Kodi Baibulo limene timawerenga ku Malawi kuno linachokera dziko lanji?

  Рет қаралды 29,413

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

11 ай бұрын

Пікірлер: 113
@sakmosmediatv7015
@sakmosmediatv7015 11 ай бұрын
Am a Zambian and a keen follower of this page continue with the great work
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 11 ай бұрын
Ndiwe dolo pa history m'makwana bg. Thanks very much. Muzinde mmiyoyo ya anthu aziwe choonada allah bless you
@alimonngwinja9514
@alimonngwinja9514 11 ай бұрын
Enlightened. Now we can understand why they are so many inconveniences in the bible.. zambiri mzopeka
@AshrafJumah9665
@AshrafJumah9665 11 ай бұрын
Keep up good work. mumatitsegula maso brother
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 11 ай бұрын
Thanks for the extensive variety of information we get from your bank of knowledge Continue providing a well and extensive information daily
@afritouch4660
@afritouch4660 11 ай бұрын
Zikumveka wawa..!! Keep it up
@shadreckmatenje6629
@shadreckmatenje6629 11 ай бұрын
Thanks bro for your update
@feldoxdax2787
@feldoxdax2787 11 ай бұрын
Keep up Good work
@wilsonsawasawa3794
@wilsonsawasawa3794 11 ай бұрын
Thumbs up Bigman!
@clementmanyesa
@clementmanyesa 11 ай бұрын
You are best brother umavesa kukoma mix chichewa eeee timavesatu bwino heavy
@geee7672
@geee7672 10 ай бұрын
....your skills are getting better and better
@ZahnoorMilan-pe3ys
@ZahnoorMilan-pe3ys 11 ай бұрын
Q.U.R.A.N z de best ever Mumakwana big
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Munamuchosesa mbili yachisilam,mumuuze abwelese mbili yachigawenga Muhammad pano,anachoselanji mbili yachigawenga
@ismailkhuneya3346
@ismailkhuneya3346 11 ай бұрын
Your nothing but a hero of history we proud of you brother ❤❤
@harrisonnavayah6480
@harrisonnavayah6480 11 ай бұрын
You're my number one
@kubengovender6996
@kubengovender6996 11 ай бұрын
Your tops brother man!!
@footballskillsandhighlight7974
@footballskillsandhighlight7974 11 ай бұрын
keep your good work mumatha
@user-is8mi3wi8w
@user-is8mi3wi8w 11 ай бұрын
Your #1
@KingsleyWakusa
@KingsleyWakusa 11 ай бұрын
Brother you deserve much respect....Malawi its so blessed by dis historical wisdom from heavy... I wish I will know you in my life,b4 death,coz you a teachest man,in my life,,may the Lord keep you safe from enemies,,, Good Luck...
@papelariareis.e.
@papelariareis.e. 11 ай бұрын
Respect brother
@tamimaosman7674
@tamimaosman7674 11 ай бұрын
Noted with Thanks🙏
@salaam1089
@salaam1089 11 ай бұрын
Respect
@ziwani3682
@ziwani3682 11 ай бұрын
BIG 👍
@jamestsabola1376
@jamestsabola1376 11 ай бұрын
Pa 5 seconds ndayamba kuwonela timakunyadilani big man my first comment
@yasinkamwendo-jf7sc
@yasinkamwendo-jf7sc 11 ай бұрын
Lov❤ bro
@frstyhavoc6678
@frstyhavoc6678 11 ай бұрын
And the King James Version is the greatest version
@ishmaeldouglas5962
@ishmaeldouglas5962 2 ай бұрын
Yes and it has grave mistakes😂
@isumailahuseni9394
@isumailahuseni9394 11 ай бұрын
Keep up the good work bra
@user-uh3wg5oq9j
@user-uh3wg5oq9j 11 ай бұрын
Ndakaika ngati angakwanitse
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Mumuuze abwelese mbili yachigawenga Muhammad pano, anachoselanji mbili yachisilam
@user-pt1fy3qg4u
@user-pt1fy3qg4u 11 ай бұрын
Never give up
@user-nz8mq4ff3e
@user-nz8mq4ff3e 11 ай бұрын
Timakuyamikani brother
@irenechirwa9710
@irenechirwa9710 11 ай бұрын
Brother munazayankhulapo mbiri yachi silamu panali part 1&2 koma sikuwoneka pa utube panu bwanji.
