Ovota kumudzi alibe driving license tiyen chabe pa ground ana mwachepa
@RobertPhiri-gt2cr36 минут бұрын
Mr phiri muumatha kulankhula
@ChifundoThomas2 сағат бұрын
Chokani inu mukunaniza ndani mbava ngati inu ?
@jomochirwaСағат бұрын
Boma limapanatu ,lakupananitu kkkk
@isaihmagani56974 сағат бұрын
Ben Phiri kulankhura ndi katakwe palibeso ku DPP uko mpaka ku MCP konse akuchepera Ben Phiri ndi a katundu field Marshall ndavomereza
@elsontmsukwa43566 минут бұрын
Why my fellow malawian 😢
@PeterRabson-z3wСағат бұрын
Pakupaku iwedi ukuwaona mmanja mwako phiri
@JamesDzonzi-t7u3 сағат бұрын
Atha ma plan awa
@inessmsiyambiri8517Сағат бұрын
Iweyo
@NtchindiChirwa-l8oСағат бұрын
Munayamba kuba ndinuyo ndiye mwaona mmene zimawawira kkkkkk simunat mpaka 2030 wooooooo
@JonesChingaya-yf4ggСағат бұрын
Visit again your opinion, Ben phiri ndi azinzake sangavutike kwenikweni koma amphawi akumudzi, so 2030 ukunenayo ovutika so Ben phiri.
@AyandaPhungula-bg9ql19 минут бұрын
Chakwera wayipha Malawi eish
@jomochirwaСағат бұрын
Kulibe dziko limene mzika yopanda l.d imakavota ,ngakhale wopanda l.d passport sipangidwa,ku bank account singatsekule.mayesa ma l.d kudalibe nthawi ya kale koma mudayambitsa ndinu a dpp ndiye lelo zakupsindaniso kkkk
@user-ux3ed3ni1p3 сағат бұрын
Ndie mutant, why is MCP holding the country hostage?
@ChristmasChapeta4 сағат бұрын
Readership is very poor
@dalitson3558Сағат бұрын
Ben phiri ndi Dolo kwambiri
@AliceChapita4 сағат бұрын
Dpp my vote
@SelinaGamaliyere-q8v33 минут бұрын
Chakwera ndi chipani chake alephera ndalama zathu angoba
@MacleanChatsika4 сағат бұрын
Mwamukonda lero adpp poti adamwalila
@LinoVilimunthumbo-y1o4 сағат бұрын
Kupakula
@PatrickChikhawo31 минут бұрын
😂😅😅😅Change gool mwalilanayo inu a dpp munativentsa kuwawa khalani ku option konko sitikufunani mu boma mwayiwala kuti munkayankula PA chinkuza mawu kuti munaba?
@chimwemwelungu193427 минут бұрын
Ukasiidwa umalankhula zambiri. Politics is a dirty game. Lero mukufuna kukhala madolo yet munthawi yanu mumapha, uhule and kusakaza chuma. Vomerezan ur on the losing side. Achisale, cash madam n all money heist musaone ngat anthu anaiwala. U dont want to help Malawi but continue pomwe munalekezera kuba. U hated Chilima thats why he left. Dont act like u care whilst his death is a relief to u. Truth z palibe chipan chomwe chingathandize a Malawi kuposera kuyambapo kudziimira pawekha n working hard.
@JacquereenPereira4 сағат бұрын
Athu akudya chitedze Ambuye ati thandize chikangawa Eish