CHAWEZI BANDA WAVUNDULA MADZI ACHITATA KATONDO PA KANDIVELERE |

  Рет қаралды 12,088

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 116
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 ай бұрын
my vote MCP 🗳 ❤❤❤
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 2 ай бұрын
I will vote for mcp
@emmanueljamali7746
@emmanueljamali7746 2 ай бұрын
Agree or not...there are some grains of biasness here..
@DimakatsoMolaba
@DimakatsoMolaba 2 ай бұрын
Achisiru achaweziwa.
@TRUSTDAVID-yt5um
@TRUSTDAVID-yt5um 2 ай бұрын
Chawezi amalakhula ma wise okhaokha more 💥💥💥💥
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 ай бұрын
Onse DPP and MCP had no opposition to leadership. No Democracy.
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg 2 ай бұрын
Program ya makape sadic miya mesa munaphaso ndye mukulubwalubwa chan apa ana agalu inu
@ThomJohn-e6v
@ThomJohn-e6v 2 ай бұрын
Ngati Pali program ndia zisilu ziwili zimenezi
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 2 ай бұрын
Kuphunzila kwa kuno ku Africa ndi memory chabe saziwa kupanga zinthu koma amasungila zomwe anaphunzisidwa kuchoka ku America
@FocusPanje-nd2pr
@FocusPanje-nd2pr 2 ай бұрын
Chawez ukufuna mp ku blantyre city east uzitenge bwino coz anthu aku bt akukumva ukudzipanga wekha de campaign,,, uzibaya mmaso wamva uzitenge bwino kuno sikwa mcp,,, deusi nawenso ukufuna mbali yomweyo play ur cards well OK??? Museseleka muona
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 2 ай бұрын
Kodi program imeneyi amene amapanga sponsor ndi chipani cha mcp eti mukutinyasa kwambiri
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 ай бұрын
Chawezi uzinverako mzakoyo,,ukumafotokoza kwambili wekha
@EmmanuelMoyo-hy5ni
@EmmanuelMoyo-hy5ni 2 ай бұрын
Victor amayankhula bwino kusiyana ndi uyu wa Chikangawa party
@robsonmapeto1911
@robsonmapeto1911 2 ай бұрын
Za zii
@David-z9o4m
@David-z9o4m 2 ай бұрын
Zot Chawezi awina ndakaika,kamunthuka ndka MCP,komanso program iyi ndadana nayo
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 2 ай бұрын
Zoona munthu kukhala Dr koma saziwa za mankhwala kapangidwe kale koma kukumbukila kapelekedwe ka mankhwala basi
@Sofi-p1v
@Sofi-p1v 2 ай бұрын
Chawezi Get out Usova dpp boma 2025 Wadya zambiri za MCP
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 2 ай бұрын
Chawezi ndimamuwona ngati ndi mutumbuka wa nzeru koma ayi chisilu cha chabe chabe wozikonda basi
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 2 ай бұрын
Amafuna azikusangalatsa Iweyo ? Kuti Iweyo wagwira ntchito yanji . Chokhacho chongotchula kuti Mtumbuka , Iweyo waonetsa kuti ndiwe watsankho , komanso wopanda nzeru
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 ай бұрын
Mcp idabwela kuzakhala ndiposo palibe zoluza ndiposo tidakoza kale zobera ngati mene amabera a dpp
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o 2 ай бұрын
Osamamvera program yi
@towerankhoma1380
@towerankhoma1380 2 ай бұрын
Ndipo ndasiya, nyasi
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 2 ай бұрын
Zikubeba
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 2 ай бұрын
uyuyu chawezi banda ndi wa mcp mboloyako chitsilu galu ife amalawi taonetsetsa for sure kuti mau akulu amakoma akagonela
@jamessheki4293
@jamessheki4293 2 ай бұрын
Nanga angapikisane ndi Chikangawa ndani?
