DZIPANI DZOTSUTSA ZALEMBELA KALATA MEC NDI NRB KUTI ATULE ADINDO ATULE PANSI UDINDO KUMENEKO

  Рет қаралды 21,111

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 109
@marryphili5419
@marryphili5419 5 күн бұрын
💪💪💪💪 Ambuye timenyereni khondo sitikufuna zimene zikuchitika ku Mozambique achakwera akufuna kuzabera mavoti tatopa ndikuzuzika ndi MCP
@ThokozaniBondo-em9fr
@ThokozaniBondo-em9fr Күн бұрын
Keep it up guys ❤❤❤❤
@DoreenMaida
@DoreenMaida 5 күн бұрын
Nice to hear that keep it up please
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 5 күн бұрын
Only one tree can not make a forest , keep it up oppositions join ing together osaopa Dziko ndi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@SymonChimwaza
@SymonChimwaza 5 күн бұрын
Bravo the Opposition Parties, keep it up
@OwenMindozo
@OwenMindozo 2 күн бұрын
Please, Mabwana, The Lord sees what happens every where, he is watching us, whether we do good or evil. Pastors let's pray a soaking prayer, Our God is hearing our cry, He answered the children of Israel in their trouble and hard ship, He will answer us the poor and needy people in Malawi.
@IdahKadewere
@IdahKadewere 5 күн бұрын
Zake zamudela chakwera😅😅😅😅😅
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 5 күн бұрын
Good ❤
@bandaBanda-d5v
@bandaBanda-d5v 5 күн бұрын
Good opposition
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 5 күн бұрын
I like this, now opposition parties are with malawians 🔥🔥🔥💪💪💪 go deeper , go harder osaopa osafooka osagonja uyu akutengela nyengo za kamuzu koma waiwala kuti ino ndi nthawi ya democracy 🔥🔥🔥 opposition parties
@LimzeySande-b9n
@LimzeySande-b9n 4 күн бұрын
Atule pansi udindo bas chirungamo ichi
@amoskamwela5514
@amoskamwela5514 5 күн бұрын
Good coming Bravo opposition parties 🏃🏃🏃🏃🏃😂😂😂
@KhirChisale
@KhirChisale 5 күн бұрын
Good atuliletu pansi zisankho zisanafike
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc 4 күн бұрын
Anthu awawo a MCP akadzangowina dziko muno simudzakhara mutendele
@AnyelwisyeSikwese
@AnyelwisyeSikwese 4 күн бұрын
Kuzavuta mcp ayiwara kut analowa mmu boma chifukwa cha mademo
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 2 күн бұрын
Ndipo ineo ndidzakhala mmodzi oyambitsa nawo dziwawazo chifukwa ndikudziwa kuti mcp yafa kale nde wina adzandiuze kuti cikangawa wawina iii akulu sidzagwila antaah olo pang'ono tidzaphanamo muno
@omarejussa8703
@omarejussa8703 4 күн бұрын
Dziko lino ndi la Mulungu Choncho munthu alibe mphavu pa munthu aliyetse kupatula Mulungu mwini adamulenga Iye ndi amene ali ndi mphavu. Mulungu wabwino nthawi zonse satisiya tikuvutika ndi Boma la samunda
@StanleyChamasowa
@StanleyChamasowa 2 күн бұрын
Iwe beach anabele please tisiye ife malawi timakonda ntendele
@ChikondiNkhata-g5x
@ChikondiNkhata-g5x 4 күн бұрын
Am agreed with this point
@Pangolinimw
@Pangolinimw 4 күн бұрын
❤❤🎉🎉🎉🎉 yes athu awa achoke
@khaleedsaidi6232
@khaleedsaidi6232 4 күн бұрын
Koma inuyo ndi wakulu ❤❤
@kazembemaulana1gmail554
@kazembemaulana1gmail554 5 күн бұрын
Nice congratulations opposition takunyadiran tikurepela kubwelera kumuzi kamba ka chikangawa party
@Giftsungani
@Giftsungani 5 күн бұрын
Nkhaniyi ndiyoona anthu amenewa akuyenera kutula pansi udindo.
