🤣🤣🤣🤣🤣 Koma Ziliko liko komabe Utsogoleri usinthidwa. Anyway I love BAKILI MULUZI TV, History is the best teacher ✍️✍️
@DantonKaipa-v8i2 күн бұрын
Kutheka ndi yemweyu, pajatu chilungamo chimasakanikilana ndi mwana.l always proud with bmtv he is real the best teacher, now and forever.
@YusufAjida-t8r3 күн бұрын
Zachamba izi akufuna kuononga Zina la bakili muluzi TV koma akunama kwambili Ana achepa timamukonda ❤❤❤❤ kwambili bakili muluzi TV
@PromiseSaidi5 сағат бұрын
Mn akupanga post ekha bakili muluzi tv km chifukwa chachikulu ndichoti bakili muluzi tv amakonda DPP ndie dalitso kabambe wakana kupanga alliance ndi chipani cha DPP
@msatisi.reangfordphiri3 сағат бұрын
@@PromiseSaidinde moti a Kabambewo akuti ali nayo 50+1 yotchaira Chimwendo?
@LeonardEnock-e1t3 сағат бұрын
Bakili muluzi tv anayamba nkale kumung'alura chilima anangosiya apa atamwaliramu koma ndiyemweyu ndinthu BMT 😅😂
@SulaimanIssa-b2h2 сағат бұрын
Ea ndima haka amene aja ineso ndavera nawo muli zofooka zambili zimene zikusonyeza kut siwa bakili muluz tv
@yusufu-g6e3 күн бұрын
iyi Nd bakli muluz TV yaa mcp
@LinlyMathewe6 сағат бұрын
Kaya ndi yemweyu Kaya zopeka but never give up UTM my vote ❤❤❤
@SulaimanIssa-b2h2 сағат бұрын
Ayi sibakili muluz TV ndi mahaka amene aja. Muivele bhobho ndi fake voice. Page imene ija yapangidwa haki ndi athu a boma ndiofina kuononga chipani cha utm. Ndiye choyamba akuyenera kuipisa mbili ya chilima. N mu audio imene ija muli zofooka zambili zimene zikupeleka chikhulupililo kut siwa bakili muluz TV
@denndavie60413 күн бұрын
Ndipo ineyo chilima sindingamu bakile. He was indeed a bad guy with Lucius Banda.
@HOMEAWAY-h7t3 күн бұрын
The ever best tv in mw we still love the people who are manengng this ❤❤❤
@ThokoMsonkho-hy4uc3 күн бұрын
Pamene page yomweyo ikawulutsa nkhani ya maliro a Chilima mumati ndiyabwino chifukwa akangofuna kukuthandizani kuti a UTM mumuziwe CHAKWERA pazomwe amapanga Chilima kufikira imfa yake. Koma kunena chilungamo inenso ndinamuona kuti Chilima uja anali wamwano ndiponso anali chitsilu pa ndale. Kuzichotsa yekha kwa PETER kenako kudzalumikizana ndi Chakwera pamene paja anapusa pa ndale potengera mbiri ya MCP mbuyomu. Munthu amapanga mistake koma pokhapa ndimamukonda kuti ndiwadyera komanso ndiwamwano ndinso alibe nzeru zautsogoleri. Mmene amamulankhulira BAKILI MULUZI purezideti wapuma uja ndinamuwona kuti tsogolo panalibepo mwa iye. Anali wa mwano kwa akuluakulu amayenera kumwalira basi
Zatembenuka, ng'ombe zayang'ana ku joko. Yomweyo... 😆😆🤦🏽♂️❤️.
@AlfredGanizani-v9f3 сағат бұрын
😅😅 tingodikira kut give zambili my vote to my chakwera is number one
@wisdomlimbe94833 күн бұрын
Olo zitakhala zoona, who cares about DK's private life? All I know he can run the economy way better than the current situation. Malawi is not looking for munthu yemwe sananyengepo. Tikufuna munthu woti atsogolere kukonza chumachi kuti wolimbikira azidya thukuta lake. Enafe we don't care kaya akhala Chakwera yemweyi, kaya Enock Chihana, kaya APM, kaya Atupele kaya DK, kaya wa Bakili Muluzi
@usherjamson1743 күн бұрын
Amene waja ndichi machine 😂🎉
@HenryNanthuwa3 күн бұрын
Nosense get lost bakili muluz zoputsatu izi
@NenaniMoyenda3 күн бұрын
Ma pulopaganda a MCP awa ndipo BMT akangotukila musambulidwa🤣
@GeoffreyMarko-v3s3 күн бұрын
Chilima anasocheresa dzikoli😢😢😢😢😢
@harrisbanda58913 күн бұрын
Akubweletsa nkhanizi siwa bakili muluzi tv, ndiena mwa afisi achikangawa kufuna kuipisa ndikuononga mbili ya utm , komabe tinene mosapsyatila pano , chilima ndamene anationongesela malawi wathuyu , after all anangoti duuuuu ngati akumetedwa osafuna kususa nkhanza zomwe zilimdziko , nayenso chikangawa kukapha mzake pambuyo poti amabela limodzi y?, y dd u do dat chikangawa?
@MorrisDzonzi2 сағат бұрын
Zazii kumudetserela Kabambe akumuopa awa,,Zonse nchabe koma Chakwera walephera achoke basi
@WilliamNhlane-fd9hi3 күн бұрын
I don't think this is bakili muluzi , awa ndi mcp akufuna tisalankhule imfa yachilima .
