын
Nankhumwa akunama choonadi akuchidziwa wangobisala
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Zoti amupeza ndi mfuti ndi zaboza angosowa zifukwa zomumangira bon but god will protect you bro shame on you chakwera ndani sakuziwa Kuti ndiwe yoyipa mtima watizuza ife amalawi Koma ndife tomwe tinakulemba ntchito
@RattoWholesalers
@RattoWholesalers Ай бұрын
Zowonadi nkhani Yonse ikuchokera Kwa Nakhumwa ya egi limiti
@NumbDee
@NumbDee Ай бұрын
Snake in the grass Nankhumwa
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju Ай бұрын
Bon kalindo wathu wathu
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Aaaa zafuti bodza apefza nayo kuti poti iye ili ku police nde zatheka bwinji ndekuti futiyo inali ndi police wo angonamidxila MCP mamvuto zedi
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Ай бұрын
Malawi ndimadabwa nayo ,mumapanga lamulo nthawi yoti mwawona Kuti pali wina akufuna kupanga chinthu . Why panopa mukuti pakhale lamulo loti no over 80 years Kuti Asayume pa chisankho . So shame
@user-ce6hy6tp7e
@user-ce6hy6tp7e Ай бұрын
Akalindo musadandaule pamene mukukhara mulungu ali nanu musataye mtima, okumbira nzake dzenje lamanja amagwelamo yekha
@Patricia-db9yl
@Patricia-db9yl Ай бұрын
Apapa ndipamene taziwadi Kuti boma rachakwera ndirorephera .likilephera kuthana ndi mavuto amene Ali pa ground. mirandi ukuru ikuru ya Duna komaso vas prasedent .komano ndikumakalimnana ndi Bon kalindo actives yekhayo Wasa Kuno kumarawi wachirungamo izizi aprasedant komaso azikhare ng'oma mukuyenera muzithenge bwino muzamazimvetu Kuti ndinu madora chifukwa Muri m,boma pamene Muri buys kurimbana ndi azanu muziziwa Kuti pariso ena akukuwonani ndipo akukuwerengani ndipo muzanong,oneza bondo
@user-iw6cz5ft2l
@user-iw6cz5ft2l Ай бұрын
Mfutiyo apezaka nayo kupolice komweko?
@mussamapira801
@mussamapira801 Ай бұрын
Akumwa amenyedwatu
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Nankhumwa ndimbuzi
@user-lz5tl7gn4v
@user-lz5tl7gn4v Ай бұрын
Mutsogoreli wosutsa boma wachipani chiti ?
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o Ай бұрын
Koma ine ndiri pa mbuyo pa dc
@user-yf3st5yb1n
@user-yf3st5yb1n Ай бұрын
Nankhumwa nzeru alibwe angayendese ziko galo ameneyo?kodi amene akuwononga zinthu apa ali ndi zaka 80?vuto amakhala kut ndimunthu osati zaka ayi ganizani popanga malamulo anuwo.msakhale ndimantha kut mkhomerere anzanu
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Malawi ndioyamba shame
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w Ай бұрын
Boza alibe mlandu kalindo
@karimshaik4485
@karimshaik4485 Ай бұрын
Chakwela stupid president fighting with kalindo instead of fighting poverty in Malawi
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Eti eti
@user-jd9yz5hp7y
@user-jd9yz5hp7y Ай бұрын
Chakwera ndiwolephera alibe mzelu zawutsogoleli he's a failed big time ndipo pifunika adzamangindwe munthu ameneyu
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s Ай бұрын
Azikhale ng'oma 😅😅😅😅😅😅 kkkkkkk
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du Ай бұрын
Boza limeneli kalindo alive mfuti
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Ай бұрын
Abwela wina woposa dc muvutika chaka chake ndi chino
@user-ki2pq2md5y
@user-ki2pq2md5y Ай бұрын
