ZOMWE AYANKHURA A DAVID MBEWE LERO KU NSONKHANO WA CHIPANI CHAWO CHA LEF NDITHU ZIYAMBISA MAPOKOSO

  Рет қаралды 7,310

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 78
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 2 сағат бұрын
Koma Abusa tawayesa kale,,inuyo musayesere,,musakhale agalatiya oyamba ndi uzimu,,kutsiriza ndikuthupi,yu r anointed man of God
@TheresaNtodwa
@TheresaNtodwa Сағат бұрын
Vote yanga ikupita ku dpp basi❤❤❤❤
@JOHNOlesmasCosmas
@JOHNOlesmasCosmas 18 минут бұрын
Chonde mufikitse uthenga kwa pastor mbewe kut amuze uyoyo amati yessss asiye zakezo siku church kumeneko zikumatinyasa heavy mxeee
@HanifaAdam-tm9yv
@HanifaAdam-tm9yv 15 минут бұрын
😂😂😂😂😂
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 44 минут бұрын
Zotizi ahaa! ahaa, yes zisiyeni please, Simchalichitu umu muli pa msonkhano wa chipani osati wa chalichi ayi
@DoddridgeNkalapa
@DoddridgeNkalapa Сағат бұрын
Aaaaah! Kodi mukulankhula ma president angati???? muzilankhula nokha popanda ochemulira...akutinyansa kwambiri winayo.....ife musamatione ngati zitsiru zotseweresa.
@HakeemJossam
@HakeemJossam 38 минут бұрын
Akuona ngat mu church
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa Сағат бұрын
Mr President Atabaya Ndakoka Wawo Wa Hot Pink, Koma tsono akuyankhulila pambali panuyo akunyasa kobasi. Muuzane zithe muzikapanga mu kachisi
@MascotAnderson
@MascotAnderson Сағат бұрын
Koma ndikutha kuona kukuchitika ma demo opsa kwambiri
@EDSONKAMVAZAANA
@EDSONKAMVAZAANA Сағат бұрын
Satanic yeniyeni azibusa lero? Zopusa Malawi aluwonongeka ndi anthungati amenewa ubwino akungobwela kuti adzalemelepo. APM ndiye chiyembekezo Cha Ife amalawi enanu kapangeni Zina
@SternMoyo
@SternMoyo 42 минут бұрын
Ulaliki weniweni ukuchitika apa, ndale sizikhala ndi opasulira ngt malilime
@HanifaAdam-tm9yv
@HanifaAdam-tm9yv 11 минут бұрын
Pangosowekera pa verse kkkkk
@samiyatsmart-u4p
@samiyatsmart-u4p Сағат бұрын
Winayo akuyankhulanso bwanji aziyankhula yekha kaa
@YassinWilles-i1k
@YassinWilles-i1k Сағат бұрын
Mmm kachikena m,Busa. Aja ankati chakwela chilichonse Pano chakwela awa ndi LEF sioyimbira Mpira 😢😢😢😢😢😢mabodza adadi bwaaaaa
@HanifaAdam-tm9yv
@HanifaAdam-tm9yv 13 минут бұрын
Kkkkk kma kumalawi abale nkokoma... kma anthu ali ku church kapena ku nsokhano😂😂😂 oh yesssss mpakana
@MusstafaJalasi
@MusstafaJalasi Сағат бұрын
Ulaliki ku church mpaka omasulila malilime 😂😂😂
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa Сағат бұрын
Hahahahahahaha ine kudabwa kuti dabwiii
@EdwinJumbe-u5m
@EdwinJumbe-u5m 31 минут бұрын
Siyanitsani ku church ndi msonkhano wa ndale
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 Сағат бұрын
Kkkkkkkkk awaso osangopanga zanu bwanji? Mukulimbana ndi munthu amene samakuyankhani mukamanyoza.