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 2 ай бұрын
Koma chawezi u can talk the truth ,times television inaluza munthu
@jameskadete2196
@jameskadete2196 2 ай бұрын
Victor chipofya alikuti Boma ndilomweli coma president tikusitha
@CathrineKumwenda
@CathrineKumwenda 2 ай бұрын
Osamuopsyeza chawez Mwamva Chawez ndi munthu ophunzira vwino amaziwa zomwe akuyankhula
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 ай бұрын
Kodi iwe ukulimbana ndi muthalika bwanji chakwela bwanji kunalibe ofuna kupikisana naye
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 2 ай бұрын
Chawezi 2030 uzagwila ntcĥito mu state house ntchito ija Brian banda analepherà
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 2 ай бұрын
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo 2 ай бұрын
Chawez iwe sukuziwa kuti ku MCP kulibe ufulu waiwala kuti ku MCP ukangoyakhula kuti mundisiyile nane ndiyimileko anafa ndichikangawa waiwala iwe bolani ku dipipiko anthu sakufa amasiyana bwinobwino
@lacksonkim9622
@lacksonkim9622 2 ай бұрын
Chawezi iwe umalandila ndalama Za MCP kape iwe
@Littlefair7
@Littlefair7 2 ай бұрын
Koma buns imene wadya Chawezi kodi yellow buns kapena chani? Achakwera analephera kumusoyira mnyamata Chilima, ma buns akuwononga atolankhani.
@GraciousBilly
@GraciousBilly 2 ай бұрын
Akulu nkhani ndi usogoleri osat zanuzo
@crytoniegrantliffa2431
@crytoniegrantliffa2431 2 ай бұрын
Chawezi mukulakhulira izi chifukwa cha kwiyo yoti anakuchotsa ntchito ku mbc............zako izoo
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 2 ай бұрын
Chakwela alindizaka 65 wapangachani chothandiza amalawi chawezi uzingonyopola ndalama zaku MCP ufune usafune APM akulamula next year
@alecahkaluza9557
@alecahkaluza9557 2 ай бұрын
Chawezi wa MCP
@michaelcharles-p9v
@michaelcharles-p9v 2 ай бұрын
Chawezi wa Mcp galu uyu
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 ай бұрын
Ndipo ine amandinyasa ndale zake amafuna kampando kena kake
@ShukuraniTonex
@ShukuraniTonex 2 ай бұрын
Ndalama za MCP zikukoma Achawez 😢
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 ай бұрын
Nanga peter akachezera sakagona uku anthu akanva mikonono ya munthu wamkulu
@StevieTaiza-r9j
@StevieTaiza-r9j 2 ай бұрын
Chawez ndimbuzi yamunthu
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 2 ай бұрын
iyeyo chakwera ngati ankanenadi zimenezo ndiye kuti ngwabodza nanga bwanji wamupha chilima mnyamata amene amalawi ambili timamudikilila mmalo mwake amalawi ambili taonakuti chakwera ndi mutharika it's better mutharika abwelele pampando akonze dziko limene agalu akuba amcp aliwononga
@KumbukaniChimbalanga
@KumbukaniChimbalanga 2 ай бұрын
Inu mavizi amanu
@IssahNsaliwa
@IssahNsaliwa 2 ай бұрын
Chawezi machende ako
@emmanuelmaomba5163
@emmanuelmaomba5163 2 ай бұрын
Achawez nd a MCP
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 2 ай бұрын
mutharika atupele muluzi adatiuza ife amalawi kuti mukasanga mcp mavuto siizi kodi amalawi manyi akutinyela achakwera palibe chimodzi akudziwa pangani yoyendetsa dziko ndiye chifukwa chake chinachilichonse mmalawi muno chili upset down because we choose arearner to drive along distance that was abig mistake we have done
@MikeArthur-jd2ij
@MikeArthur-jd2ij 2 ай бұрын
What is MCP then 🤷
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Mutharika ndi wamtendere
@ThokozaniAlfred-w2u
@ThokozaniAlfred-w2u 2 ай бұрын
Programm yonse kunthera nkhani yofoira ngt imene ah or kuika nkhani zoti zitukule dziko ah
@WanangwaSokochikwete
@WanangwaSokochikwete 2 ай бұрын
Inu simunaphe chilima chifukwa champando wa president
@ayamichaponda1113
@ayamichaponda1113 2 ай бұрын
Chawezi tikudziwa zonse kuti ndiwe wa MCP, ndipo mmutumwako munazadza mwazi nde palibe ungatiuze .zaku DPP zisakukhudze iwe ndi mbuzi .zoti APM analengeza kuti wapuma pa ndale ,npomwe enawo ankaonesa chidwi sudziwa? Koma anthu atamupempha APM kuti awaphule pa moto wa MCP nde enawoso akanakaimila chifukwa chani? Munya muyankhatu milandu mukuopayo tikakuchotsani pampando
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy 2 ай бұрын
Chomwe achawez mmawaikira pama problem sindimachidziwa chifukwa amayankhula zofoira always
@PeterPhiri-di1ux
@PeterPhiri-di1ux 2 ай бұрын
achawezi bambo anu atakalamba ana siya kukusamalani ndinu achitsiru
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu 2 ай бұрын
Dzadziii,dzotsakoma
@stensapala9242
@stensapala9242 2 ай бұрын
ndiwa mcp
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 ай бұрын
I like this program chawez mulungu akusunge
@moniqb7373
@moniqb7373 2 ай бұрын
Ndiye mwati mudziyankhula kuti adapita, adaona, adali, tidaona, etc kuti mysanduke achewa kuti akukondeni? Heeede!😂
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 2 ай бұрын
Vote for MCP ❤️‍🔥❤️‍🔥❤️‍🔥❤️‍🔥 2030 woooooo!!