Zompusa zokha zokha basi Malawi muno amene ali ndi futi opanda chilorezo ndi born kalindo yekhayo basi?zompusa basi mukungomuda born kalindoyo
@AkiduMustapha-vq2nt
@AkiduMustapha-vq2nt Ай бұрын
Zaboza iziii munthu akamangidwa amamusecha pokalowa mu selo sono amupeza bwanji ndimfuti pomwe akutuluka? Wayitenga kuti
@user-nm8rv9vn8y
@user-nm8rv9vn8y Ай бұрын
Komatu tsiku lina
@CheloyaaChikwatuu-ob2mt
@CheloyaaChikwatuu-ob2mt Ай бұрын
Boma rozikondera
@DalitsoChinkhombe
@DalitsoChinkhombe Ай бұрын
Mfuti achita kukayika aMCP
@WilsonLimited
@WilsonLimited Ай бұрын
Chakwera mbolo ya mako
@MizeckSambo
@MizeckSambo Ай бұрын
Mumayitha man
@ishumeilajidaajida7124
@ishumeilajidaajida7124 Ай бұрын
Bakiri TiVi marawi
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w Ай бұрын
Mapeto anthuakwiya akamutulusawokha kundende
@ishumeilajidaajida7124
@ishumeilajidaajida7124 Ай бұрын
Bakiri TiVo marawo
@jaydee1236
@jaydee1236 Ай бұрын
Why 🇲🇼
@MatthewsIsaac-sp1ft
@MatthewsIsaac-sp1ft Ай бұрын
Zaziii
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 Ай бұрын
Mfuti zabodza izi akhala bwanji ndi mfuti
@JamesChimera-hw1nv
@JamesChimera-hw1nv Ай бұрын
Koliritsa kang'oma sikachedwa kung'ambika
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Chisiru iwe kwabasi
@ishumeilajidaajida7124
@ishumeilajidaajida7124 Ай бұрын
Bakiri TiVi malawa
@InnocentDalikiya-tz8go
@InnocentDalikiya-tz8go Ай бұрын
Koma nchifkwa chan anthu akuletsa a Peter mutharika kuyimira pulezideti wa kwa a mereka ali ndi zaka kupitirira 90 president wa ku Rasha ali ndi zaka kupitirira 90 sono bwanji anthu akulimbana ndi mutharika
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju Ай бұрын
The Dc❤❤❤❤anthu onsewo ali ndi mifuti ku malawiko simukuwamanga bwanji??mfuti mwaiona ndi ya kalindoyo? Mulungu ateteze kalindo🎉
@HarryZinyanya
@HarryZinyanya Ай бұрын
Abon ayi tchito mukuigwita
@JamesChimera-hw1nv
@JamesChimera-hw1nv Ай бұрын
Kuopsyakuja ndikumeneko kuli mumfuti
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j Ай бұрын
Mbolo yako, chitsilu mwana wa hule
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Ай бұрын
Zopanda chere
@user-yj4sd7nm2x
@user-yj4sd7nm2x Ай бұрын
Wamangidwanso? That's terrible.
@zakunotv
@zakunotv Ай бұрын
Eyatu wamangidwaso akuti wapezeka ndi mfuti 😂😂😂😂 ku Malawi nkobeba
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Ай бұрын
Propaganda
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
A kalindo muwalipile pa zomwe mukuwachita
Grand Angle  : les États-Unis  en pleine crise de leadership ?
14:39
TV5MONDE Info
Рет қаралды 49 М.
Fierce fighting on Russia-Ukraine border signals new front in war
6:37
How To Choose Ramen Date Night 🍜
00:58
Jojo Sim
Рет қаралды 51 МЛН
когда одна дома // EVA mash
00:51
EVA mash
Рет қаралды 11 МЛН
ISSEI funny story😂😂😂Strange World | Magic Lips💋
00:36
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 116 МЛН
Зу-зу Күлпәш. Агроном. (5-бөлім)
55:20
ASTANATV Movie
Рет қаралды 410 М.
Why American Automakers Are Failing In China
16:34
CNBC
Рет қаралды 978 М.
Jay Jay Cee ft Giboh Pearson - Eya ( Official Music Video )
4:20
Jay Jay Cee Mw
Рет қаралды 197 М.
Militärmanöver "Steadfast Defender" probt Angriff an der Ostflanke
12:51
ZDFheute Nachrichten
Рет қаралды 443 М.
How To Choose Ramen Date Night 🍜
00:58
Jojo Sim
Рет қаралды 51 МЛН