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Anaichosa asilamu ambili anakwiya,mbili ya chisilamu ndiyoipa,sangainene poyera,
@irenechirwa9710
@irenechirwa9710 11 ай бұрын
@@user-nt4fr2le3f vuto safuna anthu aziwe zoona angofuna aziwapusitsa koma ndi kuwalakwira anthu.
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
​@@irenechirwa9710 chisilamu ND nkhondo,atanena zamuhammad asilamu ambili anakwiya , Muhammad ndchigawenga ,
@richmondkilembe5449
@richmondkilembe5449 10 ай бұрын
Umakwana brother mulungu akudalise umatuziwisa zambili
@eddiechiumba2381
@eddiechiumba2381 11 ай бұрын
Iweyo ndi washing machine mbambande
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 9 ай бұрын
Kupanda inu ndikulumbila sibwezi Aitel ndi tnm akundidziwa pa mofaya ndi pamtsetse akuganizileni. Komatu bukuli lasinthidwa kwambiri and zoona umu ndizochepa ndithu eishhhh azungu anatipweteka
@Misasi19
@Misasi19 11 ай бұрын
Tadziwa nao thanks
@happygondwe4774
@happygondwe4774 11 ай бұрын
No voice why?
@Razzaq2010
@Razzaq2010 7 ай бұрын
Dzimvele wekha mbale wanga
@NgalandeRobert-to2mz
@NgalandeRobert-to2mz 11 ай бұрын
Wadza wadza😂
@khalifacalvinajass9998
@khalifacalvinajass9998 11 ай бұрын
Koma adha awawa eeeeee ndi machine
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Tabwelesaniko mbili ya chgawenga Muhammad ,tibveko,zachikhilistu mwanena tabvako,Nanga mbili yabuku lokugwa kuziwanda la Quran munena liti,tanenaniko za chgawenga Muhammad
@folamitowing238
@folamitowing238 10 ай бұрын
Utiuze iweyo plus ma umboni onse kuti kuran ndi buku la ziwanda.osati zongo lota mubwerwtse ma umboni tikumveni.Mwayaluka inu mwakhala mukutsatila mdima
@ishmaeldouglas5962
@ishmaeldouglas5962 2 ай бұрын
Luka 19:27 Mr gututu tawerengani msetezi
@user-ul4pm3bq4c
@user-ul4pm3bq4c 11 ай бұрын
❤❤❤❤❤🎉
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 11 ай бұрын
Ulemu wanu bro
@user-tl1jq2gc5b
@user-tl1jq2gc5b 11 ай бұрын
Chocho zikuonekatu kut baibuloli anangolemba azungu ,koma Leni Leni la mulungu Lili kut?
@aggogokina8992
@aggogokina8992 11 ай бұрын
Abale ndimadabwa mabaibulo kuchuluka omatsutsana zokamba, zili zongoyambitsa achina Jemusi aaa. Ndithu mau a Mulungu namalenga ndi Quran bas ndipo ndiimodzi yomweyo dziko lonse lapansi. Allah Akbar!
