COMRADE NTANYIWA - SATURDAY MR PRESIDENT AKUKASEWERA MASEWERO A GOLF

  Рет қаралды 7,835

Mpungwe-Pungwe mw

Mpungwe-Pungwe mw

Күн бұрын

Пікірлер: 29
@HamzahMiles
@HamzahMiles 15 минут бұрын
Pali anthu ena amene simumusata munthu yi, please ma post ake sananene kuti president wafa koma anati Ali ku chipatala cha Garden city hospital basi
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 20 минут бұрын
Kunkuyu wachamba, panopa maiko usi akukozekela kunka ku state house, mkadakonda manganya akadantulitsa pasi udindo chimwendo kkkķkkk mimba njuu kulibe kusintha atsogoleleri kwa manu konko
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer 3 сағат бұрын
Mwat born kalindo akamamusak saoneka km ndasekatu 😂😂😂😂 man of God glory to God born kalindo pangolin my brother
@AmickKammalele
@AmickKammalele 34 минут бұрын
Golf akamenyela kuti muthu wamwalira kkkk tiyeni only 2days
@GideonKodimba
@GideonKodimba 4 сағат бұрын
Kkkkk wabodza iwe umati chani uli ndi pakamwa
@EnriqueLemitton
@EnriqueLemitton 9 минут бұрын
Iwe ndi galu kwabasi..izi sizoona lumikiza a Malawi kuti tigwirizane
@FreserAaron
@FreserAaron 16 минут бұрын
👍
@BrightLuciano
@BrightLuciano Сағат бұрын
Ntanyiwa sananenepo kuti president wamwalila apo pokha musanamizle
@babranzima8120
@babranzima8120 3 сағат бұрын
Chipita ndi chitembo ??
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 4 сағат бұрын
Tidzaona mawalo kuti chakwera akusewera nawo masewero agolf
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 4 сағат бұрын
Ntanyiwa umangidwatu iwe ndi bodza lako misleading Malawian ndi za bodza,ngati ulibe zolankhura kumakharako chete pena,ngati momwe amachitirako a Bon Kalindo amazakharako chete pene osati kubwetuka
@rodrickwiskes
@rodrickwiskes 48 минут бұрын
Pajatu boma ili silimanena chilungamo
@GrecianWyson
@GrecianWyson 4 сағат бұрын
Esh osamafaritsi khani ya ifa Koma arimoyo esh zopusa bwanji
@AnyuxyJulias
@AnyuxyJulias 3 сағат бұрын
Aaa gofo sasewela nkono umoz
@IsaiasIsaias-yq7zg
@IsaiasIsaias-yq7zg Сағат бұрын
Koma achakwelawo iwowo pamene akhala amangukhala ndidziwembubwanji osamasangalatsa amnthuawo akasakebonikalindo chifukwachiani bonikalindo safuna zopusa komaso iwowo adakamatopa ndikuganizakuti mdzikomuno amnthu adwachitedze ndipange bwanjikuti ndapulumutse kodi mesapaja adali abusapaja lelo mudziti mmatenda aaa kkkk kaya
@Desmond-q7r
@Desmond-q7r 4 сағат бұрын
Antanyiwaso u misleading ppo nanuso mumati watisiya now u changing
@YusufJimmy-v1o
@YusufJimmy-v1o 4 сағат бұрын
Ntanyiwa sananene kuti wamwalila...Tikumutsata bhobho...osamunamizila
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 4 сағат бұрын
Ntanyiwa sadaneneko kuti Chakwera wamwalira mukatelonso amene mukutelonu mukunama, ndatsatira bwino MA vn ake onse kuyambira dzuro atasowa kwa kanthawi koma zomwe ine ndinamva ndi zoti Ali ku chipatala cha Garden city ku south Africa, komanso musayiwale, 2018-2019-2020 mu nthawi ya Peter muthalika ambiri amakambanso nkhani ngati zomwezi president akasowa,nde monga ine sindikuwona cha chilendo choti mpaka Ena azimangidwa nazo, anthu akufuna Baba wa dziko atiwuze kuti wayenda bwanji ku UNGA koma kuli ziiiiiiiiii😢😢😢😢
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 4 сағат бұрын
Mwayankhula zoona
@MoosaTrouble-o7p
@MoosaTrouble-o7p 3 сағат бұрын
Ine ndamunatu chakwerayo akumwa magagada
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 3 сағат бұрын
@@MoosaTrouble-o7p broh wationjeza abusatu aja
@MagretDaniel-m8c
@MagretDaniel-m8c Сағат бұрын
Musamunamizire ntanyiwa munthu wamulungu uyu
@BrightMbewe-fz5zf
@BrightMbewe-fz5zf 5 сағат бұрын
Aaaaa mwachedwa nayo,
@LonexWataya
@LonexWataya 2 сағат бұрын
Che macdonald kachala ndi iwe wa mcp eti
@MaxwellMalisawo
@MaxwellMalisawo Сағат бұрын
Mumaitha a mtanyiwa
@MemoryMankhwazi
@MemoryMankhwazi 2 сағат бұрын
Ntanyiwa mabodza usiye
@TamalaKambanje
@TamalaKambanje 3 сағат бұрын
Munthu wakulu nthanyiwa
@MacDonaldkachala-cm5gc
@MacDonaldkachala-cm5gc 2 сағат бұрын
If you don't have news, you don't have it's not a crime, if you keep broadcasting false news, you will lose followers, that's my advice
India Bids Farewell to Ratan Tata | Vantage with Palki Sharma
10:12
SHAPALAQ 6 серия / 3 часть #aminkavitaminka #aminak #aminokka #расулшоу
00:59
Аминка Витаминка
Рет қаралды 2,8 МЛН
My Daughter's Dumplings Are Filled With Coins #funny #cute #comedy
00:18
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 23 МЛН
Incredible: Teacher builds airplane to teach kids behavior! #shorts
00:32
Fabiosa Stories
Рет қаралды 12 МЛН
Policewoman arrested for allegedly killing six people to claim payouts
8:57
OYENDA NDI LUPANGA/CHOIPA CHITSATA MWINI - NZWANYA CHARLEY PATACHE
6:16
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 4,9 М.
Alleged 'fugitive' kidnaper tells journalists he has not fled SA
12:40
Newzroom Afrika
Рет қаралды 4,5 М.
SANKANDILORA KUTULUKA PANJA - KANGAUDE PART2 WITH GOD KNOWS
55:02
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 13 М.
ABWANA PAULENDO - BLESSINGS CHIMANGENI
5:20
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 32 М.
SHAPALAQ 6 серия / 3 часть #aminkavitaminka #aminak #aminokka #расулшоу
00:59
Аминка Витаминка
Рет қаралды 2,8 МЛН