@JudithSadi
@JudithSadi 5 күн бұрын
Well done
@ImannchisomoHakhimu
@ImannchisomoHakhimu Күн бұрын
Nkhan ndiyomweyo mai awa achoke abwelele komwe anali ntima kuipa ngat bambo ake atembo
@MarkMasangwa
@MarkMasangwa 5 күн бұрын
Mayi ameneyi sandiwaza or pang'ono
@WishesBanda-v9p
@WishesBanda-v9p 5 күн бұрын
I think a opposition ayambapo kuonetsa kuti ali mbali yotsutsa tsopano
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Күн бұрын
Koma zinazi zingosoyeza kubalalika kwa opposition nthawi ikupita mukalembera MEC olemba ntchito ali pheee ku ma stand za ziiiiiiii, pitani pa ground ndi fundo.
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga 5 күн бұрын
Smartmatic ife aii sitikufuna dziko muno zizachitike za ku Mozambique
@OsmanAssimaUsi
@OsmanAssimaUsi 4 күн бұрын
Chofunika Boma lizimvela anthu ochuluka oachifukwa ichi.anawina chifukwa anthu ochuluka analankhula kt tikufuna MCP.leloso anthu ochuluka akuti no anabelo.no smartmatic bomaso limve zosezo zichoke.
@LameckNgwangwa-g3p
@LameckNgwangwa-g3p 4 күн бұрын
It's true and live
@NdaonaMsowoya
@NdaonaMsowoya 5 күн бұрын
Ndipo mulungu wayankha simatimak yafoila akataye kkkkkkk
@catherinekadwala3839
@catherinekadwala3839 4 күн бұрын
Ndipo ndiye zakhala bwino, Achithuphya party zawaonekera
@OsmanSangala-r1r
@OsmanSangala-r1r 5 күн бұрын
Kupewa zoipa MEC kapena president avomeleze zomwe otsutsa akumana. Pali zifukwa zomwe maiko anavomeleza kuti padzikhalaso otsutsa boma
@MrArif-tc2cu
@MrArif-tc2cu 5 күн бұрын
Smartmatic azikawerengera omwe alowa nyau kudambwe not Election for our country, usandichimwise Lazalo
@AlickMDayi
@AlickMDayi 5 күн бұрын
😂😂You can said that again my brother 💪🏼🇲🇼
@NgomaRaheem-k2t
@NgomaRaheem-k2t 5 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 5 күн бұрын
Watichimwisa kale garu uyu koma akawerengere kwabambo ake
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 5 күн бұрын
Smartmatic.......yafoila uku....anthu ...Afa ndi Bp ku State house😂😂😂😂😂😂
@AlickMDayi
@AlickMDayi 5 күн бұрын
@bridgetmajor3646 💪🏼💪🏼💪🏼🇲🇼 Makape amenewa amawona ngati Amalawi alero ndi osawelenga eti 😂😂😂😂 angwanayo yomweyo yowelengera pa MANUAL yo 💪🏼💪🏼💪🏼
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 4 күн бұрын
Vuto zipani zosutsa mukumagona kwambili plz amalawi akudalila inu kodi pomwe pafika malawi lelopa atati watengatso dziko kachikena mukuganiza kuti amalawi azakhala bwanji
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 4 күн бұрын
Ameneyi asayendetse ma vote.olo,azakumbukila kupita kwao,ku Lesotho.koma,ngati akufuna machete,tili okhozeka kutelo,atule pasi.ndipo,wakulu wa army,azayetsele,kutulutsa anyamata,tikakumana,koko.this,is our nation.
@EmanuelGambuleni
@EmanuelGambuleni 5 күн бұрын
Ndipo a choke 😂🎉🎉🎉🎉
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika Күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@cwsteve8233
@cwsteve8233 5 күн бұрын
Atule pansi komaso smartimac sitikuifuna.
