Malawi in Shambles Oh !!! MALAWI wangaaaaaa 😭😭😭😭Mulungu wathu wamoyo tithandizeni Mdyerekedzi uyu ali pakati pathu akuzumza mtundu wa ana anu 😭😭😭😭 Lazarus ndiwe munthu wotani komaaaa. This is Worse Lazalo. God bless you Brother Mtanyiwa you are a truly freedom fighter,stay blessed and protected in God's Power ❤❤
@FunnyDimSum-hk1so2 ай бұрын
Ambuye yesu khristu chitirani chifundo dziko rathu chosan jaburoso ali pampandoyi akudzuza mizimu osarakwa
Vuto lilipo ndiloti wankulu wa police ndi wa nkulu wa army ali mbili ya chakwera ndiye pofunika apa kuthana ndi amenewa ndi chakwera pamenepo dziko rathu rizasitha
@SumanjeMankhwalaZulu2 ай бұрын
Yambani mademu osokonezeka Inu
@StewartGoma2 ай бұрын
What Mr Ntanyuwa is bringing on the social media is really helping all Malawian to wake up even the soldiers must also wake up Why the Government is doing this buying wipons while people are eating kalongonda wake up soldiers
@ManganiStanley2 ай бұрын
a Malawi ndife ogona tulo tiyeni tizidya chitedzechi basi ena anazolowera
@yusufbakali2 ай бұрын
Chakwela must park and go kukasiya
@MariamJaffali2 ай бұрын
❤❤❤❤ tihakane basi ndi mr chikangawa ❤❤❤❤❤❤comrade ntanyiwa mumakwana inuyo
Malemu chilima anati tisaope tisafooke tisatope chimandiwawa ndichakuti anakhulipilidwa nditundu wa Malawi ose sindili kumalawi koma azibale anga ali ku malawiko
@willardsimwaka73602 ай бұрын
I beg comrade please uziyakulako kwambiri muchizungu kutiso azungu aziva nawo
@MussaChilembwe2 ай бұрын
Allah alipo atichosera muthu ameneyu muthu oyipa kwambili ngati idya amin koma nayeso azafa ndiye asamatenge ngati kuti amalawi akusangalara
Ku malawi. Tilibe achitetezo ndie pot. Kulibe. achitetezo. Ifeyo. Monga. Nzika za malawi. Tatiyeni. Tiyambepo. Uyu. asafike. Pot anthu. a vote so. Tatiyeni. Uyu achoke. Nthawi. Ndiyomweyi. amalawi. Tiyeni. Timuchotse. Uyu
@yusufbakali2 ай бұрын
Chakwela is not past chakwela is criminal
@ChristinaMdeza2 ай бұрын
zikomo kwambiri a ntanyiwa tiyamik Ambuye potipas inuyo Mulungu yemwe yo aziyika chitetezo pa moyo. wanu, komtu chikangawa Ambuye akumuona ndithu, kodi afuna zilamulira ndani?
