Panopo a Malawi sakufunanso zoti wina ayesere akukumbukiri momwe zinaliri nthawi ya Mutharika zinalibwino APM my vote
@mayesojameskatete2 ай бұрын
APM uja osazaphwekesa
@WanangwaMfune2 ай бұрын
Kodi Malawi palibetso Munthu wina muno mmalawi?
@hamiltonsolomon37562 ай бұрын
Chilungamo chokhachokha.....Osewa Chakwera ndi Muntharika....Mother Malawi wathu akusauka chifukwa cha athu ngati awa....Mmmmmmmmm.Andalewa atibera ndalama zambiri zamisonkho yathu.?90% zimalowa matumba mwawo 10% chitukuko.....60 years of Independent no Modern Bus Depot...Blantyre...Mangochi..Lilongwe and Mzuzu ma Depot abus ngati pabwinja......Ndalama nkhaninkhani zalowa matumba a Andale athu😂😂😂😂😂
@samsonmtumbati48552 ай бұрын
Mbuzi iwe ngati wasowa zolankhula pita uko
@AishaChibwana-b8o2 ай бұрын
Koma zoonadi kunena chilungamo onse ndi olephera palibe wabwino 😂😂😂😂
@marryphili54192 ай бұрын
Zako izo chakwera sitingamufanizire ndi chakwera ife tasiyanisa DPP pomwe inali muboma zinthu zinali bwino ndarama yinali yamphamvu mapassport amapezeka palipose fertilize wunali pamutengo WA bwino tinalindi chimanga chokwanira iwe chimutu chako cha mamina tiye wuko ku kura kulibe ntchito zomwe tikufuna ndi zeru
@Lazarus-qo1sl2 ай бұрын
Muchilungamo DPP idayesess
@MsondaBanda2 ай бұрын
Kkkkk ngwapamulomo uyu
@PatrickMacheso-r6z2 ай бұрын
Iweyo Mutu wako sugwira. APM did not go to close conversion for security reasons if you don't know. MCP inakonza chiwembu over APM using convetion. APM is not just a man who is looking for moqndo and money
@thulambale28362 ай бұрын
Nkhani ya bwino dada
@StevenGJohn2 ай бұрын
Atumbuka ena ndi a nzeru koma ena ndiopusa ngati uyu akupha akupembeza Chakwera galu Chikangawa bolanso Muthalika
@ELLENZAPS2 ай бұрын
Lamulila iweyo ngt ukuti Pieter ngolephera mbuzi
@HumphreyKachepa2 ай бұрын
Aaaaaaaa uyu ndie opusa zedi sinawone Muthu kusiya kadzi ndi kubweleranso nkulu iwe ndi opusa
@MiddayDeleza2 ай бұрын
Mukhonza kunena kuti wonse ndi wolephera, azipani zonse mbuyomu sizinapangepo zikuchitika leroli Mcp nde yatiwonjeza mpaka kumupha munthu oti anawapangila kampeni ayi zikomo, APM WOYEE, ADAD omwewo basi
@SangwaniNkosi2 ай бұрын
Boma siligawa ndalama,Koma ifeyo tikusiyanisa nthawi yamnthalika ndi chakwela.bolani mnthalika.
@WinerdShadreck2 ай бұрын
Zako zimenezo
@RobertLuka-wy9cl2 ай бұрын
Iwe chitsilu chamunthu wosavinidwa machende ako iwe chakwera ungayelekeze ndi peter iwe chitsiku
@JANDULEYUSUFU2 ай бұрын
Mbolo yanu inu osaganiza ndi inuy akutumani chakwera mokuopa kuphedwa
@SangwaniNkosi2 ай бұрын
Ngati iweyo sukuwona ubwino wa DPP ndiweyo mbuzi
@AlexArmandomasswaganheMasswang2 ай бұрын
maka maka wa nyauyu ndiye akuonjesa komaso inuyo kodi chimanga chinali ndalama zingati tayang.anani zitukuko zimene adapanga
@StephanoMaganizo2 ай бұрын
Imilani inuyo ankolo u prisedent mukufuna upure
@AngolanChinga2 ай бұрын
Iwe mutu wak ndiwosagwila machende ako nthawi ya Peter siyinali ngat pano chitsilu iwe
@chesterkumwenda2 ай бұрын
Umafuna tisankhe iwe
@isaaczuze2 ай бұрын
Abura sindikuziwa kuti akutanthauza chiyani .....pano moyo ukuvuta kwambili nthawi ya chakwera .....nthawi ya Dpp zinthu zinali bwino ...50 kg ya chimanga linali 6000 ,chakwera four years chimanga chafika 5000o inu simukuona kuti chakwera waononga ziko
@PreciousDzonzie2 ай бұрын
Eeee Bora 50000 alimi tipinduleko uyosalima zake 6000 ukunenayo imatipha thawizna mpaka 2500 50kg mmmmm umbava