@GivenKitha
@GivenKitha 57 минут бұрын
Womasurila plz plz akuwononga speach yanu boss atsiye uyo
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 53 минут бұрын
Amenewo ndiye mawu big kulakhula kwacha muna mopanda matha ayi, anyamata tsegulani manso
@chrisboyce2
@chrisboyce2 2 сағат бұрын
Panopa a Malawi anataya chikhulupiliro pa azibusa too much corruption (APM 💙✅)
@MISHECKBANDAH-m3h
@MISHECKBANDAH-m3h 28 минут бұрын
Mmmm koma uyu akuyankhayi akuona ngt ku fellowship 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Сағат бұрын
Kungofuna kugawa mavote kumwera kuti MCP chigawo chapakati ipeze mavote
@beatsbymcstevens
@beatsbymcstevens Минут бұрын
Is it just me kuti zikumveka ngati church service not a political rally mpaka hype man aaah zoona
@MosesDicostar
@MosesDicostar 2 сағат бұрын
Kumalawi kulibe yemwe akubwera ndifundo zogwilika zotukula Malawi nonse mungonyozana bas
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 29 минут бұрын
Ambewe atopa
@jacquelinChitsulo
@jacquelinChitsulo 36 минут бұрын
Kkkkkkk mpaka ma press ups kkkkkkkkk ndaseka!!!!
@VioletMbale
@VioletMbale 2 сағат бұрын
Eish zinazi tichimwa nazo tikazionela konko zisiyeni zikulire limodzi😅😅😅
@TsuzenThomas
@TsuzenThomas 2 сағат бұрын
Ndukuuzani 😂😂😂
@eliasgondwe
@eliasgondwe Сағат бұрын
President wanji wongofikira pa Mademo, kuuza mbava kuti zikabe, Kutumikila ambuye salengeza kuti ndapuma ine!!! Mkwiyo wa Mulungu ukupezani pompano
@LukasBamus
@LukasBamus 48 минут бұрын
Oyamba ukukanthe iweyo olambira Santana iwe chakwera pankholo pako
@MusstafaJalasi
@MusstafaJalasi Сағат бұрын
Ulaliki ku church mpaka omasulila malilime 😂😂😂 10:47
@AndrewSilwimba-o6s
@AndrewSilwimba-o6s 2 сағат бұрын
Go ahead Mr David
@KheniNagwandu
@KheniNagwandu 3 сағат бұрын
Tikudikira inuyo Mr president
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 сағат бұрын
Zazii mademo amasiku ano alibe chikoka ndiposo iwe nyamata wotchedwa mbewe ndiwe ndani pa Malawi kachipani ka
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 2 сағат бұрын
Iwe ndiye mbuzi ya munthu ulibe mfundo pitani ku ma demo mukawina zisankho mulungu simumudziwa agalu inu
@JamesDzonzi-t7u
@JamesDzonzi-t7u 2 сағат бұрын
Kkkk Bank mkhonde kodi ?kazingodya chakhucho mbuzi iwe mzako ukulimbana nayeyo sanyoza munthu
@SEEJSHJEFFREY
@SEEJSHJEFFREY 2 сағат бұрын
Mavalidwewo eeeeish 😂😂😂😂😂😂😂
@KhadijaMsosa-d7z
@KhadijaMsosa-d7z Сағат бұрын
Eeeeshii🙌🤣🤣🤣🤣
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 58 минут бұрын
Ndakoka at its best
@NigatuUmuro-wh8wi
@NigatuUmuro-wh8wi 3 сағат бұрын
Seems he z preaching
@MusstafaJalasi
@MusstafaJalasi Сағат бұрын
Chipani chanji cha x mikono sichifanizo cha satana chimenechi? km mabusa enawa mmmm shame on you mr no name
@MagretBula
@MagretBula 25 минут бұрын
Kkkkk ndangofutsamo😂😂
@EnelessBanda-x5n
@EnelessBanda-x5n 2 сағат бұрын
Zaziiii nae mfundo alibe nkhan ndiyamaliro bas
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 2 сағат бұрын
Zaziiii, kusowa fundo zowawuza anthu.