@HusseinMofatt2 ай бұрын
Zoonadi MCP ndi manyienieni tisaope achoke bas osadikilaso 2025
@rashidadan25332 ай бұрын
Chakwela wachotsedwatu mzelu , Anakayendela ng'ombe , mmalo moyendela anthu , And we know technology ,palibe kubela mavoti , not 60s or 70s , we're in high tech
@johnjoachim38202 ай бұрын
Koma asilikali mwati akuteteza dzikoli
@GeshoMwakitwileАй бұрын
Vuto iwe ntanyiwa uli mbali ya dpp ukanakhala kut ukuyumila a Malawi bwez timakusata koma uli pa kampeni ya dpp nde wauponda simubwerelanso boma inu alomwe kulibwino ndilamulilidwe ndi mtumbuka
@PatrickSomanje2 ай бұрын
Koma zovuta ziko lathu chakwela atipha
@MolosonMisitala2 ай бұрын
Tiyeni tipemphele kt dpp idzalowe m,boma ose apolice, army nose mudzachoka chifukwa sadziwa ntchito yawo chifukwa adatenga kl matenda a hiv😊
@JimmyMhone-b5p2 ай бұрын
Tsopano ndazindikira kuti anali mbusa wa ng'ombe zoona
@MandalaChaona2 ай бұрын
Shame on you Lazalo You are a Failure. President wosadziwa kanthu President wakhamza,wokupha watsankho. Aka Chikangawa boy 👹👹 your days are numbered man God will punish you 👹👹
@JoelCHIHANA-y6p2 ай бұрын
School fees,
@shenwaahabdulhakim2 ай бұрын
Amalawi pa chilichose amafuna mtsogoleri ku army ukoo tikufuna mtsogoleri kuti tithane ndi izi chifukwa dziko lino lilowa khondo
@HusseinMofatt2 ай бұрын
Ndi zoonadi amtanyiwa
@ManganiStanley2 ай бұрын
auzen zitsilu za ma soldier kulanda makala basi
@AnthonyPhiri-e3g2 ай бұрын
But sure malawi why🤔
@DeenesNurudMekeАй бұрын
AMALAWI Ndiomvesa chisoni kwambiri esh
@NuneAxmed2 ай бұрын
Mr ntanyiwa timakunyadilani mulungu azikudalisani
@peterlowole78412 ай бұрын
Asilikali athu alimutulo toopsya, MCP idali nadi payoniya ndikomwe kamuzu amapereka zida za mphamvu ,osati Malawi army, ndizomwe zidabwelesa opaleshoni bwezani.pano akutumiza anthu ena ku maiko ena, ati aphuzire upolisi 😊 ndiboza amenowo ndi ma MCP leboz . Trust me
@VeronicaMatiki2 ай бұрын
Comrade Ntanyiwa kulinso Nyumba ya Mk15000 ku Malawi, ingakhale NYumba ya bwanji imeneyo
@jameskachulu81412 ай бұрын
Malawi amavutiza munthu wabwino Peter amavutiza akukhuta pano akumuopa wakuphayu
@KondaniPhiri2 ай бұрын
Tatiyeni a. malawi. Tidzike. Ma vote asanafi ineyo. Ndikufuna anthu. Mundipange. Sapot. Tiyambepo. asafike. Ameneyu. 2025
@chifundobuledi2 ай бұрын
A Ntanyiwa bweranitu mudzayambitse ma demo anyoo ngati aku kenya aja ifetu mtima ukutiwawa ndi zomwe akuchita chakwerayi
@LumbaniNeba-d9n2 ай бұрын
Malawi army basi muli pheeee!! Mukugona kwambili
@SophieLupiyaАй бұрын
Mumakwana
@UseniMailosi2 ай бұрын
R 1550 koma kumalawi
@GeshoMwakitwileАй бұрын
Tilipo ambiri omuvotera chakwera osat zilomwe innu
@Homeofpeace3212 ай бұрын
I remember chilima amapeleka salary yake to help covid, may his soul rest in peace but I know chakwela Adakakhala Kuti wafa ndimwana wako chinchija padakamangidwa anthu
@HarrisManda2 ай бұрын
Dead walking..
@wisdomchilanga7232 ай бұрын
The leader who is leading Malawi is not chakwera .shameful Malawi
@AlgentChilangaАй бұрын
Koma ntanyiwa mnthuyu akuyesesa kuti ziko lathu lipulumusike koma eee akulu akulu ankungomuvera chabe basi
@GeshoMwakitwileАй бұрын
Nde anakuuza kut wazimangilila kamba ka mavuto achuma anali ndi zifukwa Zina ,chitsiru iwe ntanyiwa
@BoscoKalua2 ай бұрын
Too bad indeed
@SumanjeMankhwalaZulu2 ай бұрын
Pusitsani ana osat ozindikira,usatitayitse nthawi sunakhalepo mtsogoleri,iweyo ngat sizikuyenda usalankhule mmalo mwa amalawi khala pansi