BRIAN BANDA KUKHAULITSA ANTHU NDI MAFUNSO KU NSONKHANO WA PROPHET DAVID MBEWE LERO KU NDIRANDE

  Рет қаралды 23,614

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 40
@RiteRoderick
@RiteRoderick 3 ай бұрын
Awaaa angozivutitsa ndithu, APM ndiyemwe tikumudikilira ifee amalawi❤❤
@KinziWindasoni-h4b
@KinziWindasoni-h4b 3 ай бұрын
Kodi nonsenu mwabwelela mbeweyo. Kapena mwabwelela oimbawo .kusowa zochita eti .Nanunso a Times cover chilichonse Zina muzizikana
@VitumbikoKaunga
@VitumbikoKaunga 3 ай бұрын
Malawi akati avotele mbuzi iyi nde Mitu yawo sigwira akuwazuzayo Ndi munthu wamlungu ndi akavotereso mbewe nchimozimozi. Munthu kudya manyi ako 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 Malawi changamkani. Please
@RiteRoderick
@RiteRoderick 3 ай бұрын
Sangavoteredweyi uyu, APM akutenga bomaaa❤❤
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 3 ай бұрын
Akudikira kugudwa ndi chikangawa bas mtima wadyera bas nakha Pali zoti ztithandiza ife a Malawi apa😢
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 3 ай бұрын
May God bless you papa
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 3 ай бұрын
Ambewe sangalowe chikangawa nawomso amadana nacho cha mcp Tisawalakwile pliz Awatu akufuna mgwilizano ndi DPP Ambewe ndi mzawo wa Bon kalindo,sangalowe mcp
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 3 ай бұрын
Bola atagwirizana
@AlexiousAllano-p6n
@AlexiousAllano-p6n 3 ай бұрын
Brian sazatheka 😂😂😂😂😂
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 3 ай бұрын
Congratulations papa
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 3 ай бұрын
Ovinawo ngati chiterera😂😂 sangawine galu ameneyo kusowa zochita azimayi ukuuu kalimeni
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 3 ай бұрын
Aganyu ofuna kuzagawa mavoti 2025 zimenezo nde za ulendo uno pa Malawi pano chisankho a Malawi ochuluka apanga chisankho chawo kale
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 3 ай бұрын
malo munena xool panja nkhachan kd awaso abewa mungapite kt😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 ай бұрын
Ngati chikangawa anakadzapingira.majim ake aja dzulo Lija analathawa ndi miyala kugendedwa.anakamuohadi osati kunamizira kuja kwa kufa kuja nope
@KinziWindasoni-h4b
@KinziWindasoni-h4b 3 ай бұрын
Kodi comvetion iyi akupangila kunyumba kwa mbewe bwanji .kapena ndi banki mkhonde
@MalumeMalume-ki8iq
@MalumeMalume-ki8iq 2 ай бұрын
Kuvotera nbusa sinzachitanso ine jyaaaa mbalame zaanthu iz
@IMMACULATEKAMBALAME
@IMMACULATEKAMBALAME 3 ай бұрын
Apapa bola ndye kundivotera ine😂😂
@AnthroGondwe
@AnthroGondwe 3 ай бұрын
Talephera Kaye ndi azibusa onyengawo sitingaponye votilanga pa bewe azikapitiliza zaubosao azawo achakwera analimbubusa km pano anyera mubali
@KondwaniGulonyonyo
@KondwaniGulonyonyo 3 ай бұрын
Zovotazi zinakangotha sizikupindulila osauka ayi akupindula nawo ndi olemela okhaokha
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 3 ай бұрын
Apm boma bass olo mcp ikuziwa zimenez
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 3 ай бұрын
Ambewe nawonso akulota za u pule
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 3 ай бұрын
Brian mwamusiyakuti mawulidi lero
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 3 ай бұрын
Kuipatsa moto Brian banda
@AffectionateGondola-cv7qj
@AffectionateGondola-cv7qj 3 ай бұрын
After 2025 Dpp will be like that as udf,afford. PP. There are
@GabrielMunkombwe
@GabrielMunkombwe 3 ай бұрын
😂😂kkk teyeni nazo
@KinziWindasoni-h4b
@KinziWindasoni-h4b 3 ай бұрын
Kodi tizipani tonseti tili NDI phindu yanjiii aaaáaaaa chipani CHOTI ngakhale mp sichingamupate or half .osangokalowa mu DPP bwanji
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 3 ай бұрын
Kodi ambewe abwelesa chimanga ngati sanabwelese musawa votele komaso adad pasani anthu chakudya ndalama mulinazo know chimanga know vote
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 3 ай бұрын
Kuganiza ngat mwana bwanji aise😂😂😂😂😂 of course njala yafikapo
@KinziWindasoni-h4b
@KinziWindasoni-h4b 3 ай бұрын
Cathe maulidi timawu tá nthetemiya .alikuti aaaa amuna nokha nokha sizikukomatu apa
@giftlisimba6628
@giftlisimba6628 3 ай бұрын
Kodi oyimbawo ndi anawa?
@kachisuzimwale5641
@kachisuzimwale5641 3 ай бұрын
Boma sitikusinthatu kod inu zimukumva eeeeti Mungowononga timachenjeto iyaa
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly 3 ай бұрын
Iwee makosana ukonze channel chakocho usamationongele nthawi wamva camera yakoyo ili fokolo sound yakoyonso uichose
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 3 ай бұрын
Ankubwera ndi mphavutu uyu
@HasheemSalade
@HasheemSalade 3 ай бұрын
Abrian ndakatundu
@Enless-n2c
@Enless-n2c 3 ай бұрын
km zikundivuta kumvesa kd omwe mukukamba lerowa ndi amalume anu chemapwesela
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 3 ай бұрын
Kma Brian 😂😂😂😂
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 3 ай бұрын
😂😂😂 burian carthy alikut
@MynessChirwa
@MynessChirwa 3 ай бұрын
🤧🤧🤧
@GabrielMunkombwe
@GabrielMunkombwe 3 ай бұрын
😂😂kkk teyeni nazo
REAL or FAKE? #beatbox #tiktok
01:03
BeatboxJCOP
Рет қаралды 18 МЛН
We Attempted The Impossible 😱
00:54
Topper Guild
Рет қаралды 56 МЛН
2024 Matric results announcement
SABC News
Рет қаралды 16 М.
REAL or FAKE? #beatbox #tiktok
01:03
BeatboxJCOP
Рет қаралды 18 МЛН