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 5 күн бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose aliyese wokhudxiwa ndi ifa ya chilima awona pomuyika
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 5 күн бұрын
Nkhani yabwino atulepasi udindo satana anabelu
@BenjaminKapale-k1f
@BenjaminKapale-k1f 5 күн бұрын
amayi awa anthu adzawapakula nyembatu akapanda kusamala
@JeniferKananji
@JeniferKananji 3 күн бұрын
Chichokedi chimay chimenechi tikufuna one by one
@KennedyChikapa-v1p
@KennedyChikapa-v1p 4 күн бұрын
😮Akukakamila chifukwa chani machine kuti achoke I inali plan yao ndikale yofuna kubera
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 5 күн бұрын
Anabel mtalimanja ife a Malawi tikuti smartmatic machine sitikuyifuna ok
@IbrahimIsmael-h2w
@IbrahimIsmael-h2w 4 күн бұрын
Akuluakulu amaiwa achoke aononga kale zinthu😂😂😂😂
@AliyuhUsumanah
@AliyuhUsumanah 4 күн бұрын
Sitikumufuna ntalimanja ife
@DanielNangoma
@DanielNangoma 4 күн бұрын
Simartmatic stiyifuna komanso anabelo ndi mwamuna wake wa RNB achoke atsatiwonongele chisankho, tikufuna manual igwire ntchito mamuna awoneke
@BennettNjedza
@BennettNjedza 5 күн бұрын
Achoke amenewa
@HarrisonBiscuit-c8l
@HarrisonBiscuit-c8l 4 күн бұрын
Izi ndizoonadi or ndilingati ine bambo anga anali chipani chomwe chinkalamura pano chikulamulaso sindingalore kt chiluze , koma dzikoli ndila democracy kungovomeleza bc palibe chokakamira athu ngati sakutifuna .
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 19 сағат бұрын
chikalatacho,sichiphula,kanthu,mukadakhala,mumatsat,malamulo,akadakhala,atachoka,kalekale,chifukwa,lidamuika,,ndilamulo,
@MasterMwela
@MasterMwela 4 күн бұрын
Smartimatic sitikuyifuna ndiponso Anabel Mtalimanja atule pansi udindo mwaulemu wawo
@ChifundoBeston
@ChifundoBeston 4 күн бұрын
Aaaa zipani zotsitsa boma zikuopa chisankho chifukwa chani?
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx 5 күн бұрын
Smartmatic yawo IJA yaonongeka maina omwe amafuna kubela afufutikamo mitu yawo siikugwira ntchito
@EDWARDBANDA-x1t
@EDWARDBANDA-x1t Күн бұрын
Smartmatic ayi ku malawi ti ma user manual zoputsa ayi komatso Process ya registration ayambiretso Pali zotsamwitsa zambiri we don't need chikangawa government
@HawaHussein-o5k
@HawaHussein-o5k 4 күн бұрын
Zichodi palibe akuzifuna zabweletsa mavuto ku mozambique ifeyo takanitsitsa za kuba kuno ayi atisiye tiponnye vote mwa mtendele ndi zotsatila zake
@EliaSiska-n6r
@EliaSiska-n6r 5 күн бұрын
No need to use Smart Matic during; votes. Bravo oppoxxtied,
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 күн бұрын
Good atuledi pansi
@edsonndalama2334
@edsonndalama2334 2 күн бұрын
Mzimayi uyu otchedwa Annabel yu sakuyenera kutsogolera zisankho mdziko muno chifukwa kupyolera mu zochita zake zaonekeratu kuti Ali partisan ndipo ngosamva. Uyu azatibweresera mavuto uyu mdziko muno. Paja akukananso kuti onse amene analephera kulembetsa mu phase 1 koma ziphaso anali nazo kuti pano asalembesenso. Uku ndi kuphwanya ufulu wa nzika osankha atsogoleri a ku mtima kwawo. Uyu azipita uyu, ntchito ndi zambiri mu boma mu, mupaseni china chochita.
@ChifundoBeston
@ChifundoBeston 4 күн бұрын
Apite ku court akafotoze bwino zifukwa zake. Akunenazi ndizosamveka, munthu amachotsedwa pa udindo akalakwitsa. Jean ansah tinamudandaula atabera chisankho izo zinali zomveka ndipo dziko lonse linachitila umboni kuti achoke. Auzane sakutula pansi udindo
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly Күн бұрын
Atule asatule kom gule kwawo mapilikano ngati ......