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Ngat kuli buku losokelesa ND Quran,buku lopeka, Muhammad sintumiki ayi koma chgawenga
@aggogokina8992
@aggogokina8992 11 ай бұрын
Palibe chimene ukudziwa zipangani za Jemusizo bas ndizomwe mudazolowera. Zipangani malilimewo 😀😀😀😀
@irenechirwa9710
@irenechirwa9710 11 ай бұрын
​@@aggogokina8992 inu mbiri yanu tinaimva kale muuzeni bakili muluzi ayipangeso post apa anthu omwe sanayimvele amve, anena apo kut amatanthauzira kuchoka muchiyankhulo china kupita ku chingelezi
@ganizanichisale1449
@ganizanichisale1449 11 ай бұрын
Mavuto sazatha kumusindilira mulungu
@luciascharles4345
@luciascharles4345 11 ай бұрын
Aaaaa ndale zidaononga dziko lapansi , chifukwa kusintha koseku Kwa ma Baibulo ndizifikwa za ndale
@petermasenti2084
@petermasenti2084 6 ай бұрын
Mumakwana big
@idrissaeliassa
@idrissaeliassa 11 ай бұрын
I'M a Muslim there's no such destruction
@mosesdyelathu
@mosesdyelathu 11 ай бұрын
But some people the agreed
@mishackstanour8747
@mishackstanour8747 11 ай бұрын
You don't know what you r talking about........go deep in Islam you will see the difference
@mosesdyelathu
@mosesdyelathu 11 ай бұрын
@@mishackstanour8747 but this guy he has never mentioned Islam so how come 🙄
@mishackstanour8747
@mishackstanour8747 11 ай бұрын
@@mosesdyelathuBrother...... I thought you know how to read ....... first read the message yakeyo then yangayo
@phillipchiotcha3197
@phillipchiotcha3197 11 ай бұрын
I remember Papa amagulisa tima bukhu kwa akhristu ndikumawauza kuti akagula ndie kuti matchimo awo akhululukidwa iye amatero powauza kuti zalembedwa mu Bible panthawiyo kupeza Bible kudali kovuta amadziwa kuti anthu sangalipeze kuti aone pomwe palembedwa koma Martin Luther atapeza mwayi owerenga Bible adapeza kut zabodza zimenezo ,ndipo adalesa anthu kumagula tima bukhu tija zomwe zidapangisa kuti Papa amutchose Martin mu Roman Catholic
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
Read surat AL kahf 18vs85 86 even mohamad being a last and favorite prophet but he didn't even know where the sun set ,,as he said the sun set on a mouldy hot water
@davidmaulana9277
@davidmaulana9277 11 ай бұрын
Komatu azungu amenewa atidyesa manyi koopsa tiwabwezere baibulo lauli bas
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Anakudyesani kale manyi,manyiwotu ND Quran ndchigawenga Muhammad,odyedwa ND nkhumba
@Razzaq2010
@Razzaq2010 7 ай бұрын
Kkkkkkkkkkkkkkk
@Razzaq2010
@Razzaq2010 7 ай бұрын
​@@user-nt4fr2le3fmanyi ndi awa mukudya a tindaly 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂,,bishop bible, mateyu bible nde chani zimenezo 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@user-ps9nu6se9k
@user-ps9nu6se9k 6 ай бұрын
Who is erusmas
@user-mz8nw6nx6p
@user-mz8nw6nx6p 4 ай бұрын
Kaya tiwuzeni kuti lenileni lilikuti,,,,nangalowona ndiliti,,,,nanga tikhulupilila bwanji Bible poti lenilenilo analibisa,,nanga analibisilanji,,,kodi mulizowona ndimuti?
@mzatimsash5598
@mzatimsash5598 7 ай бұрын
Ndiwe dolo kwambir
@christopherbottoman9131
@christopherbottoman9131 11 ай бұрын
Zikomo kwambiri ambuye akudaliseni mumayesesa kutisangalasa
@robertrichman9376
@robertrichman9376 10 ай бұрын
Pena ndichifukwa chake azungu ambiri sapemphera coz they don't trust bible
@phillipchiotcha3197
@phillipchiotcha3197 11 ай бұрын
Komanso ndipezerepo mwayi mukapeza mpata tifufuzireni chiyambi cha Football ena amati mpira udayambira ku Egypt ena ku Greece according to their gods
@salaam1089
@salaam1089 11 ай бұрын
Uruguay
@cephasnkhoma2301
@cephasnkhoma2301 10 ай бұрын
Koma ma Hebrew amatipo bwanji pachisokonezo ichi?