@EmmanuelkpPraise3 күн бұрын
Aaa zazii uyu si wabakili muluxu tv
@SulaimanIssa-b2h2 сағат бұрын
Ea ndima haka amene aja. Akayambileso. A mcp amaonatu ngat amalawi ngogona kwabasi kkkk
@harrymicah61403 күн бұрын
😂😂😂😂 uyu nde ndakayika kut ndi Bakaili muludzi ukadusa wez history is the best teacher aa tabwali uyu
@AlexanderTraffick3 күн бұрын
Nkhani izi zokomera Kwa Anthu atambara wakuda.mcp
@RinosChilumpha-y2dСағат бұрын
Zimachitika koma bakili muluzi TV sayimila mbali ai palipose amang'alula bass
@FrancisNyayi4 сағат бұрын
Who said ahhhh Like me here when listening
@TaniaMphalumo2 күн бұрын
Ayi.izi akupanga ndi mayiko usi ngati simukuziwatu ndi manganya akupanga zosezi😊
I don't think that this is Bakili Muluzi TV kaya mwina
@EmilyKanyika3 күн бұрын
Machimo
@ChavuksFrancois3 күн бұрын
Nkhani zonsezo a Malawi akudzidziwa, kaya chilimayo, kaya Kabambe a Malawi akuwadziwa. Nkhani za personal sizingasinthe chilichonse kwa a Malawi zotsatira UTM
@Gwedeza-q3f2 күн бұрын
Ndi bodza ili ndi propaganda ya mcp, uyu siwaBakili muluzi TV 😂😂😂😂😂 ndidzabodza ndi aganyu awa a mcp
@mbelengamavuto25173 күн бұрын
Zosamveka izi mukuyakhulazi
@KnowxySainet6 сағат бұрын
Uyuu c bakili TV weniweni anthu a mcp awa muone kumapeto kwake akukakamila mau oti history is best teacher nonsese
@ishaqyassin50015 сағат бұрын
Ubwino wake Chisale ndi wa kuba Kabambe mbava ya munthu
Mwakhaula Uyutu si mtanyiwa ai oti tsiku ndi tsiku odzingolimbana ndi chakwela ai
@CharlesKaujole3 күн бұрын
Dars
@AustinAllan-lh5ij2 күн бұрын
Ku Chikangawa uku guys 😅😅😅
@AngolaChinga3 күн бұрын
Inu uyu si wabakili muludzi tv kapolo wa mcp uyu
@SolomonNjolomole3 күн бұрын
Doud Suleman ndi azizake kuyesera machine agula aja apa game mbola.
@SmartMailos2 күн бұрын
Sizona siiye
@MimiKapito3 күн бұрын
Zaboza uyu
@tasiyanakasalu62283 күн бұрын
Ndiyomweyo kungot akangana bax kkk
@NoahPhiri-f7m3 күн бұрын
Sibakili tv ameney ndiwa mcp
@ErickCPatrick2 күн бұрын
kabambe,wakuba
@KhirChisale3 күн бұрын
Eeeeshiii koma ine
@KennedyPhiri-h9h3 күн бұрын
Sibakili muluzi TV imeneyo ndi propaganda
@Mustapher-fb4qp3 күн бұрын
Chirima ineso sindingamuyikire kumbuyo
@NelesonchibwanaMandera42 минут бұрын
Bakili muludzi TV imanena zoona ine ndimankhulupililad amankhala kut waziwona kale sogolo lake
@MikeLodzi3 күн бұрын
nkhani izizi siza bakili muluzi tv anjanjawidi angolowelelapo
@natashamathala87152 күн бұрын
Yaaaaaah a mcp mwafika patali, koma mukunama naye wa bakiri muluzi simumukwanitsa ayi mwachepa dikilani akuyankhani nzanuyo akubwela ndithu chifukwa uyu si wathu wathu wa bakili muluzi ayi ine ndakana izi.
@EvanceSungani-cv9jk3 күн бұрын
MCP paja yakunga chiwembu kwa bakili muluzi TV this is plan ,,,,,
@ShamimuBisani3 күн бұрын
Zaziiiii mwalephera kumusaka .mukhaula
@YounusWabullah3 күн бұрын
Ndi propaganda iyi zamkutu bas
@ChikondiMusaya-x6n3 күн бұрын
Sibakili muluz ameneyo
@greycianmbewe45733 күн бұрын
Lankhulani koma timuvoterabe
@PatrickZinenanie2 күн бұрын
Si bakili muluzi ameneyo ndi zigawenga za chikangawa party mcp
@AlexanderTraffick3 күн бұрын
Komatu TV imeneyi imakhwefura munthu kkkk achina kamajekete Ali ziiii
@DonaldBanda-qi7yw3 күн бұрын
Ndale zaku Malawi ndi zosokoneza anthu
@DonaldBanda-qi7yw3 күн бұрын
Ndi kunena zoona Ana amasiku ano sakudziwa kuti Kodi Atsamunda amalamulira bwanji dziko lino. Chimene akudziwa ndi kulemba Nkhani ZOSOKONEZA A MALAWI pa SOCIAL MEDIA basi, komanso kuwapatsa Bomali popanda masankho sangathenso kulamulira dzikoli adzangokhala mavuto okhaokha basi.
@Extratremendouszeus3 күн бұрын
But you have to check because there are many bakili muluzi TVs...else you bakili muluzi never does this
@MCDAISONNKHWAZI3 күн бұрын
Mmm page is hacked history is the best teacher wa baliki TV wen wen amakhala in small letters ndipo kwambr amakonda ma audios not ma letters ndipo samapanga pafupi pafupi chonch
@KondwaniChaponga3 күн бұрын
Mkamalimbana ndi BMT mutha ngati makatani
@BrightLuciano2 күн бұрын
Zazi SI Bmtv uyu 😢😊
@AugrinNgunga3 күн бұрын
Mayaz sibakili muluz tv uyu aaa timatha zimenezo kulemba pa page yamuthu