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 19 сағат бұрын
otsotsa,amakanika,kutsegula,pakamwa,pagulu,chifukwa,chamanyazi,
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 5 күн бұрын
Panyini pake Mai opanda zokoka pantumbo pake bambo Ake a John Tembo mboleyao
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 5 күн бұрын
Iiiiiiiiiii😂
@ChrisKapila
@ChrisKapila 2 күн бұрын
1:03 Kkkkkkkkkkkkkkkk
@OfesiMakuwalo
@OfesiMakuwalo 4 күн бұрын
Komano asafokeyi apitilize kutelo chifkwa pali anthu tufooka chifkwa cha machine awo sitikuwafuna
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 5 күн бұрын
Ndpo Mulungu mwini ulamuliro kumwamba ndi pansi atichosere satana amene watizungulirayu ndpo asogolere azipani zosusa Mulungu ikani mtendre zipani zosusa akhale anthu ogwirizana Ambuye imvan kulira kwa akapolo anufe
@BobJoshua-q5n
@BobJoshua-q5n 4 күн бұрын
Achoke makani akukakamira bwanji? Makani osathandiza
@DaudBonomali
@DaudBonomali 5 күн бұрын
maganizo anga ndi akuti akachilola chimachini chimenechi kuti chingwire ntchito pa chisankho musakayike kiyamahyo ndiye yachilhalile i zabwera ndipo kiyamah yaketu eeee kaya
@HendresonNambazo-u4i
@HendresonNambazo-u4i 5 күн бұрын
Mwayitha pamenepa atule basi
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 19 сағат бұрын
zoti,mungamuchose,ntalimanja,popanda,malamulo,mukunama,anaikidwa,ndilamulo,achokeso,ndilamulo,musapusitse,bomalamulo,ndilomwe,lingachotse,zomwe,inuyo,mukufuna,musakakamize,boma,,,,,,,,,,tsatanimalamulo,,
@IsmailAhmed-i4l
@IsmailAhmed-i4l 5 күн бұрын
my name is ismail Ahmad koma mwina kuti zimveke kwa ifeyo tonse amalawi ndilankhule muchichewa ndiyambe ndikuti ndikupempha azipani zotsutsa nonse mudziko lathu chonde chonde tagwilizanani tagwilanani manja nonse muitem
@IsmailAhmed-i4l
@IsmailAhmed-i4l 5 күн бұрын
muitenge nkhani iyiyi very serious chonde ineyo ndikugwilizanananu kuti anabelo ntalimanja ndizoona osakayikaso ndimwanadi wa malemu jz tembo ameneyu adamubweletsa dala achakwara chifukwa adadziwakuti sangadzawine chisankho koposela amutenge ameneyu kuti azawabeleke kunsana winanso ndi uyuyu sambo ndi original mcp member chonde chonde azitsogoleli otsutsa musabwelele mmbuyo awawa anabelo ntalimanja asambo achoke chifukwa mukapanda kuwachotsa anthu awawa mutiphetsa ifeyo anthu osaukafe .
@IsmailAhmed-i4l
@IsmailAhmed-i4l 5 күн бұрын
ndikuuzeni izizi zikuchitikazi zikadakhalakuti ndiinuyo otsutsa amene mukulamulila panopa mcp mkukhala ili opposition bwezi anabelo ntalimanja asambo atachoka kale koma zikutenga nthawi yaitali chifukwa inuyo a opposition akukuonani kuphusa chifukwa u don't take action very serious mchifukwa chake anabelo ntalimanja akadali mpakana pano
@IsmailAhmed-i4l
@IsmailAhmed-i4l 5 күн бұрын
ineyo ndili okhutila kuti mukayitenga serious nkhani iyiyi ndiye kuti anabelo ntalimanja asambo achoka
@IsmailAhmed-i4l
@IsmailAhmed-i4l 5 күн бұрын
ndikubwelezanso kena kachiwili kuti chonde musalole ngakhale pang.ono kuti anthu awawa awiliwa apitilize kutiona kuphusa ngati mmene akutipangila nthawi yonseyi chonde please
@MosesTangwe-q8o
@MosesTangwe-q8o 3 күн бұрын
Stikufuna smatmatic tiwelenge manual
@MarthaGama-q1o
@MarthaGama-q1o 5 күн бұрын
Ndipo zimene zalembedwa mu chikalatazo ine monga mmalawi ndikugwilizana nazo , Annabel atule pansi komanso smartmatic sitikuyifuna , kodi akukakamila chinthu chakuti aMalawi tikuchikana chifukwa chiyani?