@Howard-c1q
@Howard-c1q 2 сағат бұрын
Kalalikireni ku chalichi osat ndale,mavuta sangathe ndi inu
@Yanjanani
@Yanjanani 2 сағат бұрын
Kd ndizakalekale kapena utumiki?
@JamesBrown-gx8my
@JamesBrown-gx8my 58 минут бұрын
Anthu akuba awà
@CharlesBanda-kv8bh
@CharlesBanda-kv8bh 2 сағат бұрын
Galu ameneyi akafufuze iyeyo mumati adapha ndi chakwera ndiye mukuuzanso emweyo kuti afufuze koma mutu yanu imagwira ndithu? Chamba kapena mwasuta chochuluka? Za mademo anuwo tilibe nazo ntchito kapangeni
@mikesandali8425
@mikesandali8425 3 сағат бұрын
Azitumiki katumikileni Ambuye ndalezi zikuonongani
@fredrickmatanda5766
@fredrickmatanda5766 Сағат бұрын
Ndiye masanjetu ngati tilikokalapitsana machimo
@HenriqueFrancis-cv6zc
@HenriqueFrancis-cv6zc 2 сағат бұрын
Ofunikadi zatsopano enawa tawayesa palibe chanzeru
@MillieMalakam
@MillieMalakam 2 сағат бұрын
Chidzindikilo chimeneco akugwilisila ntchito uyuyu chikuthandauza ciyani
@MarkKumpoto
@MarkKumpoto 2 сағат бұрын
Thyrod&staff comfort me,Divine lordsprotection
@ElizabethAlick-e6b
@ElizabethAlick-e6b 2 сағат бұрын
Asadzavoteso anthu oipa awa aringati chikangawa awa
@SonickMwale
@SonickMwale 3 сағат бұрын
Lumbe wamunthu uyu kkkk😂😂😂😂
@PrinceBwanali-vy9md
@PrinceBwanali-vy9md Сағат бұрын
Zachibwana zokha zokha
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 2 сағат бұрын
Tsisi osathilako easy easybrack man zayesa kuti cheeeeeee
@ruthchikhoswe6028
@ruthchikhoswe6028 Сағат бұрын
Teketeke
@MosesSoko-y8h
@MosesSoko-y8h 2 сағат бұрын
Jama yako iwe!
@ThomasDulla-p4n
@ThomasDulla-p4n 2 сағат бұрын
Kodi athuwo sakhala panse
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 2 сағат бұрын
Zaaaaziiiii
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 сағат бұрын
kung'alula, kung'alula basi
@MarkDominico
@MarkDominico 3 сағат бұрын
Zaziii
@AndrewMachemba-j2u
@AndrewMachemba-j2u 28 минут бұрын
Zamphamvu
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 2 сағат бұрын
No more paster to luling our country you bring saternism too much
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 сағат бұрын
Takalalikileni za ambuye mwana wa satana iwe
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 41 минут бұрын
Komatu muthuyi sakulakwa a malawi 🇲🇼
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule Сағат бұрын
Kkkkk
@jestinanamkonda1495
@jestinanamkonda1495 8 минут бұрын
Mulibe chikondi the so called man of God. The Holy Spirit is not in you. You are full of anger.
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 2 сағат бұрын
Kodi abwerenso m'busa wina!!!!!!
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 2 сағат бұрын
Tsisi osathilako easy easybrack man zayesa kuti cheeeeeee
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma 2 сағат бұрын
Kape iwe wasowa zokamba
@babranzima8120
@babranzima8120 2 сағат бұрын
Zaziii
My Daughter's Dumplings Are Filled With Coins #funny #cute #comedy
00:18
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 25 МЛН
Who’s the Real Dad Doll Squid? Can You Guess in 60 Seconds? | Roblox 3D
00:34
My Daughter's Dumplings Are Filled With Coins #funny #cute #comedy
00:18
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 25 МЛН