@abdulsalammkwepu3321
@abdulsalammkwepu3321 6 ай бұрын
Nde wina adziti bible original ndi bukhu lopatulika ndilo mau a mulungu ... wamvatu apa mubale wanga
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 5 ай бұрын
Koma pa nkhani ya Mau a Mulungu uku musapiteko mulakwisa man zikufunika anthu.opemphela izi
@ishmaeldouglas5962
@ishmaeldouglas5962 2 ай бұрын
Monga inuyo eti?😮
@aggogokina8992
@aggogokina8992 11 ай бұрын
Awa ndi akamuna katundu omanga ndi mawaya awuzen big
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Mumuuze aneneko mbili yachigawenga Muhammad,wanenako zachikhilistu tabva Nanga mbili ya Muhammad chgawenga chigwililira anena liti,
@aggogokina8992
@aggogokina8992 11 ай бұрын
Sizingatheke kuti anene sinanga mtumiki Muhammad peace and blessings be upin him si jemusi nchifukwa chake olo bukhu la quran ndi limodzi dziko lonse lapans. M'bale chilungamo chimaineka chokha.
@AsibuJames
@AsibuJames Ай бұрын
​@user-nt4fr2le3f anagwilira mayi ako?
@eunicemoyo6024
@eunicemoyo6024 11 ай бұрын
Zikukhala ngat king James uyu adaliko owopako mulungu 🙄🙄
@cephasnkhoma2301
@cephasnkhoma2301 10 ай бұрын
Koma ine mwandipangila zomwe ndikafunafuna. mau a YHV sana lembedwe bwino ndintu mukawerenga 1 samuel 13:vs1 muma bible monga (KJv) (mbuku lopatulika) (chi lenje or Cina mukuni ) ndi (TANACH Hebrew English version ) eee inu nacheepa ine.
@lastonkachala6624
@lastonkachala6624 11 ай бұрын
Tilitonse
@JeofreyNamalima-yn4tj
@JeofreyNamalima-yn4tj 11 ай бұрын
Inu nkatundu bigy
@androidgame7484
@androidgame7484 11 ай бұрын
Lachizungu or english
@leyydavido-qd9gv
@leyydavido-qd9gv 11 ай бұрын
Mumakwana malume
@user-uh3wg5oq9j
@user-uh3wg5oq9j 11 ай бұрын
Ndekuti mipingoyi ili ndiayini ake anthu osati mulungu eeeeeee ife tikuti lowani mchipemphezo chamulungu yemwe adakulengani pachiyambi kwaiyenso mkomwe tibwerele tonse
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Chisilamu ndchipembezo chamafano, Muhammad odyedwa ND nkhumba chgawenga ndamene anayambisa chisilamu,ngati ukulesa muuze abwelese mbili yachisilamu,anachoselanji mbili ya Muhammad ,
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
​@@user-nt4fr2le3ftrue brother,,even me ,am now out of that cult,,,sanadyedwe ndi nkhumba,,koma atafa anamusunga masiku atatu mnyumba akuti azuke ngati momwe yesu christ anazukila koma zomvesa chisoni amaola asanakatikidwe mmanda so agalu ndi ntchenje was everywhere
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
Brother go and read surat AL Imran 3vs 64,,which said ee inu eni a buku (la mulungu) Ayuda ndi Akhrisitu,,they didn't say Aslam why??? Which means the owners of book of God is jews and christians
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
And go to surat 5vs68 AL ma Idah which says ee you people of this book,quran,,,you are nothing pachipembezo until muimilile kusatila malamulo a ma book a Taurat( old testament ) and Injili(newest testament) which means the book of God was allready there before quran
@aggogokina8992
@aggogokina8992 11 ай бұрын
Anthu ali bhize kulibashika mmatchalitchi ndi zinthu zongoyambitsa azungu ku Britain😂😂😂😂😂
@user-xc1xt2qd7t
@user-xc1xt2qd7t 11 ай бұрын
𝐊𝐤𝐤 𝐧𝐝𝐩 𝐤𝐤𝐤𝐤
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 11 ай бұрын
Ineso kudabwa anthu busy kumenyesa pasi zipumi ,chinthu choyambisa chgawenga Muhammad , odyedwa ND nkhumba uja
@aggogokina8992
@aggogokina8992 11 ай бұрын
M'bale upange ma research mokwanira udzadziwa kut tingamulambile bwanji kulambila sikuvina ndikuyimba za achina jemusi mumasiyanitsa bwanji ndi disco kapena ku tavern😀 Uwerenge mokwana udzadziwa yesu kut amalambila Mulungu motani
@aggogokina8992
@aggogokina8992 11 ай бұрын
Usakhale busy kubakila zinthu zachina jemusi zilakamize kufufuza chilungamo kut ukhale munthu ozindikira jemus ndi martin luther sangakuthandize kanthu
@ganizanichisale1449
@ganizanichisale1449 11 ай бұрын
Mpaka kulemba mau nkumati amulungu
@bravemsiska8039
@bravemsiska8039 11 ай бұрын
Azungu anango masulira ndimene wafotokozera m' baleyu koma kuti uonetsetse upezakuti Moses anelembanawo ku old testament after ataudzidwa ndi mulungu. So it was written in Hebrew and Greek language.