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 5 күн бұрын
Malawians are not robots.Therefore,it sounds naive and bizarre to transform Malawian democratic manual dexterity to smartmatic robotocracy.
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 5 күн бұрын
Maganizo ndiomweo anabelo achike sambo achoke smartmatc ayiso
@NgomaRaheem-k2t
@NgomaRaheem-k2t 5 күн бұрын
Manuel azagwira ntchito bas
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 5 күн бұрын
Ambuye tithandizen tachepa
@InnocentMkhoma
@InnocentMkhoma 5 күн бұрын
No smartmatic and Mec chair/Nrb chair should with immediate effect stepdown. No copmrise
@UncleShopRite
@UncleShopRite 5 күн бұрын
Smart matic yakeyo Ife ayi MCP yatikwana ife
@ChrissyBenito
@ChrissyBenito 5 күн бұрын
Atule pasi udindo kodi zikuta pati
@DeavncKapesi
@DeavncKapesi 5 күн бұрын
Akutitu 👊🤓🔥💯
@MaulanaIriyasa
@MaulanaIriyasa 5 күн бұрын
Ndipo anyamuleso smartmaticyo a pite nayo
@MwinkhulanaLulu
@MwinkhulanaLulu 5 күн бұрын
Atuledi pansi udindo
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 5 күн бұрын
Musabwelere mumbuyo achoke basi
@FarookStambuli
@FarookStambuli 5 күн бұрын
Eya achoke kmso smartmatic wawoyo achokenso
@ChristopherChilambe-g4z
@ChristopherChilambe-g4z 4 күн бұрын
Good move most people are supporting the idea ,malawi dzuka malawi dzuka
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 күн бұрын
Osainvayi guys osalora munthu mmodzi asazationongereyi ufulu wathu
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 5 күн бұрын
Achoked
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 19 сағат бұрын
usanamize,anthu,,dpp,ikukakamiza,boma,kuononga,ngwilizano,mobisa,iweyo,ukulankhulawe,sukudziwa,kt,pamene,amakagula,mashin,a,MEC,,,chipani,chilichose,chidasaina,kt,anabe,agwile,ntchito,ya,MEC,komaso,zipani,zose,zidasaina,kt,mashinio,ndiololedwa,ife,tikuti,musakakamize,,anabelo,ntalimanja,kuchoka,paudindo,ingotsatani,komwe,munakasaina,kuja,kt,malamuloagwile,ntchito,popanda,kutsata,malamulo,simukwanitsa,kumuchotsa,tsatani,malamulo,adziko,osakakamiza,kt,wina,,adzawoneke,uchisilu,mawa,chifukwa,choononga,malamulo,adzoko
@EdwardMagaleta
@EdwardMagaleta 5 күн бұрын
Kkkkk
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 19 сағат бұрын
mukamakamba,zakumozambiki,mulakwa,zankhondo,,kuno,kumalawi,palibe,akuopa,ndipo,anthi,aliokozeka,kukwapulana
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 4 күн бұрын
Chisankho chikhale cha manual not smartmatic
@MichaelpenielPhiri
@MichaelpenielPhiri 5 күн бұрын
Koma abale
@BrightonChidzalo
@BrightonChidzalo 5 күн бұрын
Ndipo Achoke asakakamile sitikumufuna
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w 4 күн бұрын
Atule.chire.mai.oo
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 4 күн бұрын
Chisankho chikhale cha manual not smartmatic
A KALUWA NAWOSO AFIKILA KUING'ALULA __11 January 2025
54:46
A NAMIWA KUYANKHA MAFUSO ATOLANKHANI 🙌😱
21:23
HOT 265
Рет қаралды 29 М.
“Don’t stop the chances.”
00:44
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 62 МЛН
小丑女COCO的审判。#天使 #小丑 #超人不会飞
00:53
超人不会飞
Рет қаралды 16 МЛН
My scorpion was taken away from me 😢
00:55
TyphoonFast 5
Рет қаралды 2,7 МЛН
ZOMWE WALANKHULA PRESIDENT LAZAROUS CHAKWERA KU CHILEMBWE DAY LERO
17:17
Joseph Nkasa - Atcheya Tiwayamikile Ali Moyo
4:06
Zake Muluzi
Рет қаралды 37 М.
“Don’t stop the chances.”
00:44
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 62 МЛН