@LingaSaidi
@LingaSaidi 2 ай бұрын
Pansana pako ase
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 ай бұрын
Ndipo ndiwe opusaaaaa aise abale Ako sakuvutika iwe
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 ай бұрын
Sikupusa koma ngati ndizopangilana ngati opusa ndiweyo kaya
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 ай бұрын
Iweyo ulibe sana eti
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 ай бұрын
Ambuyakoo
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Kachilingamo kamabaya moti ena akutukwanani mmalo molakhula fundo mungodziwa kuti chalungamo kabaya
@NolityKondowe
@NolityKondowe 2 ай бұрын
Munthu ukakalamba you lose memory.Zinthu azichita kukumbutsa.Ndiye wina wozongulira mutu kumati Apm 2025 boma.Akagwere uko.Dyera basi.
@abeckbanda846
@abeckbanda846 2 ай бұрын
Chawezi ngati wadyetsedwa badzi dzidya ndinkadziwako osatiife chilima alikuti katitengele chilima timvotele osati chakwerayo ife tatopa naye 50kg maize K55000 galu iwe ndithu😮
@LisaKamanga-l3z
@LisaKamanga-l3z 2 ай бұрын
Tchende lako chawezi
@GreyMwanyimbo
@GreyMwanyimbo 2 ай бұрын
Chawezi amayankhula chilungamo
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 2 ай бұрын
Chawezi ukandiona utave. Ulibe nzeru ngati tate wako Kamuzu analysis kupha anthu nikuaponyera kung'ona. Choka apo mwana wam'fwiti. Palibe kanthu udziwa
@BillySaukani
@BillySaukani 2 ай бұрын
Bro chawezi banda sure supsatila umafotokonza ngamo akwiye akwiye.
@mercybiziweck
@mercybiziweck 2 ай бұрын
Ng'ona party
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 2 ай бұрын
Idont like this program
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Chakwera ndi wonama, ananama kuti achita resign after 2years
@Nilakay07
@Nilakay07 2 ай бұрын
Chawezi ndi dolo
@VeraVermaak
@VeraVermaak 2 ай бұрын
Mutharika ndi Ntaba amatafuna malibino sangawine misozi ya athu alibwino singalole
@mercybiziweck
@mercybiziweck 2 ай бұрын
Iwenso unkadya nao ma alubinowo ndie kt
@VeraVermaak
@VeraVermaak Ай бұрын
@@mercybiziweck pita ku court u will gate file of Ntaba and your APM not my Name
@JonhKapatjika
@JonhKapatjika 2 ай бұрын
Chawezi ndiwe business ya muthu wadya za malawi kogolise iwe waziwa kuti ddp gulu wamuthu
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o 2 ай бұрын
Chawezi samandiwaza
@stensapala9242
@stensapala9242 2 ай бұрын
this guy is very biased
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 2 ай бұрын
Nanga Chakwera wachichepele apanga chani kumalawi?komanso dziwani kuti ngati panalibe wodzutsa zanja ku MCP kuti apikisane ndi Chakwera pa undindo wapulesidenti ndichifukwa choti amawopa kuphedwa ngati chilima,ngati iyeyo Chakwera amalola anthu kupikisana nawo bwanji sanasunge lonjezo la pakati pa iye ndi Chilima kuti wina aliyense azalamulira 5yrs?,pamwamba posasunga lonjezo wamuphanso,ndiye muziti Chakwera wabwino amalola anthu kupikisana naye pa upulesidenti?.Sadiki Miya anali wachiwiri kwa Chakwera ndipo anangomwalira mwazidzidzi,Chilima anali wachiwili wa Chakwera naye wangomwalira mwadzidzizi,pano pali Manganya,muzandifunse ngati manganya atafike 2029 ali moyo
@CleverMagaleta
@CleverMagaleta 2 ай бұрын
Akupempha kuzakhala n'neneli ku state galu uyu
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Chawezi amanena zowoona zokhazokha
@nicksonjohnjumbe8382
@nicksonjohnjumbe8382 2 ай бұрын
APM akuladii alikuti achichepele at 85 next year is a shiiit