@argentchilanga3246
@argentchilanga3246 11 ай бұрын
Am Malawian but we are really blessed with this historic man .God bless you
@ganizanichisale1449
@ganizanichisale1449 11 ай бұрын
Mukuti bwanji mbiri ya quran achalume kapena simuziwa kanthu ndinu bububu pa zimenezi
@irenechirwa9710
@irenechirwa9710 11 ай бұрын
Akuyiziwa A to Z anazapangapo post apa part 1&2 koma inu munalibe kabwino mbir yake ndi yoopsa enafe tinayimvesera ndithu. ndeno ati asilamu anamuukira kut achose nanga si anadziwa kut anthu akaziwa chitsitsi chawo ndeku zinthu zaipa
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
And did you tell people that Allah had three daughters AL lat,,,AL uzah and manat??
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
Why can't you bring nkhani ya Mohammad yogonana ndi mwana Poor little gal Aisha at the age of 9
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
Even the quran itself seems like a copy of Taurat and Injili
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 8 ай бұрын
Useless information 🚮🚮🚮🚮🚮🚮🚮
@maviekuwili378
@maviekuwili378 11 ай бұрын
Tikufuna mbili ya Quran ngati uli dolo
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 4 ай бұрын
Tell him to tell us about mohamad who went to snatch his son wife zynab from zayd and sleep with little child Aisha at the age of 9 shame while he was 53
@AsibuJames
@AsibuJames Ай бұрын
​@@shakiraameen8001zinalembedwa pati
@user-xc1xt2qd7t
@user-xc1xt2qd7t 11 ай бұрын
𝐊𝐞𝐞𝐩 𝐮𝐩
@twaibuselemani6035
@twaibuselemani6035 11 ай бұрын
Zikomo
DRIVING SCHOOL- Episode 166
15:17
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 16 М.
Mbiri ya mpingo wa Seventh Day Adventist.
23:22
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 52 М.
Kitten has a slime in her diaper?! 🙀 #cat #kitten #cute
00:28
Akufuna kubera chisankho pogwiritsa ntchito ana
16:30
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 8 М.
Times Exclusive featuring Sameer Sulemani - 13 April 2024
1:00:14
Times 360 Malawi
Рет қаралды 84 М.
Mnzake wa Putin waomberedwa ku Europe.
6:50
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 8 М.
President Lazarus Chakwera | John Chilembwe day 2024
16:37
Malawi Page
Рет қаралды 26 М.
Mbiri ya kusowa kwa malo ku Nyasaland (now Malawi)
24:31
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 11 М.
Landing In Blantyre Malawi - Air Malawi
3:02
Muslim Xplorer
Рет қаралды 12 М.
Nicholas Dausi at MCP, facing President Lazarus Chakwera
21:04
Malawi Page
Рет қаралды 125 М.
Malawi Bloodsuckers History.
17:22
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 35 М.