@HamidMasamba
@HamidMasamba 2 ай бұрын
Akulu inu mulibe nzeru, omwe ali ndizaka zochepezo akupanga chan? Ndiomwewotu aliyika dziko pa moto. Iwe nde ulibe nzeru wadya zambiri za mcp galu iwe
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Mutharika siwowopsa chakwera ndi satana wakupha
@henryhenry6632
@henryhenry6632 2 ай бұрын
Chawezi banda mwana wakwithu ❤
@JonhKapatjika
@JonhKapatjika 2 ай бұрын
Gati akupasa ndalama mcp igodya ndalamazo anthu akuvutika tikufuna iPhone mcp ndipo ddp ikalowa tizasiyila anyamata tingofuna kuchosa nyasi zilipozi
@LawrenceBelson
@LawrenceBelson 2 ай бұрын
Machende ako chawezi mbole yako peter kod anakulakwira chani
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi 2 ай бұрын
Chawezi umakondera Congress
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Alamulirabe mutharika ufune usafune
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
Chawezi ndiwe galu achinyamatawo akupanga chani kwawo ndi kupha ndi kuyendayenda ndi wumbava basi
@henryhenry6632
@henryhenry6632 2 ай бұрын
Iwe machende amako wava cadet mboli yamako refugee
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
@@henryhenry6632 iwe Mavi yako na yakwadada wako chimbuzi chaminokusi
@henryhenry6632
@henryhenry6632 2 ай бұрын
@@marryphili5419 panyin pamako kapolo, cadet machende ake peter munthalika nyelo zanu ma refugees
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
Pamusundu pako pavigawenga imwe munapha chilima ndiwe chikangawa
@henryhenry6632
@henryhenry6632 2 ай бұрын
@@marryphili5419 chilima inamupha ndi nyin yamako
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Ku mcp anthu sanafune kupikisana ndi chakwera kuopa kuphedwa chakwera ndi wakupha
@StoneckJali
@StoneckJali 2 ай бұрын
Komatu Pali fundo mwa a nyamatawa muzawavomereza ku mtsogolo
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Chawezi khala chete iwe suziwa kanthu
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Iweyo usavote uvotere chakwera wakoyo
@PiusChawinga
@PiusChawinga 2 ай бұрын
Chilungamo ichi
@laston-rj2qs
@laston-rj2qs 2 ай бұрын
Chawezi ndiwe galu
@KumbukaniChimbalanga
@KumbukaniChimbalanga 2 ай бұрын
Panyero pamanu
@kondwanivyalema9449
@kondwanivyalema9449 2 ай бұрын
Chisilu cholezera pa program chi Chawezi zopusa basi ndisiyaso kuvera bwande
@NyangwaKoma
@NyangwaKoma 2 ай бұрын
Chawez machende ako umalimbana ndi dpp bwaji panyelo pako
@ScrarNation
@ScrarNation 2 ай бұрын
Dziko silingasunthe bcoz of zaka za munthu Mutharika might be old but his ideas are fresh and needed for Malawi's progression
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 2 ай бұрын
True Malawi can become Singapore within a year lol
@SurprisedDarts-di6fs
@SurprisedDarts-di6fs 2 ай бұрын
CHAWEZ WAYAMBA JUJIYA YA PAINIYA
Fact-checking and trust in times of fake news
32:00
Eurostat
Рет қаралды 16 М.
Human vs Jet Engine
00:19
MrBeast
Рет қаралды 145 МЛН
Mom had to stand up for the whole family!❤️😍😁
00:39
KANDIMVELERE....KUFUKULA NKHANI  ZIKULUZIKULU .....TAMVANI NKHAN ZOMWEZAVUTA
30:49
Siyatha News | 06.00 AM | 26 - 10 - 2024
10:53
Siyatha News
Рет қаралды 3,1 М.
HOT CURRENT - 11 AUG 2017- NICHOLAS DAUSI ON PUBLIC SECTOR REFORMS
58:40
Times 360 Malawi
Рет қаралды 95 М.
ZURAH- AYOGEDDE LWAKI BULI MUSAJJA GWAYAGALA ASIRAANA | Unveild Experience
53:47
Dr Sam Kazibwe: Akalulu ka America kengedde! Obunkenke mu kooti e Kenya
1:03:01
SamKazibwe Dispatches
Рет қаралды 13 М.